Madala mulungu akudaliseni ndi mau omwe mwawagawira anthu onse mudziko lathu la Malawi. Mwalankhula bwino mopanda manthu, ndipo anthu ngati inu ndi amene akusowekela kuti dziko lathu liphulidwe mu msinga za moto. Well done papa
Komano Bon kalindo as omenyera ufulu sakuyenera kuimilira chipani komano aziyima pa choonadi . Kalindo is the last man standing indeed. Ndangokonza pa Bon kalindo kuti aime poyera ndikulowa DPP/UDF mm ndizomwetu Mtambo wathela zolowa chipani
Komano mukudziwa kuti Bon kalindo adapepesa kwa A Malawi pachimene chidachitikaAnd We all know that no One is perfect,Freedom fighter Mr Bon kalindo is trying His Best.
Mwalankhula bwino koma koma pomutchula boni kalindo mwalakwitsa kozi iye anabwera poela nkupepesa ntundu wa amalawi ndipo amalawi anamukhululukila nchifukwa mukuona kut akalindo akalankhula amalawi akumawamvela ndi chidwi end next time osazanyozaso kalindo
TH-cam yaphweka, munthu wandale kuyankhula zopepera chonchi, muzamanga mtambo, iwe ndi wa police? Kudzichemerera koma kuyankhula zopusa, paja umbuliwu ndi andale omwe eti? Tangoperekani maganizo anu osutsana ndi mtambo ndi andale koma akhale maganizo olongosoka osati zopusa ngati izi.
Mdala iwey according to your speech tikuziwa kut ndiwazipani ziwiri watchulazo km born kalindo musiye pliz leave that Guy alone pliz,fundo zako ndizabwn ndithu km panga zako
I doubt the claiming here in that he is a seasoned and shrewd politician. Sound knows nothing other than being a blind royalists. He is a just a supporter of DPP and UDF as he voluntarily confesses herein. Cant understand what he is up to begging for DPP and UDF sympathy. He thinks he can advise Nankhumwa yet he needs advice himself. Nankhumwa will shame them by dividing the DPP vote. He understands very little about the Nankhumwa effect, talking about 'alibe ndarama zopangila' ma branch, what a warped political mindset. And praises fello tribesmen what do does he think he will succeeds from such mindset. He thinks kuyankhula bwino its about god washipping kkkkk and boot licking. The tongue can tell who what he is up to. To hell with your DPP
Speaker has just expressed brutality no connection to the mentioned kongoresi munthuyundi mwana pa ndale. You are not even a political man. UDF komwe ipite uzizimuka. DPP AND UDF ilipo?
Musayelekeze kumuyipisa born kalindo we love him ❤
Bon kalindo please is only one man standing who is fighting for us bt sorry for including him in your audio but powerful speaking.
Ivemtimacona boni kalindo musa muymise kuyangura ndimundu wabwino❤❤❤❤❤we love you boni kalindo ❤❤❤❤
Ifeee tilipabuyo pa boni kalindo❤❤❤❤❤❤🎉🎉🎉
Bon kalindo akudzudzula osat kusonyeza chibale ayi bon kalindo alibe mbali amapita kulikose musiyeni ndiyemwe akumatidziwitsa zobisika musiyeni bon kalindo
This man is so insightful...
His political observations and sayings are epitome of truth...
Very good kumeneko nde kulankhula, Auzen avesese bwino bwino anthu wa
Bon kalindo anawapepetsa amalawi babaPolani moto kumbali ya Bon kalindo ngati pamutupanu Pali nzeru mugwirizanenaye kalindo ndipo Dpp imagination zisankho chifukwa cha Bon kalindo
Kalindo Muchoseni akulu cz iye anapepesa kale
Madala mulungu akudaliseni ndi mau omwe mwawagawira anthu onse mudziko lathu la Malawi. Mwalankhula bwino mopanda manthu, ndipo anthu ngati inu ndi amene akusowekela kuti dziko lathu liphulidwe mu msinga za moto. Well done papa
Perfect said but pomuika Bon Kalindo mu gulu limenelo nde mukulakwitsa Bon Kalindo ndi president wa amphawife we proud of him
Walakwisa kwambiri
Fire 🔥 my fada
Aaa akulu mwapalatu pamenepo kalindo anapepesa ndipo amalankhula zonveka zonzeka mwinatso kupotsa inuyo the DC nd katundu omanga ndimalamba
Good message zoona
Congratulations Mr. That's great 💪
Sure bwana.
Born kalindo anapepesa mukululukileni, koma pachiyambi anasokonekela, koma anatutumuka athu atataisa kale, koma uyuyu uyu aaaaa tayeni akufuna kusokoneza wabhaletayu ndimagalaziyu,,
Ife takhala tikunena boni kalindo ndiwamisala Bambo awa akulakhula zazelu osati za boni kalindo Zija ai koma macadet opanda zelu basi bze kuombela mmanja boni zazii
Ndale ndi bodza...
Anthu mpwetekana🤣🤣🤣🤣🤣
Very good 👍👍👍
Well spoken but leave our president alone, Bon Kalindo doesn't have issues only fighting for the poor Malawians.
Akulu musakhale oweluza musireni mulungu
@@user-nc4vi1jt5g aaaa aaaa waweluza ndani apa? Muzachila 2025
After all a bon kalindo anapepesa komanso saliku chipani chilichonse
Kumpoto nkwachilima ndi afod not dpp nde 50+1 mukaitengakut
❤❤Zikomo
DC msiyeni,kwinako tamva
Zimenezo ndizakale kalindo adapepesa kale musiyeni pano ndi president wathu
Muwauze asatanawo anthu oipawo anankhumwa sangakhale pulezident
Iyi ndimisala to the maximum. Nonse ndi ntambo mix MCP
The dc trusted for us
Ameneyu atisamale mambo chitsiru cha munthu kuchoka ku Zambia uko
Lankhulani Zina osati za born Kalindo mukusowa zonena ndimunthu yekhayo akufera ife Malawi osauka choti mudziwe
Nthawi yonseyi munali kuti osayankhula bwanji yankhulani zanu musiyeni Kalindo
Komano Bon kalindo as omenyera ufulu sakuyenera kuimilira chipani komano aziyima pa choonadi .
Kalindo is the last man standing indeed.
Ndangokonza pa Bon kalindo kuti aime poyera ndikulowa DPP/UDF mm ndizomwetu Mtambo wathela zolowa chipani
Komano mukudziwa kuti Bon kalindo adapepesa kwa A Malawi pachimene chidachitikaAnd We all know that no One is perfect,Freedom fighter Mr Bon kalindo is trying His Best.
Zingayambe kuyiwalika
Malawi it's for us let's stand en fight for our rights we nid to make malawi better dats it guys malawi yapoila hvy
Tangolankhulani zoti mzapange mkawina zanzeru please 25yrs Mndale koma zaziii
Eti ayise
Nice speech but kalindo anapepesa, so let's fight together
Mwalankhula bwino koma koma pomutchula boni kalindo mwalakwitsa kozi iye anabwera poela nkupepesa ntundu wa amalawi ndipo amalawi anamukhululukila nchifukwa mukuona kut akalindo akalankhula amalawi akumawamvela ndi chidwi end next time osazanyozaso kalindo
Kutokota kwabwino kwambli big man
Mukhale ngat akuluakulu abon kalindo anapepesa kale kmanso amanena kt alibe cipani
Yes your right but only kalindo
Leave him he is innocent man
Mulungu si Jacob a ziona asiyeni atase amenewo adzaithawa malawi
Bon kalindooooooo
Kweeee
Muthu mulala wayowoya 200 %
Amen
Mdala uyu kwamuvuta mkunvetsetsa born kalindo amadzudzula ndipo sakunama born kalindo
Bon kalindo yekhayo, muchotsemoni abale.
Awa ndi a DPP. akumva kuwawa mmene anachoseledwa muboma ndipo simuzawina wina even come 2025
Kulakhula mwanzeru
Timothy mtambo asawatenge Malawi ngt zitsulu, iye ndi Mc p yakeyoso adatikwana tionana pathawi yomvotayo
A Malawi tisamakhare anthu oyiwara tiyeni tiphunzire achina mtambo anatipusitsa nde achinyamata osamalora zopusa ayi
Akalindo anapepesatu nde mwaiwalatu adala bwanji mwayaka mototu
Mau amphavu kwambiri dziko Lili paminga
Koma kalindo anapepesa
Please abwana mwayankhula bwino komano zolimbana ndi kalindo ayi kalindo ndi womenyera ufulu mwachilungamo ndipo akumenyera ufulu wa anthu osauka
Kalindo sakupanga nawo zopusa
Nambo kweleko kkkkkk.
Yakusawusya
Aaaaaa nthawi imene ankapepesa born kalindo iyeyo Anali kuti? Ayimva kale audio yanuyi a born kalindo sakuyankhani.
Nanga ukufuna achite kuwawuza anthu kuti azavotele Dpp anthu okha akuziwa kale amene azawavotela nde inuyo mungodila achimwene
Uku ndiye kuyankhula mosapysatira
Munthu wanzeru uyu
Iwe ngati ukudana ndi ka LINDO ndiye ndiwe wa M C P osati zinazi
Komano Bon kalindo adapepesa let's forget about the past and move on together
No no no no we won't forget
Bon kalindo nd I pangolin
Wa onse alliance uyu, musamuwone ngati ndiwa udf ayi, kuteroku alipa divide and rule, watch out!!
Auzeni mwina ayiwala kwatenga ngati amalawi ndi opusa auzeni akumbukile
No Bon Kalindo amabwera poyera ndikupepesa kuti pepani pamene enawa sanapepese ndiye he is innocent
Chitsiru iwe
UDF thetsani ilowe mu DPP...
Kd akulu mwayambapo liti kuwamenyera amalawi ufulu?amalawi akuziwiranitu kt mufuna mugulidwe eeeeee mwayichera.mwachera kumwezi nkhanga zaona
Mumakwana bigman....chakwela and his cabinet should fired out.....agwa basi this 2025...APM boma.....
Osadera nkhawa Dpp ikubwereraso m,boma ndithu
Kkkk kkk kk
Msanawako basi sitikuvotelaniso kuno kumpoto a dpp
Dpp
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂❤❤❤❤
Kkkk
DPP anthu akuba zaka6
Aribe ntchito ndipo paribe chomwe angapange
TH-cam yaphweka, munthu wandale kuyankhula zopepera chonchi, muzamanga mtambo, iwe ndi wa police? Kudzichemerera koma kuyankhula zopusa, paja umbuliwu ndi andale omwe eti? Tangoperekani maganizo anu osutsana ndi mtambo ndi andale koma akhale maganizo olongosoka osati zopusa ngati izi.
Iwe ndiwachamba kwambiri uzayelekeze kummanga ntambo uzaone kut kumpoto ndiziko palokha
Ntambo akuyenera kumagidwa, woipa
Uchisiru wanu ndiumene unakutulutsani dpp and udf ure not holy ndipo am promising yu guys simuzawina unless muzasinthe kachitidwe kanu
Mdala iwey according to your speech tikuziwa kut ndiwazipani ziwiri watchulazo km born kalindo musiye pliz leave that Guy alone pliz,fundo zako ndizabwn ndithu km panga zako
Uyu ndichitsilu kwambiri, ife ngati amalawi amaliseche akumwera sitikuwanaso iyeyu afune asafune tonse alliance iwinaso. Padziko lonse lapansi tikati zitukuko ndikumanga maziko atsogolo la mawa. Galu iweyo tanena zomwe amaliseche akumwera ndi DPP ndi UDF zomwe anachita zomwe zikupindulila amalawi lero lino kwa zaka 6 zomwe analamulira amalisewo ukuwatamawo. Kumangoyika Miyala basi ndalamazo mkumagawa kwa anthu akumwera chimenecho ndi chitukuko? Mbombela university ndalama aGalu inu adpp ndi UDF mwakhala mukutenga kwa zaka 6 zonse pa budget yaboma koma mpaka tinakuchotsani m'boma musanamange mbombela university. Sizokhazo ndizambiri ndipo iwalani zoti muzalowaso m'bale aGalu inu loko MEC chair person akatakhala mwana wa amaliseche akumwera simungawine chisankho. Anthu oipa inu kwambiri akudya anthu ndi mafupa omwe
😂😂😂 agalu kusekana zikundo , chakwera wako wapanga chani apart from devaluation, kukwera Kwa zinthu ndi corruption. Zogawa ndalamazo Aku Lilongwe kukasiya Mesa akumalandira ma 700 thousand pezan zina zolankhula akulu
Ameneyudi ndi ofoyila sangaone anthu mmene akangulula njinga zamoto ndi mmidzi momwe. Kabaza sanayamba nthawi ya DPP. Pano mumuuze akayime mmaboda akaowone ndi njinga zamoto zingati or zakapalasa zikulowa
I doubt the claiming here in that he is a seasoned and shrewd politician. Sound knows nothing other than being a blind royalists. He is a just a supporter of DPP and UDF as he voluntarily confesses herein. Cant understand what he is up to begging for DPP and UDF sympathy. He thinks he can advise Nankhumwa yet he needs advice himself. Nankhumwa will shame them by dividing the DPP vote. He understands very little about the Nankhumwa effect, talking about 'alibe ndarama zopangila' ma branch, what a warped political mindset. And praises fello tribesmen what do does he think he will succeeds from such mindset. He thinks kuyankhula bwino its about god washipping kkkkk and boot licking. The tongue can tell who what he is up to. To hell with your DPP
Speaker has just expressed brutality no connection to the mentioned kongoresi munthuyundi mwana pa ndale. You are not even a political man. UDF komwe ipite uzizimuka. DPP AND UDF ilipo?
Mani tangokambani zina ngati zokamba zatha siyani kulankhula koma sitepe mwalowayo palibe chomwe mupezemo boooooooooooooooooon kaliiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiidooooooooooooooo mmmm man timamukonda kwambili
Mutha kunyoza enawo koma The Dcccc analapa ndipo he is here to stay uyu alowa UDF /Dpp pompa
Musiyen bon kalindo ndi pulezindet wa anthu osauka ndipo ndiyenkhao akulimba mtima kumenyela nkhondo amalawi
Inuyo mutu suli bwino ineyo sungandiyankhile zopusa iweyo ndalezo unapangapo chani kuchita kuzichemerera za ugalu basi