Ifeso ngakhale tilikutali from south africa komaso ifeso tikumva kuwotchamtima zikutiwawa kom cz mwaiwala bwanji ma boma ochulula akumva kuwawa enafe tikulephela kubwelera kumalawi kamba ka iyeeee chakweraa😢😢😢😢😢😠😠😠😠😠
Chakwela achoke basi tatopa naye ameneyu mbuli palibe chimene akudziwa dzokhudzana ndi u president amati ndikaphudzilakomweko ndiye sikunotu ayi kumalawi ayi machendako iwe chakwela
Chilungamo ma comrades, a Malawi akuzunzika kwambiri ndipo anthu ndi okwiya kwiya , osati chifukwa cha maliro a Chilima ayi, koma Chifukwa cha mavuto ali mu dziko, boma silikuyenda bwino. Chakwera achoke basi
Madestrations samakhalaso opempha president ai amangodzuka from no where like here in south africa they dont even ask for any 1 who called him self boss no
COMLAD TAKUMVANI BWINO KOMATU MADEMO AWAWA OSATINSO ZOTI A MALAWI AKAPEREKE MADANDAULO KWA TSOGOLERI AYI NKGANI NDI YOTI ACHAKWERA NDI OMUZUNGULIRA ACHOKE AZIPITA NDIPO MADEMO AWAWA APOSE A KU KENYA CHAKWERA MUST GO
Anyamata tili kuno ku South africa 🇿🇦 tiyeni titumize rand tatopa ndichakwela makolo athu akuvutika pamodzi ndiife tomwe .malawi sangasithe popanda ife kulimba mtima .chakwela asatenge malawi ngati mudziwake ndi dziko lathu malawi boys moo 🔥 fire 🔥 👌
Come to nkhatabay ndipo zikhhale Ku nkhata asabwele kuno ngati akufuna kubwela kuno nkhatabay abwele ndi chilima
Ngati akufuna achakwela mademo asakhelepo abwelese chilima wathu
TIZAKALA KONKO OSAOPA NO PAIN NO GAIN WANING TWO CHAKWEL KUNKUY CHEMWENDO BANDA AD TIKUBWEL PA STREET
Ifeso ngakhale tilikutali from south africa komaso ifeso tikumva kuwotchamtima zikutiwawa kom cz mwaiwala bwanji ma boma ochulula akumva kuwawa enafe tikulephela kubwelera kumalawi kamba ka iyeeee chakweraa😢😢😢😢😢😠😠😠😠😠
Chakwela you mast go president oipa kwambili iwe
Tikumva kuwawa mademo ankharepo amphamvu 💪💪
Pelekani ma number account abwana tithandizapo
Power voice comrade, more 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥 am with you always
Chakwera you mast go
Chakwelayi achoke ndithu tatopa naye ndizochita zake,nzeru zautsogoleri alibenso.Munthu wosaziwa zilizonse akhala bwanji president wa dziko lino? Langa ndi funso apa amalawi😢😢
Chakwela achoke basi tatopa naye ameneyu mbuli palibe chimene akudziwa dzokhudzana ndi u president amati ndikaphudzilakomweko ndiye sikunotu ayi kumalawi ayi machendako iwe chakwela
Azibusa ndi ena omwe akupita kwa chakwera akungofuna ndalama sakuziwa kuti amalawi ndi omwe ndi owawidwa mutima kuposa chakwelayo
💪💪 osafooka ndikale anthu akhala akuyakhula,mwina pa 10 pa akamvese
Tililimodzi ngat kupha akatiphe tonse zopusa tatopa nazo
Chakwela pa kholopako uchoke watikwana R1000 singakhale 100pn Malawi kwacha
Asalemphere ndipo achitike palibeso boma mpamenepo police 🚔 inkhare gulu yomenyedwa akalowerera boma
Lilongwe kuno tiona kuchedwa
More fire 🔥🔥🔥🔥 Flames osaopa
Chilungamo ma comrades, a Malawi akuzunzika kwambiri ndipo anthu ndi okwiya kwiya , osati chifukwa cha maliro a Chilima ayi, koma Chifukwa cha mavuto ali mu dziko, boma silikuyenda bwino. Chakwera achoke basi
Chakwela you mast go
✌Moto buuuuuu🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Ndalama ikungwa dairy tatopa ife pa nseu ine kuno ku USA
Mademo awawa avuta koopsa zedi
More fire
Tayikani nambala tinyikeko ka ndalama yisanafike 10yoooooo
Amenyedweso apolice ngati akuletsesa mademo ngati ili nkhundo basi timenyane nawo mwazikumwazi amalawi tatopa nazo
Guys tikavute koopsa kumademoku tikaphwasule state house ndi Parliament pokhapokha Chakwera achokeeeee
Wait u will see uzakuumudwa iwe ukuona ngati chakwera wakoyo anga wine
Nkhani ndi imeneyi osaopa nkhondo ikufunika ku Malawi anthu achenjele chifukwa ndife opusa kwambiri
Ndipo mademo akhalepo ndithuu tikajende ku state atijaila
Mademo amenewo mmmhhh dzikolatha likupita kut mkhazazi bwanji boma la nkhazali lichoke basi
Nkagova zama demo moyo wangawu umachita kuva bwino bwaji😂😅😊TITHAMANGE NOW
🤣🤣🤣🤣🤣 tiyeni limodzi pa tsewu
@@Pangolinimw Ndipo ndili konko 🤣🤣🤣
Kayatsen moto tiyen tiyen tiyen
Tiyeni tiyeni kukavute koopsa zedi tikaphwasule state house ndi parliament pokhapokha Chakwera achoke
Zaziiii ukaluze moyo chifukwa chazithu zopanda nzeru ngat izi
😢😢😢😢Tikulira misozi yathu sidzatha ndithu
Madhemo apangike .chakwela achoke paphando.tatopa ndinyasi za chakwela.
Achakwera komwe muliko tangoyimikiranitu manja musanawone zokuda, haaa cooking oil 2 ltrs kukoma 10,000 malawulo sindinaziwone chibadwire zimene zikuchitika panodzi
Dzoona zimenezo mademo achitike bass kufuna osafuna chifukwa Malawi tingovutika
Zaphavu kumeneko 💪🏼💪🏼💪🏼💪🏼💪🏼
Yoooooooomweyo tilnanu pamozi ngakheare tirìmusasafirika
Chakwera must go imidiatly
Tili konkho ku msewu agalu amenewo atikwana
Kuswa kuswa bas💪💪💪💪💪💪💪💪✊✊✊✊✊✊✊✊✊✊
Kenya kenya pa 10
Tilipanseu basi pa 10nipa
Powerful....
😂😂😂 awuzen adzinvere achakwerawo apakire kumeneko
Tiyen tiyen komweko
Go koko Mcp yationesa mbwaza
Mafumuwotu samapita kukapeoetsa koma kukapepha njala mmamidzimu yavuta kutero mmakomo mwawo munalibe kanthu ndiye amanamidzira kuti akukapepesa maliro koma njala njaja mafumuwo
Ineso moto wanga ndamva bwino ndamva za mademo
President wama devaluation galu kwa basi kwacha kungogwa opanda mwadongosola galu kwa basi kungopha anthu
Madestrations samakhalaso opempha president ai amangodzuka from no where like here in south africa they dont even ask for any 1 who called him self boss no
Tili komko
Zamphanvu 🙏
Ziko lathu likupita koipa tabwelela kumbuyo kwabasi athu timalimba ntima chifukwa cha olemekezeka Dr chima ndie afa ife tipange bwanji? Ziko lathu ife tikulifuna
Blantyre we are ready
Tipange zapa Kenya basi !!!¡
Osaywala popta Ku nseu osaywala kutenga Petulo komaso mateyala Moto ukayake
Za ziiii
Abale tiluzenso miyoyo ina aaa achakwera ganizani bwino
palibe vuto tikaona komweko
Km nanga ana amayesowa inu?
COMLAD TAKUMVANI BWINO KOMATU MADEMO AWAWA OSATINSO ZOTI A MALAWI AKAPEREKE MADANDAULO KWA TSOGOLERI AYI NKGANI NDI YOTI ACHAKWERA NDI OMUZUNGULIRA ACHOKE AZIPITA NDIPO MADEMO AWAWA APOSE A KU KENYA CHAKWERA MUST GO
Tipatse madetail anu titumeko kenakake pa mukuru
Koma ya ipase Moto kit buuuuu
Zowona tili chile ife kudikila mademo amenewa
🫡🫡🫡
Kuno kulilongwe takozeka
Kukapereka madandaulo kapena kuti kukamuudza cakwera kuti acoke sakufunika
Go konko osaopa😅😢
Bze ndizinthu zoti sizingatheke kuzolowela umphawi kapena kaumbuli chakwelatu sakuchoka ndipo 2025 mudzakhudwa bvuto simayenda basi kwanuko muli chakwela timuchotse maloto achumba
Machende ako kwa chaka chose
chakwela achoka muona nyani iwe
Machende ako chewa iwe
😂😂azilamulira kunyumba kwako aise
@@MaggieChiomba 🤣🤣🤣🤣 ndipo aona apolice awo aphedwa pa 10
Zazii zenizeni
Inunso mapwala ako
Athu enanu ndulakwitsa m,mayakhulidwe
Kachisiru ako kasiyeni ife tili komweko akatiphera komweko
@@RobertChimenya indee bwana 🤝🤝🤝
Iweyo uli ndvuto kom nthawi zonse kususa zithu zacilungamo bwanji akumakutuma eti akuku tumayo waonjexa