Kathetsedwe ka mirandu ya Katangale sikakuyenda bwino. Adandaula ma CSOs Malawi

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 7 พ.ค. 2024

ความคิดเห็น • 6

  • @jamusnamwino-br2iz
    @jamusnamwino-br2iz 11 วันที่ผ่านมา

    chabwino takuvani ife tidikira inu amabugwe Bola zimenezo mwanenazi muzikwanirise kodi mulipo mungomuyang'ana chakwera akuononga zikomo ayi takuvani

  • @GrecianWyson
    @GrecianWyson 11 วันที่ผ่านมา

    Siyinu nokha amene mwakhumudwa inoso zandinyasa kwambili

  • @GrecianWyson
    @GrecianWyson 11 วันที่ผ่านมา

    Komaso mulandu wachilima waumbavawo wawuthetsa bwanji mlanduwo chanukhayo nayeso ndiwakuba

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl 11 วันที่ผ่านมา

    Galu amene akuthesa milanduyo ndi mbavanso akulandila ndalama

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 11 วันที่ผ่านมา

    Mukulu ameyu amaziva ngati wazeru ndiyenkha kuti azithesa milandu yakuba motere osapereka zifukwa wandikwiyisa kwabasi si munthu woti azikhala paudindo

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 11 วันที่ผ่านมา

    Komaso vuto amabungwe nanu si muli serious . Ena amabungwe andapereka masiku kuti ma passport sakutulukwa mokwabila minister wa immigration zikhale ng'oma atule pasi udindo koma mupaka pano akugwirabe ntchito only bon kalindo munthu wolimba mutima boma ili latitenga amalawi ngati zisilu.mcp ikanatha amene munayibweresa mitu ndiyo zungulira kwabasi anatizuza from 1964-1994 akutizuzatso 2020 -2025 hmmmm chipani choipa kwabsi sichizasintha