Mumakwana ndix takunyadilani gyz cikangawa ndi mcp yakeyo osawapatsa mita,ndi mbuzi za anthu, palibe cipanga iwo dziko muno koma kunyenga, kupha ndi kuba. Mcp ilibe tcito.jessy,cimwendo,zikhale,yolamu, ndi onse a mcp akabweranso kuno nafenso tiwagenda zibwana zawozo adzikapangila ku kasiya, pa u cisilu pa mawo agalu amenewa.
Northern Region is with you but let us remove Chikangawa with our votes. Nkhondo siyabwino ngakhale ayambise ndiwo a MCP tiyeni tiyipewe tose tikhoza kuzavutika nayo kumbuķilani kuti tili ndi nkhalamba, ana, wodwala mu zipatala, awulumayi womwe sangathe kuthawa. Central region ndi mcp yawoyo yalephera kangati ? Kuti lero azinyoza zigawo zina nkumati awina pa wokha. Ine ndimawona ngati Chakwera ndiwanzeru koma ayi dziko likuyenda ngati tilibe President. Ali busy ndi akwawo kumawalimbikisa kupanga zipolowe lero ndi izi zikufalikila palipose and yet he is quiet like a brind person.
Uthenga kwa Amanganya wadziwonera yekha kumeneko ndi kuyambika kwa nkhani ya kukakamidza kulanda chipani cha utm, Ngati manganya akufuna chipani ayambitse chipani chake
Ine kuva kukoma ndilande more fire 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Zimenezi nzopusa, no one is above the government,anthu akusiya kupanga ma business awo akukagenda.atsogoleri, umbuli uli ku Bts...
Well done a Malawi osamasekelera mzopusa...mkunawapha onse awiri manganya ndi chikhulhuyu..anthu alipa mizere kudikira mafuta moti asomve mabvuto tikungoyendayenda ...mwachi ta bwino kwambiri😮😮😮😮
Umangodziwilatuuuuuu! Well done Ndix! Mwatiimilila 🥳🥳🥳🥳🥳
Mmmmm amanganya mmadziwa kuti mukaluza musanamize anthu about the 20 million
Moto kuti wali wali kenako buuuuuuuuuuu koma kumeneko ndirande tsopano ur nickname is soweto no 2 😅😅😅😅ndirande ndi akamuna we are Malawians 🇲🇼💪💪💪💪💪💪
😂😂😂😂Soweto bwinoo!
Ndilande my vote 🗳🎉🎉🎉🎉🎉 konse kukanankhala chochi bwez zilibwino
Ndilande. Yonse well done ndirande sisunga cape
Nzopuusa izi, tiyeni tikavote, musagawanitse dziko, ndirande siili dziko lonse ayi nanga aliyense akati kudela lakwathu awo ayii ifenso awo ayii miyala idzigwira ncthito dziko will be devided ,iwowa ngati akuikana mcp akavotele amene akumfunayo,sangakwanitse kuiopseza Boma ,they should hustle for there bellies and families ndinawerengapo Burundi civil war Boma likati kitenge action pamatelela...
Ndilande your number one i like this muziwaonesa agalu amenewa anyapapi nanunso mukanatenga zikwanje kuwasema mitu ya dazi iyo .😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
❤ our own secretary chair, ndifedi ainiyake a ndirande 😂😂😂😂😂mau
kwathu ku Ndix sitimagawa ma sweet kuno l love my family ndix ville woye l love you all good job ❤❤❤and ❤
This type of politics is not acceptable, fighting each other is not a solution to our problems. Let's be peaceful people
If the President is not Peaceful then why do you preach about peace.... Fuck peace,,, this is just the beginning
Well done Ndirande.
Mumakwana ndix takunyadilani gyz cikangawa ndi mcp yakeyo osawapatsa mita,ndi mbuzi za anthu, palibe cipanga iwo dziko muno koma kunyenga, kupha ndi kuba. Mcp ilibe tcito.jessy,cimwendo,zikhale,yolamu, ndi onse a mcp akabweranso kuno nafenso tiwagenda zibwana zawozo adzikapangila ku kasiya, pa u cisilu pa mawo agalu amenewa.
Nanuso mukanatenga zikwanje 50 ku 50 anaona ngati mu lilongwe satuluka kumupoto nafe tipange zomwezo azizungulira pa lilongwe pokha apolisi akumwera or kumpoto mukalandila order above muwawuze kuti mangani kaye azikwanje akulilongwe. Kunkuyu amayakhula mwamatama kwabasi
This is not racism we're tired with MCP regime
Manganya ndiwe galu kwabasi lero chifukwa chandalama zokuba lero ukufuna ukhale dolo.
You're most welcome brother man!!
Wawa kwanthu ku ndilande. Dera lokoma😂😂😂😂😂
Kunkuyu ankaona ngati dolo ndi azikwanje ake aja kuLilongwe, Manganya olo kudzudzula ntaa. Lero waiona Ndirande. Akakhale ku Lilongwe kwakeko mbuzi yamunthu
Umbuli wakula kumalawi mukugenda atsogoleri Anu oti akuthandizeni
Akuti tithawe kaye🤣🤣🤣 cameraman sathawa nawo
😂😂😂😂
Awa ndi achitsilu nzeru alibe. Manganya asatipusitse uyuyu ndi waganyu wa MCP ndipo kunkuyu. Ndi manganya mukanangothana nawo
Umbuli umenewo
Iwe mayiko usi ndiwe munthu woyipa mtima kwambiri kodi Saulosi chilima atamwalira unalankhula chiyani?
Akuti manganya akudutsa kkkk anyway komano ngati dziko sitimayenera kumafika pa mlingo umenewu, adindo kuboma komanso onse adzipani dzotsutsa, ntchito yobweletsa anthu pamodzi ikukukanikani, mapeto ake ndi nkhondo pakati pa mitundu ya anthu.
Aaaa dzofuna mene dzamvutila ku Malawi wina adziti mcp MANGANYA CHISILU
Good action osasekerela zamanyi(zopusa)
naeso Michael usi mfundo zopepela ngat zimenezo
Amene mukuwapotawo nawonso ayenda. Campaign sapangila konko ku ndilande akamenyedwanso nawo Madera enawa.
Iwe kodi azikwanje ku Lilongwe a M C P anapangapo chani?
Zako izo Bola agendedwabe
Akulu inu mzeru mulibe etiii azikwanje aja ndi akuti achewa mumajaila kwambl mumaona ngt kumwela ndi anthu ogona well done ndix
❤❤
Mr vp akumveka ngati ayamba ubusa😂
Aaaaa manganya ulimuzereza ukaona kuti wamuluza iwe 20 million wakawevyeso
Osamasekelera zopusa welldone
Wawa kwathu Ku Ndilande
Singing Cody Sangalas song
😅😅😅😅 anthu mwakwiya eti😂😂😂😂😂
Akuti udindo alive nawo ntchito ndiye kuti anthunso alone nawo ntchito manganya ndichitsilu
Mwina akupanganso program ya gululu
Mcp inayambisa yokha ziwawa mziko apa mwachita bwino kuwawonesa akuzorowera ana achikangawa very good guys munthu pena umafika potopa
Well done kwathu
First time to hear good words of wisdom, Dr usi
Ndix hozaaaaaa!!!!!! Mwatiyimilira kwambiri
Ndilande guys well done
Mumakwana
Mumangidwa
Alakwa chani...😂😂😂😂😂😂
😂😂😂😂😂 Koma ndie kunali kutsokomolatu Eni akundlande.
Ndix siyisekelela zopoila 🔥🔥 well done madolo🔥
Chipongwe chaku lilongwe abweza ndi Aku ndilande 🤣🤣🤣
More fire ndilande akabwelaso mudzangopheratu
Nanga nthawi yonseyii inu mumalekeranjii kumathandiza anthu ovutika
Kd ku Ndilande munayenda bwanji?
Ndinkakonda mukufelanji coz munali malangizo ndizonse zochitika ndziko muno anthu ambiri amaknda tikufelanji koma pano mmmm mr😢
Ine nakana kupereka tuwente million🙄🤣
Zonyadilitsa Zikhale iziii?
Amanganya zosamveka zoyankhulazo. MCP inapanga convention ndi ndalama zingati? Achitabwino kukugenda ukhaula sunati
Dziko lonse lamalawi likanakhala logwizirana Ngati anthu akundix kkk bwezi zili bhoo ndirande ndi Mogadishu kale 😂
Unadziwa kuti sungawine. Chakwera wako uja akugawa ndalama zophera anthu? Ukufuna kupusisitsa ndani?
Dziko lomvetsa chisoni Malawi 😢
Kutu moto buuuuuuuuu ndilande woyeeeeeee💃💃💃💃💃💃💃iya osamangosekerera zilizonse Michael usi mmmmmm bodza ilo mwazionatu ku ndilande
Good job ndirande😂😂
You had a problem Mr vp, ndale izi zizakusiya pa mabvuto chifukwa onse akudzungulira ndi afisi ukhoza ku khala munthu wa bwino koma enawo Ali oyipa
Thanks ndirande
MCP inapita ndi Chilima ndipo inu a MCP muziziwa kut anthu Ali ndi mkwiyo ndipo 2025 akuonetsani. Iwe Usi vomereza kut anthu Ku UTM akukana, chikhala kut amakukonda ukanakaima nawo ndipo ndalamayo ukanapereka.
20 million ikanalowa mmadzi opanda kukuvotera. Ukabwenze ndalama za anthu a mu msika usanakalimire nkhalamba.
Hmmm kuyankhula kopanda nzeru neef ija mwatipatsa mwaiwala kuti mutinamiza kuti tirandira neef
Northern Region is with you but let us remove Chikangawa with our votes. Nkhondo siyabwino ngakhale ayambise ndiwo a MCP tiyeni tiyipewe tose tikhoza kuzavutika nayo kumbuķilani kuti tili ndi nkhalamba, ana, wodwala mu zipatala, awulumayi womwe sangathe kuthawa. Central region ndi mcp yawoyo yalephera kangati ? Kuti lero azinyoza zigawo zina nkumati awina pa wokha. Ine ndimawona ngati Chakwera ndiwanzeru koma ayi dziko likuyenda ngati tilibe President. Ali busy ndi akwawo kumawalimbikisa kupanga zipolowe lero ndi izi zikufalikila palipose and yet he is quiet like a brind person.
Tikuvutika...ndixville more faya 🔥
Dikira ku Lilongwe muzatemedwe
Nyelo wako
Chosadziwa chimaombera Mfiti mmanja
👹⚒️🔨⛏️🐊🐊👹
Amanganya zoti anthu aphwanya malamulo zija nmangonama eti khani ndi 20 million
@@SaidSamuden chitsiru Manganya anapha Chilima ankaona ngati angolowa u president wa utm. Converntion imapangidwa kuti yaulere, alibe manyazi munthu opanda nzeru, nchifukwa chake dzikoli silikuyenda nzeru zake ndi zimenezi zopusa. Wachita manyazi ankaona ngati iliphereka. Wamunamiza Chakwera ali anthu a utm anditsatira ndikapha Chilima. Lero waona mmudzi mwa Chilima.
Well done chani mukuwona ngati MCP ingaluze chifukwa Cha ndilande mwawuponda
Speech ya ugalu dza dzi ,usi nzeru alibedi
A Kunkuyu ndi a Kwa Manase.
Akupoto kuno tiyeniso tipase moto azibwerera kulilongwe komweko monika kuno sha uwelele kwenekuko
Awachita bwino boza lachuluka😅😅😅😅😅😅😅
When. It comes to Ndilande we don't share Sweet's🎉
Achita bwino bola akanangomupha kunkuyu ndi manganyayo
Malawi wanga ine Inu nkunkuyu ndi usi angamapange misonkhano panopo mdziko muno pamene zililimu? Chifukwa chani nduna zaboma ili zili zosaganiza? Anthu akuvutika kwambiri muno fuel ndi amene wafika posowa chonchiyu Iwo ndithu ndikumapita kumakapangisa nsonkhano zinazi aziganiza amati anthu akawalandira bwanji mmmmmmmhu 🤔🤔
Umakwana ndilande tatopa ife iyaaa😂
Chifukwa chiyani inu anthu wonse a ndale Mukubweletsa kugawikana kwa anthu mdziko? Kodi anthu amene mukufuna kuti mudzawa lamulire ndi ati?
Gzonena zasowa kkkkkkkkk Andale Anawumba kusauka akuona panopa Hehede campaign yonama Tatopa nanu Tionana 2025 Kuchenjera pakamwa
USI wa MCP, viva Sks
Ameneo akufunika malegeni bas
Amazing angatani
Amafuna za ulele kapena amafuna angosakhakhidwa ku UTM tikufuna commitment people
Uthenga kwa Amanganya wadziwonera yekha kumeneko ndi kuyambika kwa nkhani ya kukakamidza kulanda chipani cha utm, Ngati manganya akufuna chipani ayambitse chipani chake
Uyu akuti Manganya uyu ndiosonedza kwambiri. Apitira limodzi ndi Chikangawa uyu. Zake zada basi.
Kkkkkkkkkk
Manganya eeee
Kkkkkkkkk
Mtima zikupweteka 😂😂😂😂😂
Apa a Chakwela ndie axiti chani?????
Mwazigenda pang'ono mbamvazi iyaa ndipo dzilibe manyadzi
Zowona zikuchitikadii ku Ndilande ?Eeeeshi zowophyq,
Sadati aziona,kapena tinene kuti a zigwola2025 Moto
Inu ndix ija imakhara busy kusaka ndrama basi inu kungovumburuka mmaganiza bwanji koma
Ndipo lolemba pano paseu osaphwekesa achokedi agalu amenewa aiwala azikwanje awo aja lero zawapweteka chifjwa ndiwowo😅😅😅😅
Nde Monday anzanu sabwezera?
"Anthu amafika potopa" ndakatulo ikhale imeneyo by Robert Chiwamba.
Mfundo yako ya bodza iyo,ndipo umkadziwa kale kuti ku convention ukaluzako ndipo panalibe amene adakakuvotera ,osatinamizapo apa iyaaaa
Mmakwana hi guys kumagende kumene, Ife ikudikila wakulu wameki
Usi akunama akufuna atipusise kuti apeze mavoti.Malawi yonse ikuvutika.
Wasala chakwera iye tizangomusinga basi azapite mtembo
Sukanawina Palibe akanakusankha
😂😂😂😂Waziwa liti?
Ndipo asamazione kuchenjera Buluzi ameneyi akapandanso kusamala Ku MCP komweko amupanga Kanyenya musiyeni
CHILIMA ANAFOILA KUTENGA NYAPAPI AMENEYU. NGATI ZILI ZOPANDA PHINDU ZISIYETU PANYERO PAKO
Kodi anthu amayimbila mmanja chani?
Kod sangabweleko kusalima nafeso tizawagendeko
Manganya mfundo zabodza izo..... kuti uganize mavuto onse akwanu sudzamwa fantatu
Ndirande yomweyo😅😅😅😅😅 mulibho
Musawope 💪💪💪✊✊✊💪akupangasopuzanditu tatopanayenditu✊✊✊💪
Sindikuiona galimoto ya Michael usi
Ulemu ndiwofunika😊