Za ugalu basi mwauze kuti kuno ku Ntcheu alipo azibambo awiri omwe anathawa last month pa 25 Dec ku ndende koma atumize anyamata a MCP kuti adzawatenge coz ndiye Zigawenga mudziko Muno...
Tiziwagwira imfe ngati ntchito yathu ndi ya police tizigawana salere yanuyo za ugaru yeti ngati wathawa wayenda ndi mimba yake basi simuli buys kulimbana ndi abakili muluzi TV
You have managed to create poverty in Malawi . MCP reaching the extent kupasa anthu maganizo oti azisaka akaidi kuti apeze thumba la chimanga bac aaaaa szoona anthu ali ndi zochita zambiri ku dzikoku A Malawi omwe takhuzidwa ndi izi mzeru poka voter zikhalapo ndi mapemphero this is my plea
Mwazindikila now kuti nyala yafika pachimake athawe kumene ngati nyalayo ili out of ndende what about inside ndende athawe kumene ogwilayo mupeza kuti mphamvu yogwilira kaidiyo ayipesa kuti MCP ndi boma la sisiludi
Boma loyendesedwa ndi zitsilu zokha zokha
Olo nditamuona sindinganeni ndipeleke munthu mavuto chifukwa chachimanga
Kkkkkk mpaka ukamuona kuthamangira kuti ukatenge chimanga koma tiphedwa ndithu
Kkkkkk njara yafikapo
Bwanawe kasongo
Chimanga ndi golide😂😂
Kundede kukusowa chakudya ndiye mungakhale ndichimanga chongawa kkkkk kuteloko tigomusiya athawe coz akaidi achuluka ku ndede zathu
Ine ndikagwila ndikufuna matumbo achakwela awole
Amene amatengeka ndi1000 zaugalu bs
Naeso ndi Muthu apulumuke
Amene angalore ndan zmenezo
Agalu omwewo iopawo ndamene angalole
Ineyo ndikangwila ndifuna mutu wa chakwela
Za ugalu basi mwauze kuti kuno ku Ntcheu alipo azibambo awiri omwe anathawa last month pa 25 Dec ku ndende koma atumize anyamata a MCP kuti adzawatenge coz ndiye Zigawenga mudziko Muno...
Kaidi apose chakwela ndazizake osamangidwa amenewo bwanji chakwela
Zopepela basi kachimanga nkachani nkaidi ndimunthu alindiufulu nayenso
Awuze a nyamata a zikwanje akamugwire nkaidiyo cause alibe chimanga ma nyumba mwawo
Tiziwagwira imfe ngati ntchito yathu ndi ya police tizigawana salere yanuyo za ugaru yeti ngati wathawa wayenda ndi mimba yake basi simuli buys kulimbana ndi abakili muluzi TV
Anthu oputsa amene akuthandiza ndiopenga ndiposo alipo amene amagwira ntchito imeneyo
MCP ikumasewera ndimoyo wa anthu mulungu akulangani
What is that now .
Aaaaaaaaaaa 😂😂😂😂😂 inu makape aboma
😂😂😂😂😂 Koma nkhan zake 😂😂😂😂😂
Koma aporisi akhuta chanikodi sindinga fere thumba rachimanga ayi
😂😂😂😂😂 abwampini awa inu chomwe aona ndi chimangacho aaa kulephera ndinthu ineyo akandipeza ndimponyera zovala asinthe ndi ndalama asweke zopusa et 😂😂😂😂
Sizabwino amwene akathawa wachitamwai
Kkkkkk boma lapanika
Akaidi omwe anathawa ku ndende ndi aja akumayenda ndi zikwanjewa ndiye bwanji apolice akumaleka kumawagwira kuti chimangacho azilandira iwowo bwanji
Inu a ku Boma zopusazo muzikapanga mnakwanu ndi azibale anu, sikuti Ngati Mdziko Muli Njala mufike powatola nawo Anthu Uchitsiru. Muzipase Ulemu
Omwe mumapeperesawo mkumakusekererani muzipanga ndi omweo.
You have managed to create poverty in Malawi . MCP reaching the extent kupasa anthu maganizo oti azisaka akaidi kuti apeze thumba la chimanga bac aaaaa szoona anthu ali ndi zochita zambiri ku dzikoku
A Malawi omwe takhuzidwa ndi izi mzeru poka voter zikhalapo ndi mapemphero this is my plea
Agalu inu ine sindingapange zimenezo mmalo mwake ndiziwathandiza
Malawi wake suyu , palibe angachite zimenezo zopusazo.
Kulephera kwa boma mapeto ake ndi amanewa kupanga mfundo zopusa
Aaa malipilo oputsa kkkk koma akayidi akuvutika ndi njala nsono chimanga ndechikhaela chopedzele kayidi Othawa aa malawi watha basi BOMA NDILOMWELI KOMA MCP KALAMULA KWANJI UKU KWA DZIKO ngati olondela ndende achepa ongolemba ena bwanji ndalama mwagulitsa nyanja dzija boma lamakape okha okha
Koma kubomako ngati mwatopa apaseni Ena ayendese zinthuzi mukuleka kugwila akubawa akuwonekawa ndiye munthu ukampeleke zako chifukwa cha thumba LA chimanga 😢😢😢
Chakwera police ndiyo foira kufanana ndi chakwera
Mbava yaikulu ndi chakwera choyamba tikamusiye chakwera ku ndende njala anachita kuipanga munthu mavuzi ndu kuthako ungakagule feteleza ku buchary
Ayambe kumenya ma deal ndi akaidi
Nzeru za anthu opanda nzeru😂
Mmmm
Zafika pa BATA system😂😂😂
Amugwira a mcp
Angapange ndani zombwambwanazo
Ine olo atakhala ten ndiwasiya zopusa mpata ukapezeka idyani mphazi 😂
😂😂 Mkaidi zake zinada atha kukupha ka😂
Ine ndamugwira mkaidi otchedwa Chakwera kuno
Zopusa dzeni dzen
😂
Kuli akaidi olemela kumeneko awa awa chose chito anenazi
Thumba la chimanga, osati 50kgs ya fertilizer?.
😆😆😆🙆🏾♂️.
Tumani anyamata anu azikwanje zautsiru
Zangotivuta basi Malawi
Mwazindikila now kuti nyala yafika pachimake athawe kumene ngati nyalayo ili out of ndende what about inside ndende athawe kumene ogwilayo mupeza kuti mphamvu yogwilira kaidiyo ayipesa kuti MCP ndi boma la sisiludi
Chaka chino ndimugwira chimwendo banda
😂😂😂😂😂Kwachemaaahhj
Koma guys 😅😅😅😅
😂😂😂😂 dzausilu
Kkkkk Kom mcp bc akuziwa kut CHIMANGA chimufunikad
Zoopsatu
😂😂😂😂😂😂 Koma mcp midzimu ikuwakunthadi
😂😂😂
Kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk mafuto kumarawi kom mbuzi zaandu
Dzopoyila 😂😂😂😂😂
😂😂😂
Foolish!