List ya Nyawani ya nduna za tsopano mwaiona? mukuganiza bwanji 😂😂😂 zili umu onerani mpaka kumapeto.

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 6 ม.ค. 2025

ความคิดเห็น • 132

  • @crosbeygondwe5403
    @crosbeygondwe5403 5 วันที่ผ่านมา

    😂😂😂😂😂 Zikhale

  • @MzadziWanga
    @MzadziWanga 6 วันที่ผ่านมา +14

    İ think chakwera wabalalika mmutu sizikuyenda, vuto plan yopha chilima cabinet yonse inakhudzidwa mmapangira limodzi ma upo lero ndi izi mulepera kupanga ziganizo zolondora mukuopa kuwachosa Kt angakuikeni poyera😅

  • @DangerYaokingYaoking-m3c
    @DangerYaokingYaoking-m3c 6 วันที่ผ่านมา +13

    Wachedwa kwa kwambiri

  • @JamesPhiri-h7p
    @JamesPhiri-h7p 6 วันที่ผ่านมา +11

    Awa zao zada bas okupha chilima

  • @MakabaBauleni-c2i
    @MakabaBauleni-c2i 6 วันที่ผ่านมา +8

    Paja nduna zonsezi sangazichotsetu cifukwa onsewa adatengapo mbari pa imfa ya Chilima nde kuwachotsa amaopa kt wina angaambe kuulura ndi chifukwa chake kamajekete angomutsintha position kma sizoti angamucotse ai ,ndipo dziwani kt anthu boma likazasintha ena mwa nduna zilipanozi azathawa dziko muno cz azakhla akudziwa kt palibe azawateteze

  • @ibrahimJasten
    @ibrahimJasten 5 วันที่ผ่านมา +2

    Kkkkk kumati asitha chani pamenepo kkkk😂😂😂😂 mutu siikugwila chakwela ndithu

  • @emmanuelkapelula6142
    @emmanuelkapelula6142 5 วันที่ผ่านมา

    🤣😂kamajekete kwake kwatha amenei

  • @HarrisonMwanga-xy4sc
    @HarrisonMwanga-xy4sc 5 วันที่ผ่านมา

    Wow 😂😂😂😂😂.wawona nyenkhwe basi eee

  • @Lizzie-h1k
    @Lizzie-h1k 5 วันที่ผ่านมา

    Aaaaa...palibe chasintha pamenepa

  • @Lizzie-h1k
    @Lizzie-h1k 5 วันที่ผ่านมา

    Koma Chakwera akupenga...bwanji osangoti akuchotsa Zikhake

  • @LukeMapukusa
    @LukeMapukusa 6 วันที่ผ่านมา +5

    😂😂😂😂 chakwera wasintha chani apapa ugaru wake ndthu

  • @Extratremendouszeus
    @Extratremendouszeus 6 วันที่ผ่านมา +11

    Manyaka okhaokha...mumuuze mowa wa pa Christmas wamupweteka chikangawa

    • @VeronicaChirwa-ct4os
      @VeronicaChirwa-ct4os 6 วันที่ผ่านมา +2

      Mbwerera zokha-zokha palibe chomwe chingasinthe

  • @RonnMtafya
    @RonnMtafya 5 วันที่ผ่านมา +7

    With our economic Crisis he better had reduced cabinet by Half and use only Principal Secretaries.The country is poor for such booted economy.

    • @henryphiri6100
      @henryphiri6100 5 วันที่ผ่านมา

      Zigawenga zonsezi ati ma minister, dziko lathu lokhoza kuyenda ndi nduna 10 koma opanda deputy ministers. Kugwiritsa ntchito ma principal secretary. Zoona

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl 6 วันที่ผ่านมา +4

    😂😂😂😂😂😂 Kumalawi kuli mavuto

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 6 วันที่ผ่านมา +5

    Chenji golo wauponda anayesa kunama kuti ndimchewa

    • @Betty-fe9ql
      @Betty-fe9ql 5 วันที่ผ่านมา

      😂😂😂

  • @FytonRichard-t3w
    @FytonRichard-t3w 2 วันที่ผ่านมา

    Kkkk chimwendoso anakamuchosa

  • @AlexKaunda-w7l
    @AlexKaunda-w7l 5 วันที่ผ่านมา

    Pambuyo pake

  • @ChristopherJohn-u5i
    @ChristopherJohn-u5i 5 วันที่ผ่านมา

    Tikufuna black box chonde

  • @JamesChiphazi
    @JamesChiphazi 5 วันที่ผ่านมา

    sikuona kukula pali ena akulu kwambili komaao opanda zelu nde ndizimenezi olo anakasiya osasakha chimozi mozi

  • @IssacMateyo
    @IssacMateyo 3 วันที่ผ่านมา

    Osachotsaso chitholayo bwanji galu chakwela kwambili

  • @NgeyasjuWadeya
    @NgeyasjuWadeya 5 วันที่ผ่านมา

    Zopusa zenizeni

  • @Mustapher-fb4qp
    @Mustapher-fb4qp 5 วันที่ผ่านมา

    Mbava zokha zokha

  • @NgeyasjuWadeya
    @NgeyasjuWadeya 5 วันที่ผ่านมา

    Tindalama tochepachepa koma nduna mpwiiii zachani?? Mukamamva kuti kusowa kwautsogoleri timanena zimenezi palibepo Cha new apa

  • @BwanaliMtwiche
    @BwanaliMtwiche 6 วันที่ผ่านมา +1

    Sanasite Awa

  • @ArnoldSefasi
    @ArnoldSefasi 5 วันที่ผ่านมา

    Kkkk sindikuonapo kusintha ,kusintha adakamusintha chimendo banda ,munthu mmodzi maudindo 3,sg,leader of opposition,local government.ayi ndithu palibe kusintha

  • @paulpaseli6310
    @paulpaseli6310 5 วันที่ผ่านมา

    Nane kuwona palibe chasita chiyakale yomweyiija. Koma tiziwavesa zomwe anapaka kuchikangaka zinja sangamachosane chifukwa kugokuchosa eeee utha kuulula😂😂😂

  • @JulioChiwalo-t4f
    @JulioChiwalo-t4f 5 วันที่ผ่านมา

    Idyani ndalama za a Malawi za misonkho miyezi 8 yatsalayi kenako tiuyambe otuluka mboma

  • @AbdulsharifulKalipinde-m6u
    @AbdulsharifulKalipinde-m6u 3 วันที่ผ่านมา

    Agulukunyenda amenewa opanda mwayi
    Pakuti akuchoka mu September mu ndiye tilibe nawo ntchito

  • @Jafari-s3c
    @Jafari-s3c 6 วันที่ผ่านมา +4

    Palibe chomwe chasintha

  • @DumiMhango
    @DumiMhango 6 วันที่ผ่านมา +3

    Kamajekete wapita😂😂😂

  • @chirwaellace1093
    @chirwaellace1093 6 วันที่ผ่านมา +2

    Aaaa nde angochotsa akamajekete nde asinthapo chani za ziiiiiiii

  • @Givenjnr
    @Givenjnr 6 วันที่ผ่านมา +3

    Umakwana

  • @TiyamikeSibale
    @TiyamikeSibale 4 วันที่ผ่านมา

    Palibepo ndaona kusitha apa wabalalika galu uyu

  • @AbrahamGaluwapananji-vj7mj
    @AbrahamGaluwapananji-vj7mj 5 วันที่ผ่านมา

    Chayanganamuno....walowa Malo mwa Harry Mkandawire.....
    Komabe it's a Central Region dominance

  • @FundoGama-c9y
    @FundoGama-c9y 5 วันที่ผ่านมา

    Chakwera wabalalika ndinthu 😂😂😂😂😂😂😂

  • @CharlesJames-f1w
    @CharlesJames-f1w 6 วันที่ผ่านมา +2

    Sanasinde

  • @maviekuwili378
    @maviekuwili378 6 วันที่ผ่านมา +3

    😂😂😂zikhale ng'oma zawavuta😂😂😂😂

  • @MathewsMpanga
    @MathewsMpanga 5 วันที่ผ่านมา

    Palibepo Cha nzeru apa.Pali ena omwe alibe kuthekera kokhala nduna.

  • @ChisomoSaiti
    @ChisomoSaiti 5 วันที่ผ่านมา

    Nanga makaka Ali Kut

  • @ManganiStanley
    @ManganiStanley 6 วันที่ผ่านมา +3

    Mwasinthapo cani pamenepo

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 5 วันที่ผ่านมา

    Zero pa 10

  • @DumiMhango
    @DumiMhango 6 วันที่ผ่านมา +1

    Mwachedwa

  • @HandEllah
    @HandEllah 6 วันที่ผ่านมา +3

    😂😂 Guys list iyiyi ndiyamanyi asinthapo chan apapa😂😂😂

  • @sparkdymon3429
    @sparkdymon3429 5 วันที่ผ่านมา

    Hhhhh palibe kusitha apa manyazi basi kuopa kuwulula za ifa yachilima koma tilinanu ndipo achakwela chisilu chamuthu

  • @giftbanda7690
    @giftbanda7690 6 วันที่ผ่านมา +2

    Kamajekete aona kuti asangochosa opanda kumalowesa Salary... Koma akhale Kaye Ku mining Ku potengela Miyezi yasalayi basi apakule komaliza

  • @fredgabrielnyangulu
    @fredgabrielnyangulu 6 วันที่ผ่านมา +2

    Koma iyi ndie Mbuzi ya munthu basi reshuffle yanji iyi opanda woti ntchito yake yatha ndipo bola anakapanda kupanga zomwe wapangazi kuti onse mu September muno azipita coz munthu sungangosintha unduna umodzi ai kuchoka kum ministry defence force ndikupita ku ministry of mining ndie tiziti chani koma uyu ndie ndikapolo wa president basi kuteroko azimzake amunamiza choncho koma guys ngati sitisintha utsogolere ndithu tikhala pa mavuto azawoneni coz izi sizowona ai

  • @JulietKapata
    @JulietKapata 5 วันที่ผ่านมา

    Zopanda ntchito

  • @MaxonKambazithe
    @MaxonKambazithe 5 วันที่ผ่านมา

    Adye komaliza panyo pawo sawinaso aiiiiiiiii

  • @EDSONMahamand-v2z
    @EDSONMahamand-v2z 6 วันที่ผ่านมา +2

    Boza lokhalokha achakwela

  • @KhadijaMsosa-d7z
    @KhadijaMsosa-d7z 6 วันที่ผ่านมา +1

    Eee kaya tsopano ubwino wake nduna zoyambazo sindizidziwanso😂

  • @AdamKay-q1l
    @AdamKay-q1l 6 วันที่ผ่านมา +2

    Galu ndi galu aguluku nyinda amenewa out 2025

  • @Halima-i4x
    @Halima-i4x 6 วันที่ผ่านมา +1

    😂😂😂😂😂😂 Kom zina ukamva

  • @MarySinjirani
    @MarySinjirani 6 วันที่ผ่านมา +2

    Ndiye wasinthapo chani apa chakwela

  • @edsonnyasulu5394
    @edsonnyasulu5394 5 วันที่ผ่านมา

    Kkkk koma lazalo ndiwamadrama

  • @MsomaraphaelMbewe
    @MsomaraphaelMbewe 6 วันที่ผ่านมา +2

    Kkkkk km pali kusitha apa kd mwina ndine buli

    • @VeronicaChirwa-ct4os
      @VeronicaChirwa-ct4os 6 วันที่ผ่านมา

      Ayinso sikuti ndinu mbuli ayi koma ndi momwemo palibe kusintha

  • @SamuelLimban
    @SamuelLimban 5 วันที่ผ่านมา +1

    Zikhale eeee sorry sorry wanya basi zikhale 😅😅😅😅😅😅😅

  • @rashidadan2533
    @rashidadan2533 5 วันที่ผ่านมา

    It's too late , vuto ndiloti mavuto omwe tikukomana nawo sangathe miyezi yasalai ,
    Zakanika kuthetsa mavuto 4 years

  • @Mrnaumi-bz4os
    @Mrnaumi-bz4os 6 วันที่ผ่านมา +2

    Palibe chimene ndasintha chilichose

  • @ChifundoNinje
    @ChifundoNinje 6 วันที่ผ่านมา +2

    Kamajekete wapita

  • @darlingtonkamanga4858
    @darlingtonkamanga4858 6 วันที่ผ่านมา +2

    Mwachotsa
    Zikhale Ng'oma Bakili Muluzi TV sizikomatu

    • @JJ-in-the-hut
      @JJ-in-the-hut 5 วันที่ผ่านมา +1

      Sanamchose, angomusintha udindo kunkhala minister of mines.
      Harry Nkandawire yache yaumapo

  • @Malekano-k3x
    @Malekano-k3x 6 วันที่ผ่านมา +1

    Mwasitha chiyani tsono

  • @WarriorKB-l3i
    @WarriorKB-l3i 6 วันที่ผ่านมา +1

    Inu idzidzi wangotaya nthawi nkhani ili pano ndi ya feteleza, mafuta, cakudya, kobili dzinthu zimenezi zili kuti? Dzosintha ma unduna tilibe nazo ntchito chifukwa sidzisintha kanthu dza chikape zongofuna kutipusisa. Mcp nthawi yanu yatha basi pachilani chifukwa APM ndiyemwe timvotele .

  • @MathewsMakina-z6n
    @MathewsMakina-z6n 5 วันที่ผ่านมา

    Akanango siya palibepo chosinthika apa mbava zomwezo zikungoba

  • @LennieNyirenda-w6p
    @LennieNyirenda-w6p 5 วันที่ผ่านมา

    😂😂😂😂 kma kamajekete😂😂😂😂😂

  • @PaulPhiri-c5u
    @PaulPhiri-c5u 5 วันที่ผ่านมา

    Palibe kusintha apo anakangosiya mmene inalilikare

  • @PempheroMoleni
    @PempheroMoleni 6 วันที่ผ่านมา +2

    Zikhala ng'oma zavuta😂😂😂😂

  • @HusseinMoffatt-mi1fl
    @HusseinMoffatt-mi1fl 5 วันที่ผ่านมา

    Ayikapo nkholo zokhazokha

  • @Isaacdimu
    @Isaacdimu 6 วันที่ผ่านมา +1

    Palibe chomwe asinda galuyu mboloyake chakwela kungowapusitsa anthu basi

  • @ChipililoMaganga
    @ChipililoMaganga 5 วันที่ผ่านมา

    Thaw yoseyi anali kwani kufuna kwaphimba amalawi maso mudya Zakutani kale inu

  • @PhilmonNamaja
    @PhilmonNamaja 5 วันที่ผ่านมา

    Akanangoti ndasintha zikhale ng'oma kumupitisa ministry ina. Simple

  • @ElizabethMaononga
    @ElizabethMaononga 6 วันที่ผ่านมา +1

    Chizungu muzichomvetsa bwino.wanena momveka bwino kuti psli kusintha pang ono aliyense akhale pomwe angathe kutumikira bwino.Anthu timathamanga magazo kwambiri

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 6 วันที่ผ่านมา +1

    Achewa okhaokha

  • @DumiMhango
    @DumiMhango 6 วันที่ผ่านมา +2

    Satana nthawi ikamuthera amabalalika wakumotobasi

  • @edsonnyasulu5394
    @edsonnyasulu5394 5 วันที่ผ่านมา

    Kamajekete amuika ku migodi kuti azibela limozi basi palibe kusintha apa kabwila amamuika pa nyalonje basi

  • @edsonnyasulu5394
    @edsonnyasulu5394 5 วันที่ผ่านมา

    Apa amafuna kumuthothola kamajekete basi

  • @AlivetaFanizo
    @AlivetaFanizo 5 วันที่ผ่านมา

    Ndiomwe aja alib mzelu awa

  • @VitumbikoKaunga
    @VitumbikoKaunga 6 วันที่ผ่านมา +1

    Kunamiza anthu kumeneko

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole 6 วันที่ผ่านมา +2

    Chakwera uyu 🥚🥚 aphike akazake sure.

  • @BlessingsChitekwe-k5z
    @BlessingsChitekwe-k5z 5 วันที่ผ่านมา

    Kkkkkkkkkkkkk 🤣😅

  • @gospelmcandawire2817
    @gospelmcandawire2817 5 วันที่ผ่านมา

    Kkk aiyi ching'oma China😂🤣

  • @PatriciaFostino
    @PatriciaFostino 5 วันที่ผ่านมา

    Chake ndi mbudzi ya Muthu pamenepo mkumat wasitha Chan 😂😂😂 akuopa azakewo kut akachosa aing'alula kut anapha chilima kkkkkkkkk ine pheee 2025 akuchoka bas

  • @felixjoseph8161
    @felixjoseph8161 5 วันที่ผ่านมา

    Palibe chasinthika apa mbole yako chakwera wangotitayitsa nthawi kumvetsera Za kunyini ngati zimenezi

  • @JamesSaiti-h1l
    @JamesSaiti-h1l 5 วันที่ผ่านมา

    Asithapo chani apa kungotiputsitsa basi

  • @charleskhomolina2385
    @charleskhomolina2385 5 วันที่ผ่านมา

    Palibe chasinthapo apa

  • @AbrahamGaluwapananji-vj7mj
    @AbrahamGaluwapananji-vj7mj 5 วันที่ผ่านมา

    Appeasement Cabinet....same PPO though moved around....maybe Kabwira... for appeasement....
    Generally it's not ticking.....
    No wonder listening to the presidents speech...it was nothing but just empty. Anthu awa sangatayane....joker mistake ndi Chikangawa....sangasiye munthu kunja....ziululika....

  • @AndersonBishop-i2t
    @AndersonBishop-i2t 6 วันที่ผ่านมา +2

    Za chamba basi pamenepo asintha zichani chakwera nyeteteyako

  • @HusseinMoffatt-mi1fl
    @HusseinMoffatt-mi1fl 5 วันที่ผ่านมา

    Ndiomweaja akubaokhaokha zamanyitu basi

  • @RajabAssan
    @RajabAssan 5 วันที่ผ่านมา

    Palibe chimne asnthapo apa

  • @AaliyaKalembo
    @AaliyaKalembo 5 วันที่ผ่านมา

    😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @InnocentnMbale-zq8pk
    @InnocentnMbale-zq8pk 5 วันที่ผ่านมา

    Comanda kulephera kupanga command kukasaka ndege

  • @ZivanaiGwatura
    @ZivanaiGwatura 6 วันที่ผ่านมา +1

    Same pple ka palibe kusintha

  • @henryphiri6100
    @henryphiri6100 5 วันที่ผ่านมา

    Zigawenga club. Kufuna kuphiphilitsa za imfa ya Chilima

  • @HusseinMoffatt-mi1fl
    @HusseinMoffatt-mi1fl 5 วันที่ผ่านมา

    Zikungo banana ndi manyiokhaokha

  • @AdamJames-x7x
    @AdamJames-x7x 6 วันที่ผ่านมา

    Kusitha kuri patipo ?kkkkkkkk chakwera pamtumbo pako wava nkhope kunyasa ngati konyerera, udapha chilima iweeeee mwana osalakwa

  • @MisheckAselo
    @MisheckAselo 6 วันที่ผ่านมา +1

    Apa ndiye ngati asintha mkomwe zikhale ng'oma ekhayi ndiamene wasintha position basi

  • @ExcitedBreakingWaves-oh3zb
    @ExcitedBreakingWaves-oh3zb 5 วันที่ผ่านมา

    Zachibwana zokha zokha basi.timuchotse basi chikangawayo chaka chino.Dpp boma 2025.

  • @MuhammadBAKILI-kl2mj
    @MuhammadBAKILI-kl2mj 5 วันที่ผ่านมา

    Asakhana achwwa wokhawokha

  • @AngellachifundoMwale
    @AngellachifundoMwale 6 วันที่ผ่านมา

    Big up mr pulezident😮

    • @Extratremendouszeus
      @Extratremendouszeus 6 วันที่ผ่านมา

      Azikwanje ..kubisala mmbatata?

    • @bridgetmajor3646
      @bridgetmajor3646 6 วันที่ผ่านมา

      Palibe chomwe wapanga iya.....chimwendoyo nangano 😅😅😅😅

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani 5 วันที่ผ่านมา

    Sndinapite kusukul ine ndye sndikumvesatu znthuz apa pliz Bakili Muluzi TV where r u now tiuze chomwe chachitika apa idont understand pliz broh

  • @Shem2
    @Shem2 6 วันที่ผ่านมา +2

    Mumba alipo?