Chimwendo Banda adzatiudze bwino çhifukwa ciani sanakwere nawo ndege ija. Even atakhala Kuti Madam Chilima ndi bodyguard wawo akanakwera ndege ija Malo a munthu mmodzi akanapedzekamo. Why why why sanakwere nawo.
I think awa kaya mukuti ndani akunama kuti akumva nawo kuwawa pa imfayi. I agree kuti kuti ena akufuna kutchukilapo koma kumapanga anthu kuti asanene za kukhosi ndi momwe zinthu azionela. Kodi anzeru ndi inu nokha ingolankhulani maganozo anu koma you should not overruel maganozo awena. Inuyo munakhutila ndi report khutilani ena sanakhutile asiyeni. The Lord in heaven sees the heart
Ndipo satikwanitsadi mpaka tidziwe chilungamo. Anazolowera Kuti a Malawi sitichedwa kuiwala iyi yokha iyi. Ndikuti iyi yokha iyi mpaka chilungamo chituluke basi
Osangotulutsa black box bwanji ngt chilima simunachite kumupha?a commission of inquiry sanakambe zot amawauza achakwera zot ndenge inakafka ku mzuzu ndi ndani why?.uyu siujayo amanamizila kut ndi mzika yongokumana nayo panseu kumakamba za zitukuko zomwe at MCP yapanga uja uyu.?komanso zikungosonyeza kut ndale zapa Malawi sadzitsata.zot chilima wafera alliance asakudziwa ndi ndani?za ziii bas
Maka maka mbc ndi mcp mbuzi zimenezi dzikufuna dzidzitiopyeza dziko muno koma tiwauze kuti sigwiila antaah amene dzikumuwawa akadzimangilire we dont care koma a malawi sitisiya kulankhula dza chikangawa pokha pokha mcp ituluse black box. Sangamange munthu bcoz onse omwe anapha ndege ndi a mcp.
ndimaona ngati ukamba za nzeru koma ndiwe mbuzi komanso mapwala Ako , akanakhala kuti ndi ankolo Ako mwa m'modzi omwalira aja bwezi lero ukumakamba manyi akowo? ngati wasowa chochita khala chete mtchende lako galu
Kasakula ndi anzake ndi zitsilu kwambiri, A MCP adachita kukonza imfa ya Chilima chifukwa cha udindo. Aliyense anamvela zomwe adapangana Chakwera ndi Chilima.
Ndiwe galu kobasi ndi chakwela wakoyo, ndiwe chitsilu kwambiri......
MALAWI MALAWI 🇲🇼😢😢
Uyu mumuuze kt panyapake zed!!!!!!!!
Mtengo wakankhande ndie chikangawa
Mukamalankhula muziziwa kuti kuli anthu Ena azelu kuposa inu musamaone ngati tosezisilu ngati wadya bazi khala chete
Ngati ukutelo brack box ilikuti bs umboni ndiumenewo
But why? 🤔 SKC and other 8 can't be forgotten!
This shall live with us forever. Zidzakambidwa kwambiri MCP ikadzaludza pa 16/09/25. Ndipo tidzatokota mtundu wonse
Chimwendo Banda adzatiudze bwino çhifukwa ciani sanakwere nawo ndege ija. Even atakhala Kuti Madam Chilima ndi bodyguard wawo akanakwera ndege ija Malo a munthu mmodzi akanapedzekamo. Why why why sanakwere nawo.
😢akulu opusa awa ,ati akujiya zazii zopanda nchele omwe
Inu amen mukudya ndalama zopanda tukuta muzakabula Nazi patsogolo
I think awa kaya mukuti ndani akunama kuti akumva nawo kuwawa pa imfayi. I agree kuti kuti ena akufuna kutchukilapo koma kumapanga anthu kuti asanene za kukhosi ndi momwe zinthu azionela. Kodi anzeru ndi inu nokha ingolankhulani maganozo anu koma you should not overruel maganozo awena. Inuyo munakhutila ndi report khutilani ena sanakhutile asiyeni.
The Lord in heaven sees the heart
Zalowa zawekha ife sitiinga site kukamba
Correct big up will still saying that forever and we will write the book for SKC history how he died he was our last hope to change Malawi
IWE ULIBE CHISONI MWANA WANJOKA UZAFA NGATI NGALU PANYELO PAKO KHOPE NGATI CHITUMBUWA
Aaaa mwadzuka wa munthu supita padela dzizadziwika
Achewa awa amadyandibomawa ndiamene zimwakwiyisa ndipo satikwanisa
Ndipo satikwanitsadi mpaka tidziwe chilungamo. Anazolowera Kuti a Malawi sitichedwa kuiwala iyi yokha iyi. Ndikuti iyi yokha iyi mpaka chilungamo chituluke basi
Zitsilu inu
Limbikirani mwina akuninkhani unduna😢😢😢😢🎉
Uyu ndi mwana wanjoka ndithu
Ndi iwe ngalu kwabsi
Kkkkkk kapologram kopusatu aka anthu ake ali biii ungalimbane ndi kabambe iweyo
Osangotulutsa black box bwanji ngt chilima simunachite kumupha?a commission of inquiry sanakambe zot amawauza achakwera zot ndenge inakafka ku mzuzu ndi ndani why?.uyu siujayo amanamizila kut ndi mzika yongokumana nayo panseu kumakamba za zitukuko zomwe at MCP yapanga uja uyu.?komanso zikungosonyeza kut ndale zapa Malawi sadzitsata.zot chilima wafera alliance asakudziwa ndi ndani?za ziii bas
Timvetse sitimamverera
Nonsenu ndichikangawa
Ndingayanbe kutukwana ndisunge mlomo
Maka maka mbc ndi mcp mbuzi zimenezi dzikufuna dzidzitiopyeza dziko muno koma tiwauze kuti sigwiila antaah amene dzikumuwawa akadzimangilire we dont care koma a malawi sitisiya kulankhula dza chikangawa pokha pokha mcp ituluse black box. Sangamange munthu bcoz onse omwe anapha ndege ndi a mcp.
Yankho la zonse ndi black box. APO Biiiiiiii munya ndithudi. Kupha kotero kopanda nako manyadzi agalu inu.
Tulutdsani black box anthu advice chomwe chidaphetsa anthu
Black box ndie yankho ya zonse tikukanganadzi. Anthu akupha Chikangawa party.
Choka iwe chakweraso ndibusa bwaanj anapanga zimenezi
Tabwela Bande uzaime ngati MP wa DPP ku nsanje north uwina ulendo uno
ndimaona ngati ukamba za nzeru koma ndiwe mbuzi komanso mapwala Ako , akanakhala kuti ndi ankolo Ako mwa m'modzi omwalira aja bwezi lero ukumakamba manyi akowo? ngati wasowa chochita khala chete mtchende lako galu
Ndipo wamutukwana mokwana ine ndingowonjedza Kuti kuthako kwake konukha sasambako ameneyu.
Utipangitsa tiyambe kutukwana Makolo AKO pano. Usadzabwerenso pa air ndikuyankhula mapwala ako apa khumba iwe
Awa ndi zitsilu ndithu
Maganizo ako amenewo black box ilikuti
Kasakula ndi anzake ndi zitsilu kwambiri, A MCP adachita kukonza imfa ya Chilima chifukwa cha udindo. Aliyense anamvela zomwe adapangana Chakwera ndi Chilima.
Zitsiru zaanthu inuyo galuwe munamupha basi
Akulu mukama kamalankhula za mulungu lankhulani zawona chifukwachiyani dziko lapasi lina khazikitsa makhothi ndiwe munthu wowukira iwe sufuna kukhala pa chilungamo m'moyo wako chi fukwa chiyachilungamo chikhale chilungamo nthawi zonse ngati msusa anawona kuti apa palibe chilungamo chalakwika ndichyani? Iweyo wukupanga opposition yako uli mbali yomweyo anthu amenewa
Black box ilikuti ,
Zaziiii
Pa
Zoona kasakula
I thought you wanted to tell Malawian exactly what happened but now I see where you heading to with your statement please be honest to the public