Sugar Crisis Malawi. Anthu kudya phala la Mchere

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 22 เม.ย. 2024

ความคิดเห็น • 82

  • @user-un6qv6sj3h
    @user-un6qv6sj3h 15 วันที่ผ่านมา +3

    Sugar wadula ndithu kuno ku South Africa 2kg R50 imene kumalawiko ndi 5000kwacha koma kumalawi 1kg 4000 it's too much

  • @malawigeneralguide1646
    @malawigeneralguide1646 15 วันที่ผ่านมา +4

    All these days where were you??? We already lost hope in all government and non governmental organisations in Malawi 😢

  • @elishamael-shadai
    @elishamael-shadai 15 วันที่ผ่านมา +3

    Amene amaiziwa M fucken CP sanavotere chipani chopanda chisoni ichi. Chinapha anthu ofunikira,anthu alephera school because of fucken MCP. Kodi njoka ukaiphwanga diso mkuthawira ku mphanga pakapita five months imazakhala njoka kapena buluzi??? Chipani Cha Richard Amestrong ichi

  • @user-ez8uk7py8n
    @user-ez8uk7py8n 15 วันที่ผ่านมา +6

    A malawi sitimva agalu awa anaziwika paka mpain kuti sangakwanise ndiizi lero anthu tikulira muzaonaso 2025 MEC ikupanga chinyengoso

    • @user-pn7cj9hb3t
      @user-pn7cj9hb3t 14 วันที่ผ่านมา

      Iwe ndee wanena zoonadi

  • @user-uc1pd1tc2x
    @user-uc1pd1tc2x 15 วันที่ผ่านมา +4

    Sugar Peter Munthalika anali pa K700 😂😂😂😂😂😂 koma panopa Ali pa K4000😂😂 my Malawi 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂 MCP ai zikomo tiyeni nazoni😂😂😂 Bagamoyo party

  • @frankchirwa2301
    @frankchirwa2301 14 วันที่ผ่านมา +2

    Amalawi ife ndife anthu opusa kwambiri,osaziwa zimene tikuchita anthu akuononga ziko tikumawa yang,anila, tiphesa ana amalawi zukani osagona

  • @HarrisonMwanga-xy4sc
    @HarrisonMwanga-xy4sc 15 วันที่ผ่านมา +3

    Ngati zithu sidzitsika,tionana pa 2025, alliance ichoke, Anthu akuba kupotsa dpp,tionana pa May pano.ndipo,kulozedwa kuba vote yanga,tikutyolani ma kosi one by one.

  • @user-uc1pd1tc2x
    @user-uc1pd1tc2x 15 วันที่ผ่านมา +3

    Amalawi amakhalira kuthamanga daily atii Peter Muntharika achoke lero, chimanga 60 thousands kwacha thumba by Chakwera nthawi ya Peter Munthalika chimanga Thumba linali 3500 basi chimanga kumapezeka paliponse kubwera sugar Anali mbweeeee Koma panopa amalawi munkafuna zija ndizimenezizi ndithu 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
    Keep it up amalawi anthu otseketsa inu😂😂😂😂 ndi Chakwera wanuyo komanso Chilima wanuyo 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @dumisanimoyo3152
    @dumisanimoyo3152 15 วันที่ผ่านมา +2

    Mumati chakwera chakwera si zimenezo

  • @MmikeeMateyo-kj2pn
    @MmikeeMateyo-kj2pn 15 วันที่ผ่านมา +2

    Ineyo ndine walilongwe koma chakwwla achoke galu kwambili

  • @user-uc1pd1tc2x
    @user-uc1pd1tc2x 15 วันที่ผ่านมา +2

    2020 Chakwera akazati ndibweletsa nkhondo kungoti sindinatenge bomaa😂😂😂😂😂😂 Lero ndiizi anthu akufa ndi njala mmmmm 😂😂

  • @user-ys4lt4ev8z
    @user-ys4lt4ev8z 15 วันที่ผ่านมา +2

    Mcp ndiyoyipadi apa takhulupirira asatanatu amenewa

  • @spargomw
    @spargomw 15 วันที่ผ่านมา +1

    Ndipo compain ya MCP imkachitika ngakhale m'Mipingo😂😂😂😂😂 ndizimenezo Ambuye adayankha.

  • @user-ps9nu6se9k
    @user-ps9nu6se9k 15 วันที่ผ่านมา +1

    Nice talk bakili muluzi TV simanama

  • @lenneckmanja7051
    @lenneckmanja7051 15 วันที่ผ่านมา

    Malawi okomera tonse uja ndi ameneyu.. Tankhala tikumulilira uja ndi ameneyu

  • @FrancoKaunga-rq2ki
    @FrancoKaunga-rq2ki 15 วันที่ผ่านมา +2

    That's what you wanted malawians! You know that mcp is a party of vilombo.

  • @mphatsojuliostandy4918
    @mphatsojuliostandy4918 15 วันที่ผ่านมา +3

    Mumafuna kuona zina ndizimenezi

  • @IssacMuhaye
    @IssacMuhaye 9 วันที่ผ่านมา

    Zowonadi shuga wakwera kwambili chilichonse m'malawi Chakwera ndithu ndiye amalawi yesesani kuchitapo kanthu..mapeto ake anthuwa akungofuna kuti pochoka M'mipando afuna azatisiye pamoto

  • @GeorgeKatundu-or1uf
    @GeorgeKatundu-or1uf 15 วันที่ผ่านมา +1

    President wanthu ndichisilu kwabasi
    Kumakweza zinthu ngati wagwa manyii
    Iwe Lazarus iwee

  • @user-ev6bi7jr7g
    @user-ev6bi7jr7g 15 วันที่ผ่านมา +3

    Munkauzidwa za MCP Koma kusamva lero mukulira ndiye akutitu mpaka 2025 ndipo adzawinadi mwachinyengo ngakhale mudzapite Ku khothi mudzaluzanso chifukwa akhothi wo nso adawagula

    • @user-gh1yc3mu5r
      @user-gh1yc3mu5r 14 วันที่ผ่านมา

      Eeee komatu apa ndiye olo azayitanise MDF yose koma kungochitika chibwana chimenecho sitizamayendaso misewu komano makomo mwawo, komaso ma khothimo kukawapasa war yomwe iwowa akhala akuipepha kwa nthawi yaitali and they will get it if they try such nonsense

  • @MikeMalinga-xx8ys
    @MikeMalinga-xx8ys 15 วันที่ผ่านมา +3

    Ndizomwe mumafuna amalawi.. mademo Anu aja ndi amenewa munaika anthu okuba

    • @user-pn7cj9hb3t
      @user-pn7cj9hb3t 14 วันที่ผ่านมา

      Eti eti akulira chani?

  • @chitanibenito1109
    @chitanibenito1109 15 วันที่ผ่านมา +4

    Ndinu nomwenso azimayi mukutengeka ndi ma k2,000.00 akugawidwa ndi zitsiru za mcp.

    • @user-uv1vu6ub5o
      @user-uv1vu6ub5o 15 วันที่ผ่านมา +2

      Ndipo palibe muthu opwetekesa mtima ngat mzimayi, mmmmm

    • @FrankDingah-if7vz
      @FrankDingah-if7vz 15 วันที่ผ่านมา +1

      Eti sukunamadi nda usiru azimayiwa amangotengekq

  • @user-cd4df3vg4y
    @user-cd4df3vg4y 15 วันที่ผ่านมา

    Satana ali nkati mwaomo mwa atsogowo 😢

  • @NgomaRaheem
    @NgomaRaheem 15 วันที่ผ่านมา +2

    Azimai inu ndi ausiru busy nditima 2000 kwatcha

  • @frankchavula3594
    @frankchavula3594 14 วันที่ผ่านมา

    Athu tikuvutika ku malawi chifukwa cha president chakwera

  • @DannielOnions-fy3dc
    @DannielOnions-fy3dc 15 วันที่ผ่านมา

    Thanks so much keep getting please its too much

  • @user-gh1yc3mu5r
    @user-gh1yc3mu5r 14 วันที่ผ่านมา

    Amalawi vuto lake timavota ndi emotions chifukwa choti chakwera ndi Chilima wakugulirani nthumba lachimanga, wakupasani tindalama toti simungadye even in two days inu mwati uyu ndiye ndi deal azatisunga osadziwa kuti akukutchelani matchela, kuvota kotereku kwa wonongesa Malawi lero kodi muzayamba liti ku vota ndi dzeru? Onena adanena, olakhula anakuuzani musapatse chiongolero munthu yemwe sakudziwa za m'boma inu mukamuseka kumuona ngati ndi mwana komaso chitsilu lero ndi izi mawu akulu amakoma akagonera. Malangizo anga ndi oti tamavotani ndi dzeru please osati mwa emotions chifukwa mukatero inuso muli gulu lovuladzitsa amalawi ndipo ndi zija amakuyakhani kuti ine sindinakutumeni kapena kukukakamizani kuti mundivotere.

  • @chikokaSagonja
    @chikokaSagonja 9 วันที่ผ่านมา

    Boma ilili ndi agalu okhaokha angokumana

  • @user-el8to1te3l
    @user-el8to1te3l 15 วันที่ผ่านมา +1

    Sitilowelela mayi muphuzile

  • @MustafaLikaomba
    @MustafaLikaomba 15 วันที่ผ่านมา

    Allahuma yarabii amiin ,mpangen kakanthu chakwela musasiyesiye mupange kanthu

  • @WitnessNyondo
    @WitnessNyondo 15 วันที่ผ่านมา

    Sugar waduladi kaya timwanso tea yo kaya?

  • @geraldtuwaga-iz6ll
    @geraldtuwaga-iz6ll 13 วันที่ผ่านมา

    Chonchi nkumakakamira itsogoleri mbava zimenezi

  • @FefieTenisha-du7ge
    @FefieTenisha-du7ge 15 วันที่ผ่านมา

    Government is composed of three categories
    1 Reason(rulers)
    2 Guardians(soldiers,
    Judiciary etc)
    3 Appetites ( civilians)
    It is the responsibility of the rulers to come up with reasonable decisions and actions to see to it that the needs(Appetites) of the citizenry are timely addressed ....
    The guardians ( soldiers, judiciary) have a responsibility to see to it that the rulers are protected...
    Sugar is a one of the most important basic nutritive food value that the body needs daily for it's energy source and sound functioning
    Denying energy to the citizenry is akin to almost killing them...life is energy ...one can not act or think well without energy
    It's confusing to understand what this gvt is priotizing on
    This leadership is insensitive to the needs of it's people and doesn't deserve to continue being on the driving seat of government affairs

  • @user-vt4xw5px5h
    @user-vt4xw5px5h 8 วันที่ผ่านมา

    Zokhumba moyo kuzuza sure

  • @shayrafernandeslatif9556
    @shayrafernandeslatif9556 10 วันที่ผ่านมา

    Sugar wa malawi ali ku Zimbabwe koma ali wochipa,kodi akupitista sugar kunja ndindani???

  • @FortuneTungo
    @FortuneTungo 5 วันที่ผ่านมา

    Pathumbo pawo anyani amenewa

  • @AustinYusuf
    @AustinYusuf 14 วันที่ผ่านมา

    Chakwera why 😢😢😢😢

  • @innocentkandulu2825
    @innocentkandulu2825 15 วันที่ผ่านมา

    kkkkkkkkkk akwefule ndani iwowo ndizomwe akufuna. ndizomwe amalawi amafuna

  • @enockdaisi1306
    @enockdaisi1306 15 วันที่ผ่านมา

    Vuto ndi usogoleli nothing else. even ma passport kulibe

  • @IMAAMABINA
    @IMAAMABINA 8 วันที่ผ่านมา

    Zikomo chakwera

  • @MmikeeMateyo-kj2pn
    @MmikeeMateyo-kj2pn 15 วันที่ผ่านมา

    Khani ndiyakuti amalawi adziwe kuti chakwela ndibuzi kwambili chitsilu akapanga zobela mavote koma akunama sawina ziona komaso akangoluza amangidwa aziona

  • @dumisanimoyo3152
    @dumisanimoyo3152 15 วันที่ผ่านมา

    Kuvotera gure wankuru kuyipa kwake nkumeneko

  • @JamesSaidi
    @JamesSaidi 15 วันที่ผ่านมา

    Zimene mumkafuna amalawi simunati munakalira Inu ndithu kuvotera mcp

  • @user-wi9hz8fk8i
    @user-wi9hz8fk8i 15 วันที่ผ่านมา

    Eeeee koma nkhani ya sugar tiyang'aneni ma bwana.

  • @FefieTenisha-du7ge
    @FefieTenisha-du7ge 15 วันที่ผ่านมา

    Sounds like Malawi is more of a capitalist economy than a socialist economy

  • @WysonMpatama-cv1mc
    @WysonMpatama-cv1mc 15 วันที่ผ่านมา

    Chakwera mchilima pathumbo panu

  • @innocentkandulu2825
    @innocentkandulu2825 15 วันที่ผ่านมา

    mwayamba kukamba zopusa sopano mesa ndizomwe mumafuna? pano PETER akufuna abweleleso mukuyankhulaso zopusa kusonyeza kuti kuti kumalawiko dzinthu zikuyenda bwino

  • @michaelkallyz2425
    @michaelkallyz2425 15 วันที่ผ่านมา +1

    The same courts that helped u ascend into power u now blaming them. Why do u NGOs comment when MCP is being disadvantaged?? Courts are always favouring Nankhumwa for leader of opposition in parliament but u are not commenting. U have to be impartial for people to put trust in you. Otherwise fighting Illovo is fighting against your own fiscal that allow for price elasticity. I have noted with regret that DPP has been losing almost 100% of their court cases, most oftenly unfairly but none of the NGOs stood for DPP. I f u need people to stand with u, stand with DPP first to remove Nankhumwa as leader of opposition.

  • @MmikeeMateyo-kj2pn
    @MmikeeMateyo-kj2pn 15 วันที่ผ่านมา

    Chakwela akufuika musamuvoteleso ndi galu kwambili chitsilu kwambili machende ake ameneyu

  • @jameskachulu8141
    @jameskachulu8141 15 วันที่ผ่านมา

    Unya manyi sumathi ukufuna kusinda dziko kwachosa adad

  • @George-zd5le
    @George-zd5le 15 วันที่ผ่านมา

    Amalawi saziwa kuvota

  • @user-un6qv6sj3h
    @user-un6qv6sj3h 15 วันที่ผ่านมา +3

    Chakwera mbava chimwendo mbava mkaka mbava kunkuyu mbava agalu inu mwaononga Malawi

  • @user-sw2rn3xn3g
    @user-sw2rn3xn3g 15 วันที่ผ่านมา

    Zoonadi sizikuyenda ayi

  • @JamesRoben-dy7bx
    @JamesRoben-dy7bx 15 วันที่ผ่านมา

    Kkkk alipheee chakwela zosamukhuza olo half kod akukweza sugar kulibeko

  • @user-sw2rn3xn3g
    @user-sw2rn3xn3g 15 วันที่ผ่านมา

    Vuto amalawi timadziwonongela tokha...kukonda kulemekeza chibwana

  • @Christopher-xc2ey
    @Christopher-xc2ey 15 วันที่ผ่านมา

    President uyuyu

  • @bokaalfan9146
    @bokaalfan9146 15 วันที่ผ่านมา

    Akupanga zithuzopusakwambili athuamanamizilanji alangidwebasi agalu opusa

  • @EmilyMwale-ly3fb
    @EmilyMwale-ly3fb 12 วันที่ผ่านมา

    Koma mose muja tayambila mpaka pano sakutsika sugar ngati kulibe president abale ai zikomo .mesa president akalakhula zithu zimatheka pompo pompo koma ai ndithu kuli ziiii

    • @eliffagondewe8214
      @eliffagondewe8214 11 วันที่ผ่านมา

      Deal ndi yake akumakagulitsa kunja apeze ma dollars adziba bwino nde angalankhule chani???

  • @AbuOsman-ts6ef
    @AbuOsman-ts6ef 15 วันที่ผ่านมา

    Mukamuvotera mfiti ameneyo mmmmmm mudzalira kuposa pamenepa akuti anali m,Busa wanji ameneyu

  • @user-im3gn6bp4e
    @user-im3gn6bp4e 15 วันที่ผ่านมา

    Mayo mowa ujaso wakwera bc

  • @chikokaSagonja
    @chikokaSagonja 9 วันที่ผ่านมา

    Sugar akhale pa mk900

  • @user-ln3zx6wo4w
    @user-ln3zx6wo4w 15 วันที่ผ่านมา

    Bagamoyo mcp 😂

  • @mishecksipolo7153
    @mishecksipolo7153 14 วันที่ผ่านมา

    Akapito a CAMA ati ziiii bwanji adya chibazi?

    • @eliffagondewe8214
      @eliffagondewe8214 11 วันที่ผ่านมา

      Kkkkkkk paja adati boma ili ndilosamva, mwina atopa nalo

  • @AlexManuelMisomali-sv1vn
    @AlexManuelMisomali-sv1vn 15 วันที่ผ่านมา

    💪💪

  • @user-cn3bp1cr6r
    @user-cn3bp1cr6r 15 วันที่ผ่านมา

    Atsitse basi

  • @Moses51
    @Moses51 15 วันที่ผ่านมา

    Tiyenipaground

  • @henrynandolo4520
    @henrynandolo4520 15 วันที่ผ่านมา

    Very sad situation.

  • @muhaspader3593
    @muhaspader3593 15 วันที่ผ่านมา

    😂😂 😂

  • @user-hq6dq7zr1e
    @user-hq6dq7zr1e 13 วันที่ผ่านมา

    I dont like Mcp,

  • @tachaallen
    @tachaallen 15 วันที่ผ่านมา

    I as a Malawian am very sure that this sugar crisis is politically influenced. There certain people who are behind this crisis so that MCP should be blamed. ILOVO should be inquired.

    • @FefieTenisha-du7ge
      @FefieTenisha-du7ge 15 วันที่ผ่านมา

      I don't think so...your assertion would be reasonable if we could have seen gvt taking some serious steps to work hand in hand with the responsible companies on how skyrocketing of these prices could be contained or cushioned...but i am sure you can agree with me that government is just quiet as if nothing is happening...
      This explains the weakness and insestivity of this Onse Alliance Gvt