Moya inuyo mumatha ndipo koma ndiye mumafukula nkhani zobisika thank you keep on updating us osaopa okufa lero safa mawa tonse tikudikira tsiku lakufa lomwelo basi iyaaaaa
Mr president wathu timakunyadilani always mmm zinthu zavuta akugawa ndrama amalawi akuvutika tikunena pano kumachinga ana awili amalila kamba ka njala km dziko muli president ife tili pa mavuto srs. Mr timakunyadilani ndipo ine ndizakhalaso nanu mpaka mpaka srs ulemu wanu la 40 likubwela agalu amenewa.
Moya inuyo mumatha ndipo koma ndiye mumafukula nkhani zobisika thank you keep on updating us osaopa okufa lero safa mawa tonse tikudikira tsiku lakufa lomwelo basi iyaaaaa
Ambuye azikutetezani brother mukumenyera Nkhondo mtundu wamalawi
Mumatiyimilira born calindo ndinu mfumu ya history
Pa 10 tili konko 💪💪💪💪💪
I love you brave man. I always follow your speeches . I am In Zambia and wish we had one man like you. Osaopa BOMA
Muthu waopsa kwambili 🎉
True and straight
Boss bon kalindo ❤❤❤💪💪💪
Auze akwiye akwiye
The dc mwana ooopsa kwambiri from njedza village
Bravo!
Apa bwana president mwayankhula chilungamo. Madera ambiri akumangobwera mwachisitsi kugwira ntchito kukakgala tsiku limodzi ndipamene akulengedza ndicholinga kuti olembetsa Cha dzika akhalr ochepa. Ndipo anthu amakumana ndi mavuto a kuti mafomu atha.
Kuswakuswa
Only God knows ❤
Boss kalindo,, 🫡🫡🫡🫡🫡
Dangerous child Dcccccccc
The DC KOMA OTSUTSA BOMA OTSALOLA ANTHU AYAMBE KULAMBETSA VOTE ANTHU AMBILI AKUMWELA NDI KU POTHO ALIBE MA ID NDE akakamidza aboma kuti ayambe kalembela mene dzililimu NOTSE OSUTSA MUPANGE DZIWONETSELO MUTSADALILE BON KALINDO NEYESO NDI MUNTHU AMAMVA KUWAWA POMANGA PAFUPI PAFUPI SICHINTHU CHAMASEWELA AYI MCP YATIKWANA NDE MUKAPANGA MISTAKE KUTI 2025 IKHALETSO BOMA iiiiiiiiii tafa amalawi CHONDE CHONDE A MUTHALIKA ACHIHANA ATUPELE NDIENA OTSE AKUFUNILA MALAWI ZABWINO A MCP AWA ATIPHA NDIMAMVUTO ANYO ASAWINE 2025
Munthu wakulu the DC
Mmmm kma guys bon kalindo tizamukumbukilatu serious tikuona zlango nd MPC Kachikena nangat osazamala
Kalindo is the best asset Malawi has ever had in freedom fighting 💪🏾🙏❤️🇲🇼🇲🇼🇲🇼
Ndipo Malawi tigwilane manja tizipanga zithi pagwilizana chimozi ngati tawona kuti akubwele ndichinyengo menyani otumidwayo kuti achimine asazabwelezeso kuvomela kutumidwa zanyasi Malawi tazuzika mokwana
Ukunena zoonadi moluphwana.funso langa ndiloti why zipani zotsutsa ndi mabungwe alichete akugona kwambili.osapanga zionetselo bwanji?otsutsa boma agalu inu osadzatinyansa chaka chamawa kut tiyeni pansewu pomwe ife mwatizunza kukakuvotera koma chifukwa cha tulo tani tidzangokuyang'anani coz mwagona kwambili.akakupusitsani musadzalire especially afford,dpp;udf mwagona koopsa inu.mulidi serious kut mukufuna kudzalowa bwalo inu?angokuyalani basi palibe ndimodzi akuyankhula otsutsa kapena mukuopa kumangidwa mmmmmxiiiii zitsilu za anthu mukutiwawisa mitu kwambili.
Mr president wathu timakunyadilani always mmm zinthu zavuta akugawa ndrama amalawi akuvutika tikunena pano kumachinga ana awili amalila kamba ka njala km dziko muli president ife tili pa mavuto srs. Mr timakunyadilani ndipo ine ndizakhalaso nanu mpaka mpaka srs ulemu wanu la 40 likubwela agalu amenewa.
Powerful warning ⚠️ DC
Long live The DC ❤❤❤❤
Pa 10 tili komweko
God is with you born kalindo worry not Malawians we're praying for you
Big up our president
Chilungamo❤
Olotu atavoteledwa kwao komweko komabe sangawine
🥳📯📯🎤🎤
Kma nkhawa ili poti kodi kuika malo ochepa a NRB mu chigawo cha kumwera kuno kutithandiza bwanji
Winiko iweyo ndi mbambande
Munthuyu akunena zoona amalawi titseguke maso
Umakwana tikavota no id
Mulophwana timakunyadila
THE DC we love you
THE DC KEEP UP
Brave man
Chenjezo ndlimenelo
Ndiye tipange bwanji chifukwa kuno ku Gambula athu alembendwa 100 sanakwane,
akumanamizira at maform atha
Big up mr DC😂
Tisogoleleni mademo amwene, awopositioniwa satithandinza konse ayi, akuwopa kumangidwa ndikuphedwa 😂😂😂😂
Zolembela chawumzika zithe immediately, tizavote mmene tinavotera mmbuyomu ngati 1994 , 1999
Long live the DC. We r not happy at all with the way things are
Bon Kalindo mumatiimirira ndinu olimba mtima ngati John chilebwe Mulungu azikutetezani❤❤
Tipemphe konse komwe akumanama kut machine awonongeka ,,, muwagwile amenewo muwakwapule ,,muwaumbuze kut naonso atengelepo phunzilo ndi owatumao
The DC'S mwana woooopsa kwambiri vuto a Malawi ife timachita mantha kwambiri
Together we gonna build our country
𝑰𝒘𝒆 𝒏𝒅𝒊 𝒐𝒏𝒆 𝒂𝒔𝒆
Amene akunena kuti ngalu winiko amawuluka ndimasana omwe ndipo sakufunila Malawi zabwino limenelo ndingulu la chakwela osalidabwayi ngulu lokupha
Mulungu adzikutetedzanibe mulungu anakupasani ntchito yowombola ana ake akudzuzika
I support the DCs God bless you all the time.
Solid brave man keep standing on our behalf
Big up DC no one be like you❤❤❤😊
Eeeeee I love dis guy 🎉 chivibe
ife ana mwatizegula Maso bwana kalindo ulemu wanu ukufikilen❤❤❤❤❤
anengeza tivota opanda chazika ulendouno
MR DIIIIIIIIIIIIIIIIIIIIIC WE LOVE YOU
❤❤❤❤ brave man the DC
Ndakuva DC
The DEE CEE🔥🔥🔥
Anganga ❤❤❤
Powerful massage
Very true
Bon Electric kalindo
Following
Inu nd mbambande mr the DC
The DC ❤❤❤❤
Ulemu wanu❤
Mkatundu
kalindo ❤❤❤❤
Mpanje
Yyyyyyyyy❤❤
Karido💪💪💪💪❤❤❤❤❤❤❤
Chigalu chikalindo chilungamo palibe usiye kunena za utm unatuluka kale utm tisiye tikulila marilo azibale anthu amene anatisiya ndipo ndiwe galu yamunthu utisiye kambwe iwe chisilu
Inuso nde chani nanu fotsek
Iwe Galu eti?
Iwe mutu mwako simugwira eti. musiyen the DC. Atilakhulile
Akukuunikilanitu koma olo mumutukwane muzazindikila liti kodi???
Kupusatu uku kunyoza Dccc
Ndiwe chitsilu palibe chomwe chingabwele Cha zelu ife timapeza ndalama timagwila ntchito
Nanunso mukutionetsa usilutu apa..... who's talking about money here
@@PeterTheka kuuyanika pambalanganda Usilu otendera