Kodi Mulandu Wa Chilima Ndekuti Watha? Bon Kalindo

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 22 เม.ย. 2024
  • On Nyasa VoiceBox, Bon Kalindo is asking if the trip taken by Right Honorable Saulos Chilima, Vice President of Malawi to Tanzania signifies the end of Chilima’s corruption trial.
    Ku Nyasa Voicebox, Bon Kalindo akufunsa ngati ulendo womwe Right Honourable Saulos Chilima, wachiwiri kwa President wa dziko la Malawi kupita ku Tanzania ukuonetsa kutha kwa mlandu wa Chilima.
    #malawi

ความคิดเห็น • 89

  • @dontreybanda278
    @dontreybanda278 14 วันที่ผ่านมา +4

    Good job

  • @moyorobert9801
    @moyorobert9801 14 วันที่ผ่านมา

    True man of Malawi 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥we love you Mr bon

  • @RobertLongwe-er2kr
    @RobertLongwe-er2kr 10 วันที่ผ่านมา +1

    Mawu! Mawu!

  • @user-vu5gy8wf8y
    @user-vu5gy8wf8y 8 วันที่ผ่านมา

    Mwana ooopsa kwambili 🔥🔥🔥🔥🔥

  • @user-nc1uv3be1v
    @user-nc1uv3be1v 10 วันที่ผ่านมา

    Bad Bone.. ❤GET UP Stand Up Malawi yoyoyoyo

  • @Henry-vw2cz
    @Henry-vw2cz 14 วันที่ผ่านมา

    Bon Kalindo Double salute

  • @Moses51
    @Moses51 14 วันที่ผ่านมา

    The DC rast man standing on true kunkhadxulu kunkhadxula The DC bon kalindo

  • @user-iw6cz5ft2l
    @user-iw6cz5ft2l 14 วันที่ผ่านมา

    We're follow you bwana DC ipondeni fadar congress yatikwana koopsa

  • @RobertLongwe-er2kr
    @RobertLongwe-er2kr 10 วันที่ผ่านมา

    Malawi tikufuna anthu ngati bone

  • @user-wd9yd1bg9n
    @user-wd9yd1bg9n 10 วันที่ผ่านมา

    Poyamba ndimaona ngati chilima ndi oona patali koma ayi ndithu, khwangwala weniweni

  • @KafosiChisale
    @KafosiChisale 11 วันที่ผ่านมา

    Go ahead boss

  • @user-po9yj6io3c
    @user-po9yj6io3c 12 วันที่ผ่านมา

    We are here bcoz of our economic depression.

  • @user-vu5gy8wf8y
    @user-vu5gy8wf8y 8 วันที่ผ่านมา

    Mr Bon Kalindo mumakwanila inuyo 😂😂...

  • @ThoccoBondo-mx7vt
    @ThoccoBondo-mx7vt 14 วันที่ผ่านมา

    Salute

  • @user-ee6be5kl5o
    @user-ee6be5kl5o 14 วันที่ผ่านมา +2

    Akungomubwadika chilimayo ndi munthu osaona patali monga anthu ena , mwachidule ndi osaganiza ngakhale pangono za zaka zonsezi anabanidwa ndi chakwera , amuoma kupusa chilima akanangokana osapitako

    • @sufiammadi
      @sufiammadi 13 วันที่ผ่านมา

      Akudziwana awa aaaa

  • @BesterWatson
    @BesterWatson 14 วันที่ผ่านมา

    Bon kalindo big of the biggest

  • @andrewchirwa2193
    @andrewchirwa2193 13 วันที่ผ่านมา

    Bonnie kalindo 🔥🔥🔥🔥

  • @AshleymuwemiNgosi
    @AshleymuwemiNgosi 14 วันที่ผ่านมา

    I wish I could meet you DC

  • @MaploNyirenda
    @MaploNyirenda 8 วันที่ผ่านมา

    Moto moto moto bwana zowona

  • @chitanibenito1109
    @chitanibenito1109 14 วันที่ผ่านมา +1

    A president anthu, problem after problem.

  • @MphatsoGona-px6bq
    @MphatsoGona-px6bq 14 วันที่ผ่านมา +2

    😅 kalindo the 1

  • @CholapitsaSamson
    @CholapitsaSamson 14 วันที่ผ่านมา +1

    Pangolin akatakwe

  • @VincentNgabuhvincent
    @VincentNgabuhvincent 14 วันที่ผ่านมา

    The DC mwana owopsa kwambiri umatiyimilira ife amphawi ife

  • @user-dk6yc8pl2m
    @user-dk6yc8pl2m 14 วันที่ผ่านมา

    The DC ❤❤❤❤

  • @KafosiChisale
    @KafosiChisale 11 วันที่ผ่านมา

    Neabor moto moto go ahead

  • @nedsonchanache7822
    @nedsonchanache7822 14 วันที่ผ่านมา +1

    Milandu ikudzigamula yokha apa basi....Chilima ndi machine bambo siza m'busa ofooirazi apa zonse akudzipanga apazi a MCP akummenyera Chilima Campaign ndithu

    • @herbertchazuka5649
      @herbertchazuka5649 9 วันที่ผ่านมา

      Palibe akumenyeredwa Campaign apa bwana koma akudzikoleka onse kuti wina asaoneke ngati ndi wabwino..nkhani ijatu ikukhudza onse nchifukwa Chilima amapempha kuti immune ya President ichotsedwe.

  • @user-uc1pd1tc2x
    @user-uc1pd1tc2x 14 วันที่ผ่านมา

    Koma yaaaah Nyanja yalandidwadi ndi Tanzania?????😢😢😢😢😢😢😢

  • @AmoniNicholas
    @AmoniNicholas 13 วันที่ผ่านมา

    Fuso lilipo kut kodi, Abon Kalindo, mwathandizapo athu agati omwe mutawadziwa kuti amalawife tikuvutika ndi njala, tikuvutika ndi uphawo osowa ndalama,
    Monga inu a president athu ifeosawukafe mwationetserako chithandizo chanji popatul kutiyakhirirak kuboma?

  • @user-im7sc2my4w
    @user-im7sc2my4w 14 วันที่ผ่านมา +1

    AMalawi pepani boma likukomera Anthu womwe ali kustsogolo ,Malawi wanga tikanalipo kuzunzika ndi Anthu andalewa

  • @chrisneySwanepoel-yu5vd
    @chrisneySwanepoel-yu5vd 13 วันที่ผ่านมา

    Kalindo makwanira kwambri

  • @ThoccoBondo-mx7vt
    @ThoccoBondo-mx7vt 14 วันที่ผ่านมา

    Pangolini Bon Kalindo

  • @leonardjika2100
    @leonardjika2100 11 วันที่ผ่านมา

    A NEW THINKER WILL GOVERN OUR LAND SO HELP ME GOD

  • @user-wd9yd1bg9n
    @user-wd9yd1bg9n 10 วันที่ผ่านมา

    MCP and tonse alliance manyaka enieni

  • @LuteSynos
    @LuteSynos 14 วันที่ผ่านมา

    Azibabo 2:56

  • @andrewchirwa2193
    @andrewchirwa2193 13 วันที่ผ่านมา

    Apa zikusonyeza kt chilima alibe mulandu 🤣🤣🤣

  • @user-le9su3mt7r
    @user-le9su3mt7r 14 วันที่ผ่านมา

    Kalindo huma kwanaaa

  • @carloshthezacarloshtheza6024
    @carloshthezacarloshtheza6024 13 วันที่ผ่านมา

    Uyu ndiwamisalad

  • @user-lu6oo9zx3h
    @user-lu6oo9zx3h 14 วันที่ผ่านมา

    Ndie chirima azizati sindkuramura nawo ndgaru chirima

  • @JamesmolesSekan
    @JamesmolesSekan 6 วันที่ผ่านมา

    Pangolini eeeee

  • @frankdonovanntambira
    @frankdonovanntambira 14 วันที่ผ่านมา +1

    Chi Pangolin Bamboo Lastman Standing 🤣🤣🤣

  • @user-nz7bd7lm4i
    @user-nz7bd7lm4i 14 วันที่ผ่านมา +1

    Awa anabwela kuzatipha bas

  • @SheenahMwalabu-iz3pr
    @SheenahMwalabu-iz3pr 14 วันที่ผ่านมา

    Sinditha kugona osamumvera DC ndipo ndendimamva Naye kukoma nkamamumvera Kalindo ndipo osamasowa baba 😂😂😂

  • @user-qp8kh2hj9o
    @user-qp8kh2hj9o 14 วันที่ผ่านมา

    Pamenepo ndipo we mungadziwe kuti Chilima alibe mulandu ndizongopeka akanakhala ndi mulandu so Bwenzi atapasidwa ulendo ngati umenewo komanso zachita kuoneseratu kuti Chakwera akumuopa Chilima that's why nkhani yatero SKC 2025 BOMA ❤❤❤❤

  • @BendictoPhiri-ku1lj
    @BendictoPhiri-ku1lj 13 วันที่ผ่านมา

    The DC mwana oophya kwambiri.....Chakwela ndi Chilima ndi mbuzi za anthu

  • @MatthewsJanuary-wr3rf
    @MatthewsJanuary-wr3rf 13 วันที่ผ่านมา

    Go deeper the DC

  • @ChimwemweNgulube-dk5wf
    @ChimwemweNgulube-dk5wf 14 วันที่ผ่านมา

    Justice Kapindu ndidolo analamumula kuti passport ya Chilima asunge kumpanda pano watumima Chilima ku Tanzania 😅😊😮

  • @DannieChimenya
    @DannieChimenya 14 วันที่ผ่านมา

    The DC

  • @EdwardGeorgeKasabola
    @EdwardGeorgeKasabola 12 วันที่ผ่านมา

    Ana amuna obadwa masiku okwanira munthu opanda mantha kulankhula true story

  • @user-hq6dq7zr1e
    @user-hq6dq7zr1e 13 วันที่ผ่านมา

    😂😂😂 mr bon mmakwana

  • @MikeMalinga-xx8ys
    @MikeMalinga-xx8ys 14 วันที่ผ่านมา +1

    Akalindo ine ndimakhala kuno ku TANZANIA.. Koma zomwe zirikuno mwina CHIRIMA akanafkila pantete anthu akanamugenda chifukwa ASWAHIRI amadana ndi munthu okuba.. nde anthu akuno ndi okwiya kwambiri ndikubwela kwa CHIRIMA.. akuti kwabwela mbava yakumalawi kuno

    • @user-eh1mg3ww6d
      @user-eh1mg3ww6d 14 วันที่ผ่านมา

      Mmmm nanga Chocho athu oipa ameneo osamawalandila m,thamangitseni ndi miyala

    • @nedsonchanache7822
      @nedsonchanache7822 14 วันที่ผ่านมา

      Akulu kukhara mbava Chilima sakadatumidwa ndi boma ai komanso ndindale izi nanu tamazitsatani......Chilima akanatha kumutuma ku America ndipo zikanatheka koma eishhhh palowa ndale apa

  • @isaacchiwaula731
    @isaacchiwaula731 13 วันที่ผ่านมา

    I think n I bliv kut munthu uyuyu ndichitsiru chazitsiru zonse m'malawi muno

  • @Chisomomataya
    @Chisomomataya 14 วันที่ผ่านมา

    pangoline katundu waboma ndweyo born kalindo

  • @AlbertomachavaMachava-gc8mn
    @AlbertomachavaMachava-gc8mn 5 วันที่ผ่านมา

    Munthu opanda mantha uyu 😂😂

  • @moseskathekeni8848
    @moseskathekeni8848 14 วันที่ผ่านมา

    President wa anthu osauka kuno kumalawi. Boooon kalindo. The pangolin

  • @user-jc9gy9ou3v
    @user-jc9gy9ou3v 13 วันที่ผ่านมา

    😂😂😂 khaaaaa khoooo

  • @chrisboyce2
    @chrisboyce2 14 วันที่ผ่านมา

    Our pangolin 🔥 The DC mwana Woopsa Kwambiri BON ELIAS KALINDO 👍🔥

  • @johnw.posomanchanel4023
    @johnw.posomanchanel4023 14 วันที่ผ่านมา

    Zomvesa chisoni angowononga ndalama

  • @ahmedsema1880
    @ahmedsema1880 14 วันที่ผ่านมา

    Abusa opanda chiyembekezo awa

  • @LumbaniNeba
    @LumbaniNeba 14 วันที่ผ่านมา

    Matchine bambo

  • @PrinceKachimanga
    @PrinceKachimanga 14 วันที่ผ่านมา

    the Dc...ulemu wanu😅😅😅😅😅😅😅

  • @user-uc1pd1tc2x
    @user-uc1pd1tc2x 14 วันที่ผ่านมา +1

    Guys ndimatsuleni za Nyanja yathu pls, Mukufuna muzindiuza kuti Nyanja ya Malawi yalandidwadi basi ndi Tanzania?????😢😢😢😢😢😢😢 Pls reply me fast if it is possible

    • @user-eh1mg3ww6d
      @user-eh1mg3ww6d 14 วันที่ผ่านมา

      Ndimomwemo m,bale basi tiyeni tingosamuka m, Malawi muno kkkkk

    • @user-uc1pd1tc2x
      @user-uc1pd1tc2x 13 วันที่ผ่านมา

      @@user-eh1mg3ww6d 😃😃😃😃😃Eishiiii koma Tri ndie ndafooka nditanva Izi wanva mmmmm ndie tisamukire Kutiko m'bale wanga kuonera???😃😃

    • @user-eh1mg3ww6d
      @user-eh1mg3ww6d 13 วันที่ผ่านมา

      @@user-uc1pd1tc2x kwa amelica m,bale wanga bolasotu ngati passport uli nayo ngati ulibe wanya basi kkk chifukwa nao ma passport anasiya kupanga tili ku bagamoyo tu paja osaiwala kkkk

    • @frankbanda7333
      @frankbanda7333 13 วันที่ผ่านมา

      Yes

    • @user-uc1pd1tc2x
      @user-uc1pd1tc2x 13 วันที่ผ่านมา

      @@frankbanda7333 Koma MCP abale Anga inu ndi chani???? Ziwanda kapena chani??? Mmmm😭😭😭😭😭😭

  • @sahaluhanga5727
    @sahaluhanga5727 3 วันที่ผ่านมา

    Drama yokhayokha

  • @tasmania527
    @tasmania527 14 วันที่ผ่านมา

    Kalindo udzafa ndi nsanje. Keep fighting for DPP until 50 yrs if you will still be alive. Ndiwe munthu wokwana, wongobwebweta ngati galu wankutu. Pangani za phindu ku family kwanu osati kulimbana ndi atsogoleri. Mulungu adzakukanthamula. Ukuwanamiza a Malawi kuti ukuwamenyera ufulu and yet it's about your stomach now and then, and if DPP would win which is an impossibility. You lost your soul through anger and bitterness so watch yourself Mr Kalindo.

    • @gamammwenye
      @gamammwenye 14 วันที่ผ่านมา

      i hope ndiwe mulendo ku Malawi, coz uthenga uwu ukanawawuza a Timothy Mtambo ndi anzawo a Gift Trapence, who lied to multitude of people to vote for Tonse alliance as a game changer, yet the alliance is failing to organize themselves. so musiyeni kalindo aziyankhula. Malawians have opened their eyes. sangaputsitsidwenso

    • @VincentNgabuhvincent
      @VincentNgabuhvincent 14 วันที่ผ่านมา

      Ngt uli foreign usatinyase ndi nonsense ukukambazi

    • @tasmania527
      @tasmania527 13 วันที่ผ่านมา

      @VincentNgabuhvincent Ukunyasa ndiwe ndi umbuli wakowo ongosatira munthu without reasoning. Kalindo is being used by a political party coupled with his frustration in the Tonse government, which didn't provide what he expected as a personal gain. Now, what is making Kalindo hate the idea of Chilima going to Tanzania? Is he the judge and the jury? Does he have presidential powers? The fact is he's just another bitter dog trying to score a point from his sponsoring party and blind followers like you. Otherwise, akukamba zamanyi and zotsathandiza a Malawi. Kalindo is always negative even when something looks positive and worth the praise-a testimony to his bitterness and hatred of the leadership. Ngati Chakwera kapena Chilima amakunyasani , palibe adzakukakamizeni kuvotera iwowo, zavotereni Adadi anuwo. Choti mudziwe ndi chakuti anthu akuziwa za mkwiyo wa Adadi anuwo ndipo alibe chance chozawina chisankho, mark my words bro. Vuto ndi loti mumakonda ndale za mtundu, and that's a disadvantage to DPP in 2025; do not say I didn't alert you on the impending loss of your party in 2025.

  • @NumbDee
    @NumbDee 14 วันที่ผ่านมา

    Dc anakonza

  • @user-gj4li2gc8o
    @user-gj4li2gc8o 14 วันที่ผ่านมา

    Chofuntha ichi

    • @frankkutsala255
      @frankkutsala255 14 วันที่ผ่านมา

      Ofuntha ndiweyo ukumvera bwanji Za munthu ofuntha.

    • @frankkutsala255
      @frankkutsala255 14 วันที่ผ่านมา

      Ofuntha ndiweyo ukumvera bwanji Za munthu ofuntha.

  • @KiddErraveda-ym5ir
    @KiddErraveda-ym5ir 12 วันที่ผ่านมา

    🤣🤣🤣

  • @frezarphiri3480
    @frezarphiri3480 14 วันที่ผ่านมา

    😂😂😂 chisilu chakwela akuwona ngati ife amalawi ndife Ana ake stupid Lazaro iwe

  • @Amgwagwa
    @Amgwagwa 14 วันที่ผ่านมา +1

    Kulepheraso chizungu kkkk

  • @stevenfrancism3638
    @stevenfrancism3638 14 วันที่ผ่านมา

    😂😂😂😂 pangolin

  • @user-vf9bs9vz2g
    @user-vf9bs9vz2g 14 วันที่ผ่านมา +1

    This guy speaks for he's on benefits not Malawians I still remember the video window made saying amalawi siwowafela and what ever this guy does it's for he's own good

  • @pilcooliveiravictor1599
    @pilcooliveiravictor1599 14 วันที่ผ่านมา

    Komatu kalindoyi nsanje ikumupweteka,
    Iwe ukuganiza Kuti boma litakupeza ndi chifukwa chokwanila silingakumange

  • @Maliet-nh6kf
    @Maliet-nh6kf 14 วันที่ผ่านมา

    😂