Sameer Suleiman akuti ngakhale akufuna kutipha koma tiwachotse a Chakwera

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 6 ม.ค. 2025

ความคิดเห็น •

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl 6 วันที่ผ่านมา +2

    Sulemana ndi katundu womanga ndi mawaya God bless sulemana 🙏🙏🙏🙏🙏🙏

  • @WachiyawoWangalusa
    @WachiyawoWangalusa 6 วันที่ผ่านมา +1

    Soleimana.keep.going.

  • @YvonneZekka
    @YvonneZekka 6 วันที่ผ่านมา +1

    Your not alone Suleman 🎉🎉🎉 don't be afraid ndi boma lopanda nzeru yo iTunes isafune ichoka posachedwapa imeneyo ndipo iyambe kupakila now is 2025 amaona ngati chaka chili kutali

  • @MemoryMteketi
    @MemoryMteketi 5 วันที่ผ่านมา

    Dpp. Woyeeeeee chakwera wakhawura

  • @MayesoCave
    @MayesoCave 6 วันที่ผ่านมา +2

    Akudyelela pa Malo pake Ku Cape Maclear.... Amatha zithu

  • @blessingslikagwa823
    @blessingslikagwa823 6 วันที่ผ่านมา +2

    Happy new year Malawian Cameras 😅🎊

  • @jackalview7491
    @jackalview7491 6 วันที่ผ่านมา +1

    Yes big boys are in Dpp

  • @goodwellnyirenda651
    @goodwellnyirenda651 6 วันที่ผ่านมา +2

    Koma tikudikila chani chikangawa achosedwe before September

  • @paulpaseli6310
    @paulpaseli6310 6 วันที่ผ่านมา +1

    Koma kuti tikhale ndachakwela 5 yrs ina eee tifadi.

  • @AndersonBishop-i2t
    @AndersonBishop-i2t 6 วันที่ผ่านมา +1

    Ife tagona pa flingstation km mafutawo osawapezaso 😂😂😂

  • @DouglasDazuKamwendo
    @DouglasDazuKamwendo 6 วันที่ผ่านมา

    Mwaona ma comment a 2025 amene akubwelera pa Malawian Cameras 📸 oho musamaletu madolo osamangotsuysa zilizonse ayi pena kumavomereza.

  • @gracetjomane-jj3ib
    @gracetjomane-jj3ib 6 วันที่ผ่านมา

    Koma guys suleman atamusiyila adadi u president bwanji,,kabambe uja nkuzakhala wachiwili bwanji

  • @FrankMakulumiza
    @FrankMakulumiza 3 วันที่ผ่านมา

    Katundu auzile mayeso

  • @goodwellnyirenda651
    @goodwellnyirenda651 6 วันที่ผ่านมา +1

    Tisazave kuti MCP yawina zikoli tizawotcha moto

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg 6 วันที่ผ่านมา

    Vuto chakwera akumwa kwambiri gondolosi akuyenda ototatota

  • @FrankMakulumiza
    @FrankMakulumiza 3 วันที่ผ่านมา

    Suleman palibe angakupheni mulungu salora. Komanso kulimbana ndi anthu kulimbana ndi mulungu.

  • @ahmedmsume1489
    @ahmedmsume1489 6 วันที่ผ่านมา +1

    Koma kuli ma beeef😂😂😂😂

  • @OssmanAbubaker-v7t
    @OssmanAbubaker-v7t 6 วันที่ผ่านมา +1

    Sulemana ndi wa look sharp ndipo amakonda ife A Malawi