Mukapita pa online mupeza kampani ina Ku America ikupanga ndalama,Ku Malawi a reserve bank amangopanga print mwachitsazo U s a yapereka Ku boma la Malawi 20,000 kwacha sikuti America imatumiza ndalamayo ai amangotumiza authorisation Kuti apange print
Amen, inudi mwandimasula, kupita ndindalama yomwe amanena umva ikufunulika pano ndiyakuti mmmm zachabe
Ndasaka ndalama zimenezi kwa nthawi ndithu Kona ndimayamika Mulungu kuti anandipulumusa tsiku lina ndikugona malemu mai anga akundikwapula kundiuza kuti ndisiye ndikusokela ndipo nditaika
Palibe chuma chobwela mophweka dele tisamale,
Mulongosole bwino timvetse❤
Mulongosole bwino timvetse❤ bwino.
Zikomo kwambiri 👍 you collect 100 percent
Amen thanks potitsegula maso
Am following from ntcheu
Amen ndathokoza chifukwa cha uthenga wopambana osamva asamve koma chilungamo chimamasula Ambuye adzilemekezeka mu nthawi zomse.
😊
Ine wina wake anandipezako kuti andigule koma ndinamukaniza chifukwa ndili nawo
Basi ndasiyaa
Amen mwatitsekula maso.
Amen
Thanks and 🙏
Ndilinayo ine tiki ya mkondo wautali pakati ananisiyira a ngwazi😂😂😂
palitu one penny ya 1944, 1951, six pence 1964, 1967, one tambala ya 1971, 1974, 1982 and florin ya 1964
Kikikiki awa atiseketsa mwee... ati kuti? Masofotomiya? Or Mesopotamia😅😅
Ambuye chitani ndinu pa ife
Zikomo potichenjeza
Ame
Following
Who makes money and in which country do the makeup
Ine ndifuna one kwacha ya 1999 ndipange Ring 💍
palitu one penny ya 1944, 1951, six pence 1964, 1967, one tambala ya 1971, 1974, 1982 and florin ya 1964
simukamba zomveka bwino
Vuto ndi inu amene simukunva koma ofotokozawa akuchita ngati asasiye
Koma tipulumuka athufe mulungu atimenyele khondo patokha sitingathe
🤔🙄
Kusonyeza kuti ndalama iliyonse ndiya satanic?
Kodi ndalama amapanga kuti?

Shaaa
Amen
Amen