Zopusa. Ojiya aja abwelanso ndi nyasi ina. Lyton Mangochi ndi nzika ya ku Karonga. Anakwatira komweko,ali ndi ana komweko ndipo wakhala zaka zambiri komweko. Lyton Mangochi amachita bisinesi ku Karonga Iye ndi M'Malawi ndipo ali ndi ufulu okhala kulikose mdziko muno.. Komaso ngati dzina lamga ndi Dick Dedza sindiye kuti ndine wa ku Dedza.
Zibwana zenizeni anthu Aku kalonga ngat Aku panga zimenedzi nde kutiso anthuwo ndiwopepela coz anthu a Ku karonga Ali Pena Pali pose mziko la Malawi nde why akufuna kupanga zimenedzi manyaka enieni
Zibwana zeni zeni , kupasana malire tose a malawi
Mau olombikisa amalawi thanks pastor
Ndiye Hon Samuel Lwala uja nayenso amathudzula zitani
Osayamba mwanthamangitsa ma islayeli bwanji agalu inu
Ndipo agalu amenewa azithamangitsa Malawi mzawo pomwe akulandira ma islayeli. Boma la chabe
Together as one tonse ndamodzi palibe kuthamangisana
Taziyambeni ngati mungazikwanitse
Ndipo singagwile imeneyo muyelekeze mutiziwe kt ayawo nafe timatan tikulowesan jando muwona
Akaterotu awapatsa ndalama zoti achite zimenezo
A pastor shumba mungapange chani inu pa karonga ka chitsiru iwe
A pastor shumba mukungunena simukuyiziwa karonga
Tigawana pompano , bola musazadandaule , chifukwa kukarongako ndiye ndikutchile
Ndiwo uchitsiluwo! Sizingachitike zimenezo.
Eish politics, tsopano yikubwela ndi tribalism. Atsogoleri andale khalani pasi mukambilane zobweletsa chisokonezo pakati pathu sizabwno.
Anyamata akukaronga ndinu zitsiru .Layton mangochi msamuopseze. Kumpto sikwanu nokha .ndinu agalu kwambiri nanga nkumasekelela mcp
Kkkkk macadet kuyikilana kumbuyo
Kkkk mcp sichipani chabwino chinapangikila kuti chizipha kuononga ndi kuba
Zopusa.
Ojiya aja abwelanso ndi nyasi ina.
Lyton Mangochi ndi nzika ya ku Karonga. Anakwatira komweko,ali ndi ana komweko ndipo wakhala zaka zambiri komweko.
Lyton Mangochi amachita bisinesi ku Karonga
Iye ndi M'Malawi ndipo ali ndi ufulu okhala kulikose mdziko muno..
Komaso ngati dzina lamga ndi Dick Dedza sindiye kuti ndine wa ku Dedza.
Ayambe amuthamangitse kaye chakwera 😂😂😂😂 ndi dzitsilu zimenezo
Never ife tsankho lanuro ife ayi Layton mangochi ali kwawo akhoza kukhala kulikonse komwe angafune ndi dziko lake lino be free Mr Layton Mangochi
Chimwendo Banda ndamene watuma anthuwo koma tayelekezani muone manyi
Zikangochitika tingawana madera, a paramount abwere kaye kuno kudzatenga anthu awo basi 50 50
Zibwana zenizeni anthu Aku kalonga ngat Aku panga zimenedzi nde kutiso anthuwo ndiwopepela coz anthu a Ku karonga Ali Pena Pali pose mziko la Malawi nde why akufuna kupanga zimenedzi manyaka enieni
Mukunena zoona, tose ndife aMalawi
Pastor pitanikoni zomwe ayamba a mcp ndi nkhondo timanena ija awona kuti alephela kulamula dzikoli nde awona kuti apitilize kupha kuti akapeleke msembe imeneyo sigwila tiwauze a mcp kuti zomwe akudalirazo ife tili nazo× 3. Tikufunilani kuenda kwabwino pastor mutidzuwise mmene dzikhalile chifukwa dzauchisilu mmalawi muno sitifuna.
Amenewo si anthu aku Karonga koma andale omwewa Lyton amakondedwa ndi anthu ambiri pa Karonga
Kodtu olo muphe kaya mutan koma tizaonana ku ballot box kudyako mukudya nokha koma nthawi ikwana muzaziona
Achita bwino achokeko kwathu ku karonga azipita kwawo
Kalongaso kachani ayelekeze tiwapeza koko asasamba amenewo alandila ma 2pn mix zamba
MCP kusowa zochitatu
CHONDE CHONDE MOKUPEMPHANI OSANGOTENGA CHISAWAWA MAINA.
MKANGO WA AYUDA NDI YESU YEKHA.
SORY NGAT NDAKULAKWIRANI.
Ndiye atumbuka omwe akupezeka kumangochi kukoma nawomso ayambe nafe kuno tiyamba ndpo muwatsimikizile kuti timaboat ta atumbuka anzawo tili Kunoti tisamuke
Kma nyau kupusa
Ayi anthu aku karonga nawo asamuke ngati ali ma boma ena
Anthu mwayamba kutulilana malile kd?😢 Malawi
Koma agalu a mcp kkk
Zisilu basi anyamata opusa inu mesa mumapha somba inu tikuonani mubwelera kwanu mukuvutika ndichikangawa manyaka basi
😂😂😂😂, inetu ndi mayetsa, kuti azipita kwaoko, ndiye kuti ndi obwela.koma ku Malawi kokuno iyaaa,aziyambitse,zimenezo tione ngati sitiwatyola makosi abale awo,ali kunowa.ayiyambe, imeneyo.mcp,itha ngati makatani.
Osaiwala kuti atumbuka ena ndi opusa panya pao
Sizingatheke,taziyambeni tikuonereni
Chakwera mfiti imeneyi sinkhondo galu iwe chimunthu chosamva
im not a fan of mcp koma mudzinena zoti zili ndi umboni,,