- 149
- 2 896 278
Balanço semanal CK & Govate
South Africa
เข้าร่วมเมื่อ 23 พ.ค. 2022
Onelani nkhani zosiyana siyana pa chanel imeneyi ya B S. Cezito Kadewere & Govate Samuel Lazaro.
Zikomo kwambiri aziphuzitsi wathu . zabwino zonse pa tsiku lanu
Zikomo kwambiri aziphuzitsi wathu . zabwino zonse pa tsiku lanu
มุมมอง: 1 060
วีดีโอ
Adzukulu ayika bokosi la maliro mu nyumba ya anfumu kamba kosapita nyama kumanda
มุมมอง 4.7K19 ชั่วโมงที่ผ่านมา
Adzukulu ayika bokosi la maliro mu nyumba ya anfumu kamba kosapita nyama kumanda
Tiyeni tikavote pa 9 mwezi wa nambala 10 chaka chino cha 2024
มุมมอง 2.3Kวันที่ผ่านมา
Tiyeni tikavote pa 9 mwezi wa nambala 10 chaka chino cha 2024
phuzitsi wina amene anamwalila, waonekera Kwa achibe wake
มุมมอง 14K14 วันที่ผ่านมา
phuzitsi wina amene anamwalila, waonekera Kwa achibe wake
Anthu oposera 5 avulala pangozi ya panseu
มุมมอง 4K28 วันที่ผ่านมา
Anthu oposera 5 avulala pangozi ya panseu
nzimai wina wapezeka atafa mosadziwika bwino, BS channel inafika pamalopo
มุมมอง 7Kหลายเดือนก่อน
nzimai wina wapezeka atafa mosadziwika bwino, BS channel inafika pamalopo
Munthu wina wavulazidwa, panyumba pake patapezeka mwana wa miyezi 8
มุมมอง 21Kหลายเดือนก่อน
Munthu wina wavulazidwa, panyumba pake patapezeka mwana wa miyezi 8
wakuba wina wapulumuka dzenje lokumbakumba
มุมมอง 11Kหลายเดือนก่อน
wakuba wina wapulumuka dzenje lokumbakumba
Mai wina wakwirira ku munda mwana wake obala ekha...
มุมมอง 15K2 หลายเดือนก่อน
Mai wina wakwirira ku munda mwana wake obala ekha...
Pambuyo pa ma holiday, tafikanso ife a BS channel ndi nkhani zosiyana siyana
มุมมอง 1.1K2 หลายเดือนก่อน
Pambuyo pa ma holiday, tafikanso ife a BS channel ndi nkhani zosiyana siyana
MWANA KUSAKA BAMBO WAKE OMWE ADAMUSIYA DZAKA 30 DZAPITADZO
มุมมอง 2K2 หลายเดือนก่อน
DZINA LA MWANA: Fernando Elidio morais. DZINA LA A BAMBO: Elidio morais da camara. number za mwana: 876188840;847459513 GOVATE SAMUEL LAZARO: 862229354 CESARIO PEDRO INACIO -CK 875112269
MAFUNO ABWINO KU NDENDE RADIO COMUNITARIA DE ANGONIA 13/07
มุมมอง 8K2 หลายเดือนก่อน
MAFUNO ABWINO KU NDENDE RADIO COMUNITARIA DE ANGONIA 13/07
Oyimba wa ku Malawi Skefa Chimoto, akudzayimbanso mwa ulele ku Domue
มุมมอง 2K4 หลายเดือนก่อน
Oyimba wa ku Malawi Skefa Chimoto, akudzayimbanso mwa ulele ku Domue
munthu emwe anasowetsedwa ndi dzigawenga , tsopano wapezeka
มุมมอง 10K4 หลายเดือนก่อน
munthu emwe anasowetsedwa ndi dzigawenga , tsopano wapezeka
satana wandinyenga wandisokeretsa ine....full vídeo
มุมมอง 4.6K5 หลายเดือนก่อน
satana wandinyenga wandisokeretsa ine....full vídeo
tsatane tsatane wa nkhani ya Ngozi ya track
มุมมอง 6K5 หลายเดือนก่อน
tsatane tsatane wa nkhani ya Ngozi ya track
takozeka kupereka nkhani zambiri Chaka chino.
มุมมอง 1.9K5 หลายเดือนก่อน
takozeka kupereka nkhani zambiri Chaka chino.
nyamata wina wa dzaka 20 emwe anasaukitsa makolo wake waphedwa Ku tsangano
มุมมอง 8K6 หลายเดือนก่อน
nyamata wina wa dzaka 20 emwe anasaukitsa makolo wake waphedwa Ku tsangano
Nyamata wina wa luso , wapanga njinga ya moto ya olumala wina Ku nthini
มุมมอง 10K6 หลายเดือนก่อน
Nyamata wina wa luso , wapanga njinga ya moto ya olumala wina Ku nthini
Vila yagwedezeka ndi kubwera kwa Namadingo pa 7 de Abril
มุมมอง 3.2K6 หลายเดือนก่อน
Vila yagwedezeka ndi kubwera kwa Namadingo pa 7 de Abril
TSATANE TSATANE WA NKHANI YA FITI YOMWE YAGWA KUMPANDA WINA KU VILA ULONGUE
มุมมอง 38K7 หลายเดือนก่อน
TSATANE TSATANE WA NKHANI YA FITI YOMWE YAGWA KUMPANDA WINA KU VILA ULONGUE
banja lina liri m'manja mwa apolici kamba koliganizira kuti lagulitsa mwana wawo wa ntundu wa albino
มุมมอง 24K8 หลายเดือนก่อน
banja lina liri m'manja mwa apolici kamba koliganizira kuti lagulitsa mwana wawo wa ntundu wa albino
nzimayi amene anatha dzaka 10 asakuyankhula, anayamba kuyankhula pa nthawi ya njira ya ntanda
มุมมอง 6K8 หลายเดือนก่อน
nzimayi amene anatha dzaka 10 asakuyankhula, anayamba kuyankhula pa nthawi ya njira ya ntanda
Ena mwa anthu ofuna kwabwino, ali okhudzidwa ndi kuvutika kwa ana.
มุมมอง 4K8 หลายเดือนก่อน
Ena mwa anthu ofuna kwabwino, ali okhudzidwa ndi kuvutika kwa ana.
wana 6 a banja limodzi akhoza kufa ndi njala pa vila Ulónguè, ngati sitingapangeko kathu...
มุมมอง 10K9 หลายเดือนก่อน
wana 6 a banja limodzi akhoza kufa ndi njala pa vila Ulónguè, ngati sitingapangeko kathu...
BS ( Balanço Semanal) channel igwire bwanji ntchito mu chaka cha 2024 ????
มุมมอง 1.5K9 หลายเดือนก่อน
BS ( Balanço Semanal) channel igwire bwanji ntchito mu chaka cha 2024 ????
Anthu akonzeka bwanji kufika kwa Driemo ku Angónia???
มุมมอง 7K10 หลายเดือนก่อน
Anthu akonzeka bwanji kufika kwa Driemo ku Angónia???
wina waphedwa chifukwa cha pakamwa pake, kuyankhula kwambiri akamwa mowa.
มุมมอง 35K10 หลายเดือนก่อน
wina waphedwa chifukwa cha pakamwa pake, kuyankhula kwambiri akamwa mowa.
Mzimayi wina waluza moyo kamba ka Masheya (bank khonde )
มุมมอง 30K10 หลายเดือนก่อน
Mzimayi wina waluza moyo kamba ka Masheya (bank khonde )
wana awiri abweretsa mpungwepungwe pomwe aulula kuti ndi nfiti, ndipo amatamba. audio via rádio
มุมมอง 7K10 หลายเดือนก่อน
wana awiri abweretsa mpungwepungwe pomwe aulula kuti ndi nfiti, ndipo amatamba. audio via rádio
Good job Ndimanyada
Akuyenela kusitha khope chifukwa akhalitsa
Kulikose amachita manyazi akabwela
Sasani ntchentche mai aaa
Zabwino zonse malume ulemu wanu
Much love guys 🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲 from Zambia 🎉🎉🎉🎉
Zimu wamuthu ndi ovuta
Lwachitk malodza kom momwe akuipondabe msima kkkkk😂😂😂
Zabwino zomwe
Ine Harold kaliati Kodi mumadziwakuti kuno ku Qatar tima onelaso bs chnl 🇲🇼🇧🇭🇲🇿
Dziko lili pa moto
😢😢😢😢ndisame kulakwa kwambili
Parabéns, Viva 12 de Outubro Dia do Professor!
😂😂😂😂 bamboo uyo ndi fiti uyo muzimu wa mwana uli nd umulungu
Watching from Blantyre malawi
Obrigando 🙏 todos senhores🎉
Parabéns sucesso sucessivos para todos vocês senhores professores anivel de todo Moçambique 🎉🎉🎉
Am watching from Soweto
Thanks
Alemekezeke. Munthu ali ndi mphavu zopha thupi.
God is good all the time
Zikoma govati pamozi ndi azanu pitilizani kutipasira mavidio koma mmmm zosayenda
Watching from Pretoria paboma penipeni anyakwawa mowa too much 😂😂😂😂
Kkkkk
Nyakwawa bibida anamupweteka mukanamutapa nkwikoso nyakwawayo
Kkkkk
Mbambande timakunyadirani kwambili a Gova ndi a Cezito, komano nyakwawa kuthawa bokosi ???? Kakakakaka
Kkkkkk mwinaso anyakwawawo analezela kkkkkk
Kumapha mwana ena ena akumusowa
Mas força
Mmmmmh mmmmmh abare
Koma a Mozambique muzipemphela mwanva but anyway agova ndi sizitu to the world
Timapemphera koma mulungu anayiwala dziko la mozambiki
Ooooooo ndaivano mbuzi anyakwawa sanapatsidwe
Nyakwawayu ananenadi koma ithink anawalonjeza koma muchimowamowa
Mulandu umenewo umayenera a police not afumu
Am from Malawi mangochi makanjira I love this channel BS channel and Bakili muluzi chaneel guys continue ndimakunyadila guys thanks ❤❤
Zikomo kwambiri
Tiripano
Tete
Dj kamwana Mark 2 dedza boma zosakhalatu bwino
Govati mumakwana musamasowe, km kumozambiqu dziko lankhaza amakonda kuphana nkhan ya mowa
Watching you guys from Mangochi Malawi (zosaenda)komano Dela limenelo ndizaendelako kumachitika daily zodabwisa 😢😢😢
Zambia Lusaka
Following you from south Africa original home Malawi
Kulakwa abale kuchotsa moyo wamzathu
Following you brother from South Africa but am from malawi
Komatu ndizochititsa manta
Anthu umunthu alibe like serious kupha zawo chfkwa cha magalas a mmaso? Really? Amangidwe amenewo
Tizangophatikiza Mozambique nd Malawi 😂
Nkhani yomvetsa chisoni kwambiri.Pakakhala vuto ndibwino kukambilana mwamtendere.
Following you guys from sourth Africa but am from Malawi keep it up chibade may rest in peace
Onerani tsatane tsatane wa nkhani yonse
Team Govate mumakwana watching from Lilongwe area 3
Zikomo kwambiri
Watching from area 3 Lilongwe. From Kafere. Uko kwa Salati. 😢
@@joyceellis9045 ndiye ukatanthauza chani ukamati kafere uko kwa salati?
Zovetsa chisoni kwambiri Moçambique wathu khaza zikuchuluka.