Zaululika, Iyi Ikuzizimusani, Msilikali Winanso Kulongosola Zonse Mene Zinakonzedwela

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 13 มิ.ย. 2024
  • #chilima #skc #chakwera #mcp #utm #malawi #trending #viral

ความคิดเห็น • 256

  • @idrussosman1346
    @idrussosman1346 4 วันที่ผ่านมา +3

    Our Ibrahim Toare the likes of Bokinafaso President. Thanks my Fellow Wasili

  • @JohnAsendi
    @JohnAsendi 16 วันที่ผ่านมา +12

    Ulemu wanu munthu wankulu ndiinu nzelu mukuimila amalawi asati zinazo zikungozinenepela ngati njovu chilungamo kumachiona koma kuchibisa akufuna udindo Allah adzakukhaulisani tsiku Lakiyama lnshaallh 🙏🙏🙏🙏

  • @ChimmsRichardOrden
    @ChimmsRichardOrden 10 วันที่ผ่านมา +10

    Mulungu akutetezeni Big man

    • @mayamikozimanyeta8633
      @mayamikozimanyeta8633 8 วันที่ผ่านมา

      Ooowooo ngat mukufufuzabe nde mukutiwuzilanji maumboni okwanilira musanapeze why phuma nanga

  • @samdiverson9733
    @samdiverson9733 14 วันที่ผ่านมา +3

    Big up to you brother may almighty God protect you

  • @mosesjnrnyamyola9149
    @mosesjnrnyamyola9149 2 วันที่ผ่านมา

    May God protect you brother man till chilungamo chifike pa ground

  • @ibrahimalfred6539
    @ibrahimalfred6539 16 วันที่ผ่านมา +4

    We need something like this sir ayalukedi

  • @Hussen-nb9fy
    @Hussen-nb9fy 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    ❤ Malawi ndidziko laufulu Koma galuyu akutiphela ufuluwathu

  • @user-xw6ic1gj1p
    @user-xw6ic1gj1p วันที่ผ่านมา +1

    God bless you and protect you 😢😢😢😢

  • @SaidDayton
    @SaidDayton 16 วันที่ผ่านมา +16

    😢😢😢😢 mlungu simuthu chilungamo chiziwika Soon in sha Allah
    . allah Akbar 😮😮

  • @leahkasiwa5033
    @leahkasiwa5033 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Tikukhulupilira mulungu my brother akuteteza

  • @corretabanda7685
    @corretabanda7685 13 วันที่ผ่านมา +2

    Thanks so much. More fire osawopa

  • @AdamMwale-y3y
    @AdamMwale-y3y 2 วันที่ผ่านมา +1

    Sitikufuna kuvaso zimenezo ayi zilibe tchito ikakwana yakwana basi Mulungu analemba anafa atumiki amene amalankhulisana ndi Mulungu ndye mukanene achilima

  • @DOLOTHYMAKINA
    @DOLOTHYMAKINA 16 วันที่ผ่านมา +6

    Osaopa mulungu akutetezerani ululani ndithu galu ameneyi sawina 2025

  • @IsaacKachala-ny9km
    @IsaacKachala-ny9km 16 วันที่ผ่านมา +4

    Commando wathu iweye big up kuyimila chilungamu

  • @user-dh8ho2qt4h
    @user-dh8ho2qt4h 16 วันที่ผ่านมา +2

    ❤❤❤❤ sangakuchoseni ntchito bwana 😢😢😢. Tilinanu pamozi

  • @abrahammalunga5132
    @abrahammalunga5132 12 วันที่ผ่านมา +3

    Kodi ulikuti ukuoneka bwanj😂😂

  • @EuritaDeric-fz3ds
    @EuritaDeric-fz3ds 16 วันที่ผ่านมา +2

    Big God bless you 🙏

  • @GoldenNsomba
    @GoldenNsomba 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Thanks bwana kulidi mulungu kumwambaku

  • @EgreySagawa
    @EgreySagawa 15 วันที่ผ่านมา +2

    May Good Lord protect you🙏

  • @Hellenistic109
    @Hellenistic109 12 วันที่ผ่านมา +2

    Its Bwana Mumandinyasa ndisakubiseni 😂😂 for me

  • @murraykaliwo6638
    @murraykaliwo6638 12 วันที่ผ่านมา +3

    Aaa koma ndiyetu asilikali ake ndiopoilatu, ndiye kuti apha nao ngati anachita kuphedwadi

  • @WillySocrates
    @WillySocrates 11 วันที่ผ่านมา +1

    Or utafa ukaona ufumu wa Mulungu pot kulibe wambeu ku dziko lapansi God bless u soldier 🙏🙏🙏

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y 16 วันที่ผ่านมา +10

    Thanks alot my brother good Messnge Chakwela you mast go

  • @JimThomeson-jw8yf
    @JimThomeson-jw8yf 11 วันที่ผ่านมา +2

    Big up!!!

  • @JUNIORMAXWELL-le2mc
    @JUNIORMAXWELL-le2mc 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    God bless you 🙏🙏

  • @fahadwalipeya8656
    @fahadwalipeya8656 15 วันที่ผ่านมา +3

    Thanks u so much solder for good reporting Allah continue bless you 🙏🙏

  • @user-dh8ho2qt4h
    @user-dh8ho2qt4h 16 วันที่ผ่านมา +1

    ❤❤❤ zilibwino kumayankhula chillungamo tchimo ndilachakwera yekha. Mulungu akudaliseni bro 😢😢

  • @rexakalua-dd2qg
    @rexakalua-dd2qg 2 วันที่ผ่านมา

    A Malawi ndinu oputsa osandipsetsa mtima mwamva ngati ndizoona bwanji osamunyanyalira Chakwerayo kuti atule udindo 😢

  • @SteinAustineSakala
    @SteinAustineSakala 2 วันที่ผ่านมา +1

    Bwanji simunaulure Ngozi isanachitike . Tipinduranji panopa a Vice president athu Ali Mmanda . Mkanaulura Ali Moyo bolani

  • @ronaldjere5651
    @ronaldjere5651 14 วันที่ผ่านมา +2

    Mbusa Chakwela wapha Chilima.............

  • @user-dn3gp6yi4y
    @user-dn3gp6yi4y 16 วันที่ผ่านมา +4

    Thank you brother polankhula chilungamo mulungu azikudalisani komaso akutetezeni pa choipa chilichose 😢

  • @saulosjeque8115
    @saulosjeque8115 15 วันที่ผ่านมา +1

    Thank you very much???

  • @HajeerahBeib
    @HajeerahBeib 16 วันที่ผ่านมา +1

    Inshallah mulungu akutetezani mpaka chilungamo xhiziweke

  • @nickmzozodo4163
    @nickmzozodo4163 15 วันที่ผ่านมา +1

    Good job sir

  • @ResponsibleWelding
    @ResponsibleWelding 14 วันที่ผ่านมา +1

    ❤ kukanakhala olo plan yabwino ya asilikalinu kwa nonse amene simuyanjana nane kuphatikizapo ineyo kunyomushuta bas galu ameneyo

  • @kingsleymsampha2260
    @kingsleymsampha2260 16 วันที่ผ่านมา +5

    Ukutsutsawe do your audio dzitchule dzina nafeso tikumve fundo zako on public. Simple.

  • @AbraoEliseuJone
    @AbraoEliseuJone 11 วันที่ผ่านมา +1

    Zimawawa kwa wina aliyense zoona kwa obadwa ndiponso wobhereka@❤

  • @user-qv4yu2ir2k
    @user-qv4yu2ir2k 16 วันที่ผ่านมา +5

    Ulemu wanu munthu wankulu apa ofunika audio muilengeze mu English kuti imveke ziko lonse lapansi

  • @CalvinTonyWaluma
    @CalvinTonyWaluma 14 วันที่ผ่านมา +4

    mumaziwa ndiye simudaiteteze ndege bwanji ........inuso mwapha nawo chief

    • @damianokachingwe3531
      @damianokachingwe3531 14 วันที่ผ่านมา +1

      Mbwerera za anthu aku Malawi ndi zimenezo akufuna kuoneka anzeru pano.

    • @user-zj1xx1ic2m
      @user-zj1xx1ic2m 14 วันที่ผ่านมา

      The son of MCP stupid

  • @user-ie5pc4ox8i
    @user-ie5pc4ox8i 15 วันที่ผ่านมา +1

    Ine chetee waiting for mapenalty monday kutcheu chakwera ngopusa

  • @GloryAdulla
    @GloryAdulla 11 วันที่ผ่านมา +1

    Mmmh zovuta bwanji, I pray for your protection

  • @harrymicah6140
    @harrymicah6140 15 วันที่ผ่านมา +3

    Big up chief❤❤❤ ndipo mizimu yao yimusowese ntendere naye asowe

  • @AtupereMwenefumbo
    @AtupereMwenefumbo 14 วันที่ผ่านมา +1

    Aaaaah thank God chilungamo chixiwike

  • @samueljuly8129
    @samueljuly8129 15 วันที่ผ่านมา +1

    Thanks so much our good brother . We really need the truth on this matter .

  • @davidbulla5128
    @davidbulla5128 16 วันที่ผ่านมา

    GOD BLESS YOU

  • @user-lg2ws2ki3d
    @user-lg2ws2ki3d 16 วันที่ผ่านมา +7

    We're crying all as a nation 😭 but this is totally nonsense!!!!

  • @murraykaliwo6638
    @murraykaliwo6638 12 วันที่ผ่านมา +1

    Ndipo akanangokhala osaululanso nanga simunthuyo wafa kale 😂😂😂

  • @SuwemaHafizaayami-gy2hn
    @SuwemaHafizaayami-gy2hn 12 วันที่ผ่านมา +1

    Big up aise pambuyo pako

  • @user-wp3fu7eu1d
    @user-wp3fu7eu1d 15 วันที่ผ่านมา +2

    we are behind you comrade, we don't fear anyone.

  • @janetchinga695
    @janetchinga695 16 วันที่ผ่านมา +7

    😢😢😢 mulungu alipo sakumangani ndithu

    • @user-jh8tj5in3y
      @user-jh8tj5in3y 13 วันที่ผ่านมา

      Mulungu sateteza anthu amabodza ngati uyu!

  • @JusticehawaMaloya
    @JusticehawaMaloya 16 วันที่ผ่านมา +2

    Well done sir continue fighting for your country

  • @VincentChipwere
    @VincentChipwere 14 วันที่ผ่านมา +1

    Akanakhalapo asilikali onga inu 10 zinthu zikanatha kulongosoka Lazaro ndi wakuphadi

  • @faithmwanga6078
    @faithmwanga6078 11 วันที่ผ่านมา +1

    Bwana kunyansa zoona, you're heartless chakwela

  • @SheikhupileLoprhdemah
    @SheikhupileLoprhdemah 15 วันที่ผ่านมา

    Appreciate

  • @user-xp3qc9hd1p
    @user-xp3qc9hd1p 5 วันที่ผ่านมา

    Mr Chirima 😭😭😭😭😭😭😭

  • @NahwaalPalmer
    @NahwaalPalmer 16 วันที่ผ่านมา +1

    Ulemu wanu m'fumu ❤

  • @Bthula
    @Bthula 16 วันที่ผ่านมา +5

    If it is that soldier talking then he must be careful as chakwera and his gang are mafia they are now playing games they are out to kill so brother be careful

  • @LabKazembe
    @LabKazembe 3 วันที่ผ่านมา

    Panyini pamake chakwelayo ndipo imfa yake idzankhala yogendedwa ndi miyala ameneyo

  • @ChikondiGlibert
    @ChikondiGlibert 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Iwe ndiye chitsilu chothelatu udziwe. Komwe uliko

  • @AhamadiYusuf
    @AhamadiYusuf 13 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    There's no secret on the Earth

  • @Lexkasonkanji
    @Lexkasonkanji 15 วันที่ผ่านมา +2

    Good boy😢😢😢😢😢😢

  • @RaymondKaumba
    @RaymondKaumba 13 วันที่ผ่านมา

    Kubisala ku South Africa mkumati wabisala akupeza

  • @milanzichikondi7330
    @milanzichikondi7330 15 วันที่ผ่านมา +1

    Black board??, Benzene (this is just a small component in gasoline) how did they suck it? , Every pilot before flight makes a check list. We need real facts gents. We are with you but we need facts.

    • @koncyk7138
      @koncyk7138 13 วันที่ผ่านมา

      Olo ngati driver amapanga check ma tyres, engine coolant, engine oil. Galimoto likalila amaonso all warning ⚠️ lights pa dash board and levels of fuel. Should we say gage ya fuel mu ndege inali yokufa. If at all they use a dip stick, sanapange zimenezo? Facts are really supposed to be laid osati trying to trigger unnecessary riots.

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz 16 วันที่ผ่านมา +4

    Guy's let's work up fighting for chakwera go

  • @murraykaliwo6638
    @murraykaliwo6638 15 วันที่ผ่านมา +4

    Nanga bwanji samauulula zisanachitike

    • @bostonbanda4774
      @bostonbanda4774 14 วันที่ผ่านมา +1

      Zabodza izi unatani kunena zisanachitike

    • @BenPhillip-fw8hi
      @BenPhillip-fw8hi 12 วันที่ผ่านมา

      Eti eti

  • @eliasmatewere1403
    @eliasmatewere1403 15 วันที่ผ่านมา

    God be with you brother

    • @user-jh8tj5in3y
      @user-jh8tj5in3y 13 วันที่ผ่านมา

      God could not be with this brother!

  • @KelvinPhiri750
    @KelvinPhiri750 16 วันที่ผ่านมา +1

    Mpaka pano mu chaka cha 2024 ,tikanaganizabe kuti Otilamulira ndi milungu, kuti iwowo imfa singawakhudze.😢 whether assasinated or not its all death😢

  • @augustinechibbalazi8897
    @augustinechibbalazi8897 7 วันที่ผ่านมา

    You are more than a Christian Saint in the paradise.

  • @user-yk4by8iy8k
    @user-yk4by8iy8k 15 วันที่ผ่านมา

    Good job

  • @chancychikoko-ns5nl
    @chancychikoko-ns5nl 15 วันที่ผ่านมา +2

    Mvuto Malawi timankhulipira social media 😅

    • @LTTechnician-xp2zs
      @LTTechnician-xp2zs 13 วันที่ผ่านมา

      Timakhulupilira ndikumene cz sizonse zimakhala zabodza. Kachilungamo kamakhala in one way or the other

  • @RichMavoko-nx8cn
    @RichMavoko-nx8cn 9 วันที่ผ่านมา

    Nzimu wake uwuze muntendere 😢 our yourng vice president

  • @salimmkumakumakitombi-yc7pw
    @salimmkumakumakitombi-yc7pw 16 วันที่ผ่านมา

    nkhaniyi ndiyabwino kwambili ndipo zikomo..koma mwafurumira kuibweretsa pa air before kumalidza kafukufuku wanu.chifukwa anthu awawa atha kukumangani or kukuphani before kubweretsa zomwe muli nadzo

  • @user-wt9vb1vb5v
    @user-wt9vb1vb5v 12 วันที่ผ่านมา +1

    Umbuliu ndimatenda pena.kodi who chose the plane as veep transport to mzuzu

  • @RajanaBaluwesi
    @RajanaBaluwesi 13 วันที่ผ่านมา +2

    Uyuyu amutuma ndipo amutumawo ali chete. Satana akafuna kusokoneza dziko amalisokoneza. Muganiza kuti anthu akulionera kukondwa ndikoli? Olo mutasintha atsogoleri ambili mbili muganiza kuti zinthu zidzasintha? Poti wina pamenepa akumenya campaign kuti adzadyerenso aMalawi, tsegukani mmaso watumidwa uyu. Munthu wachilungamo sabisala apite direct akafotokoze kuti aMalawi asiye chiwewe.

  • @murraykaliwo6638
    @murraykaliwo6638 15 วันที่ผ่านมา +1

    Ndipo munthu akuyankhulani bodza limene kaya mukuti ndindani, koma ndi opusa kwambiri! Bwanji samanena asanakwele ndegeyo

  • @MeniyaMikaya
    @MeniyaMikaya 14 วันที่ผ่านมา +1

    Ndipo olo kumuuza mwana wazaka 7 akhoza kudziwilatu kt ndi bodza ili aaa mkayidi ndiye kt chiyani

  • @user-pg9yl8jq8p
    @user-pg9yl8jq8p 11 วันที่ผ่านมา +1

    Respect

  • @MarkManyowa
    @MarkManyowa 15 วันที่ผ่านมา +2

    Big up Mr Wasir

  • @JoeMwandira-tq9rs
    @JoeMwandira-tq9rs 14 วันที่ผ่านมา

    Mno mu Malawi ngatimli anthu ngati awawa bwedzi dzikolathu likanakhala lachilungamo tsangakuphe mdzanga amalawi ose akuimililani bwana opepela okha ndi amene adzvotera mbuziyi

  • @CharlesBanda-kv8bh
    @CharlesBanda-kv8bh 15 วันที่ผ่านมา +1

    Anthu ambiri kumalawi adayaluka mitu sigwira ntchito zoona kuthiradi ndamanga pazinthu zoonekeratu kuti munthuyu akukamba zabodza Malawi ovetsa chisoni

    • @KelvinKachere
      @KelvinKachere 3 วันที่ผ่านมา

      Iwe auze amalawi zoona coz olira sasekedwa pakamwa ngat tikuziwa kt kafukufuku wawoyo saphula kanthu agalu amenewa dziko la Mulungu ili

  • @JimmyIsaac-xd4ef
    @JimmyIsaac-xd4ef 15 วันที่ผ่านมา

    Zikomo m'bale chilungamo chidziwike, komaso a Mbuye akhale mbaliyanu

  • @WilliamMasauko-su1wx
    @WilliamMasauko-su1wx 9 วันที่ผ่านมา

    Osaopa ,osafooka kulimba mtima basi mmakwana inuyo mulungu azikutetezerani

  • @shepherdkingston
    @shepherdkingston 16 วันที่ผ่านมา +1

    Mulungu akudaliseni potidziwisa

  • @NescotNyamwela
    @NescotNyamwela 15 วันที่ผ่านมา

    Ine phe ku capetown za Malawi ndinayiwalako

  • @KelvinJpchimphepo-sh6nc
    @KelvinJpchimphepo-sh6nc 14 วันที่ผ่านมา

    Apa sipakuyenera kuwopa chifukwa zikatero mawa zizachitikira kwayena ndiye tizivomeleza zimenez mpaka liti apha anthu asogoro lawo angat pangani zomwezo bwana anthu ali pambuyo panu, tima dikira anthu ngat inu ndipo izi zowawa kwabasi, titeteze dziko osat kuphana tokha tokha ngat ndife anthu ndife obwera zoona

  • @DanielErnest-ez1qw
    @DanielErnest-ez1qw 3 วันที่ผ่านมา

    No comment

  • @ChisomoChikwiri
    @ChisomoChikwiri 15 วันที่ผ่านมา

    Mulungu akumenenyeleni nkhondo sir

  • @samuellimited2705
    @samuellimited2705 14 วันที่ผ่านมา

    koma yaaa anthu muli ndi mtima oyipa yooo😭😭😭

  • @JoeMwandira-tq9rs
    @JoeMwandira-tq9rs 14 วันที่ผ่านมา

    Chilungamo ndichofunika ake atinyatsadi uyu presdent kupha anthu chochi fuseki

  • @user-wr9rl3il8t
    @user-wr9rl3il8t 5 วันที่ผ่านมา

    Mmmhm kuzuza mizimu yosalakwa mhm

  • @AaronJaccob-us7xn
    @AaronJaccob-us7xn 4 วันที่ผ่านมา

    zabodza izi umbon mwadziwa bwanji kut fuel anali ochepa osatinamiza apa ayi asilamu pajad mtopola vuto mulowetsa ndale

  • @leoleonard2103
    @leoleonard2103 9 วันที่ผ่านมา

    Izii ndiye zowona osati zomwe akunama chakwela

  • @Milesweled
    @Milesweled 16 วันที่ผ่านมา +1

    Timva zambiri chirungamo chidziwikepo apa akumanama kuti akufufuza Fiona apeto ake

  • @aishamakisudi3220
    @aishamakisudi3220 14 วันที่ผ่านมา

    Koma ngati zili zoona analakwa ndithu 😢😢😢

  • @HusseinJumah-nz7mm
    @HusseinJumah-nz7mm 7 วันที่ผ่านมา

    Timenyana ndi boma basi ndukanguliratu gan yanga gyz

  • @ZestCee
    @ZestCee 8 วันที่ผ่านมา

    Chilungam chiyende ngt madzi ndili kumbuyo kwako bro..... zikom pa luntha lko

  • @lungujohn2672
    @lungujohn2672 15 วันที่ผ่านมา

    Chakwera lamulo limutsate 😭😭😭😭😭🙆🙆

  • @user-yk5xv4dt7v
    @user-yk5xv4dt7v 13 วันที่ผ่านมา

    Imeneyo singozi ai masewera

  • @emiliaumali8360
    @emiliaumali8360 12 วันที่ผ่านมา

    Ambuye amulange munthu ameneyu kupha anthu 9 because of money mzimu ukutsata ndipo usowa mtendere

  • @KelvinJpchimphepo-sh6nc
    @KelvinJpchimphepo-sh6nc 14 วันที่ผ่านมา

    Vuto ndinu asilikali simufuna kugwilizana ndizimene akulira anthu chifukwa zmene zikupangidwaz mawa zizachitikira kwa asilikali ena chifukwa akamatero akusonyeza kut alibe chikondi ndi ogwira ntchito azawo