Manganya Wa sambwaza nose amene mukujama ya iye pomwe akugawa zinthu

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 6 ม.ค. 2025

ความคิดเห็น • 32

  • @MfipaKapwera
    @MfipaKapwera 2 วันที่ผ่านมา +1

    Watching from Limpopo RSA, i think it is necessary for Vice-president to go and distribute Maize, becouse it is the duty of Minister of Agriculture.

  • @ChrispinKashosha
    @ChrispinKashosha 2 วันที่ผ่านมา

    More fire usi asakugwetse mphwayi akufuna uzisiye kenako aziba Kuma gawana osauka asalandire

  • @FebbyPhiri-n7j
    @FebbyPhiri-n7j 2 วันที่ผ่านมา

    Kuimbira nyimbo za ulere koma malawi ayi dzikomo 😢

  • @FresherShaba
    @FresherShaba 2 วันที่ผ่านมา

    Congratulation vp you did good job 🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉

  • @patassonelucaszovuta3431
    @patassonelucaszovuta3431 2 วันที่ผ่านมา

    Kodi ku Malawi kulibe mabungwe oti angagawe zinthu zimenezi vp chilima adapitadi

  • @GeorgeTambala-j1m
    @GeorgeTambala-j1m 2 วันที่ผ่านมา

    Watching from Johannesburg in south Africa but from machinga olo mutatani mwalephera basi 16 September paulendo anthu olephera inu musapusise anthu akumuzi chifukwa cha umphawi what a shame

  • @INNOCENTMOFOLO-io8tg
    @INNOCENTMOFOLO-io8tg วันที่ผ่านมา

    azimayi nthawi zonse amakhala ofoila pachilichonse chomwe chikuoneka chatsogolo ndichani apa kukonda dzaulele ndingozi

  • @MadalitsoNdomondo-r8n
    @MadalitsoNdomondo-r8n 2 วันที่ผ่านมา

    Othandiza sadziyeneleza or kudziwonetsela coz zomwe dzanja la manja la mazele lisadziwe.ndiye mulungu awayendele ndikuwazindikilitsa choonadi.

  • @patassonelucaszovuta3431
    @patassonelucaszovuta3431 2 วันที่ผ่านมา

    Ndie pamenepo anthuo akudya zao kapena zolandila

  • @InnocentHassan-m3r
    @InnocentHassan-m3r 2 วันที่ผ่านมา

    Kuyamba kuwona VP kugawa zakudya Ku Malawi

  • @JamesMachunga
    @JamesMachunga 2 วันที่ผ่านมา

    Iweyo manganya usalakhule ngati zinthu ukupelekazo ndiza nyumba mwako wamva ndizamabungwe zimenezo

  • @HenryKatopola
    @HenryKatopola 2 วันที่ผ่านมา

    Kape manganya

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl 2 วันที่ผ่านมา

    Allah atimvele chisoni amalawi 😭😭😭😭😭😭

  • @MosesTangwe-q8o
    @MosesTangwe-q8o 2 วันที่ผ่านมา

    Akuona ngati anthu tingakopeke chifukwa cha chimanga kapena za dodmazo.akungobetsa

  • @kaphika
    @kaphika 2 วันที่ผ่านมา

    Kodi mtakanayo ndi wokwatiwa? Koma Dr. Usi

  • @NgomaRaheem-k2t
    @NgomaRaheem-k2t 2 วันที่ผ่านมา

    Naye Manganya uyu nde mchitsiru akuganiza ngat malawi alimtulo et

  • @ernestphiri5507
    @ernestphiri5507 2 วันที่ผ่านมา

    Mulungu muthandizeni munthu uyu siakudziwa chimene akuchita chimanga si chache

  • @AcctyhBuno
    @AcctyhBuno 2 วันที่ผ่านมา

    Apa wandinyansa manganya chimangacho wachitenga nyumba mwamako chimangachotu ndichogawilidwa chiti apasidwe amalawi komanso wogawa simanganya ndibungwe la dotima amalawi alelo samala nawoni muzalila musaone ngati sakudziwa uzakhumudwa manganya

  • @ManganiStanley
    @ManganiStanley 2 วันที่ผ่านมา +1

    Mphawi sizinthu mulungu atichitile chifundo

  • @KonzekaniMwamwituMwaungulu-q1h
    @KonzekaniMwamwituMwaungulu-q1h 2 วันที่ผ่านมา

    Zopempha kumatheranaso mawu kkk😂

  • @Hdsagdf-t1n
    @Hdsagdf-t1n 2 วันที่ผ่านมา

    Koma zopenphetsa zomwezi mpakana kumathela mau mmm

  • @jameskachulu8141
    @jameskachulu8141 2 วันที่ผ่านมา

    Sangasange

  • @MustaphaCassim-t7g
    @MustaphaCassim-t7g 2 วันที่ผ่านมา

    Shame off VP zooonadi tikhalile kuphempha zoona a usi

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 2 วันที่ผ่านมา

    Eyetu iwe galu kwabasi ndi mcp chimanga chopasidwa paka kumalemba mayina antu okuba ndalama bomamu iwe ndi mcp yakoyo muli sika chimanga chopasidwa kuchokela kudziko loti lilitso pankhondo uko iwe ulibechitsoni chimanga kumapangala chokopela anthu kuti avotele mcp anthu amagadzi.iwe wamitsaladi NJALA YABWELESA NOKHA CHIFUKWA CHA MCP YAKOYO KUBA NDIKUNDULITSA FETELEZA KUBA NDALAMA AMITSONKHO YA MALAWI INU DZISILU DZEDI

  • @zimmekapachika6784
    @zimmekapachika6784 2 วันที่ผ่านมา

    😅😅😅😅😅😅😂😂😂😂yomweyo manga 😅😅😅😅😅😅😂😂😂😂

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole 2 วันที่ผ่านมา

    Aaaaaa 😂😂

  • @MavutoNKhoma-pz7qb
    @MavutoNKhoma-pz7qb 2 วันที่ผ่านมา

    Munya manye bola mukulandila

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 2 วันที่ผ่านมา

    pachoka nzako Pali Malo,akuluwa akumva kulyolyopeka koma paja yatsala 8 eeeti

  • @MussaWilliam-q3l
    @MussaWilliam-q3l 2 วันที่ผ่านมา

    Chimangacho sichanu koma mwayamba kuyika ma postar ya mcp

  • @MsondaBanda
    @MsondaBanda 2 วันที่ผ่านมา

    Better to ask than to steal very good vp stealing it's bad

  • @RomeoLapken
    @RomeoLapken 2 วันที่ผ่านมา

    Ndiye iwe unayamba ku DODMA?