Ching'aning'ani comedy, ft Ngiringande
ฝัง
- เผยแพร่เมื่อ 21 ส.ค. 2024
- President Chakwera laughing hard at Ching'aning'ani ndi Ngiringande comedy. December 2023.
SUBSCRIBE here for more videos goo.gl/aYvIXK
Malawi's videos in English and Chichewa, here is Ching'aning'ani 2024 preview stand-up comedy.
So far we still hav a long way to go ...we need pple like winiko,izek
Pamapirisi apo chakwera uveserepo kwambili wanyozedwa apo 😂😂😂😂😂😂
Chakwera ali mwetuuu osadziwa akumunena😅😅
Anawa anali ndi uthenga...koma achimwene awo saanaumve!😂😂😂😂😂😂...
😂😂😂😂😂 achakwera mukunenedwa apo
More 🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Chakwera kuzikonda popedza ndi opusa sanetengepo kanthu 😂😂😂 akumunena alichikhalire satana wamunthu
So far so good guys
😂😂😂Koma munamucheza chakwela ndi anzake onse amene akuba ndalama Za anthu osauka kubela amphawi mbuzi ndi ndizi eti kumamwetulira kuteleku samadziwa Kuti anena iyeyo 😂😂😂
Koma madolo awawa eeee
More fire 🔥🔥 ching'aning'ani
Musamapange comedy ND mawu a Mulungu plz
Bwana
More more amalawi
Achipwanya akuti tizimasuka ndi brother wathu, uti ? Uyo aliapo chakwera 😂😂😂😂 iiiii koma achipwanya
Umakwna Ching,aning,ani
Akumwa ekha chakwera akusekelera koma akumunena iyeyo
Nice
Kkkkk koma chipwanya mpaka a head
Ching'aning'ani mukukhwana❤❤
Asandukatu mwana 😂😂😂
Ching'àning'ani more fire
😂😂😂😂 more 🔥 chiphwanya
😂😂😂😂😂Apa luso luso Chakwera amusambwazatu😂😂
Akumunena chiyani
Mbambande
Ching'axy real Goat 🐐
Muwomberanji Manji yet. Pple are still struggling
Kkkkkkk koma mwamucheza🔥🔥
Wachita bwino osajoka zamukoran ukanapepesanso..😅😅
Chiphwanya , kudzaphwanya Chakwera pamenepaja😂😂😂
😂😂😂😂😅 Malawi kwachema😂
Umandivesa Ching:axs 3:27
Best lanji
Inu ndimadolo gyz
jeftre precious
❤❤ chipwanya more fire
Geat man
Sorry guys there was only 1 pair of izeki ndi jakobo
No other guys can re-do that
Kwambiri these guys analindi experience yachibadwidwe
Kkkkkkkkkkkk chingaxy wat lilime limatan
Amakwana azibambo awa eeeee
Mbambande chiphwanya
❤❤❤❤❤
😂🤣😂🤣😂🤣😂 mumatha
Umatha
chakwera koma atipha🤣
Umakwana iweyo kkkkkkkkkkkkkkk
Ndikatundu waboma
Amakwana 😅😅
Kkkkkkkk awawa koma
Chakwera amanyozedwa alipompo, mwaitha anyamata
❤
Chiphwanya ayitu 😅😅
Zosabeba kweni kweni
Chiphyanya azimuna😂😂😂
🤣🤣🤣🤣
Wayitha
Ufulu bwenzi utayambira ku parliament,zimene mukuchita aboma ku parliament kuja mukutiphwanyira ufulu kwa anthu ovutikafe
Oloso matie alimomwemo nanga simuliso mafumu
❤😂
😂😂😂😂🙌
😂😂😂😂🎉
kwachema
Kachikenanso agide 🤣🤣🤣🔥🔥
1:50
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
bon Kalindo ali ndi furu
Khn ikupta Kwa chakwera bc straight😂😂😂😂😂😂
Zaziiii😢
😂😂😂
Koma pa izeki ndi jakobo paja simungafikepo agalu inu
Ya IJA chiphwanya
Sizikubhebha
Kkkkk
😂😂😂😂😂😂
Km chipwanya amakwana
Zosabhebha ataaa 🚮
Tchulani lem bb a