Good Man ngumbuteni ..udamenyedwa i ndi maliro koma tsoka abanja adakumanganso..pepa gumbuteni..your the star😂😂😂 akubanja uwawunze akulipire ndi iwowo maliro awo adakuwaza mbama..😂😂😂❤
Zomvetsanso chisoni kwambiri,munthu kumenyebwa ndi maliro kenako nkudzamangidwanso ndi achibanja☹️☹️ anthu isayamika,,,,thank you so much for the updates, following you from Lusaka Zambia 🇿🇲
Putin delivers nuclear weapons update Vladimir Putin said that 95% of Russia's strategic nuclear forces have been modernised as he addressed Russia on the country's annual Defender of the Fatherland Day today. He said that Russia had started serial production of its new Zircon hypersonic missiles and that new strike systems, which he did not specify, were being tested. In the course of the war in Ukraine, Mr Putin has repeatedly reminded the West of Russia's nuclear capabilities.
Good Man ngumbuteni ..udamenyedwa i ndi maliro koma tsoka abanja adakumanganso..pepa gumbuteni..your the star😂😂😂 akubanja uwawunze akulipire ndi iwowo maliro awo adakuwaza mbama..😂😂😂❤
Amazing story B. S Gayz, louder and clear, Dio from Derbn South Africa.zodabwisa eti😮
Watching from Lilongwe
Too bad to the big man watching from Zambia Lusaka
Zomvetsanso chisoni kwambiri,munthu kumenyebwa ndi maliro kenako nkudzamangidwanso ndi achibanja☹️☹️ anthu isayamika,,,,thank you so much for the updates, following you from Lusaka Zambia 🇿🇲
Following from Lilongwe Malawi
Kikikiki, watching from Lusaka Zambia. Nkhani yodabwitsa imeneyi
😮😮 Abambowa analakwitsa, iwowa sanapange bwino maliro a munthu wankuru kumphunzitsa nyamata kusambika! Mzimu wa wakufa unakwiya, mwana wang'ono sangamphunzirire pa ine! Anangomenya wankuruyo basi. Maganizo anga. Prophet Isaiah kuchokera ku Tauni ya Tete
Adalakwitsadi chifukwa sadapereke ulemu pamenepo limafunika kuphunzitsa amwana mzake ky
Mauricio é meu amigo, eu sou de Nancholi a zona visinha de Mthawira.
I don't know the truth about it but will inquire when I get there soon.
Watching from Ardiya kuwait.Keep it up
Thanks
Mmmm zosamveseseka abale mpaka mtembo kumenya munthu wamoyo! Watching from Ntcheu / Malawi 🇲🇼 keep updating
kkkkk
Angonia ndi province imene inayandikana ndi Dedza komanso ntcheu kotero anthu kumeneko sasiyana kwenikweni ndi angoni a maboma awiri muzochitika kuphatikizansi chilankhulo. Thus why akuyankhula chichewa.
I like this place Angonia..I will visit this place.
Watching from Mzuzu
Thanks
Kod Mozambique ndinu achewa ngat amalawi
Jefta from Lilongwe 23 komazinazi zosaveseseka
Nkhani yi ndiyoona
Thanks very appreciate
Munthu ndiwakachaso uyooo😂😂
Masiku otsiliza mpaka kumenyebwa ndimaliro aaaaaa
Munthuyo akuoneka kut akukamba za mowaa!! Nde nikovuta kumukhulupirira!! Nkhani zinazi muziona bwino bwino ndi anthu ake!! Platform yanuyi mukuyiphweketsaa
Live in South Africa
😂😂mdalayo akuyenela kuti asiye kumwa mowa 😂😂😂
Live I South Africa 🇿🇦
Zakusimba sawulula, omwenyedwa ndi maliro anatero pokwawuza amzake lero nkhani yafika pa TV kkkkkk
From South Africa
Thanks
Ine kuvera from mpulu mathithi
Adaledzela
Keep updating
Teach your cameraman to stay quiet during interviews.
Kkkkkkkkkkkk km kumeneko
Masheya niybwino Loma anthu ndamene amalakwitsa
😂😂😂koma Maliro amenewa..zomvetsa chisono
Next time Camera man akakhale chete
Zanveka
Putin delivers nuclear weapons update
Vladimir Putin said that 95% of Russia's strategic nuclear forces have been modernised as he addressed Russia on the country's annual Defender of the Fatherland Day today.
He said that Russia had started serial production of its new Zircon hypersonic missiles and that new strike systems, which he did not specify, were being tested.
In the course of the war in Ukraine, Mr Putin has repeatedly reminded the West of Russia's nuclear capabilities.
Mundu wamkulu apa mwagwidwatu. Koma mwapeza ka children 😂😂😂😂😂😂😂
😂😂 mumatha limbikilani Kuti dziwitsa
Zili bhoo
Zaminyamatu ayikileni nyimbo ikhala ya nkasa yakwiya ndimidzimu
Mukuitha mr govati
Kodi kwanu ndi ku Mozambique komweko kapena ndinu a ku Malawi.... Chichewa chanu chomveka bwinobwino
Last days indeed
so sad😢😢😢
Kumvetsera mwachidwi kuchokela ku kasungu Malawi
😮 koma abale zinazi zonsekesa komanso zomvesa chisoni
akuluwa ndiovuta🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Zodabwisa anzan akulephela kuziwa zaka zake
Hi
Koma Zina ukamva ayi ndi2 ngat Kaya 😂😂😂😂😂😂
Sorry
komanso zafika povuta
Kkkkkkkkkk zowona komo
😮😮😮
Kodi ku Mozambique amalankhulanso chichewa chabwino chonchi?
Eya
Agovati Koma muthuyu munapatsa chithandizo chiyani ndi mabala akewo simunatiuze ai.
Nsambi kwambili 😢😢😢
So sad
Mowa si zinthu
Yooo
Ééh'eeeh!!!
ndakondamarowo abata komo choziziswa mutebo kumenyamuthu
Athuwo alimbe umuthu pomumanga bambo oti wasamala zathu opita ayi ambuye awayendere
Ziwanda
Kodi inu chilakhulo chanu ndi chani ndipo inu ndi mtundu wanji wa anthu
There is no magic from this, those who are in the health field understand,
Pitilizani ntchito a Gova ndi a Cezito , Anthu amakukondani kwa mbiri ndipo amakutsatilani zintchito Zanu pa dziko lonse ma bg
Oooooo sorry bro this is bad news
I don't know why ndikuseka😂
Following
Sadness maliro kumenya munthu asaa
Be professional akumbutseni a camera man kuti sayenera kulowelera program..ma professional samatero ayi kumakhalako serious.
Sorry
Ichi sichichewa koma chinyanja
Zomvetsa chisoni koma tingalumikizane nawo bwanji
A camera man aaaaaaà
Huuuuu
Sorry sindidzayankhulanso back on câmera
😢zo vuta
Cameraman asamafunse nawo mafunso, that's unprofessional.
Sorry, não vai acontecer de novo, desculpa
Awaso amatumidzima zithu alibe nazo umboni aaah
Big, umboni ulipo okwanira, koma kamba kofuna kutonthiza akubanja tazivomereza, olo gumbuteni pa malopo wanena Kuti zonse ndi zoona Kuti anamenyedwa komanso achiwanga akuchitira umboni , vídeo yake tirinayo koma sitikufuna Kuti mwina gumbuteni aphedwe mu matsenga
Anyamata inu a Balanço ulemu wanu
Koma adawo anakoza kkkkk
Pitilidzani kutele mulungu patsogolo 🙏🙏♥️
Zambiri zidakabwera ku Channel imeneyi tiyeni tipitilize kuyitsata gayz
Akunena mothawathawa,kalipo😮
👏👏
Kodi wa camera amakhalaso busy umalankhula nawo musokoneza muzikhala chete nthawi yojambula
Sorry
Takunyadilani
Mumakwana
So kukamba chichewaku tiziti ndinu amalawi? Kapena mli mu boda ya Malawi ndi Mozambique?
Analakwitsadi a bambo amenewa maliro amunthu wankulu mzimu wa malemuwa unakwiya
Nkhani yovuta kwambiri kwa Ngonia uko zochitika zambiri
Eeeee km zochitika pa dziko lapase mzodabwitsa kwambiri
AAAA minyama
Ndiye simudabweze wankulu?
Koma gumbuteni ai ndithu sizithu paka kuziocha
😅
Nkhani zamowa osamabweretsa apa be professional anyapapi jnu
Lipilan
Zoseketsa
Kadewele ndi govat inu ndi 1
Zili bwino
Mmmmmmm kachaso simzako
Programu yabwino kwambiri
Koma a camera many asamarankhuretso akhoza kusonyeza program
Zanvaka
Koma zosayeda
Icho chiyenera kukhala chinachake chachilendo kumenyedwa ndi dzanja lakufa.
munthu wamenyedwa ndi maliro kenaso akubanjaso kudzamumanga sanapange bwino kwambili mulungu awalange
Cameraman ur not supposed to talk while doing ur job
Eya big.... sindidzayankhulanso
Zianthu zoipa mtima zaku mozambique
you guys tazifunsani mafunso adzeru pali mafunso ambiri oti mukanatha kufunsa koma mukungoseka