Malawi wafika apa gyz? Yooooo uwu nde moyo wa Ku South Africa 😢😢 eeee ayi ife timati kumalawi mkokoma koma na izizi ayi ponseponse pali chiwembu basi eeee😢,,,,zithu zoziputa munthu wabambo mkazinso kuphedwa nawo wow 😢😢 ati ndikukudwalitsa ndine ndikufuna kukupha aa zansanjetu apa zimayendaponso; koma mwati mankhwala amaperekawo siwokuphawo koma nde zachitika zoti choipa chitsata mwini?? 😢 eshhhhiii zosayenda azudzitsa anatu apa eeeee RIP 💔💔😭😭 asing'anga Ndi Mrs sing'anga 😢
Kodi ku Mozambique ko munthu akapha nzache satengeredwa ku police? Zikuoneka kuti munthu akapha nzache nkhani imangothera konko basi kumangodandaula basi nkhani ndikuthera pompo. Mukupanga zibwana ku Mozambique ko ndithu a kilimani inu zona munthu kupha nzache inu masi kumusiya.
UMAKWANA Big up bro Dzikomo potidzitsa ✊✊✊✊✊
Am watching from south Africa ( joburg)
Tthanks Mr Gova pomatidziwitsa zochitika keep it up
Achina Govate mumakwana watching you from Area 3 🤝
Mmmmm zosakhala bwino tisaname,anyamata amene athawawo akuyenera kufufuzidwa amenewo,komaso athawiranji poti iwowo amadzitenga Kuti ndiwopambana😢
Kumeneku kuli kachiwanda ndithu anthu amangophana osaopasaso olo kudzitsittsa kapena mantha ,popha munthu amakhala ngati akupha mbuzi osati munthu kayavbwanji kaya one zimandikhudza bwanji
Am watching from Johannesburg but am a Malawian
Thanks
Malawi wafika apa gyz? Yooooo uwu nde moyo wa Ku South Africa 😢😢 eeee ayi ife timati kumalawi mkokoma koma na izizi ayi ponseponse pali chiwembu basi eeee😢,,,,zithu zoziputa munthu wabambo mkazinso kuphedwa nawo wow 😢😢 ati ndikukudwalitsa ndine ndikufuna kukupha aa zansanjetu apa zimayendaponso; koma mwati mankhwala amaperekawo siwokuphawo koma nde zachitika zoti choipa chitsata mwini?? 😢 eshhhhiii zosayenda azudzitsa anatu apa eeeee RIP 💔💔😭😭 asing'anga Ndi Mrs sing'anga 😢
Ngati zavuta kukambilana itanani akulu akulu kusiyana n kumapha a chonchi anasiya ana umasiye ndi owawa 😢😢😢
am watching from Soweto south Africa RIP
Zosayenda kumalawi ndichani😭😭😭
Zovetsa chisoni , koma Bs Channel timakunyadirani kwambiri
Kwathu ku tsangano angonia sizilibwino mulomba, akuluakulu pepani ine phee kuno ku chiuta manje-chiuta
No no no ! So unfortunate, this has to stop.
Wakupha mzake naye aphedwe muwagwile anthu amenewo ndikuwapha basi
Mmmmm Rip 😭😭😭😭 from south Africa
Afumu andisangalasa ayankhula bwino ndithu koma ndizovesa chisoni 😭😭😭😭😭
🇲🇿 Mocambique wathu what is going on
Anthu oyipa kwambiri sakufunika kudziko lino
Mchitidwe uwu ndi oipa kwambiri
Mupherananji nonse okhala mzimu wa mulungu
Tiyeni tonse tikondane monga mulungu amatikonda
Amagwetsa mvula kuwalitsa dzuwa Kwa munthu wina aliyense
Ochimwa ngakhale osachimwa
Tiyeni tidziopa mzimu wa mulungu
Anthu akumeneko ali ndi ziwanda kukhalira kuphana osaopa kuchotsa moyo wazawo
❤🎉mumaakwana a gova & ck
Zosayenda kuphana ngati njoka Dziko la Malawi likupita kuti 5:17 5:21
Zikoma kwambiri agovati koma eeee zosayenda tiyeni tizinkhala ndimtima okondana
Nmmmm,komaizi zimasautsa,kaye zaufitizi eeee ,Anfiti amasausadi,ndipo nzoowawa kumavutika chifukwa chawina? Kwa munthu amene asanazione angathe kutokota mulimosemo,komangale ndiliineyo aaaaaaaaiwoyi doit.
Mfumu yamudzi ilibe mphamvu bwanji samatenga apolice mkumanga anthu nanga mpaka anthu 10
Acompanhando a partir de lizulu. A China Gova mumakwana inuyo
Ameneyu ndichilonda chake chapamwendocho akhafire mundende
Koma ku Mozambique uko muli chibwana kuphana ngati kupha mbudzi koma munthu 😢
Kuweluza musiyilen mulungu sikwayife
Mmm zosayenda amene athawawo awafufuze basi
Very sad 😭😭
Kunena zoona chitetezo kulibe
Mmm zosaenda komano asing'angawo kuchita kuyankhula live dziko lake ili zosaenda
Zokhudza kwambiri 😢😢😢
Anthu akumozambiki ena siabwino mukupheranji muthu wathu ? Walakwanji? Jerasi BA's
Kodi ku Mozambique ko munthu akapha nzache satengeredwa ku police? Zikuoneka kuti munthu akapha nzache nkhani imangothera konko basi kumangodandaula basi nkhani ndikuthera pompo. Mukupanga zibwana ku Mozambique ko ndithu a kilimani inu zona munthu kupha nzache inu masi kumusiya.
Vuto lakwathu kumtundu wachilhomwe kungokhala ndi ng,ombe ya mkaka ati ndiwe mtiti
Zosaenda ayi
Kambilanani osaphana
Koma nkhani zake zopherana zimenezo kumudzi kumeneko kukufunika school anthu amenewo aphuzisidwe zamalamulo
Zakumidima zimathanaso nkumidima osati kumutengera chikwanje kurakwa
Mmh kulakwa abale zisamatero
Mmmm tiyeni tizikambirana pakavuta mmmm
Zovetsa chisoni kwambiri
Afumu opuma akunama munthu sangayankhule kut ndinakuloza ndine ndinayamba kale kufuna kukupha akunama akungofuna kut nkhani iwakomere
Eishiii zachisoni kwambiri 😢
Mwalaoyera Ntcheu
Tiri ma video onse momwe zinakhalira koma TH-cam imakana kuonetsa nkhani za magazi
Watching from ntaja machinga
Munasowa aGova
So sad tikuonela kuno RSA CAPETOWN
Zikomo kwambiri
Mumakwana mabig tete
Anyamata awo plz asakidweee 😢
Anthu akumwera munakhara bwanji njara kuphana kumwera muri busy kuphana mot muzipanga chitukuko
Koma inuyo ambuye mukhale thandizo eeee
Kulimba mtima koyipa kwambiri 😢
Kulakwatu koma
too bad anthu kodi umunthu wapita kuti
Zosayenda 😭😭 mzimu wao u utsemtendele 😭😭
Timakutsatilani A CK ndi AGOVATI
Dziko lapita ili sizoona ayi izi
😢 so sad eeee
Zosaenda 😢
Oooo
😭pep
Pa
Zovetsa chisoni
Nde mwati asaponsa Anu....😂😂😂😂😂 Malawi the warm heart of funnies and sad stories 😢😢😢
😂😂😂kodi ukuku mku Malawi kuno kapena Mocambique?
Mozambique boarder
Zosakhala bwino
Kumeneko kuli Chibwana bwanji?utsogoleri wake ngotani?
This is punishment
Zovetsa chisoni 😢😢😢😢😢
Koma ndalira mmmhu 😭😭😭
Zosayenda zimenezi
Zosayendatu
Timanen kt jakison wa kovid uyu athu tizingopan
Tafika
Zovuta eeh
So sad😢😢
😭😭😭 koma sachisoni
After school
😭😭😭😭
Kulakwa
Mmmm koma abale satanic yakula tu kumeneko kupha nzanu Chifukwa chongomuganizira kuti ndi mfiti? Mulungu tithandizeni, tichitireni chifundo ndithu
Maputo
Obrigado irmão
Akuti kumeneku anthu aphedwa ndi okwanira 9 kapena 10 koma akuti anthu onsewo akuphawo osagwidwa .Agwidwa ndi awawa ndiye kuti kumeneko apolice amagwira ntchito yomwe analembedwera? Kuno ku Malawi bwenzi angapo atagwidwa Malawian police imayesetsa kufufuza moreover kumeneku amaphana zokhudzana ndizaufiti ndiye kuti anthuwo amaphedwa ndi gulu ndiye a police osapeza munthu oyambitsa? Dela limenelo ndalimvera chisoni. Delalo palokha ndilakufanso. Too primitive.
True
Zosankhala bwìno
Km dziko likupita kt ambuye timenyeleni khondo
😢😢😢
😂😂😂😂😂😂😂
Perekan malamulo oghwima mudzi mwanu mchitidwe uwo siwabwino ai tisaphane pakhani zopusa bala lalowa cancer yo ingakhale lolozedw? Nayeso gagadeni wasalayo
So sad 😢
Zovetsa chisoni
😢😢