Zaululika Chimanga chija mpaka mwachitere? chachokera kuti kodi?

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 6 ม.ค. 2025

ความคิดเห็น • 89

  • @Maxielyies
    @Maxielyies วันที่ผ่านมา

    That's our pangolin, talking the truth, makape a MCP atikwana kwambiri ❤❤❤

  • @RoseMkandawire-e2g
    @RoseMkandawire-e2g 2 วันที่ผ่านมา +5

    Zazi inyani nokha chimanya chanu ifeso tikukanirani ngati mai uja anakanda ndarama uja

  • @PeterMakaika
    @PeterMakaika 2 วันที่ผ่านมา +6

    Awa ndi makape kwambr..mpaka thumba la chimanga kuli dinda 😂😂😂

  • @JohnPhiri-t2r
    @JohnPhiri-t2r 2 วันที่ผ่านมา +2

    Kusaukisa anthu ndikumabwera ndizinthandizo. Zopusa. Mmalawi siwopusa braza. 2025 tiziona. Uku ndikusazika😂😂😂😂😂

  • @MandalaChaona
    @MandalaChaona 2 วันที่ผ่านมา +1

    Koma Nyani ndi Nyani basi 😂😂😂😂 MCP hmmmm Inu ndi Afiti, komatu olo mutadinda pa Madzira tambala wanu wokudayo inu simukuwina ndipo simukulamuliranso.
    Dindani tambala yo ngakhale mma toilet koma mwatha a Mphyodza Magazi ndi mikodzo inu ana a Njoka.
    Weldone Bros Cliff Chinyama, Malawi ndi aliyense okhalamo

  • @LukeMapukusa
    @LukeMapukusa 2 วันที่ผ่านมา

    Makape amcp atitola zed chimanga chopasidwa kupangira kampen kulembapo chithyola wankhope ngat nyani 😂😂😂😂😂

  • @BrightZionga
    @BrightZionga 2 วันที่ผ่านมา

    Kkkkkk 🎉🎉🎉umatha big

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon วันที่ผ่านมา

    MUKALEMBA MAINA CHIMANGACHO MUKUONA NGATI TIKUVOTERANI MWAUPONDA 😅😅

  • @markanthony5402
    @markanthony5402 2 วันที่ผ่านมา +5

    Ndipo chimanga achitenga kuti awa akati kunyasa ngati manyi ang'ombe

  • @rashirdbanda8204
    @rashirdbanda8204 วันที่ผ่านมา

    Mumaitha big agalu amenewa alibe manyasi

  • @ChristinaMdeza
    @ChristinaMdeza 2 วันที่ผ่านมา

    Awuzen comrade wathu chilungamo cho we love you❤

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl 2 วันที่ผ่านมา +1

    Chimanga mpaka kulemba chithyola banda eeeeee koma mcp

  • @MartinNdimbwa-e1n
    @MartinNdimbwa-e1n 18 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kodi Inu zimene mukupangazi simukuziwa kuti a Malawi wozikila simungawanamize alipatali kaganizilidwe

  • @WysonChilonga
    @WysonChilonga 2 วันที่ผ่านมา

    zopusatu kwambiri,umbuli weniweni 😢😢😢,you mean mwagwiritsa ntchito ndalama zamthumba mwanu aaaa, nditukwanatu kwinako😢😢😢

  • @TysonMwenye
    @TysonMwenye 2 วันที่ผ่านมา

    Aaa koma anthu a mcp wa ngochimwitsa eti...mpaka pamenepa 😂😂

  • @MosesTangwe-q8o
    @MosesTangwe-q8o 2 วันที่ผ่านมา

    Strong enough comrade 💪 uyu ndipongolin

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 2 วันที่ผ่านมา +2

    Aaaa mcp sidzatheka basi awa galu kwabasi

  • @AgnessMakuluni
    @AgnessMakuluni 2 วันที่ผ่านมา +3

    Kalikonse tikaona😂chaka chake ndichino😂😂😂

    • @HandEllah
      @HandEllah 2 วันที่ผ่านมา

      😂😂😂

    • @TysonMwenye
      @TysonMwenye 2 วันที่ผ่านมา

      Komatu ngakhale kamene kali kupansi kwabedi ife tikaonabe 😂😂

  • @andrewmbilinte4589
    @andrewmbilinte4589 2 วันที่ผ่านมา

    Nde bwanji chimangacho sanabweletse Ku nyumba kwako kuti ukachigawe

  • @ajasikalonga3210
    @ajasikalonga3210 2 วันที่ผ่านมา

    Komanso a Chithyola ndinu mbudzi basi.Mpaka kulemba dzina lanu mlo,mbuli

  • @DavidPeter-e2o
    @DavidPeter-e2o วันที่ผ่านมา

    Zitsilu zenizeni

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole 2 วันที่ผ่านมา +1

    Ku mcp kunadzadza ma bulutu kulibeko opangako zazeru onse manyaka amalawi si ife opusatu.

  • @davidkadyakapita8836
    @davidkadyakapita8836 2 วันที่ผ่านมา

    MCP kwachuruka dzitsiru kwambiri

  • @lulamileseptember2181
    @lulamileseptember2181 วันที่ผ่านมา

    Palibe chomwe ukuziwa galu iwe . utifunse ife omwe tikuziwa

  • @andrewmbilinte4589
    @andrewmbilinte4589 2 วันที่ผ่านมา

    Wamisala iweeeee 😂 anakugulira foniyo analakwitsa.

    • @BrightZionga
      @BrightZionga 2 วันที่ผ่านมา

      Mmmmm 👿

    • @AlfredNazombe-me2ly
      @AlfredNazombe-me2ly วันที่ผ่านมา

      Iwenso mbuli siuziwanso kanthu pali iwepo uona ngat kuvala pampasi eti kkk

  • @ENOKMAKONDI
    @ENOKMAKONDI 2 วันที่ผ่านมา +3

    If achina chithyola banda ali ndi chimanga chomagawa afufuzidweso kuti chuma chimenecho anachipeza bwanji mene akumupangira triphonia mpinganjira muja tidziwe nawo because ameneuja or ali pa ndalama amaoneka ngati owotcha makala

    • @BeatriceMitayi-wt3js
      @BeatriceMitayi-wt3js 2 วันที่ผ่านมา

      Chithyola analimatu atakolora muja analimanso chothilira

  • @OssmanAbubaker-v7t
    @OssmanAbubaker-v7t 2 วันที่ผ่านมา

    Zoonadi brother Cliff chilungamo. Osaopa osafooka osatopa

  • @JanePhiri-q8n
    @JanePhiri-q8n 2 วันที่ผ่านมา

    Eeee Koma lero abale chimanga cholandilaxhi eeeeaa ayi

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg วันที่ผ่านมา

    Komaso amene akuwapasa ndalama awa a MCP ndi dzisilu akunjao

  • @StevenJana-m2e
    @StevenJana-m2e 2 วันที่ผ่านมา

    Zoona big,akuwonjeza koma anthuwa

  • @MathewsJanuary
    @MathewsJanuary 2 วันที่ผ่านมา

    Malawi siopusa ngati wadzana uja iwe umazitcha kuti chithyoa uli chidula take note.

  • @hamiltonsolomon3756
    @hamiltonsolomon3756 2 วันที่ผ่านมา

    Koma Chikangawa 😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @AnnieJumaNaitanda-qj1iz
    @AnnieJumaNaitanda-qj1iz 2 วันที่ผ่านมา

    Mhhhh zovuta

  • @GraceLimani-zw7dx
    @GraceLimani-zw7dx 2 วันที่ผ่านมา +2

    Koma anthu ena nzeru alibe agundika kulemba dzina pa chimanga cha dodma

  • @FrancisNyayi
    @FrancisNyayi 2 วันที่ผ่านมา

    Nde akwezera dara ma bundle zaziiii

  • @JJ-in-the-hut
    @JJ-in-the-hut 2 วันที่ผ่านมา

    Koma simmaesa AChakwera sbali m'buss? Zinazi sangawazuzule minister awowo kuti asamawanamize wanthu, why are they deceiving the people?

  • @MaxwellChaminju
    @MaxwellChaminju 2 วันที่ผ่านมา

    Agalu amenewa akuona ngati kuti zimene kuchita sitikuzidziwa

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza 2 วันที่ผ่านมา

    Awuze chilungamo baba we love you long live cliff❤❤

  • @FulumensioTembo
    @FulumensioTembo 2 วันที่ผ่านมา +1

    Ulibwino bola chilungamocho

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon วันที่ผ่านมา

    UWU NDI UCHITSIRU MPAKA CHOMANGA KUCHIREMBA DZINA ? UWU NDI USAVEGE WENI WENI

  • @thomphalavi5027
    @thomphalavi5027 2 วันที่ผ่านมา

    Kod mukufuna vote kapena kapena mukugawa ndi mtima othandiza nanga munthu chikamuthera abweletso adzatenge china

  • @JulioChiwalo-t4f
    @JulioChiwalo-t4f วันที่ผ่านมา

    Kuyalukatu uku 2025 September muchoka basi mu fune musafune

  • @ENOCKSEVISON
    @ENOCKSEVISON วันที่ผ่านมา

    Ngakhare nthawi ya DPP ndi zo mwezo

  • @NgomaRaheem-k2t
    @NgomaRaheem-k2t 2 วันที่ผ่านมา

    Ndipo live Tonse ndi amalawi osaopsezanadi

  • @JustinMakoka
    @JustinMakoka 2 วันที่ผ่านมา

    Amdala bambo kuima pa chilungamo

  • @stevenmwamadi3035
    @stevenmwamadi3035 2 วันที่ผ่านมา

    Onse a mcp ndi ma carward mbuzi zawathu zasatanic nzeru ziribe

  • @WarriorKB-l3i
    @WarriorKB-l3i 2 วันที่ผ่านมา

    Aaaah kodi uyu akuti cithyola nkhope ili mbuu! Kuba cibeleni koma akungotuwabe, nkhope ngati bwampini mwamkumba kuti uyu? Mcp inuo ndi makap e cimanga ici mwalima sinu mukumpusisa ndani? Olo mucilembe mayina anu ndi cipani canu ife tikudziwa kuti sicanu inu canu ciliconse ndicolephela, musataye nthawi ndikampeni a malawi akudziwa kuti inu mwalephela caka cino wakukasiya cithyolayi amakumba mbewa, akapitilize kukumba a bwampini acewo mbuzi za anthu inu.

    • @WysonChilonga
      @WysonChilonga 2 วันที่ผ่านมา

      hahaha 😂😂😂,mpaka bwampini😂😂

    • @WarriorKB-l3i
      @WarriorKB-l3i 2 วันที่ผ่านมา

      @WysonChilonga kkkk eya ka nyau zosasamba za kukasiya izi aise taonela nkhopezi

  • @BORNFACESIMBOTA
    @BORNFACESIMBOTA 2 วันที่ผ่านมา

    Mcp makape hvy yoh

  • @McDonaldbeketeNkhata-n4l
    @McDonaldbeketeNkhata-n4l 2 วันที่ผ่านมา

    Boma likanakara ndi chimanga bwezi mu adimaric mukupezeka chimanga
    Achithyola banda ndi akuba chimanga cha dotima

  • @JudithSadi
    @JudithSadi 2 วันที่ผ่านมา

    You are right

  • @patrickMakhumba-yc7rb
    @patrickMakhumba-yc7rb 2 วันที่ผ่านมา +1

    Kodi analimakuti awa!!! Akugona ngati ndife mbuli

  • @MathewKalinkhu
    @MathewKalinkhu 2 วันที่ผ่านมา

    Yeah, wawamaliza

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz 2 วันที่ผ่านมา

    Yes yes ndizitsiru zimenezi zopusa

  • @PetroLosan
    @PetroLosan 2 วันที่ผ่านมา

    Agalu awa azazivotela okha

  • @AdamJames-x7x
    @AdamJames-x7x 2 วันที่ผ่านมา

    chithyola khope ngati manyi pamtumbo pako ukulemba matumba a chimanga ngati chimangacho ndi chako , machende Ako. uchotse dzina lako pa matumba a chimanga po, ukuziona ngati ndiwe ochenjera pamtumbo pako .

  • @TauraiTsaka
    @TauraiTsaka 2 วันที่ผ่านมา

    Auze

  • @MussaRafael-d4q
    @MussaRafael-d4q 2 วันที่ผ่านมา

    Aaaaa koma abale mcp 😂😂😂😂

  • @peterkakhome6976
    @peterkakhome6976 2 วันที่ผ่านมา

    Chimanga chochokela ku Ukraine 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂

    • @henryphiri6100
      @henryphiri6100 2 วันที่ผ่านมา +1

      Chopempha Joice Banda ku Ukraine pano Chithyola Maize

  • @YusufLiffah
    @YusufLiffah 2 วันที่ผ่านมา

    😂😂😂😂😂😂 Munthu kunvutika ndikusexa nthumba la 60 kg lija kodi zotere

  • @JackMvura
    @JackMvura 2 วันที่ผ่านมา

    Iweyo chipani chako chagawa chani mbuzi Kadett

  • @McshonWilliam
    @McshonWilliam 2 วันที่ผ่านมา

    Kunkuyu alikut ndi nzake chimwendo pajatu amati ndiboza lakunguniza izi zikutanthauza chan mcp koma yatitola kwabas

  • @lucianogeoffrey4275
    @lucianogeoffrey4275 2 วันที่ผ่านมา

    Anuake chanel mukumadula ma video pakati why?

  • @ConnexKhomba
    @ConnexKhomba 2 วันที่ผ่านมา

    Manyi awa chimanga angachinye kut awa

  • @Hambalisphiri
    @Hambalisphiri 2 วันที่ผ่านมา

    Ka Gulu ka mcp ka pumphapuphatu kkkkkkk

  • @DavieDulani
    @DavieDulani 2 วันที่ผ่านมา

    Big Big time nayo

  • @KhirChisale
    @KhirChisale 2 วันที่ผ่านมา

    Koma guys mmmm

  • @ThembaniJikah
    @ThembaniJikah 2 วันที่ผ่านมา

    zophusA

  • @IsabelLuka-i8f
    @IsabelLuka-i8f 2 วันที่ผ่านมา

    😂😂😂😂😂😂😂

  • @edsonnyasulu5394
    @edsonnyasulu5394 2 วันที่ผ่านมา

    Kkkkkk

  • @AliNtolera
    @AliNtolera วันที่ผ่านมา

    Kkkkkkkk

  • @catherinekadwala3839
    @catherinekadwala3839 2 วันที่ผ่านมา

    Boma ili ayi Ambuye atithandize September ikubwerayi

  • @Maxwellmsowoya-i4x
    @Maxwellmsowoya-i4x 2 วันที่ผ่านมา

    😂😂😂

  • @Kenmoney-xp7tz
    @Kenmoney-xp7tz 2 วันที่ผ่านมา

    Amalawi ninu anthu opusa zitselekwete mbutuma

    • @WysonChilonga
      @WysonChilonga 2 วันที่ผ่านมา

      aaa bwanjinso,a Malawi kapena MCP?

    • @WysonChilonga
      @WysonChilonga 2 วันที่ผ่านมา

      aaa bwanjinso,a Malawi kapena MCP?

  • @rashirdbanda8204
    @rashirdbanda8204 วันที่ผ่านมา

    Mumaitha big agalu amenewa alibe manyasi

  • @rashirdbanda8204
    @rashirdbanda8204 วันที่ผ่านมา

    Mumaitha big agalu amenewa alibe manyasi