It would have been better if Namiwa remained in the commision chifukwa zomwe akufunsazi zikanapezeka mu report muja koma maganizo ake ochoka mu commision anapangitsa kuti report ituluke yosapsa.
It was good that he didn’t, the Holy Spirit at work. He needed to be out for us to see the weakness of this report. It would have been very difficult for him to challenge the same report that he would have signed for.
ndiwe munthu wopusa kwambiri Kodi ukusangalala ndizomwe zikuchitikazi m'dziko lino ukufuna kuti anthu asanalankhure this is a democratic country my friend
Wreakage ya ndege yogwa pa height 4.5m singaoneke chonchija. Anthu awa alibe manyazi a Chakwera. Angovomereza kuti this was a mission went wrong. Zikhale Ng'oma analakwitsa Chakwera ill advised
Koma mwawufunisisatu udindo , iwe unalikuti kuti ukapeleke umboni wako? Pomaliza or utayakhula chotani sangadzukeso anthu anamwalila aja ungothapo mawu ako .
Ngakhale atola nkhani wo angofunsira mafunso polemekeza ganyu wawo koma the truth is that they had no questions 😂 coz mafunso onse got the answers already 😂
Muyambe kae mwaitanitsa kunkuyu akatuluse black box, mkulu wa asilikali mabodza amanena pa 10 June aja + plus chakwera iye mwini akanene amene anamuuza KT ndege inakafika ku MZ nkhan ndiya straight forward ngt inalidi ngozingozi , but the moment chakwera akungabe anthu onse mmaudindo omwe amayenera kuchosedwa chifukwa Cha ngozi imenei ndekt chakwera akudziwapo kanthu
Iwe ananakusakha kt ukhale mu comeet muja chifukwa chani iwe unatulukamo . lero ukuyankhula ngat wanzeru. Zonsezi iwe unakazifufuza Amalawi tiye tizikhala pa chilungamo
Zikomo CDEDI, we salute your leadership Mr Namiwa & team.
Wauuuuuu namiwa ulemu wanu may God protect you and bless you more fire
May God bless you sir Namiwa, and we release warrior Angels to protect you sir, we need people who can stand on the truth like this.
As a Malawian we are tired of Chakwera is cruel and careless mn enough is enough must pack and go no mercy
Musowa....Chilungamotu chikuwawa,akusakani....GOD HAVE MERCY AND PROTECT YOU GUYZ
Thanks namiwa god will bless you
God is with u mr Namiwa no fear
Salute Mr Namiwa keep it up mpakana chilungamo chake chidziwike
God Bless you Mr Namiwa
Koma kantande amandiwaza amapanga zithu ngat mwana wokulila mu ghetto zowonadi Koma gyz mumandipezesa chochita mukatulusa video yanu ❤❤❤❤❤❤
Keep up Namiwa , may the good.God continue to protect you
Namiwa big up. Apaneni amenewo. Ngozi anachita kukonza
May God Almighty, please, save Comrade Namiwa. May He also make a million more Namiwas in our motherland!
Namiwa. Uja ndikatundu kwambili God bless you amalawi abomawa akutitoladi hvy
More fire
Apondeni pamtima. Aliyense wosapota mcp adapha nawo 😢
Akungo bwebwetatu azibale a anthu onse amene anatisiya sakugona tuloyi akupemphela kuti mulungu awawonese cheni cheni,big up namiwa
Koma munthu guys mhu 🙌 kuyesesa kubisa ma umboni koma atah mulungu akukana 😂😂😂
May good Lord protect and protect you
Namiwa more fire
Mr Namiwa more fire apanikizeni awulule chomwe anthu awa anachita ma futso osewa ndi omveka bwino
Rip biyeni😭😭😭😭😭
"Kodi maliro a kasambala anali opambana bwanji kuti ayendege pomwe ma politician Ena samapasidwa ndege akamwalira?" Best question
Anali Lawyer komaso zimawakhuza aboma zimenezo
Inali nyambo yofuna kuphera anthu
Namiwa ndi number one
It would have been better if Namiwa remained in the commision chifukwa zomwe akufunsazi zikanapezeka mu report muja koma maganizo ake ochoka mu commision anapangitsa kuti report ituluke yosapsa.
His fellow commission of inquiry colleagues they were trying to programme him that's why he decided to quit.
It was good that he didn’t, the Holy Spirit at work. He needed to be out for us to see the weakness of this report. It would have been very difficult for him to challenge the same report that he would have signed for.
😂😂😂koma fada mpaka kufufuza ma pic ake akuukwati 🤣🤣🙌🙌🙌
🎉❤❤100
Yes❤❤❤❤❤
Ndipo iwe namiwa ambuye akupase moyo wautali pakunena chilungamo chokha chokha osawopa osafowoka osatopa
Please Malawians can we keep quiet,,, September 16,,we gonna know everything about this story,,thawi yathera awa anthu akupha wa
The truth is there we are just waiting for it
Inunsotu akutapani.....🤔🤔 Alibe 2kolokotu,pano kwaipaa!
The guy is angry, u can feel the pain in him.
Forsure they nes kuti ndege yikukagwa mhuuuu too bad
Namiwa sakufuna zopepela
Awa ndakatundu
🙏🏼🙏🏼🙏🏼🙏🏼🙏🏼🙏🏼🤞🤞🤞Yes
Mr Sylvester namiwa , muli mugulu losakidwa ndi mcp , akufuna akusemeleni zifukwa within this month of January .
ndiwe munthu wopusa kwambiri Kodi ukusangalala ndizomwe zikuchitikazi m'dziko lino ukufuna kuti anthu asanalankhure this is a democratic country my friend
@edsongeorge8032 kuyankhula zimenezi zikutanthauza kuti ndine opusa , iweyo ndiochenjela sichomcho ???
Big up
Namiwa umandiwaza iweyo ndi #1 palibenso iweyo ndiwe dolo
Awa ndi a chitsiru chenicheni anachiyikamoso mu inquiry koma chinathawa relo chikut fwefwefwe
Iwe ndi Galu wava nde mu inquiry yija muli chilingamo? Kwinako nditukwana
Shame on you
Iweyo nde chitsiru chachikulu amayi ako akungowachinda kunjuga uko galu iwe
Akanakusakha iweyo ndi agogo ako upiteko oti uyu
Komatu chakwela kusamenyedwa galu amene uja akuziona ngat mulungu ndiyeyu
Shem skc Kodi munapitadi sindikuvesa zakachokedwe kanu pano paziko mwina muzatulukila kwinakwake? Ambuye wakumwamba pitilizani kusunga mizimu yaathu amenewo anafa ifa yowawa yochokela kwasatata pitilizani kufukula zobisika kuzela muathu omwe amakuziwani Inu atate dalisanu mizimu yawo komaso matupiawo pakuti komwe kwasala Chile moto umapita komweko Mr namiwa ulemu winu ambuye akhalenanu
Wreakage ya ndege yogwa pa height 4.5m singaoneke chonchija. Anthu awa alibe manyazi a Chakwera. Angovomereza kuti this was a mission went wrong. Zikhale Ng'oma analakwitsa Chakwera ill advised
Km namiwa umakhara siliyas
mumakwana big namiwa
Kodi achotsa bwanji anthu ena ntchito kusiya iyeyo Chakwerayo pamene iyeyo ndiye ndamene ananamiza dzikoli?Chakwera achoke analinamiza dziko ndipo chakwera ayenera kukayankha milandu ku court.....adzamangidwe.
Asanamize amalawi nganti ndi ana ayi
Ndipo 4.5 meters koma ndege kunyenyeka aaaaaah...mxieeew!!!
Following
Chakwera ananamiza mtundu wa Amalawi
Bwana apa ndiye anthuwa asakane, abale athu aja anachita chokonza
Akulu chakwera anapha chilima palibeso chakwera ndi okonda maudindo chosecho mmutu muli manthoko
Iwe mamuna anamiwa ndakupasa ulemu ndagwada
Chakwera ndiokupha apa chimene tikudikira ndi pa 16september kuti chilungamo chizaziwike
padepade we are so tired
Kodi uku atolankhani a MBC simunawayitane?
Nkhani koma imeneyi
Osati akunkuyu nkulu wankhondo, Achimwendo Banda komanso Daud Suleman okha achoke komanso Chakwera ndi Boma lake la MCP lichoke
Best TV in Malawi
🎉🎉❤🙏
Namiwayutu simuthu wamasewe ,dzeru alinazo kwambiri, zonse akuyakhula zomveka bwino kwambiri,,,,,,akuti utsogoleli omwe ukubwela osati wa achakwera udzafufudze bwinobwino za ngozi imeneyi. Mcp singawine,,chifukwa ikadzabera tidzavotaso, ,komaso oyendesa chisakho asamale kwambiri chifukwa muthu amatopa.
Chilungamo chidziwika wina afune asafune
Iweyo Namiwa wandisangalatsa kwambiri chifukwa cha umboni umenewo ndiumene unkandipweteka kwambiri
Koma mwana ameneyo mmsamalile kwambiri chonde
Koma mwawufunisisatu udindo , iwe unalikuti kuti ukapeleke umboni wako? Pomaliza or utayakhula chotani sangadzukeso anthu anamwalila aja ungothapo mawu ako .
Pangolin namiwa
Kkkkkkk ati even pa ukwati wake amaoneka chonchi.
Anamiwa mbambànde
Ngakhale atola nkhani wo angofunsira mafunso polemekeza ganyu wawo koma the truth is that they had no questions 😂 coz mafunso onse got the answers already 😂
Uku ndye kuimvesa kuwawa mcp
Namiwa Mulungu azikudalitsani
Wuyu apweteka Mcp sure
Koma zaka zino nzosilizadi, ulemu udatha ndithu😂😂😂😂
Ati pa ukwat wake anaoneka chomchi😂
Ine maganizo anga posatengera pandale ndikuona kuti aboma awatenge anamiwa zikuonetsa kuti akudIwapo kanthu zaimfa ndingozi imene inachitika kuchikangawa akalemphera kupeleka umboni awatsekulire mlandu wakuwaphera ufulu akubanja komaso kupereka uthenga omwe ulimkuthekera kubweretsa ziwawa mdziko .iwowa akanakhala solo sakanathawa mkomiti.
Muyambe kae mwaitanitsa kunkuyu akatuluse black box, mkulu wa asilikali mabodza amanena pa 10 June aja + plus chakwera iye mwini akanene amene anamuuza KT ndege inakafika ku MZ nkhan ndiya straight forward ngt inalidi ngozingozi , but the moment chakwera akungabe anthu onse mmaudindo omwe amayenera kuchosedwa chifukwa Cha ngozi imenei ndekt chakwera akudziwapo kanthu
Inu mukuti chian? Chilima anachita kuphedwa ndi chakwera basi!!
@MzadziWanga kumkuyu sanapanjitse press briefing koma awa asamatisowetse mtendere pamene atasankhidwa ntchitoyo anayithawa zitipindulira chiyani ngati Ali ndi information bwanji osangobweretsa zomwe akuzidziwazo koma izizo sizothandiza koma tikudziwa kuti akudyera momwemo akulandira funding kudzera kuzipani amene Ali katangale chabwino afotokoze Kaye kuti funding ya press briefing iyiwo nanene komwe ayitenga .zomatipusitsa ife ayi ena akupeleka ma comments apawa ndi abungwe lawolomwe amadyeralimodzi
@crytoniegrantliffa2431 inu sitingalimbane nanu kagawanani zaumbulizo or inuyo kuti tikufuseni apapa umboni palibe chomwe munganene koma apa tingoti mbuli zikugawana uthenga
Kalikose ka pasi pathambo kazuululika
Ndipo anthuwa adzafa mozunzika kwambiri,kupititsa anzawo kulichete nkhaniyake ndale mmmmm zimandiwawa mpaka pano.achibale pitani panafera anthuwo mkatapepo chiduswa chandenge olo udzu mpite kukaronga olo rumphi ndipo onse anapanga upouwu afenawo pasanathe masabata awiri.zikundiwawa ndikamaganizira
Asatenge ngati amalawi ndi opusa aphunzitseni ndithu Pali mbuli za sukulu dala chifukwa cha dyera adziwe kuti si onse amene Ali mbuli za sukulu
Koma guys MCP mwaipana machende😅
Ukanama bodza pofunika kukumbukira zomwe wanena apa MCP samakumbukira kuti Nkosi adatifotokozera kaye.
Ena azathawa 😂😂😂
Iwe ananakusakha kt ukhale mu comeet muja chifukwa chani iwe unatulukamo . lero ukuyankhula ngat wanzeru. Zonsezi iwe unakazifufuza Amalawi tiye tizikhala pa chilungamo
Chabalilie ukuvabwanji chakwela wakupusisatu
Eeee koma
Ayi zikomo kwambili namiwa koma tiyen tidekhe mulungu yekha atimenyela khondo
Mzopanda peke tinazivera kale
AMASAMBITSA MALIROWO ANALANDIRA CHILOLEZO CHA A CHIBALE KUTI ACHIPATALA AKHOZA KUYAMBA KUSAMBÌTSA MALIROWA?
Boma la mcp lapita😂😂
Zamphamvu
Kkkkkkkkkkkk koma guys
Tiwina big up bro
MCP muthawila kuti
After 4 hours really???
😂😂😂 Koma ndiokwiyadi
Yes❤❤❤❤❤❤