Anthu Andale Amadana Ndi Chilungamo - Bon Kalindo
ฝัง
- เผยแพร่เมื่อ 1 พ.ค. 2024
- On Nyasa VoiceBox, Bon Kalindo says, Politicians do not like the truth, ,even when they are fully aware of the truth. He is saying this in response to the speech made by Timothy Mtambo in Lilongwe during the AFORD rally at Chinsapo on May 1, 2024.
Pa Nyasa VoiceBox, Bon Kalindo ati, Andale sakonda chowonadi, ngakhale akudziwa bwino za chowonadi. Akunena izi poyankha zomwe Timothy Mtambo adalankhula ku Lilongwe pa msonkhano wa AFORD kwa Chinsapo pa 1 May 2024.
#malawi
fire fire kukhazura kukhazura muuzeni mbuzi yo dziko sakuyendesa bwino
may god be with you mr man bornte
Congratulations Mr Bon , good speech
Congratulation president wa amphawi ❤❤❤
Born kalindo
Zoonadi anthu andalewa ndi abodza adyela ozikonda okha mbuzi za anthu atizolowela amalawi ife
Straight talk mr DC
I don't trust them even chilima atamwela relo mbola
The D.C. ❤❤
Mr bon kalido athuwa ndi agalu machendawo a mcp wose
Kodi Inu amalawi osamalimbana ndi za ndale ndizolemba kale mwini wake mulengi tingolakwa nazo
Anangokhala tchendeeee,😅😅😅😅😅............hahaha MrDC apa nde mwa,,
Akalindo inuyo ndiwomenyela ufulu kwa athu zoona koma musamapange dzagenest ndi muthu ai timabvota ndiife akumudzi inutu mudakhumudwa atakusiyan pakabinet yoyambilila ndiye musamakhale ngati inu ndi abwino mukat andale inu simudaluze pachisakho musatitopese mudziwe
Da
AXA buses
He is confused man he has nothing to deliver to Malawi
Kkkkkkkk
This guy is finish, people have lost trust in him
Kkkkkkkkkkk Eeeeee