You can think so my brother the way that I spoken, I'm so sorry if I spoken real bad to you my brother, but to wait it takes time but not finished, the only problem even every one can have is that, can need quickly process that come with disaster. The reason is that no one can solve the problem while is in high temperature, if the judge he needed to mediation to release that anger to fall to judge properly because of avoiding rejection my my nation. So if we lose then we getting a certain explanation to explain how how was happed, then we need to be in waiting in God, then also we needed to have the same meditation while we are waiting, without judging who was wrong my brother 🙏🙏🙏
Yes, mawu athu Athan kudal chiyanjaniso, komanso mawu athunso, Athan kuwononga mimoyo yathu a ale. Thikhale mundawi imeyi chifukwa Pali late vice president amakhonda not amamusa ndalam ayi, koma that way of living, that was reacted to every Malawians, including their families also. 🙏🙏🙏
Ife achiyao tilavinidwa kuli nyimbo imodzi yomwe ikugwilizana ndi ulamulilo omwe tili lelowu nyimbo yale nayi (tatenga ufumu kupasa chelule koma chelule sapanga zabwino) tikati chelule ndi kambalame kakang'ono koma kosokoneza kwambili.Chelule wathu wathu wa lelo ndi Chakwela
See now, we can't knows all the results in peaceful even without any threat to any Malawian, but let us to try be be patient in time of this, because our mouth can create something that can bring us peace, then the same mouth can bring some thing that gonna brought many troubles to certain people who are truly waiting the results that the government saying we need to wait, then please in patiently, all we shall knows in truth what was going wrong to lose those people who was represented in harmony. Your speech sir, you are totally will brings wrong to the Malawian nations, If you had any issues with that party, yes but this time all what we need is to know what was happening without any threat of starting the war. If you speaking this words to the government while they given to us the purse to wait., then what do you of recording this record if you like Malawians sir? 🙏
Mukufuna kukhetsedwe mwazi ya anthu angat this year kumalawi kuno? Ifa zmbiritu mukuziitanazo, osangobwera uzalande bomali bwanj ngat uli wa nzeru zochuluka.
Ine ndine wa chitonga koma zikhale ngoma ndionyasa ndi mtima mwake momwe yhoooo😂 munthu amaoneka ngati golila munthu watundu wanji ameneyu koma paliamentso nayo imangolowadi ndi anyani omwee
A zikhele Ng'oma ndi a moses kunkuyu a chakwela amawangwiritsa ntchito monga chimozi chawo amene ajawo, chifunikila kwambili a Malawi ndi choti anthuwa afunika agwiridwe ndi mumenyedwa kuwopya komanso kuwotchedwa mayumba awo kuti atengerepo phunzilo komano kuononga katundu Ya ziko ndi kulakwitsa chifukwa dziko lathu ndilotsawuka ndi kale
Yes, all us that was happening mcp that was we were young, everyone knows that, but to give a blame to someone like if that was coming from God, we will going to be totally wrong, because we are not patient, then which result we can expect now, now we waiting in trusting? Please in this lose if God is inside, then there is no need to be hassle. Let's try ourselves to be patient in time of this. And please your mind is totally wrong, because you have been taken your mind with anger as the result, your followers shall going to run like headless chicken. Please sit down you need God to be derived, Be cool, we are not animals then why you troubling yourself to talking this words that going to lost our beloved families because of without patient 🙏🙏
Politics is a wrong mind desire that comes into that the real brain of any humanity who passed through that process, so when you are talking once it comes to this issue of not to getting all evidence, Take even yourself because your speech will going to brought disaster in that country before their reports comes to us to judge, my brother. Be patient please I promise, you to save others even who didn't speak about this🙏🙏💞 This is Malawian peace, not Uganda my brother, government is a government, and shall be the government for ever, if someone planned the desire to created the war, then that only certain person must be arrested before giving his problem of un understanding to the others.
Vuto la maboma omwe amasankhidwa after five years samayang’ana za momwe boma langochokalo sayang’ana zomwe ladachita mbuyomu.A Zikhale Ng’oma awa akuzunza mzika za dziko lino komano DPP iyi itati yawina,basi kuzangokhala kugona basi kuyiwala kuti anthu ngati Zikhaleyu ndi ena kuphatikiza Chakwera mwinimwiniyo onsewo akalowe ndipo apite kundende ya akaidi wamba kuti akaphunzire.
MCP yapala kuposa ma boma onse akhalapo pakatipa. Ofunika kuwamatcha amenewa. Osaononga katundu yemwe Kamuzu, Bingu ndi ena adapanga, target ma office awo ndi nyumba zawo akumanga zakuba zija 😅
Zoona guyz a Malawi ndimunthu opusa kwambili amatha kuona munthu nmodzi aziazuza koma onse chetechete kuopa kumangidwa don't u now kut no sweatt nogain
Powerful massage 💪💪💪 let's unite And fight together as Malawians
fighting together uku mukuononga dziko
I second you Sir
I salute you sir mumayankhula zoona let's not be quiet Malawians
Very interesting issues but you must more time to teach us more about this govt
You are my best Brother
Pangani what's app group as malawi concerned citizens kt tipange chimozi before pa 10
Ndipo
Komatu zikhale ng'oma dzikoli silake
Koditu adzachoka
Munthu wantundu wanji kunyasa ndi mavalidwe omwe
Amene ana winitsa mcp munapha ndiye akuwinitseni ndani
You can think so my brother the way that I spoken, I'm so sorry if I spoken real bad to you my brother, but to wait it takes time but not finished, the only problem even every one can have is that, can need quickly process that come with disaster.
The reason is that no one can solve the problem while is in high temperature, if the judge he needed to mediation to release that anger to fall to judge properly because of avoiding rejection my my nation.
So if we lose then we getting a certain explanation to explain how how was happed, then we need to be in waiting in God, then also we needed to have the same meditation while we are waiting, without judging who was wrong my brother 🙏🙏🙏
I support you bro
Yes, mawu athu Athan kudal chiyanjaniso, komanso mawu athunso, Athan kuwononga mimoyo yathu a ale. Thikhale mundawi imeyi chifukwa Pali late vice president amakhonda not amamusa ndalam ayi, koma that way of living, that was reacted to every Malawians, including their families also. 🙏🙏🙏
Very patriotic guy indeed. Safuna zachibwana
Mmmm ofunika kuchitapo kanthu anzathudi ku Kenya achinyamata ayesetsa kumenyela ufulu ana awo nafenso titelo Mulungu alimbali yathu
How can we meet and organize a protest?
Ndimomwemo bg man akutitenga ngati ife zisilu
Ife achiyao tilavinidwa kuli nyimbo imodzi yomwe ikugwilizana ndi ulamulilo omwe tili lelowu nyimbo yale nayi (tatenga ufumu kupasa chelule koma chelule sapanga zabwino) tikati chelule ndi kambalame kakang'ono koma kosokoneza kwambili.Chelule wathu wathu wa lelo ndi Chakwela
Ndipo Suleman ndi mp wacholungamo inenso ndimampatsa ulemu
Powerful message mr
Big palibe kulora nditu tilipo nditu musina lamulungu achoka 2025 chakwerawo woyama anali ndi kumalawiko pano dpp kpana UDF alamulire mzikolo inshall allah allah adalisa kumalawiko yaaa bhola zimenezo zikare chotcho
You're speaking my mind senior
Anzathu kuti Kenya atiposa maganizidwe ma protest achitike basi for the sake of our children's future
Honestly speaking boss 🔥🔥🔥🔥
Good message agreed 100%
Good Messnge my brother
Koma zoonadi . This guy is smart very smart Suleman
Njila yokhayo yoti tingathane ndi anthu amenewa nkuwawotchela katundu wawo period
Great
Zoonad brother zikoli likuoongeka ife tikuonatu, sizikuyendatu or pang,ono ndipo zikili aliyese ali ndi matha zithu zosakhalabwino ngat sife zika za ziko lino.
Wopanda zeru aw a inu muli uko mukupanga fundo zopusanzo bwerani kunoka; mudzayambe nsi ana ndazibale wanu kanako tidzakujoyineni , wosamangolankhula muli kutali mwamva.
Welcome to Nyasaland amwene koma mcp mmmmm sangakusiye aisee
I agree with you 💪💪💪💪💔
Zikhali pantumbopako Suleman ndowabwino kwambili koma zikhali akumaopseza ngati dzikoli ndilake mboleyake
Am great with you bro
Kodi vuto mumayankhula inu muli kutali komanso zikavuta simupezeka mubwele muzatsogolele ma demowo tione MCP sinabwele kuzacheza man
Zoonadi big Man ineso ndilimommo
Is true big tiyeni amalawi tingwirizane
Takozeka bg man kufela malawi, anytime ziyambika.dziko lamalawi akulamula ndi zikhale ng'oma ndi kunkuyu coz ndi amene akuona kwambiri. Tili leady
I agree with you 👌💪💪💪💪💪
Nkhani yoonadi iyi zikungofunikq aMalawi kudzuka kugwilana manja ndikuwathamangitsa
Honestly speaking
Honest sir
😢😢😢😢Lord have mercy on us 🙏
Kikikiki Nizoona my brother
Bravo guys this is the time for them to fall they fast forwarded their plans they missed out alot along the way hahaha
Kufuna ndimomwe dziko. Ma MP anu ndi ogona. Mwina kulikonse kufalitsa zonama ndi mulandu you must know this
Nanga tikuchedwa pati akanganya amenewa akuzuza nkhaza zawozi akaone kopangira, trauza lopanda size ija ativute za ziii
Ukudziwa iweyo ulikutali zomwe ukunena apazi sizabwino smple 2025 anthuwa tiwachotsa km zoyatsamoto dzikolathu lomwe mayazi nanuso anthu musamangoti zoona sakhala kuno ameneyu
Sakhala kuno koma ndi mmalawi MCP yationjeza kwambri
💯 agree
Kofunika,awone,zija zaku, Kenya ma demo akubwelawa,mpaka achoke .
Sowona ❤osalola
Only ALLAH who knows about 2025
Inshaa Allah
To be honest ma guys a mcp ndiankhanza kwambiri, let's not be quiet
😢Wb😢e😢😢😢😢😢
See now, we can't knows all the results in peaceful even without any threat to any Malawian, but let us to try be be patient in time of this, because our mouth can create something that can bring us peace, then the same mouth can bring some thing that gonna brought many troubles to certain people who are truly waiting the results that the government saying we need to wait, then please in patiently, all we shall knows in truth what was going wrong to lose those people who was represented in harmony.
Your speech sir, you are totally will brings wrong to the Malawian nations,
If you had any issues with that party, yes but this time all what we need is to know what was happening without any threat of starting the war.
If you speaking this words to the government while they given to us the purse to wait., then what do you of recording this record if you like Malawians sir? 🙏
Mukufuna kukhetsedwe mwazi ya anthu angat this year kumalawi kuno? Ifa zmbiritu mukuziitanazo, osangobwera uzalande bomali bwanj ngat uli wa nzeru zochuluka.
Aaa iwe ndiwe opupwatu look Kenya adha
Ine ndine wa chitonga koma zikhale ngoma ndionyasa ndi mtima mwake momwe yhoooo😂 munthu amaoneka ngati golila munthu watundu wanji ameneyu koma paliamentso nayo imangolowadi ndi anyani omwee
A zikhele Ng'oma ndi a moses kunkuyu a chakwela amawangwiritsa ntchito monga chimozi chawo amene ajawo, chifunikila kwambili a Malawi ndi choti anthuwa afunika agwiridwe ndi mumenyedwa kuwopya komanso kuwotchedwa mayumba awo kuti atengerepo phunzilo komano kuononga katundu Ya ziko ndi kulakwitsa chifukwa dziko lathu ndilotsawuka ndi kale
💪💪💪💪
Yes is true
💪💪
That's true my brother
Fact boss
Yes, all us that was happening mcp that was we were young, everyone knows that, but to give a blame to someone like if that was coming from God, we will going to be totally wrong, because we are not patient, then which result we can expect now, now we waiting in trusting?
Please in this lose if God is inside, then there is no need to be hassle.
Let's try ourselves to be patient in time of this.
And please your mind is totally wrong, because you have been taken your mind with anger as the result, your followers shall going to run like headless chicken.
Please sit down you need God to be derived,
Be cool, we are not animals then why you troubling yourself to talking this words that going to lost our beloved families because of without patient 🙏🙏
Kodi munthu amaoneka delo ngati chadzuka kumanda
Iwe namachende ukuti chani tikumva pain ukuwona ngati basi
Thiyendele 1bay Wan ikale wokumupa
Ma demo pa 10 mcp yationjeza
Politics is a wrong mind desire that comes into that the real brain of any humanity who passed through that process, so when you are talking once it comes to this issue of not to getting all evidence,
Take even yourself because your speech will going to brought disaster in that country before their reports comes to us to judge, my brother.
Be patient please I promise, you to save others even who didn't speak about this🙏🙏💞
This is Malawian peace, not Uganda my brother, government is a government, and shall be the government for ever, if someone planned the desire to created the war, then that only certain person must be arrested before giving his problem of un understanding to the others.
MCP iyiyi 2025 sitikuyifuna ichoke 🚮 palibe chomwe chachitika apart from kugwesa kwatcha ndi zina zobweza dziko mmbuyo
The government is allowing that
Fact
True
Nkhani mupange ziti chakwera athawe
Vuto la maboma omwe amasankhidwa after five years samayang’ana za momwe boma langochokalo sayang’ana zomwe ladachita mbuyomu.A Zikhale Ng’oma awa akuzunza mzika za dziko lino komano DPP iyi itati yawina,basi kuzangokhala kugona basi kuyiwala kuti anthu ngati Zikhaleyu ndi ena kuphatikiza Chakwera mwinimwiniyo onsewo akalowe ndipo apite kundende ya akaidi wamba kuti akaphunzire.
😂😂😂 anthu ambili a MCP bwanji amaoneka Ngati agalu ndi anyani
MCP yapala kuposa ma boma onse akhalapo pakatipa. Ofunika kuwamatcha amenewa.
Osaononga katundu yemwe Kamuzu, Bingu ndi ena adapanga, target ma office awo ndi nyumba zawo akumanga zakuba zija 😅
Sono inu mubwera liti siii mwati mademo achitike before July mubwera liti?
Zoona guyz a Malawi ndimunthu opusa kwambili amatha kuona munthu nmodzi aziazuza koma onse chetechete kuopa kumangidwa don't u now kut no sweatt nogain
That's true
Ndipo ndagwilizana nawe kakumane ndi bon kalindo and JB ndiye kuti tiyansa moto makawi
MCP singawinenso kufikira yesu atabwere
Osaopa nayeso dzinkhale Ng,OMA nayeso ikubwela thawi adzamangidwa panga talike bwanji
Chitsilu iwe,kumangokhalila kuloza zala azako,munthu wopanda ntchito iwe,galu wa DPP iwe!!!
😢iweyo udzakharapo kapena ufuna kuphetsa ana awanthu😊
Manthawa nde zokanikazo, zinthu zosiirana siziyenda
🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉
Zamphavu
Iweo ukutelo ulikut zam ukutsusa za ma demo ulikut iwe zukusangalasa
Don't compare wit Kenya Malawi kulibe anthu olimba mitima
Awa a mcp waa kwao kwatha
Ine ndi mampasa ulemu suleman
Akuopa kuphedwa MCP sikunyengelela ngati ananena live kuti izakhetsa mwazi kuyankhula ku mtundu wa anthu 😂😂😂
Go komkoooo
Eee mwatelo kd sono inuyo muzapitaso kumalawiko kd mesa muli kunja
Wopusa uyu. Afuna kusokoneza dziko.
I will be there
Paja a pule akutinyansatu, can't he just Resign please 😢😢
Komatu guys makolo kumawonana bwino bwino.bambo onyasa mai onyasa mubeleka chani? Zosatila ndizizi achina zikhalewa khope mamamammmmm😂😂😂😂
Musasiye kuwauza mau
Kodi Zikhale Ng'oma akunenedwayo ndiutiyo?😒
Ndipo makhoti Kaya akuganiza bwanji
Sulemani saopa ayi amayankhula alikonkuno, ena angotokota ali kunja kuopa kunjatidwa
Lero ndipa 28 ndie mademo B4 july mukuchedwatu osamayankhulira kutari mantha
Tiyen tigwilane manja tigwese boma
You are true bro Suleman and Kamulepo Kaluwa are Patriots.