The guy who sold Malawi to crocodile 🐊, instead of solving the problem he opted to sell the country, he came to his senses after he was fired as a minister
Chikangawa u president anawutengera ku ma demo komko.chomwe ndinganene ndichakuti anthu azinyamulidwa pa galimoto kuchoka mmadera ose adziko lino.ndipo ngati iwowo akutenga zikwanje anthuso akozeke atengeso zida,si ayamba ndi iwowo.
Koma chilungamo one I only see Aford as the best opposition and only party to rescue Malawi. There manifesto and why this party was formed is not out of greed. Its the party that fought for democracy and the former freedom fighter died for Malawi. He was never given the chance to rule Malawi to show Malawians the democracy he fought for. Let's give them the chance. They have the password. Enawatu chomwe ankafuna Chakufwa Chihana sakutha kuchitanthauzila . mayeso okopela umalemba Nazi answer polakwika chifukwa cha phuma
MTAmbo ndi oganinza boo amapita kumene kulitendele akaona zoti kuli manyaka amachoka m,Kani lero akupenzeka kumenekoo👍👍👍
😂😂Ah iwe ndale wayamba kuzitsata kumene or bwanji? A akakhala sanamuchose u minister ukuona ngati anakhala pamenepo?
Ndimwana wang'ono
❤
Chakwera anabwera kudzapanga nkhondo kumalawi osati kubwera zoti alamulire dziko ai galu ameneyu achoke ndpo mulungu timupempha alowelerepo dziko lamalawi
Inu NDI amene mukufuna kuyambisa nkhondo
Mulungu wake God Papa? 😂😂😂😂
Ndiye osabwenzera bwanji
Ma cadet ndinu mukufuna nkhondo
😂
Tatopa ndizongolankhula...let's take action 🎉
The guy who sold Malawi to crocodile 🐊, instead of solving the problem he opted to sell the country, he came to his senses after he was fired as a minister
Apatu Kwa Muthu waxeru Bora kumakhala panyumba akakutema avutika dabaleako sugamuone ntambo kapena atupere akudzakuona pamene ooo ndiye odyerera
Sinanga mukuchita zadala momo Munziwe kukada mumacha
Brave comrade mtambo we are with you poor country people don't get tired we will fight until we win victory
Awo ndimamvenda amu Lilongwe kuteteza ma shop awo chifukwa anthu ambiri sapitila mademo amapitila kuba
Ine ndimaganiza kuti tikamapita kumademo nafe tizitenga zikwanje
Yes
🥰 mtambo 🔥🔥🔥🔥💪
More fire 🔥 guys 🔥 🇲🇼 👦 we love Malawi 🇲🇼 💙
A mambo musatipusise munali konko lero mutinamizeso kuti aipa poti anthuwa munawaikapo ndinu lero mademo akukukanikani lero bwanji
Kodi awa azikwanjewa chilolezo anachitenga kuti?
Asilikali aku Malawi ndi opusa kwambiri angoyanganira dziko likuonongeka
Agaru achabechabe bro😢😢
Anthu awa ndizitsilu kwambiri bwanji mene anthu amathamanga ndizikwanje samapita koko achina mtambo ndi gulu lawo kuti akathanenawo pano akungolubwalubwa basi,
Inu mtamboyo akudziwa kt ku mcp ndiye kuli nkhondo yamademo ndi nyooo anawa achepa fwetseke anakanika Jean answer kumuchotsa ndiye lelo akuyambilas zomwezo anthu mukuombela mmanja shupt
Chakwera waonjeza akusonyezeratu kuti ndi opanda nzeru ndi po Sakuziwa zochitali walephereratu kuyendetsa dziko walephereratu
Mukuchedwa tingomenyanapo basi mesa iwo akudalira asilikali ifenso we are well trained tilowe ntchire bas
Kkkkkmmm😅😅
Ndiye anasiya apolisi akwa Nsundwe???
Amenewa awatani,popeza wina akatere,akumati akubweretsa chiopsezo kudziko,amenewa ndiye oyera,akuchita kupanga challenge?🤔🤔🤔
Iweyo pangazako usalimbane ndagoni sitidya zolandila Ifé ai tikulima Ifé auzeni atambo ndiwanawake apite ekha❤ akachotse ameneanamuikayo
Antambo ndinu wozungulira mutu munatilakwitsa ndinu pano mufuna mukhale wochenjela pamene muli opusa ife umatinyansa ukamalankhula, nafenso ufuna tikhale wozungulira mutu ngati iweyo?
Atupele..david mbewe..muli kuti anzanu ali konko
He deserves to be a president
Let's fight together guys ziko silachakwela ili machine opanda auditing antundu wanji palibe
Timothy mtambo akuyenera kulapa ZENI ZENI, iye ndi Mzake Sembeleka ndi limodzi lagwero lakuwonongeka kwa chuma cha Malawi.
Crook wachabe chabe
Kodi chimene mukukhalira ndi mkwiyo ndichani mmalo modikira 2025? Mukuonesa uchisiru wanu a Mtambo komaso Chihana,
MBOLE YAKO IWE
Iwe ndiwa galu kwabasi ukauze mbuyako chomwe akukakamira machini ndichani ayikamo zichani usatichimwitse
Chikangawa u president anawutengera ku ma demo komko.chomwe ndinganene ndichakuti anthu azinyamulidwa pa galimoto kuchoka mmadera ose adziko lino.ndipo ngati iwowo akutenga zikwanje anthuso akozeke atengeso zida,si ayamba ndi iwowo.
Polisi akudikila. Ku. D. P. P, apepese kae zija adanena achikwanje ndieno musadabwe anthu akutsata mau achikwanje
Antambo anthu asakupopeni ngati kuti inu ndi mulungu, ng'oma yolira simachedwa ku sweka enawa akungokutolani uchitsiru mukanakhala ena ngati muli ndimphamvu mukukalowa mwa anzanu bwanji zipani sizingatenge boma koma chipani osamatipeperetsa a malawi mwanjira imeneyi amphungu nokha nokha kapangeni mademowo zikukulepherani patipo?
koma zoona mmalo motenga ndalama kukagula chakudya cha anthu ovutika akagula zida zophera anthu boma lomvesa chisoni umbuli sizinthu mai Joyce Banda mulungu munakalitenga kt gulu ili onani dzikoli komwe mwalipititsa😂😂
Izi a malawi zikuchedwetsani kupeza zosoweka pamoyo wathu,andale amatifuna pakalowa njoka, akakhala pabwinopo samacheukilaso amphawi aja . Asiyeni andale azilimbilana ma udindowo asakutayitseni nthawi yokasaka chakudya ayi, chakudya simungachipeze kuma demo zausiru izi.
Zitsilu ndiinu mumakangana chifukwa chotsatira zipani zosiyana. Osangowasiya adzilimbana okha okha bwanji? Lero mumukhapa mzanu atsogoleri anuwo pa mawa simudzawawona. Ma voti anzika za kumalawi sabweletsa chitukuko zimangothandizira mbuli zandalezi kumatibela misonkho yathu mkumatupitsa mimba zawo ndi mitu yawo.
Ndikuona kuti we are too much of a talker than a doer why?? Anthuwa zomaodiradzo adzolowera.
MADEMO SAMAPEMPHA INU MUKUZIWAKUTI MA DC ANAGUDWA NDI MCP MUKUONA NGATI A DC ANGAKULOLENI
Kodi agalu akuwonesa zikwanjewo akuziwa koma kuti kwasala 10month ka video kawoko kuzakhala mboni
Live Verbal fighting in malawi will never end...but why we're fighting for?
Kodi Angoni singathe kubwera kulilongwe kuno Chirima apedwa mukuona zoona,
Ndipo inuyo antambo pangani zitheka osawagonjera agalu awa anthu chakwera ukafuna ungotipha those utsare wekha dziko Muno
Mtambo anali ndi morale nthawi yomwe ija ndiwadyela ameneyo akakhala chihana ndi wa ku Kasungu koma analuza ndi u MP chitsilu chimenecho
Ndinu zitsiru kwabasi mademo mademo achan mwaona ngati ndicho chida CHOTI muzipusitsila anthu
Munakanika kumuchotsa jeni ansa chifukwa chauchitsilu lelo ukufuna anabe ntalimanja achoke udindo ndiwe galu pantumbo pako ntambo
NDIPOMUSALOLE NDITU💪💪💪💪✊✊✊💯
Antambo mungofuna kupeza zosowazani osatikuthandiza anthu opusa akutengeni koma ngati ine koposa kupita kuganyu
Go Malawi go go!!!!
Anyambo😂😂😂😂😂 dyela
Inutu mukhulupilire kuti Mulungu akulangilani pansi pompano, muphatikizana koma zisankho simuwina or pang'ono
Zikakhala zikwanje kaya zophana analamula ndi. D. P. P, mwaiwala kapena achikwanje aku. D. P. P
Mavuto alipo pazambia pompa apa kungotulutsa mpeni ngati wayambana ndinzako amakupatsa mulandu wakupha
Mwalakhula mokwanila koma let's take action now
Good boma lizitelo MCP ndi boma!!!
Ambuye tithandizeni ziko lathu 😭😭😭😭😭
koma a mcp wo sakuwopa combination ya chisale nd mtambo kmaso mkulu uja wa cided ndiyolusa2 iyi
Kodi leroa anali kuti chisale
Mademo amayanjana ndi ulesi ndipo ndi business ya asogoleli
Tambo woyeeeeeee ❤❤❤❤
Chilungamo ndichoti mukuwopa basi, zomangobwebweteka apa koma pa ground zero. Mwakhumudwitsa anthu lero kwabasi
Zelu mulibe pitan pa graung kauzen anthu akuvotelen ngat angakuvotelen boma ndilomweli palibe kusinda zilimbanani ndimamikumanoyo chiyambi choluza ndichimenecho
Chihana uzinamiza amalawife kuti umaka wodika ife ana mumutumo ziziyendamo anthu akwathu mwatani? Mukuwonetsa umbuli mukutichititsa manyadzi kwinako mulungu akuwerudzeni mofulumira ana anjoka inu mwavala zikopa za nkhosa koma ndinu afisi inu.
Koma iweyo tambo umatiwona ngati zitsilu ET uzipita ndiosowa tchito ineyo sigapite iweyo thawinjai anakusakha munja unatani kukana
Umafuna kupusitsa zisilu zinzako. Akamat kulimbantima kwantambo anapanga zotani kukuchotsa udindo chikhale chifukwa pamnyelo pako udziwopya makape amzakowo galu chakwela timamukonda
MR Kulimba mtima osaopa
Ndipo kuberako zisakho anayambisa ndi iwowo lero aope kuberedwa komadi wakuba amaopa kuberedwadi eti ai zikomo
Iyambeni bola muimalize ife tipheni tasala panti khondo simuiziwa mwina mumangomva
Kuyambisa sivutatu Koma kuithesa eeee
Unatha iwe,TX ya mbendela imakuwawa kape
Pakufunika kuti mademo enenso akabwera titseke maboda onse including ma airport.
Ine NDE Chikangawa party imandinyasa kuposa tudzi
Chakwera amafuna mtendere koma amalawi zeru tilibe chakwera tizamulira ngat kamuzu or Bingu
Ndi ndani amamulira kamuzu
Komaso mukamati angoni mubwele adzan nzofunika kumaitana namalomba yemwe akusonkhezela moto umeneu, namalomba ifeyo timadikila iweyo wa. D. P. P
Anatembenoka mtima mtambo chifukwa anamulanda mchere bwanji nthawi ija anali pa mchere samalakhula zimenezi asatipositse ife a malawi,
That's a end of MCP
Ma demo akule moto guys shop yovulidwa tidya lunch
Who is Timothy Mtambo? Amakawi mumañgotengeka zilizonse, Timothy ndiminthu oipa uyu adatembrnuke lero popezs anamuchitsa pa udindo wa u minister
Kodi a Malawi ife timaganiza bwanji? Lero kumamuveraso Ntambo,is he not the same person ankanyoza DPP,then the same DPP is with him again now
Kumbwabwana anthu
aliyese akusala zoti mimba yake ikhute basi antambo sanatikondeko ife ndipo munthu oipa kwambili mwachudule nose andale masamala zamimba zanu zawana wanu basi osati ife amalawi
So powerful💪💪💪🔥🔥🔥
Mukamati mtambo mukufuna atchuke adatchuka kale ndidyela kufuna maudindo tamudziwa kale asatipusise galu wachabechabe
Nkhani siya mtambo apa koma kufuna kukoza dziko la Malawi mwatani kodi
Makape inu mademo akuvutani tapitani osamangolubwalubwa chisilu iwe ngati Jane ansa adachoka uyuso achoka Jane ansa adakuvuta
Ndale ndi game yopusa kwabas, mumafuna mutigwiritse ntchito anthu
Koma mukaona anthu onyamula zikwanjewo momwe akuonekela ngati sasambatu zomwe zikuonetsa kuti mavuto omwe Ali mdziko muno nawonso akuvutika nawo.
Mulipo angati kodi apo Kkkkkkk zipani 5 anthu 20 nokha Lilongwe siisekelela makapetu
Zikoli tingawana ndithu, kuthawa anthu mudapha kuchikangawa komatu mulira olo mutiphe koma ana akuweluzanibe
Kuteleko mufuna mupusise chihana, mpusiTseni nayeso ndigalu ku. D. P. P amakhaulitsa mufuse. U. T.m lelo akukunyengelelani akukhaulitsani muona
Walibe fundo awa siwomwewa adatiika pamoto afuna kukatikaso pamoto wina uwu sukuwotcha
Nice
Palibe zomwe akuyakhula zonveka makapewa ziko Lili mmaja mwachakwela basi Kodi enawo Ali m,boma wankulu was make anasankha ndiiowo kapena osusa ndipo Inu afinye mumasatila zisilu idzi kuti tiyeni ku mademo muzafela zaini asiyeni azipitako okha mtambo ndimuthu wadyela osati okonda amalawi ayi
Maybe ten months
Amtambo pano adafutha pano angogwera kotsutha nufuna upurezideti koma ndarama aribe ukunurira mophatikizana nukomoka komaso nuzinyerera purasi
Kd police ya kumalawi ikumagwira ntchito chani kulora anthu kumayenda ndi zikwanje msewu 😮
Kod simunadziwebe kut police imagwira job nd boma
More fire Ma Big man🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Iwe tambo usamatifune akakuchotsa wava thawi unaliboma munja ukatani aaaaaaaaa koma ife tisiye udatiika ndiwe ndiye ngat ukufuna kuchotsa upite wekha ndamene ukudziwa komaso Peter asakupusitseni lero ndifiti ameneyo
NDI MACKO CHIPONDE BMONDA💪💪💪💪☝️✊🇲🇼💯💯🚭🚭💯💪☝️✊
Mtambo ndiwakuba abale simukudziwakod. Ku. M. C. P. Ngat
Koma chilungamo one I only see Aford as the best opposition and only party to rescue Malawi. There manifesto and why this party was formed is not out of greed. Its the party that fought for democracy and the former freedom fighter died for Malawi. He was never given the chance to rule Malawi to show Malawians the democracy he fought for. Let's give them the chance. They have the password. Enawatu chomwe ankafuna Chakufwa Chihana sakutha kuchitanthauzila . mayeso okopela umalemba Nazi answer polakwika chifukwa cha phuma
AFORD inapita ndimwini wake Chakufwa aise,awawa ndiana ochepa sangazithe
A mtambo Pali chomwe angachite ndikape amenewo
Kma ana amenewa or akutenga zikwanje akuganiza bwanj😊
Musalole machine amenewo choonde anthu utsutsa boma akuberani ma vote
Mumukumbutse chakwera imfa ya chilima atiuze Kaye tisanavote
Mavenda anazindikila safuna zobeledwa ndi alomwe
Mtambo wachepa,kwake kunatha,sangatipusitsenso,kwakula nkulilira ya flag TX basi
Odi ndi zilira ine..
Anthu tikumva kuwawa guys tiyeni tilireni basi 😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭
😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭
Aaaaaaa amtambo paribeso chomwe angapange chazeru mukungopusitsanapo
Ntambo kkkkkkkkk wasamila nsalu ya DPP kkk wapenga muchedwa
Mtambo ndiwe osokonezeka bwanji tiveko zazako