Kodi mwamva zomwe akuti anayankhula Chilima ndege ikukagwa kwaipa osati masewera

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 22 มิ.ย. 2024

ความคิดเห็น • 376

  • @stephenkamenya6869
    @stephenkamenya6869 5 วันที่ผ่านมา +14

    Aaah the guy seems to be comfortable in his speech. Wouldn't sound like that during the act

  • @johnnyambi6187
    @johnnyambi6187 5 วันที่ผ่านมา +2

    Zopusa ndege ikukagwa he can't speak that calm...stop mudslinging the president please ngozi zimachitika

  • @SinoyaNeva
    @SinoyaNeva 5 วันที่ผ่านมา +10

    Akufananadi ndi chilima's voice

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj 5 วันที่ผ่านมา +4

    Koma anthu umbuli edit mpaka makape azikhulupirila zimenezo ngati ndi umboni pitanawoni koyenela

  • @murraykaliwo6638
    @murraykaliwo6638 5 วันที่ผ่านมา +3

    Koma inuyo ndege yoti ikukagwa munthu angamayankhule modekha choncho, kodi a Malawi mukusowa zochita ngati winiko eti. Nonsense. Palibe umboni ulionsetu apa 😂😂😂

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 5 วันที่ผ่านมา +10

    It is a voice of Chilima. Anthu akuliranso mu video imeneyi. Koma nkhanza imeneyi. Ufiti umenewo.

  • @allanwadi2579
    @allanwadi2579 5 วันที่ผ่านมา +3

    Pa ngozi ya ndege sounding as calm as this? i have my doubts over this .

    • @petrokagona1708
      @petrokagona1708 5 วันที่ผ่านมา

      You don't have to doubt anyway. This is totally cheap propaganda.

  • @rashidadan2533
    @rashidadan2533 5 วันที่ผ่านมา +12

    Tidikilekaye , chakwela waitana ma butchala ogulisa nyama aku German Kuti azayeze zangozi ya ndege

    • @MosesNdebele-kc2cp
      @MosesNdebele-kc2cp 3 วันที่ผ่านมา

      ayi Anthu amenewa Ali ndi mashop ku Germany ogulitsa nyama za Anthu kuteroku abwera kudzawoda kuno ku chipani Cha m c p, chifukwa akamati (m)payekha amatanthaudza magadzi ndiye (.c) amatanthaudza kuti chuma (p) amatanthaudza kuti pofuna kulemera.

  • @user-ri8em6my2e
    @user-ri8em6my2e 5 วันที่ผ่านมา +6

    Mau akumvekadi achilima and akuyankhula motaya mtima kuti zavutapo basi 😭😭😭😭😭😭

  • @Stvz-t3n
    @Stvz-t3n 5 วันที่ผ่านมา +3

    The fact that when he died he had his rosary in his hands, looking at how ready he was for his death when speaking during his rallies and interviews, and how fearless he was in his life on earth. Speaking with calmness was one of his well known characters, on top of that he carried his rosary in his hands meaning he had time to pull it out and start praying and he actually knew that was the end of him and made peace with it. Chilungamo chidziwika black box ikapangidwa examine
    I can't just3 if this is real or no but it appears to be live🤝

  • @MsondaBanda
    @MsondaBanda 5 วันที่ผ่านมา +3

    Vilije ntchito,ivo lindizgani dankha bapenje ivyo vili kuchiska kuti ndege yiwe,vinyake ivi mupangiskenge navo muzumbwani muchalo,

  • @user-er2jv3nn4g
    @user-er2jv3nn4g 5 วันที่ผ่านมา +14

    Aaaa ifeso tikufuna chilungamo koma uyu ndamukaikira si chilima

  • @cynthiambalawira478
    @cynthiambalawira478 5 วันที่ผ่านมา +5

    Ndi Chilima yemweyo palibe za edit

  • @PreciuseMBinga
    @PreciuseMBinga 5 วันที่ผ่านมา +2

    Inuso amavilta zith ngt izi zikafika mudxihal nazo chidwi Osapanga post mwachangu .ifa ya chilima isakhaly ngt yot ena apezerepo ndalm

  • @user-sz9do9dd4b
    @user-sz9do9dd4b 5 วันที่ผ่านมา +11

    Mmmmm ayi zongopanga edit zimenezi

  • @AlfredKachala-ni1vc
    @AlfredKachala-ni1vc 5 วันที่ผ่านมา +4

    Mabodza izooo

  • @patrickchikoti5682
    @patrickchikoti5682 5 วันที่ผ่านมา +10

    Mau awa ndi a Chilima and mungathenso kumva anthu akulira pansipansipo.

    • @user-bh9in5vv8q
      @user-bh9in5vv8q 5 วันที่ผ่านมา

      Akupusitsani si chilima edit ya yenda pamenepo ,munthu oti Ali mu ndenge yoti ikukagwa sangayankhule mwa confi choncho

    • @andrewwilliemagombo7417
      @andrewwilliemagombo7417 วันที่ผ่านมา

      Iwe nde kayatu

    • @andrewwilliemagombo7417
      @andrewwilliemagombo7417 วันที่ผ่านมา

      Great

  • @user-vb1iq5un5p
    @user-vb1iq5un5p 5 วันที่ผ่านมา +3

    Uchitsuru mukupangawu... let him rest in peace

  • @user-rl5zq1qr4d
    @user-rl5zq1qr4d 5 วันที่ผ่านมา +6

    Ngozi siyamasewera munthu ikamachitika ngozi yoti apa kupangira mwina tifa palibe angalongosola modekha amayankhulmwamantha komanso mokuwa ngakhale voice yako imathawa apa zikumveka ngati Ali mu office coffee Ali pambalipa zopeka izi ndili ndi chikhulipiliro kuti zowona zeni zeni zimveka osati izi

    • @CharlesPhiri-ds1rk
      @CharlesPhiri-ds1rk 5 วันที่ผ่านมา +1

      ❤❤❤❤❤❤

    • @monicahmtambalika2611
      @monicahmtambalika2611 5 วันที่ผ่านมา +1

      Zoona

    • @petertaulo8014
      @petertaulo8014 5 วันที่ผ่านมา

      Maganizo anthu opanda ubongo omwe mukunena apawa, zimathe ife tazionapo zikuchitika

    • @user-bh9in5vv8q
      @user-bh9in5vv8q 5 วันที่ผ่านมา

      Koyambako munthuyu mawu anawagwira but anamutaika paja wanena kuti this is the people that decided to clash the plane,pamenepo wasokonekela wawataya mawu a chilima anayamba kumunthawa

  • @MebleNgulinga-hi6rg
    @MebleNgulinga-hi6rg 5 วันที่ผ่านมา +2

    This is the voice of chilima why you killed them why?

  • @DavidJackson-ox4xm
    @DavidJackson-ox4xm 4 วันที่ผ่านมา +1

    Ndiyemweyodi ndithu nkhzanza zoyipa kwambiri

  • @MwanundaEmmanuel-nb5dk
    @MwanundaEmmanuel-nb5dk 5 วันที่ผ่านมา +4

    Exactly 💯 chilima

    • @andrewwilliemagombo7417
      @andrewwilliemagombo7417 วันที่ผ่านมา

      Kuli app yopanga voice ya munthu mverani bwino ndiyopoila

  • @IshimweLeonard
    @IshimweLeonard 5 วันที่ผ่านมา

    It's not him, the voice is calm and confident

  • @RaymondKaumba
    @RaymondKaumba 5 วันที่ผ่านมา +3

    How the hell can someone open a phone on a plane 😂😂😂. Please be honest

    • @inno265
      @inno265 5 วันที่ผ่านมา

      I'm not arguing if the voice note is real or not.... Koma what do you mean by asking rhetorically if "someone can open a phone on a plane"?
      Simmadziwa kuti munthu amatha kugwiritsa ntchito phone mundege?

  • @user-rg4du4vu9r
    @user-rg4du4vu9r 5 วันที่ผ่านมา +1

    Nde pot tinanva kt ma phone onse anthuwa ana pangidwa haki madata nde izizi zikutheka bwanji eeeee china mbararatu

  • @HaroonMaundala-lg5lg
    @HaroonMaundala-lg5lg 5 วันที่ผ่านมา +8

    Yes ndi chilima

  • @I.paulbanda
    @I.paulbanda 5 วันที่ผ่านมา +1

    Mu ndege muthu amaika phone pa flight mode how can one have an access to send voice note,, by the way did they recovered any telephone which was used by anyone who boded the plane??
    This is rubish mwabanthu

  • @AdamBwanali-kr5fw
    @AdamBwanali-kr5fw 2 วันที่ผ่านมา

    Ndi mawu a Dr Chilima ndipo gulu lini likumveka pansi pansipo likulira

  • @MustaphaCassim
    @MustaphaCassim 5 วันที่ผ่านมา +2

    Plz my br all sister osaopa asatopa bweleni poyela ndi v n ya chilima ndiyofuni kwambiri we are sic and tired with ndianthu awa ivara oversize jacket ndalama zakuba

  • @MisheckNgwila
    @MisheckNgwila ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kumakalima kuma dimba can be a best option

  • @MonicatimanyeShaba
    @MonicatimanyeShaba 3 วันที่ผ่านมา

    Ameneyo ndichilima anamupha bus ANTHU OYIPA mutima

  • @RaymondKaumba
    @RaymondKaumba 5 วันที่ผ่านมา +1

    Umbuli ndi matenda
    Thats an edit . specialists can reverse it then you can see how stupid some are

  • @user-os7qt6lw2c
    @user-os7qt6lw2c 5 วันที่ผ่านมา +2

    Nuh he isn't the one..this guy was speaking with confidence wapa ngoz akudzwa zot he's going to die sangayakhule modekha conco,even voice yao yolira bwez ili yokuwa kwambiri

  • @MEDSONGWADILA
    @MEDSONGWADILA 5 วันที่ผ่านมา +1

    Akt chakwel ndi chimwendo ndi anthu ena ndamene apanga crash the prane

  • @GeorgePhiri-ub2of
    @GeorgePhiri-ub2of 5 วันที่ผ่านมา +2

    ai simau achilima ai zikusiyana ndithu

  • @lawrentchadeluka1785
    @lawrentchadeluka1785 5 วันที่ผ่านมา +1

    He sounds so calm for a situation ya accident. Its not chilima for me

  • @HarryMsudzula
    @HarryMsudzula 5 วันที่ผ่านมา +2

    Koma pangozi ngati imeneija yandege ikugwa munthu ndiwe Malawi sungapeze mpata olankhulanso chingelezi ngati kulira umalira muchichewa Kulankhulanso kumayenera kukhala muchichewa popeza chingelezi timalankhula pamtendere choncho mawu awa ngochita kukonza maganizo anga

  • @PreciousDalitsoChiswe-dw4fy
    @PreciousDalitsoChiswe-dw4fy 4 วันที่ผ่านมา

    Wow there is God in heaven everything is about to come out

  • @user-ww1lu2ch6z
    @user-ww1lu2ch6z 5 วันที่ผ่านมา +1

    This is not voice of chilima it's just a stunt

  • @phillipchiotcha3197
    @phillipchiotcha3197 5 วันที่ผ่านมา +2

    Koma mesa kuli ena amatha kuyankhula ngat ma president

    • @yosefemichael7588
      @yosefemichael7588 5 วันที่ผ่านมา

      Exactly boss koma sali president uja amayesezera APM mesa amaveka ndendende APM

  • @user-xy9vz6jj4u
    @user-xy9vz6jj4u 5 วันที่ผ่านมา +1

    Km sikumveka mwaphuma ofcz tikufuna choona chziwike

  • @AnaffSayamika-uh6vg
    @AnaffSayamika-uh6vg 5 วันที่ผ่านมา +2

    Chilima ameneyo 🤔🤔🤔🤔 Km chakwela anena bho

  • @giftdavie240
    @giftdavie240 5 วันที่ผ่านมา +1

    Who has released the audio?

  • @adamu1287
    @adamu1287 5 วันที่ผ่านมา +2

    Komano ineyo menendavelamo ndimawu abwana chilima

  • @UlemuKamanga-yn4jk
    @UlemuKamanga-yn4jk 5 วันที่ผ่านมา +1

    Ayi ,lirimelo nanga ? angopanga edit ,idali interview inayake atachititsa msonkhano,nde angolumikizalumikiza kut zimveke motero ,mayankhulidwewo Inu mkut nga CHILIMA,zikuchita kuonetsera kut ,akuuza wina wake zangozi iye atapulumuka pangoziyo , tiyeni tilondolo galamala wachichewa ,akakumanganj muziti Boma ndiloyipa?

  • @sanidamumba731
    @sanidamumba731 5 วันที่ผ่านมา +2

    Ndi edit iyi

  • @EllanivyJimmy
    @EllanivyJimmy 4 วันที่ผ่านมา

    Aaaa zopeka iziii....pangozi sungakhare ndi pata omalakhula modekha chochi...zeni zeni ziziwika koma osati iziii

  • @marthamwenelupembe1188
    @marthamwenelupembe1188 5 วันที่ผ่านมา +5

    Ngat ndi chilimadi mulungu alowelelepo ngati za boza mulungu amulange yemwe wapeka mauo...chifukwa akulakwilanso mzimu wa Skc

  • @StevenLazaro-nm9pk
    @StevenLazaro-nm9pk 3 วันที่ผ่านมา

    This is real voice of skc

  • @jacobchimtaka3057
    @jacobchimtaka3057 5 วันที่ผ่านมา

    komaso ndani yemwe waipeza voice imeneyo musatizunguze nazo mutu ngati pali chilungamo chiwoneka chifukwa apa aliyese akhoza kupanga ngati nayeso anali mundegemo

  • @alfredbanda1693
    @alfredbanda1693 5 วันที่ผ่านมา

    A Malawi anzanga mulikonda dziko lathu tiyeni tisamale chifukwa ndife tomwe tingayambitse chisokonezo mudziko muno chifukwa kaya chofuna kutchukitsa channel chanthu or kapena ife mwini dziwani kuti khondo ya kurwanda amene anayiyambitsa anali munthu pa air like mene mukupangiramu so lets be rensiponsible fot better malawi tomorrow

  • @user-cd4df3vg4y
    @user-cd4df3vg4y 5 วันที่ผ่านมา +1

    Yes, anali chilimaaaa 😢😢😢akudziwa kuti basi uyu wankuluyu watipweteka. Antenna ekhaaa. Ndiye Mulunguyo ameneyooo . Wanva kuti pwetwe nkamwa mwake chikumbumtima chimumenyeee 😢😢😢

  • @LeonardMhone-cg1tk
    @LeonardMhone-cg1tk 5 วันที่ผ่านมา +2

    Ndi Bwana Chilima 😭 😭

  • @PreciousMazoni
    @PreciousMazoni 5 วันที่ผ่านมา +1

    Amene adaba mafoni ndege itagwa mwamugwila ndipo nthawi idalipo yodaba ndenge ikupita kwa kugwa edit imeneyo

  • @user-vm7iz6oz6r
    @user-vm7iz6oz6r 5 วันที่ผ่านมา +1

    Zomwexo ndipomwe sapatha masiku abili chilichose tichiwa

  • @douglasmakina1766
    @douglasmakina1766 5 วันที่ผ่านมา +2

    Zikunvekadi kuti ndi achilima

  • @GradwellIsaac
    @GradwellIsaac 4 วันที่ผ่านมา

    Kodi munthu pa ngozi angamayankhule mwa pa easy chonchi guys tizikhala serious mmm God have mercy of as

  • @user-ql9lo9ze5o
    @user-ql9lo9ze5o 5 วันที่ผ่านมา +1

    Rest in peace our president...we miss you chiyembekezo chathu chinali pa inu 🥲🥲😭

  • @user-ig9qk6gi6g
    @user-ig9qk6gi6g 5 วันที่ผ่านมา +1

    Mundege mumakhala network. Umbuli basi.
    This is Chilima indeed

    • @Musa1828-l5d
      @Musa1828-l5d 5 วันที่ผ่านมา

      Mbuli ndiwe audio simayendera network

  • @CathyYassimin
    @CathyYassimin 5 วันที่ผ่านมา +1

    Ndimawu a SKC amenewo koma mulungu atifungatire tonse

  • @jomochirwa
    @jomochirwa 5 วันที่ผ่านมา +4

    Esh azanga wosamatelo ayi kumangopeka zinthu mutenga nazo machimo ndithu tonsefe tili ndi chison ndi ifayi koma wosamatelo choonde amalawi.

    • @EmmanuelNkosi-ts8bn
      @EmmanuelNkosi-ts8bn 5 วันที่ผ่านมา

      Amalawi ndi anthu omvesa chisoni pazochita zawo

    • @YusufuGama
      @YusufuGama 3 วันที่ผ่านมา

      Tamakambani by goes by goes

  • @PempheroAlufandika
    @PempheroAlufandika 5 วันที่ผ่านมา +1

    Amenewa ndiau achilima eni eni ndipo ndioona koma inuyo mwaidula simunapotilize

  • @ChimwemweKondowe-nj4lx
    @ChimwemweKondowe-nj4lx 5 วันที่ผ่านมา +2

    All you who're opposing that this is not Chilima's voice are snakes because that's the pure voice of Chilima

    • @JusticeNyirenda
      @JusticeNyirenda 5 วันที่ผ่านมา +3

      This is Chilima's voice, I can hear people crying....kwinakonso ndege ikumveka

    • @DirectorSamez
      @DirectorSamez 4 วันที่ผ่านมา

      Munthu oti akupanga ngozi sangalakhule modekha chochi

  • @JohnMzenda-lq9gt
    @JohnMzenda-lq9gt 5 วันที่ผ่านมา +1

    Simau achilomawa bonza .nokha simukuwa iai

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole 5 วันที่ผ่านมา +2

    The chilima himself

  • @jawbone8901
    @jawbone8901 5 วันที่ผ่านมา

    Yes that's chirima's voice ? My fellow African the is that chilima was assassinated please you have take action to arrest chakwera & his killers

  • @grayp98
    @grayp98 4 วันที่ผ่านมา

    Koma bodza lakelo 🤣🤣🤣 mau a mu ndege nde akulirawo akulira kuti😂😂

  • @CharlesBENE-tv9wn
    @CharlesBENE-tv9wn 5 วันที่ผ่านมา +1

    Aaaa izinso ndiye ayi

  • @ulemummangisa3150
    @ulemummangisa3150 5 วันที่ผ่านมา +2

    😢yes the voice is his

  • @UlemuKamanga-yn4jk
    @UlemuKamanga-yn4jk 5 วันที่ผ่านมา +1

    Zabodza izi Si CHILIMA uyu ,nanga phokosolo ? Za edit izi ,nanga munthu womwalira angatumize uthenga ?phokoso la pa msonkhano

  • @francis12fombe54
    @francis12fombe54 5 วันที่ผ่านมา +1

    Si chilima ameneyo ngodzi simasewe

  • @user-pf5er7gc9s
    @user-pf5er7gc9s 5 วันที่ผ่านมา +2

    Simau achilima awo ai please tingolakwa chabe tatiyeni timusiye mulungu akhale mulungu.

  • @WitinerHamilton
    @WitinerHamilton 5 วันที่ผ่านมา +1

    Mawu amenewo si a chilima

  • @user-lp2sd7lt8b
    @user-lp2sd7lt8b 5 วันที่ผ่านมา +1

    Akuchita kuyankhula modekha ndege ikukagwa. Koma guys edit

  • @user-lc3sw8iz2g
    @user-lc3sw8iz2g 5 วันที่ผ่านมา +1

    It can be him, talking while he was in Panicking due to what was supposed to happen.

  • @madalitsomisomalih5411
    @madalitsomisomalih5411 5 วันที่ผ่านมา

    Mawu ndi a chilima,pasi pasi anthu akuveka akulira ndi sound ya ndege.

  • @user-wy2ij5ic8y
    @user-wy2ij5ic8y 5 วันที่ผ่านมา +2

    Exactly mawu acilima awa

  • @ANDERSONPARTISON
    @ANDERSONPARTISON วันที่ผ่านมา

    Zangopangidwa munthu oti Ali pachiphinjo sangayankhule choncho mwamtendere

  • @HallimaMakwinja
    @HallimaMakwinja 5 วันที่ผ่านมา +4

    Ndizoonadi awa analidi Mawu abwana Chilima

  • @monicagondwe228
    @monicagondwe228 5 วันที่ผ่านมา +3

    Kwa amene anapangako ngozi nthawi yolankhula modekha choncho siikhalapo chifukwa zinthuzo zimachitika mphindi zochepa kwambiri ndipo nyengo imeneyo mutu sugwira bwinobwino chifukwa kumakhala kkuti wadzdzmutsidwa mwina imfa yokonzekera ndi yomwe ungadekhe nayo choncho koma ya ngozi eeisshhh!!

    • @tamalangoma2765
      @tamalangoma2765 5 วันที่ผ่านมา

      You are very right my sister ,I agree with you 100%

    • @user-xo8ms5wh2s
      @user-xo8ms5wh2s 4 วันที่ผ่านมา

      Musaiwale dege ija inaima mphindi 10 amene anali mu 😊degewo anadziwapo kanthu ndithawi imene anthu amaganizila ndikutulutsa mau

    • @DoreenAllan-tg1dz
      @DoreenAllan-tg1dz วันที่ผ่านมา

      Zimatheka mumphavu yamulungu kwanthu zachitikanso Ngati nzomwezi anapanga ngozi anakwanisa kutenga phone kwauza anthu awili Kuti ndapanga ngozi ndikumamwalira

  • @rhodankhata3234
    @rhodankhata3234 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Koma pakumveka sound ya Ndenge ndikulira kwaazimai.

  • @MEDSONGWADILA
    @MEDSONGWADILA 5 วันที่ผ่านมา +2

    Ndi chilima meneyo ndamunvetsettsa kwambili akt

  • @VictorNyasulu
    @VictorNyasulu วันที่ผ่านมา

    Vutorano mukufuna wumboni wanji kod chilima ndaniangasowe mau ake

  • @EphraimMokwebo-yo7fs
    @EphraimMokwebo-yo7fs 5 วันที่ผ่านมา +2

    Ndiomweo abwana athu

  • @CosmasKasinja
    @CosmasKasinja 5 วันที่ผ่านมา

    Ndiyemweyo late skc chilungamo chake

  • @user-cp4qt9hs8w
    @user-cp4qt9hs8w 5 วันที่ผ่านมา +3

    Yaaa ndiyemweyo chilima fazi ina ikulila pasipasipo

    • @KennethChagunda-gn8kg
      @KennethChagunda-gn8kg 5 วันที่ผ่านมา

      Sometimes onsamangokhulupilira zilizonse gayz. Munthu oti akukwagwa pa ndege sangayankhule voice of that tone . Social media tisamaitengere kwambiri.

  • @raymondthewethe4627
    @raymondthewethe4627 5 วันที่ผ่านมา

    Bwezi nditayankhula kwambili koma ndilibe Lawyer, anyway RIP SKC

  • @AidaoChitanda
    @AidaoChitanda 5 วันที่ผ่านมา +2

    Mau amene akumvekawo sichilima ayi Takana zimenezo

  • @user-ky8eq5ek1p
    @user-ky8eq5ek1p 5 วันที่ผ่านมา +2

    Ndizoona ndimaua Achilima

  • @AudettaYohanie-fl3oc
    @AudettaYohanie-fl3oc 5 วันที่ผ่านมา +1

    Ndendende voice ya chilima and kukumbekaso sound ya ndege and kulira kwawanthuso😭😭😭

  • @MbisaOngani-g6o
    @MbisaOngani-g6o 5 วันที่ผ่านมา +1

    Ndiyemweyo ingomvani sound ya engine ya ndegeyo ndi Julie's kwa azimayiko

  • @JackKalua-vf8bo
    @JackKalua-vf8bo 6 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    What about the background noise from the audio? Should we say amadziwa ndikupitabe? Guys😮😮

  • @muhammedmkamanga1207
    @muhammedmkamanga1207 5 วันที่ผ่านมา +3

    Mu ndenge simukhala network though

  • @mussahchikwenga6194
    @mussahchikwenga6194 5 วันที่ผ่านมา +2

    Ndimawu achilima awa sindikukaika ndiomwewa 😭

  • @conique19
    @conique19 4 วันที่ผ่านมา

    Don't forget kuti kunja kuno kuli anthu amaesera voice ya munthu exactly nde sitinganene chilichonse n ankunveka kuti munthuyo anali calm as if nothing is happening

  • @GodisoneNoel
    @GodisoneNoel 5 วันที่ผ่านมา +2

    Ndichirima

  • @FadweckLifa
    @FadweckLifa 5 วันที่ผ่านมา +1

    Akumveka mau a Chilima. Mmene ndamvela

  • @arafatMtyala-bo8ev
    @arafatMtyala-bo8ev 5 วันที่ผ่านมา +3

    Voice ya chilima imeneyo, koma chomwe chingafunike ndi chokuti yemwe anatumizila voice note imeneyo abwele poyela aliwuze dziko lamalawi

    • @user-lg2ws2ki3d
      @user-lg2ws2ki3d 5 วันที่ผ่านมา +1

      Za umbuli basi ndiye adzuketu ndiye

    • @WitnessPhiri-zr9uf
      @WitnessPhiri-zr9uf 5 วันที่ผ่านมา

      Mukufuna amupheso or amumange sangazibwelese poyera akuopa kuphedwa amalawi situkufuna chilungamo

    • @YusufMillion
      @YusufMillion 4 วันที่ผ่านมา

      ​@@WitnessPhiri-zr9ufzabodza basi,azikinamizani inuyo makadetio

  • @user-pz7tf4js2t
    @user-pz7tf4js2t 5 วันที่ผ่านมา +2

    That is chilima not propaganda 😢

  • @soulmacheso3305
    @soulmacheso3305 3 วันที่ผ่านมา

    Simau ake achilima bwezi akuyankhula mwa befu komaso voice ikumveka pansi pasiyo ikumveka yochita ku balancer pa computer