- 783
- 9 401 308
Malawian Cameras
South Africa
เข้าร่วมเมื่อ 10 มิ.ย. 2018
You're welcome to MalawianCameras
TH-cam Channel Here we do these things
Reactions
News updates and commentary
Fun videos
Vlogging
So feel free to interact with with us
We need your wisdom and support
Let's build the world together with love and respect and peace
Our Contact details:
+27 63 831 2691
WhatsApp us:
Zifukwa zomwe awamangira Makosana aja Achina Sameer Suleiman
Zifukwa zomwe awamangira Makosana aja Achina Sameer Suleiman
มุมมอง: 405
วีดีโอ
Sameer Suleiman ndi Ena Anayi tukunena pano amangidwa nkhani yose ili mkatimu
มุมมอง 10K4 ชั่วโมงที่ผ่านมา
Sameer Suleiman ndi Ena Anayi tukunena pano amangidwa nkhani yose ili mkatimu
Press Briefing Ya CDEDI Sylvester Namiwa wabwera moopsya lero ndipo kuli ku player ma Audio
มุมมอง 3K4 ชั่วโมงที่ผ่านมา
Press Briefing Ya CDEDI Sylvester Namiwa wabwera moopsya lero ndipo kuli ku player ma Audio
Onse akusapota Mcp azungulira mutu Ambuye muchotseni Chimwendo ku MCP sakudziwa zomwe akuchita.
มุมมอง 2.3K8 ชั่วโมงที่ผ่านมา
Onse akusapota Mcp azungulira mutu Ambuye muchotseni Chimwendo ku MCP sakudziwa zomwe akuchita.
Born Kalindo Watulukira koma Born Kalindo ndiwamwano penapake 😂😂😂
มุมมอง 1.6K10 ชั่วโมงที่ผ่านมา
Born Kalindo Watulukira koma Born Kalindo ndiwamwano penapake 😂😂😂
Cabinet ija aizukuta uku Hot Current Yang'alura Eeeew
มุมมอง 94320 ชั่วโมงที่ผ่านมา
Cabinet ija aizukuta uku Hot Current Yang'alura Eeeew
Ife tinayamba kudzudzula Mcp ndi a Chakwera Saulos alimoyo kuti akumuzunza. Samuel Lwara.
มุมมอง 2.6K21 ชั่วโมงที่ผ่านมา
Ife tinayamba kudzudzula Mcp ndi a Chakwera Saulos alimoyo kuti akumuzunza. Samuel Lwara.
Game Changer Naye Kuseliku Sumungamuphe Apm 😳😳
มุมมอง 1.4K22 ชั่วโมงที่ผ่านมา
Game Changer Naye Kuseliku Sumungamuphe Apm 😳😳
Manganya Wa sambwaza nose amene mukujama ya iye pomwe akugawa zinthu
มุมมอง 4.3K2 ชั่วโมงที่ผ่านมา
Manganya Wa sambwaza nose amene mukujama ya iye pomwe akugawa zinthu
Manyanga wati Chakwera ndi Faraoh ndipo pomaliza anampasa mphatso ku Tchalitchi ko
มุมมอง 4.8K2 ชั่วโมงที่ผ่านมา
Manyanga wati Chakwera ndi Faraoh ndipo pomaliza anampasa mphatso ku Tchalitchi ko
Zaululika Chimanga chija mpaka mwachitere? chachokera kuti kodi?
มุมมอง 12K2 ชั่วโมงที่ผ่านมา
Zaululika Chimanga chija mpaka mwachitere? chachokera kuti kodi?
Komatu Zakumana Brian Banda ndi Patricia Kaliati 1.by 1 fuso ku fuso🤣
มุมมอง 4.2K2 ชั่วโมงที่ผ่านมา
Komatu Zakumana Brian Banda ndi Patricia Kaliati 1.by 1 fuso ku fuso🤣
A Chaponda Musatero ai takonzani apapa Anthutu amakukondani Tapakulani pang'ono pa 200 paja ka
มุมมอง 2.2K4 ชั่วโมงที่ผ่านมา
A Chaponda Musatero ai takonzani apapa Anthutu amakukondani Tapakulani pang'ono pa 200 paja ka
Ati Mukagwira Mkaidi amene wathawa Kundende......... thumba la 50kgs
มุมมอง 2.6K4 ชั่วโมงที่ผ่านมา
Ati Mukagwira Mkaidi amene wathawa Kundende......... thumba la 50kgs
Mangochi walusila A Chakwera ndi a ku Karonga omwe akufuna kumuthamangitsa.
มุมมอง 5K4 ชั่วโมงที่ผ่านมา
Mangochi walusila A Chakwera ndi a ku Karonga omwe akufuna kumuthamangitsa.
Mwazinva kodi akuti Lyton Mangochi azipitatu kwao anyamata zikwanje aku Karonga.....
มุมมอง 7K4 ชั่วโมงที่ผ่านมา
Mwazinva kodi akuti Lyton Mangochi azipitatu kwao anyamata zikwanje aku Karonga.....
Samuel Lwara yake Ija kung'alura Cabinet yanyawaniyi 😂
มุมมอง 4.2K7 ชั่วโมงที่ผ่านมา
Samuel Lwara yake Ija kung'alura Cabinet yanyawaniyi 😂
Kodi Mesa anapereka mpata oti amene ali ndi umboni akapereke ku Commission of Inquiry????
มุมมอง 7K7 ชั่วโมงที่ผ่านมา
Kodi Mesa anapereka mpata oti amene ali ndi umboni akapereke ku Commission of Inquiry????
Shehe oyamba Kung'alula A Chakwera ndi Boma la Mcp uyu zilikotu muonerenii
มุมมอง 18K7 ชั่วโมงที่ผ่านมา
Shehe oyamba Kung'alula A Chakwera ndi Boma la Mcp uyu zilikotu muonerenii
Pali Kagulu kena sikakufuna kazinva ena akukamba za Chikangawa........ koma dziwani izi........
มุมมอง 3.1K7 ชั่วโมงที่ผ่านมา
Pali Kagulu kena sikakufuna kazinva ena akukamba za Chikangawa........ koma dziwani izi........
Anthu Adad akuwakonda kwambiri adad sakugawa ndalama sakutenga oimba koma anthu ambirimbiri
มุมมอง 6K9 ชั่วโมงที่ผ่านมา
Anthu Adad akuwakonda kwambiri adad sakugawa ndalama sakutenga oimba koma anthu ambirimbiri
Triphonia Mpinganjira wanyamula 20 Million akungogawa mmisika mpaka nzimai wina amakana kulandila
มุมมอง 19K9 ชั่วโมงที่ผ่านมา
Triphonia Mpinganjira wanyamula 20 Million akungogawa mmisika mpaka nzimai wina amakana kulandila
kwanthawi yoyamba Born Kalindo wang'alura Manganya ndi wina aliyense wa....
มุมมอง 3.6K9 ชั่วโมงที่ผ่านมา
kwanthawi yoyamba Born Kalindo wang'alura Manganya ndi wina aliyense wa....
List ya Nyawani ya nduna za tsopano mwaiona? mukuganiza bwanji 😂😂😂 zili umu onerani mpaka kumapeto.
มุมมอง 15K9 ชั่วโมงที่ผ่านมา
List ya Nyawani ya nduna za tsopano mwaiona? mukuganiza bwanji 😂😂😂 zili umu onerani mpaka kumapeto.
A Chakwera akuti akufuna kusintha nduna zina za m'boma muchaka cha New 1 chi.
มุมมอง 5K9 ชั่วโมงที่ผ่านมา
A Chakwera akuti akufuna kusintha nduna zina za m'boma muchaka cha New 1 chi.
MCP imatha Ndipo ndi dolo poyankhula koma osati pochita 🤔
มุมมอง 5K12 ชั่วโมงที่ผ่านมา
MCP imatha Ndipo ndi dolo poyankhula koma osati pochita 🤔
Born Kalindo Lero Walero wabwera ndi......
มุมมอง 4.4K12 ชั่วโมงที่ผ่านมา
Born Kalindo Lero Walero wabwera ndi......
Sameer Suleiman akuti ngakhale akufuna kutipha koma tiwachotse a Chakwera
มุมมอง 1.9K12 ชั่วโมงที่ผ่านมา
Sameer Suleiman akuti ngakhale akufuna kutipha koma tiwachotse a Chakwera
A Mvula ati sakuona chodabwitsa kuti a Usi athamangitsidwa ku UTM nde pali Nzimai wina wang'alura.
มุมมอง 6K12 ชั่วโมงที่ผ่านมา
A Mvula ati sakuona chodabwitsa kuti a Usi athamangitsidwa ku UTM nde pali Nzimai wina wang'alura.
Ndipo musamati mwenye wapusa inutso mupusatu pompano ndipo summer seleman sangapuse pazithu zausilu ngati izii
ambiliwa,ali,ndimilandu,akamatukwana,anzao,zinthu,zomwe,iwowo,adachitako,amangeni,,ndikuwakumbutsa,zomwe,iwo,ankapanga,
Akutokosa mamvu pachisa, akuyiyambayo ndipelete wakumbuyo akhala patsongolo.
mumakwana big namiwa
amene,azikamba,zanzake,nkhani,yazakuba,azikhala,oti,sanabeko,,zimawawa,atakukumbutsa,umbava,wako,
Kalikose ka pasi pathambo kazuululika
God z watching,,anthu opanda mantha ndi Mulungu ngati awa simnawaonepo,,ndimawaona mma film aku Nigeria
muthalika,anati,ngat,mwagwil,wakuba,,amangidwe,awawa,akhoza,kuwamanga,tione,ngat,sanabeko,
Musataye ntima Mr Sulaiman Allah alinanu tili nanu limodzi palibe chimene angakuchiten
amangeni,anthu,awawa,ndi,amene,akumatukwa,boma,pamene,iwowo,anaononga,chuma,chadziko,
Ziwamenyerani khondo a DPP wo, iwobali pheeeee
Ndipo nde kuwamenyelatu kkkkkkk
Mmmmmmm gayez malawi watani ngati ndichimo mulungu tikhululukileni
Dpp will win sure
😂😂mcp dzawo ndiye dzambiri kuposa dza amzawodzi
Kukwera kwa zinthu ndi dziko lililonse koma kusayenda ndi kumene kwa vuta mukunenanu palibe chimene mukudziwa boma Lina lililonse ndilakuba ndi boma litilo lalamula Malawi koma sinabe kusadziwa mkufakomwe
"Kodi maliro a kasambala anali opambana bwanji kuti ayendege pomwe ma politician Ena samapasidwa ndege akamwalira?" Best question
Chakwera wationongera Mother Malawi 🇲🇼 ❤....Zomvetsa chisoni kwambiri 😢😢😢😢😢😢
Zomvetsa chisoni Malawi's boma ili lozuza kumanga anthu osalakwa akulimbana ndi opposition pamene Iwo mcp anapha anthu Kuchikangawa akubisa black box Ali free osamangidwa tiyeni tigwirane manja Malawi's mademo boma lakhaza li latikwana
Kavuleni mesa paja mumati tidzayenda maliseche😂😂😂😂
Munya muona pa muharayo ndine chidzukulu chake phalombe phwetchiwa sukuidziwa iwe
Mzopanda peke tinazivera kale
Chakwera suli mumtengo aise this is world analiko amnzako😮😮
Nthawi yakuti zipani Zose zotsutsa zigwirane manja kuthana ndi MCP 💔💔 yakwa koma Alidwooo ACHINA kabambe chihana mukutani UDF PAJATU NDIWA MCP AMANGOCHITA ZOBALALIKA ATUPERE adzazimitsidwa monga CHILIMA 💔😭 akukalamba kosaidziwa mikango akathana ndi DPP awona Inu kuti achitananu motani??
Mcp muchoka ndithu tizakumana ndi apólice anuwo
Boma ndilomweli ku mwera konko galu iwe
Amutuluss msanga mapeto ake tiwotchapo police station imeneyo
Bola angootcha po police komaso achosetso chakwera
Mulungu alipo atuluka Inshallah
Koma izizi amapindulanji akamanga????
😂😂😂😂😂😂😂 kapusa ka Mwenye kologolora
km,zifike,kukhothi,kuti,tive,umboni,okwana,okwana,bwino,tisakulupilile,zammaluwa,
padepade we are so tired
Namiwa. Uja ndikatundu kwambili God bless you amalawi abomawa akutitoladi hvy
🤣🤣🤣 a mphyodza Magazi ndi mikodzo mwatasatu kumanga a Opposition Koma mukudziwa Kuti mukudzionesa Uchitsiru Ku Mayiko ena pa zomwe mumuchita a Chakwera 😂😂 Mongokukumbusani inu a mphyodza Magazi ndi Mikodzo a MCP mudzidziwa Kuti ino ndi TERM ya Chilima,chaka cha Chilima chino, tikuonerani. Mchifukwa chake munamupha, Chakwera ukhalepotu pa mpandopo mpaka 2050 tili Pano kuonera.
Tikanangovita February basi
Aaaaa wamangidwa Suleiman 😮😮
ife,tinazitenga,kt,amanena,,solemani,ndizoona,km,apapa,chilungamo,chidziwika,kukhothi,
😂😂😂😂😂
moti,akadati,yese,wanamizila,nzake,adzisumilidwa,mulandu,zikadakhalabwino,kwambili,mabodza,akadatha,
chimwendo,kukumana,ndi,solemani,sangafusane,zankhanii,kokafusilana,ndikukhothi,basi,nkhn,isamangowanda,yopanda,umboni,
Walakwa chani
achoke asaze magazi pompano afe
DPP my vote
Shaaaa koma guys 😢
kumalawi,mantha,muthu,akamangidwa,mukuti,akufuna,kumupha,musaiwale,kt,anhu,anatchulidwa,kt,amafuna,kupha,solemani,nawoso,alindiufulu,omutengela,munthuyo,kukhothi,kt,akavetsetse,nkhani,yakupha
Kkkkkkkkkkkk koma guys
asolemaniakufuna,kutchuka,ndichifukwa,amabwela,ndinkhani,zabodza,popeza,kumalawi,timakhulupilila,zopanda,umboni,mot,apa,tikuva,umboni
Malawi's action now akutitola boma lakhazali kutsogolo kukubwera zoopsa osaiwala history is the best teacher
Achakwera amangeni asureema ngati sumunapheko munthu live live muyambe mwandipha ineyo