ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
Please a UDF pangani mgwirizano ndi UTM, DPP ndi AFORD basi mwasesa chakwera ndi MCP yake. Payekha payekha ai.
Msongoleri wanuyo akugona kwambir akukaikisa heavy 😂
Atupele wadya ndlama za chikangawa nd chifukwa akubisala amalawi musagone nd UDF
5 Characteristics Every Good Leader Should HaveDecisiveness. The ability to make decisions, particularly when under pressure, is an important skill to master. ...Trustworthiness. ...Empowerment of others. ...Clear communication. ...Resilience.
November 23, 2024
Q
Mumuuze Atupele akugona kwambili
UDF chipani changa
a UDF MUKUZINZA KWAMBIRI
Taphunzirankoni ndale zosanyozana za Chakwera.
Udf chepani changa ichi chinamvetsa amalawi kukoma
Atupele mboli yamako komwe uliko, ukuona ana akuthamanga pa ground km iweo uli chete we know ukupanga alliance ndi chakwera,machende akonso
Atupele akusinza kwambiri kkkk
President atupele ndiwozikonda akanakha la national bamboo wake Bola koma atupele ayi
Koma udf inali kale inatha ndipo ikupitilila kutha ngat makatani
Atupele Muluzi 2025 Boma
Atupere Muluzi is very slow he can't lead the party may be want to join Mcp Chikangawa
Fertilizer kumapeleka kwale chimanaga amabwelesa pamusokhano kenako akamapita nacho wosapasa anthu mutiuza chani apa linakukanikani kale boma nchifukwa anakubelani chipani anthu aku thyolo muyambeso kubwelesa ma fifty kwacha anumber imodzi
Jelasi bas muupo atupere emweyo boma
With this situation, then someone talks of chiliza and payments of dubious claims in billions, very funny Leadership.
Mwagwa kale paliso zokagwa ngati
Koma atupere sindikumumvetsa ndithu
Ollah tidaliseni chonde allah tupere alowe boma president 2025 atiwombole amalawi kukapolo komwe tiliku
Atupere Niogona kwambiri alipo koma
Atupere akukupeperesani
Chipani changa
Ati nyemba 😂😂😂😂😂😂😂
UDF boma
OK
kwawo kapande
UDF inatha
Zilibe kanthu koma ndoyomwe yatichangamutsa a Malawife,,,anthu analimu umbuli kwazaka 31,,,ambilife taphuzila sukulu ya Free primary Education yobwela ndi UDF ambilife makolo athu or azibale athu anazuzika UDF isanabwele,,,UDF inatha koma ndiyomwe inathetsa dziwe la ng'ona lomwe azathu anathelako,,,Machine omwe anthu amanyongedwela aja UDF inakataya kutali,,,anthu amayenda m'tunda kuyendela ma Primary,,,lelo ma CDSS alipalipose chifukwa chandani,,,magetsi ambilife tawadziwa chifukwa cha UDF m'madela mwathu,,,sindinganyoze UDF very shame malawi,,,,nthawi ya Kamuzu umbuli unali 75% osapita ku school UDF itabwela 75 %yomweyo Mukuzi anayisintha kukhala chiwelengelo cha anthu omphuzila,,,,,UDF tiyipase ulemu Maka omwe takula mu Democracy chifukwa tinapeza zambili zitasinthidwa end sizinali zomphweka kutelo ena analuza nazo miyoyo kuti ife tizilongolola chonchi
Kumamaliza kut ngat makatan
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂ndipo inu iwowa angayime okha zaziiii aphatikizane ndi utm bola osati dpp@@RaheemNgoma-pk1ev
Azipani fundo ulendo uno zawathela palibe chomwe angakambe kuti anthu azawavotele
Makamaka zipani zoti zinakhalamo kale mu boma ndiye nyanyi
Alibedi fundo chifukwa palibe chimene angazapange Kodi kupanda chilima kumwalira anthu andale akanatha kuyakhula chani nkhani zakuphazi zinayamba kale nthawi ya udf azimayi amadulidwa mawere pp kunali nachipati dpp malibuno antha wose ndiye tatiuzani zimene muzapange udf ngati kuli chipani chimene chinabwelesa umphawi ndichimenechi kamuzu anasiya ma company wochuluka aboma koma bakili anatha kuwagulisa Kwa mwenye
Palibe choposa kugwetsa ndege ndi kupha chilima ndi ena 8 kotero mfundo zose zagona mmenemo.
UDF INGAMAONEKE CHOCHI
Please a UDF pangani mgwirizano ndi UTM, DPP ndi AFORD basi mwasesa chakwera ndi MCP yake. Payekha payekha ai.
Msongoleri wanuyo akugona kwambir akukaikisa heavy 😂
Atupele wadya ndlama za chikangawa nd chifukwa akubisala amalawi musagone nd UDF
5 Characteristics Every Good Leader Should Have
Decisiveness. The ability to make decisions, particularly when under pressure, is an important skill to master. ...
Trustworthiness. ...
Empowerment of others. ...
Clear communication. ...
Resilience.