ZODABWITSA MNYAMATA WINA YEMWE ANAMWALIRA WADZUKASO NDIPO AKULONGOSOLA ZONSE KU MALAWI BOMA LA ZOMBA

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 22 ส.ค. 2024

ความคิดเห็น • 36

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b หลายเดือนก่อน +6

    Koma Pena Mulungu zimene amapanga eeeh zodabwitsa ndithu🙌🙌

  • @EdisonNakulenga
    @EdisonNakulenga หลายเดือนก่อน +4

    Haleluya mulungudiodabwisa

  • @ezilamasaka3637
    @ezilamasaka3637 หลายเดือนก่อน +2

    Ndinakumana naye mnyamata ameyu ku Lilongwe and andipemphandi chithazo, but malingana ndi mmene amaonekeradi ndinakana poti kunja unaopsa uku, umati ndikuthandidza munthu nati akupwyeteke

  • @user-lj7lm6ly7z
    @user-lj7lm6ly7z วันที่ผ่านมา

    Kofi bwanji osangofotokoza za mmene unabwerela kudziko kuno ukungobwerezabwereza zoti ufiti kulibe,ife tikufikilira za mmene iwe unafikira kukhomo kwamakolo ako ukungoti kumalawi ufiti kulibe mobwerezabwereza

  • @DaveKachala-of6hh
    @DaveKachala-of6hh หลายเดือนก่อน +3

    Amen and amen

  • @user-gs7wc3nx3q
    @user-gs7wc3nx3q หลายเดือนก่อน +3

    Ndipo inu ziko iri anthu achuma awa mlungu azawarange ngati chakwera uzarangidwa unamupha chirima osarakwa

    • @PreciousBandah-l2r
      @PreciousBandah-l2r หลายเดือนก่อน

      Iwe ndwe wachamb wav chilima nd ngzi chab kapen ulindiumbon chakwela alibe vuto km iwe

    • @RemzyMwenecho-oz5oc
      @RemzyMwenecho-oz5oc หลายเดือนก่อน

      akumanga ulinawo uboni

  • @TopG-h4l
    @TopG-h4l 26 วันที่ผ่านมา +1

    Zoonadi zimenezo kusalima zinachhika pano pakana pano adabeleka mwana

  • @ShadreckLevi
    @ShadreckLevi หลายเดือนก่อน +1

    Abelu zuranga I like him the the way he is doing his job

  • @GiftJulius-gx2kb
    @GiftJulius-gx2kb หลายเดือนก่อน +3

    Alihamudulillah

  • @CathyNyirenda-iw7ld
    @CathyNyirenda-iw7ld 15 วันที่ผ่านมา

    Government must change this law ,it's the poor always fill the pain 😢😢

  • @FrankKambwani
    @FrankKambwani หลายเดือนก่อน

    Yehova amayika njira popanda njira.Ambuye mulemekezeke amen

  • @user-lj7lm6ly7z
    @user-lj7lm6ly7z วันที่ผ่านมา

    Ukanafotokoza bwinobwinooo zammene unabwelera kuno kudziko kuno osamangofotokoza zaufitizo iyayi kambani zakubwera kwanu anthu titolepo fundo yogwilika chifukwa chochulutsa zotankhulayankhula anthu sangakukhulupilire

  • @user-tu8yx2on1r
    @user-tu8yx2on1r หลายเดือนก่อน +2

    Praise God ❤

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj หลายเดือนก่อน +1

    Nkhani iyi ndi yoona kumene zathu wina adamwalira kuno ku South Africa koma adakapezeka ku Malawi ali moyo pano akufotokoza chilichose

  • @user-qo1kf8ll1e
    @user-qo1kf8ll1e หลายเดือนก่อน

    Abel thank you for what you’re doing. Tadziwa zambiri zikuchitika,

  • @sakalameck
    @sakalameck หลายเดือนก่อน +1

    Zabwino zonse Willy!!

  • @marryrobert7092
    @marryrobert7092 หลายเดือนก่อน +3

    Wamaboza nyamatayo aaaaaa

    • @IssacMateyo
      @IssacMateyo หลายเดือนก่อน

      Wabodza ndiweyo kaya palibepo chimene chikukukhudzapo kaya iweyo kwako ndikuvela basi

    • @SevioursAbson
      @SevioursAbson 7 วันที่ผ่านมา

      Fiti iweyo usatipusitsepo apa

    • @SevioursAbson
      @SevioursAbson 7 วันที่ผ่านมา

      Wabodza bwanji umbon oseu

  • @FrancisZuru
    @FrancisZuru หลายเดือนก่อน

    Amen and Amen

  • @FrankYohane
    @FrankYohane หลายเดือนก่อน

    Mulimekeze Yehova dzikoli likupita kuti tilikumapeto

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj หลายเดือนก่อน +1

    Zoonadi anthu awa akufanana koma akafukule mandamo DN a

  • @TriciaDeborah
    @TriciaDeborah หลายเดือนก่อน

    Yooooo zithu zake

  • @PeterHartzeberg
    @PeterHartzeberg หลายเดือนก่อน

    Kwa mulungu wamoyo kulibe chobisika,, mulungu apitize kugwila ntchito yake

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj หลายเดือนก่อน +1

    Abele wakumana nazotu apa chilungamo munthuyo akufotokoza

  • @MtenjeHassan
    @MtenjeHassan หลายเดือนก่อน

    Nyamatayi akundionekera ochenjera kwambir, watumidwa ameneyi... iyaaa

    • @user-lj7lm6ly7z
      @user-lj7lm6ly7z วันที่ผ่านมา

      Ineso akundibowa mmalo mofotikoza zamabweredwe ake akungokimbikira zakuti kumalawi ufiti kulibe mmene wayambilaa akubowaso kobasi

  • @LacksonLungu-e2q
    @LacksonLungu-e2q หลายเดือนก่อน

    Tingawapeze bwanji

  • @frankchiwawa4795
    @frankchiwawa4795 หลายเดือนก่อน

    Eish

  • @ListerMkandawire
    @ListerMkandawire หลายเดือนก่อน +1

    Last days

  • @Zamwano
    @Zamwano หลายเดือนก่อน

    Km Ambuye atichitire chifundo