A Mvula ati sakuona chodabwitsa kuti a Usi athamangitsidwa ku UTM nde pali Nzimai wina wang'alura.

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 6 ม.ค. 2025

ความคิดเห็น • 86

  • @ThoccoChimbali-h6g
    @ThoccoChimbali-h6g 7 วันที่ผ่านมา +9

    Ngati pali munthu akundinyasa politically nde ndi mbuzi iyi yotchedwa maikolo usi

  • @PaulDaka-dc3re
    @PaulDaka-dc3re 6 วันที่ผ่านมา +7

    Ngati akumufuna amutenge alowe MCP zachamba eti

  • @patricksinyala1345
    @patricksinyala1345 7 วันที่ผ่านมา +6

    Mvula ndiwa MCP ukhaula aise UTM ilipo dikila uone iwe si Mulungu, UTM simadalila munthu mmodzi, zilibe ntchito kuti usi apita ndi anthu koma sakhla pa barot mwauponda

  • @henryphiri6100
    @henryphiri6100 6 วันที่ผ่านมา +2

    Mukuona ngati sanaunikire zoti Usi akhoza kupita kwa lawyer asanapange chigamulo chomuchotsa. UTM siyopusa. Analephera u MP kwao Manganya

  • @GiftBello-v1i
    @GiftBello-v1i 6 วันที่ผ่านมา +1

    Yudas Skaliyot anampeleka Biyeni

  • @MarthaGama-q1o
    @MarthaGama-q1o 5 วันที่ผ่านมา

    Ndmawona ngati abambo awa ayankhula zanzeru aaaa ndikuwona ngati ndi amene amamutuma manganya kuti adzisokoneza ku UTM 😢😢😢

  • @ConnexKhomba
    @ConnexKhomba 7 วันที่ผ่านมา +1

    Zizukulu za mvula chonde khalni pasi agogo anuwa muwalangize ndi akape

  • @Ayanali-cr4vy
    @Ayanali-cr4vy 6 วันที่ผ่านมา +1

    UTM yagawidwa,
    Tsogolo la Chipani chamalemu lasokonekera

  • @RaphaelWinford-t7u
    @RaphaelWinford-t7u 6 วันที่ผ่านมา +1

    Iweyo Usi unali kuti iweyo, mbuzi mesa unali tsogoreli mu thawi imeneyo....

  • @henryphiri6100
    @henryphiri6100 6 วันที่ผ่านมา +2

    Anayambira kuononga Shire bus lines. Mbuzi yazibambo.

    • @Nyampha
      @Nyampha 6 วันที่ผ่านมา

      Iiiiiih ndipo inu

  • @InnocentKajomber
    @InnocentKajomber 5 วันที่ผ่านมา

    Kagaru kachabechabe ako kufupika ngati nsapato ya mwana😮😮

  • @ChisomoSaiti
    @ChisomoSaiti 6 วันที่ผ่านมา

    Aaah iwenso ndiwokhuta

  • @MandyTawanda
    @MandyTawanda 6 วันที่ผ่านมา +4

    Auzeni Mama. 100%.

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl 7 วันที่ผ่านมา +2

    Khope ngati mafuwa

  • @DanielZunguza
    @DanielZunguza 5 วันที่ผ่านมา

    Usi akanangochoka mwaulemu,apitaso ku court akatani muthu ndi wa mcp,,mesa amakuwa ku mwaza kuti boma ndilomweli,,,aliyese akudziwa kuti usi ndiosokonedza.

  • @petertengani
    @petertengani 6 วันที่ผ่านมา

    Kodi malume, malayawo titero kuti ndi dzuwa lomwe lakulali?.
    🙏🏾😆😆.

  • @JamesPhiri-g2j
    @JamesPhiri-g2j 5 วันที่ผ่านมา

    Mbuzi yamzimayii

  • @WarriorKB-l3i
    @WarriorKB-l3i 7 วันที่ผ่านมา +1

    Aaaah za zii mmalawi muno presdent wa dzisilu nde ndiweo mvula tachioneni chimutu.Utm yamuchotsa manganya iweo mvula ndi chikangawa mumutenge akhale wanu sitimufunanso apite adzikapanga dza boma ndilomweli inu dzisilu kwambiri.

    • @RaphaelKatimba
      @RaphaelKatimba 7 วันที่ผ่านมา +1

      Ndipo mr nvula anayenela atamangidwa chifukwa ndi mbava imene inaba ndalama zankhaninkhani ku company ya ma bus a Stage Coach mu boma la Dr Bakili Muluzi. mr Nvula ndi mbava yothelatu. munthu ameneyu anagwetsa company ya ma bus ya Stage Coach ndipo company inali pafupi ndipamene pali Shop rite opposite Kamuzu Stadium. ndi chimbava ichi chakuba ndipo anayenela ali ku ndende munthawi inoyo. Ndiye iweyo nvula ukamayankhula usamaganize ngati kuti ifeyo sitimakudziwa .

    • @VeronicaChirwa-ct4os
      @VeronicaChirwa-ct4os 7 วันที่ผ่านมา

      Awuzeni a gulukunyindawa a china mvula

    • @Nyampha
      @Nyampha 6 วันที่ผ่านมา

      ​@@RaphaelKatimbaamuneyu muuzeni angoona ngati anthu anaiwala

  • @VictorJulio-v4s
    @VictorJulio-v4s 7 วันที่ผ่านมา +1

    Zauchisilu munalephela kuteteza UDF mukhale ndi nzelu Ju UTM

  • @FatimaKhan-i5p
    @FatimaKhan-i5p 6 วันที่ผ่านมา

    Angamusatire usi ndani iwe mvula ndimangokuona kani nawenso mmutu mwako muli mamina okhaokha chonchi aaaa ndiwenso mbuzi utm singathe uwonanso osokoneza ndi using your amafuna aitengere utm ku mcp chipani chakupha chipani cha nkhanzaukhaula apitako yekha nzeru zakezo akaonetse ku mcp ko olo u mp sangawine muzandivomeleza

  • @ChifuniroChisaleh
    @ChifuniroChisaleh 6 วันที่ผ่านมา

    Mapwala anu nonse kumeneko

  • @GeorgeKambwiri-xr9ri
    @GeorgeKambwiri-xr9ri 4 วันที่ผ่านมา

    Alibe khalidwe maikolo

  • @MariaDandazaraJSDmoio2024e
    @MariaDandazaraJSDmoio2024e 7 วันที่ผ่านมา +1

    Ausi alibe nzelu ndichitsilu samabva amadzitenga ngati ndiiye yekha

  • @ChifundoNinje
    @ChifundoNinje 6 วันที่ผ่านมา

    Amuchita bwino kumuchosa utm

  • @rabsonswathera738
    @rabsonswathera738 7 วันที่ผ่านมา +1

    Zopepera nzeru za mvula

    • @VeronicaChirwa-ct4os
      @VeronicaChirwa-ct4os 7 วันที่ผ่านมา +1

      Muziti mvula alibe nzeru wangokula chimutucho

  • @mishecksipolo7153
    @mishecksipolo7153 6 วันที่ผ่านมา

    Kodi mu manyengerera anthu eti? Ma tactic anu oti mudzipita ku court to confuse the
    UTM any way DPP is our next government, za umfiti wa Usi ndi MCP it's enough

  • @felixjoseph8161
    @felixjoseph8161 6 วันที่ผ่านมา

    Manganya mboleyake amaona ngati wanzeru ndi iye yekha Malawi Muno apite azikawayamwitsa mbolo ma hule a MCP

  • @GraceChenda-q2g
    @GraceChenda-q2g 6 วันที่ผ่านมา

    Ife usi sichitsilu chathu::akafike

  • @TiyaMtete-l7t
    @TiyaMtete-l7t 7 วันที่ผ่านมา

    Mutu wokulawo mbuzi iweee

  • @SydneyNyasuli
    @SydneyNyasuli 6 วันที่ผ่านมา

    Ali ndi mbili zanji mboza mayi inu nenani

  • @Martha-m6e
    @Martha-m6e 7 วันที่ผ่านมา

    Mukuwona zimenezo ndinuyo.usi sanali wa UTM.

  • @LawrenceBelson
    @LawrenceBelson 7 วันที่ผ่านมา

    Machende ako mvula mutu waukuluwo

  • @GoldenNamanguya-b1f
    @GoldenNamanguya-b1f 6 วันที่ผ่านมา

    Kasongo ameneyu

  • @allahslave7177
    @allahslave7177 6 วันที่ผ่านมา

    Akuluwa zomwe akukamba sakudzidziwa, Manganya amusiya akhale bwanji mchipani kumachita atachokamo ??? Nthawi ya Chilima yo Manganya was not behaving or acting like this ndipo bwenzi atamuchotsa kale kale, off course chitsilu chili ndi mwini ndipo Usi mwini wake ndi wa MCP !!! BOMA NDI LOMWELI NDIYE AKAKHALE MCHIPANI CHINA ???

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani 6 วันที่ผ่านมา

    Usandichimwise Mvula pa neaw year ngt lerol chimutu chachikulucho koma chadzaza ndi mamina okha okha kukamwa konyasako

  • @AdamJames-x7x
    @AdamJames-x7x 6 วันที่ผ่านมา

    Usi mutu ngati choswera malambe, isiye utm kape iweee

  • @brainsmkumbwa6267
    @brainsmkumbwa6267 7 วันที่ผ่านมา

    Chitsiru iwe Mvula

  • @NafeAlie
    @NafeAlie 6 วันที่ผ่านมา

    Nkulu onyasa iwe mutu iwe kd iwe ndi wandale muzi iwe ndimanganyako azibusa amako iwe zoti manganya ndi wa mcp ngati iwe suziwa ndipo maganga siwe wa mcp

  • @AlicksonMakata
    @AlicksonMakata 6 วันที่ผ่านมา

    Chifukwa chamau amenewa mayi iwe ndiwe wotembereredwa usowa mtendere mpaka udzabwerera kwa Michael Usi kulapa God condemning what you said respect your leaders.

  • @GraceChenda-q2g
    @GraceChenda-q2g 6 วันที่ผ่านมา

    Amvula nzeru zinatha

    • @Nyampha
      @Nyampha 6 วันที่ผ่านมา

      Anali nazo?

  • @TonyMhone
    @TonyMhone 6 วันที่ผ่านมา

    Chimvulachi ndi Manganya nzeru zawo ndi zimodzi makape wokha wokha amtengedi apite Ku Chikangawali anthu akupha inu

  • @sangwasa
    @sangwasa 7 วันที่ผ่านมา

    😂😂😂😂😂😂😂 koma Anachita kumuyamba dala, kungofa Chilima basi kumuukira Usi

  • @RosePhiri-n8q
    @RosePhiri-n8q 6 วันที่ผ่านมา

    Usi akasumila ndani poti ku convention adakana kuti akasankhidwe?amalawi zokamba zina kambani zoveka usi akufuna kusokoneza utm basi

  • @kondwanimunthali7401
    @kondwanimunthali7401 6 วันที่ผ่านมา

    Hahahaha Manganya ali ndi nzeru zanji?

  • @DanielZunguza
    @DanielZunguza 5 วันที่ผ่านมา

    A mvula ndiye mbava yoyipa moyo inagwesa company ya bus, Boma la udf.

  • @joebrown1158
    @joebrown1158 6 วันที่ผ่านมา

    Kodi iyeyo nde wazeru kuposa wina aliyese mdzikomo?

  • @mavmsusa1310
    @mavmsusa1310 7 วันที่ผ่านมา

    Makape akhokhola aku Mulanje

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg 7 วันที่ผ่านมา

    Usi nyini yamake

  • @VeronicaChirwa-ct4os
    @VeronicaChirwa-ct4os 7 วันที่ผ่านมา

    Akulu awa angokula koma ndi openga osawamvera

  • @JamesRoben-dy7bx
    @JamesRoben-dy7bx 7 วันที่ผ่านมา

    Awa akalamba akunjiya ya mcp

  • @ChrissieNyasulu
    @ChrissieNyasulu 7 วันที่ผ่านมา

    God will guide

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 6 วันที่ผ่านมา

    Lero 1 Jan ,uzichotsela activist wa boma uzayenda wa uyo uyo mdala iwe

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl 7 วันที่ผ่านมา

    Iwe mvula ndi chitsilu cha munthu mbusi ya mcp

  • @PromiseKhenzo
    @PromiseKhenzo 7 วันที่ผ่านมา

    Mvula ndi mbuzi ya munthu

  • @ChifuniloNsanama
    @ChifuniloNsanama 6 วันที่ผ่านมา

    Chisiru chili ndi mwini koma usi Alibe mwini
    Usi alibe phindu munthu owumira ngati ameneyo
    Azipita ku mcp komweko mupase zochita ku mcp komweko

  • @GonaMkuphe
    @GonaMkuphe 6 วันที่ผ่านมา

    Wabodza iwe MVULA

  • @CharlesJames-f1w
    @CharlesJames-f1w 7 วันที่ผ่านมา +1

    Wamandirama.usi

  • @PeterAlbert-w9g
    @PeterAlbert-w9g 6 วันที่ผ่านมา

    Happy new year 🎉

  • @joebrown1158
    @joebrown1158 6 วันที่ผ่านมา

    Iwe ndiwe munthu wonama kwambiri munthu wonyasa muzochitikita zako

  • @paulpaseli6310
    @paulpaseli6310 7 วันที่ผ่านมา +1

    Aaa mvula nda chisilu chamuthu uyu mesa Ali limodzi kuchikangawa party.

    • @JulianaMkonda-k2n
      @JulianaMkonda-k2n 7 วันที่ผ่านมา

      Chimunthu chopanda nzeru icho chikangawa

    • @LoyceChipwaila
      @LoyceChipwaila 6 วันที่ผ่านมา

      Onse a mcp akumyikira kumbuyo manganya pazosokoneza utm, kusonyeza kuti cholinga chao ndichimodzi.
      Chilima anakhulupilira munthu oipa kwambiri Manganya.

  • @NafeAlie
    @NafeAlie 6 วันที่ผ่านมา

    Manganya ndiwe wa mcp usasokoneze chipani chathu

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg 7 วันที่ผ่านมา

    Atumbuka zelu mulibe mbolo yako

  • @YasinterKapinga
    @YasinterKapinga 7 วันที่ผ่านมา

    Malawian cameras happy new year

  • @FlemingsMwamlima
    @FlemingsMwamlima 7 วันที่ผ่านมา

    Mudarayu kukhara mbewu kungootcha , kukura kopanda nzeru mutu 😂😂

  • @PatrickKapendo
    @PatrickKapendo 7 วันที่ผ่านมา

    Anthu ena omwe amangosatila chipani chifukwa chochikonda ndiwomwe angolankhu zopusa chipani kuti chiyambike sianthu osatila ai chimayambika ndi omwe afuna kutero

  • @SinsaKachale
    @SinsaKachale 7 วันที่ผ่านมา

    Usi watopesa kwambiri

  • @felixjoseph8161
    @felixjoseph8161 6 วันที่ผ่านมา

    Mvula mbole yako ntenge upite naye Ku MCP kwakoko mbole yako

  • @WisikiBlack-gj4gu
    @WisikiBlack-gj4gu 7 วันที่ผ่านมา

    Ussi ndigaru mfiti, akafike azipanga zake zaku mcp zo

  • @Abdul-xk8dq
    @Abdul-xk8dq 6 วันที่ผ่านมา

    Mdala uyu amandibowa kwambili alibe mfundo

  • @rashidkandulu290
    @rashidkandulu290 7 วันที่ผ่านมา

    Ojiya kkkkk

  • @JonesChingaya-yf4gg
    @JonesChingaya-yf4gg 6 วันที่ผ่านมา

    Usi ulibe manyazi, wekha unkati munatenga ndalama Ku Boma ndipo unayendetsa nawo mwambo onde 100%, lero ukusinthanso ukuti upasidwe report, ukudzitsutsa wekha. Musamazimve nzeru kuposa a malawi onse, mu UTM muja muli anthu anzeru kuposa inu. Kutengedwa ndi Chilima si nzeru ay, koma kut anakukhulupirirani kut mugwira ntchito bwino koma kunali kuzinamiza.
    Chimodzi modzinso kuwatsogoza a Chakwera sikut anali a nzeru koma kut anali munthu wozichepesa komanso anawakhulupirira kut agwira limodzi ntchito zomwe zinaonekanso kut kunali kuzinamiza chabe.
    Choncho Usi usiye kuzimva, you are not bigger than the party itself. With or without you things will keep on going in UTM.

  • @PaulDaka-dc3re
    @PaulDaka-dc3re 6 วันที่ผ่านมา

    Kukhoti kwachani ugalu eti

  • @HandEllah
    @HandEllah 7 วันที่ผ่านมา +1

    😂 Ma zoba okhaokha

  • @emmanuelmuyilaa
    @emmanuelmuyilaa 6 วันที่ผ่านมา

    As he is now talking nonsense

  • @ChifuniloNsanama
    @ChifuniloNsanama 6 วันที่ผ่านมา

    Usi tinanva kuyipa ntima mukuwonasaku ngakhale ku family kwanunso chimodzi modzi.
    Patali Mumawoneka ngat munthu wabwino km chiwanda cha mcp chakulowani mulape

  • @FrancoKaunga-rq2ki
    @FrancoKaunga-rq2ki 6 วันที่ผ่านมา

    Amvula chipani chanu chinatha komaso anakusiyani kale ku UDF! Zisiyeni izi kalimeni tomato kwa hoho.