BON KALINDO LERO PA 23 NOVEMBER WAMUSEKA MWA MWANO MOSES KUMKUYU EMWE DZULO WAGENDEDWA KU NDIRANDE

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 22 ม.ค. 2025

ความคิดเห็น • 281

  • @CathreenKadwala
    @CathreenKadwala 2 หลายเดือนก่อน +16

    Kkkkk Amozy awona mazangazime

    • @LawrenceBelson
      @LawrenceBelson 2 หลายเดือนก่อน

      Ati amozy🤣🤣🤣🤣🤣🤣

  • @Kelvin-c2v
    @Kelvin-c2v หลายเดือนก่อน +1

    Best TV in the world

  • @EMMARKKALIAPA
    @EMMARKKALIAPA 2 หลายเดือนก่อน +2

    😮Ndilande ili ngati soweto ku South Africa 🇿🇦 mmmmm amozy fire 🔥 😅😂😂😂😂

  • @DavieChisale-w1z
    @DavieChisale-w1z 2 หลายเดือนก่อน

    DC you are my number 1

  • @musicoftheviolinstudios.1109
    @musicoftheviolinstudios.1109 หลายเดือนก่อน

    Anthu ngati inu a kalindo,ndili ine ndikanangokuitanani kuseli kukufusani kuti ase ndingalongosole bwanji ngini pa ground.k9.a poti anthu timafuna kuzitukumula.ine ndi ine.

  • @UchizieFMtemela
    @UchizieFMtemela 2 หลายเดือนก่อน +2

    Kulikeda liwiro😂😂😂😂😂the DC vocals kutchaya sound😂😂😂😂😂

  • @PatrickKhutuliwa
    @PatrickKhutuliwa 2 หลายเดือนก่อน +20

    Chomwe mudzimwa a chakwela ndirande siyopa wa police wina aliyese wa ndirande payekha ndi wa army aliyese ali ndi mfuti becareful

  • @ulemummangisa3150
    @ulemummangisa3150 2 หลายเดือนก่อน +2

    Chorus ina chiyambi chothawa ndi kundirande indeeeee onse aunduna athamangitsidwa kundirande eeeeeheeeeeh 😂😂😂😂😂😂😂 ngati mufuna kudIwa zothamanga ask ndirande 😅😅😅😅😅😅😅

  • @josephjana695
    @josephjana695 2 หลายเดือนก่อน

    Iweyo ndi 1 the DC ❤ more fire

  • @GreevinWaMugowa-j9c
    @GreevinWaMugowa-j9c หลายเดือนก่อน

    Kkkkk. Akanangophapo mmodzi mwina akanaziwa Ndirande ,Chakwera ndi Galu

  • @hamiltonsolomon3756
    @hamiltonsolomon3756 2 หลายเดือนก่อน +7

    The DC...Umakwana...More fire 🔥 😍 👌❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @LucyJimmy-z6z
    @LucyJimmy-z6z 2 หลายเดือนก่อน

    Km DC kuseka kumeneko mwakhuta mwano etti 🤣🤣🙌🙌

  • @pilirani3536
    @pilirani3536 2 หลายเดือนก่อน +9

    Koma akupeza nthawi yokafika kundilande mafuta akuwatenga kuti atigayileko ife

  • @KondwaniChester
    @KondwaniChester 2 หลายเดือนก่อน

    The dc my man

  • @Mosa-b6g
    @Mosa-b6g 2 หลายเดือนก่อน

    More 🔥 ndix

  • @LovemoreAlbert
    @LovemoreAlbert 2 หลายเดือนก่อน +1

    😂😂😂😂😂😂 Amozy!!! Ndi aviator wadabwisa kwambiri

  • @mikehambeyani9081
    @mikehambeyani9081 2 หลายเดือนก่อน +3

    Munthu wankulu amatha chilichose wapha sound yachabe kalindo. Moto wako mchikulire😂😂😂😂

  • @WilisonWilliam-d9j
    @WilisonWilliam-d9j 2 หลายเดือนก่อน

    ❤ ndirande siigawa masuiti

  • @RoseMkandawire-e2g
    @RoseMkandawire-e2g 2 หลายเดือนก่อน

    😂😂😂😂😂😂😂 ndiribe chonena

  • @HawardKalipande
    @HawardKalipande 2 หลายเดือนก่อน +2

    Eeee ndiye kukhala ndi danzi kumathanga mwauchitsiru chomchi eeeee ngati cholumatu koma Ndix wandikondweretsa kwambr

  • @AngelaTebulo
    @AngelaTebulo 2 หลายเดือนก่อน +4

    Eeeeee kwathu ku ndirande dela logwilizana eeeee😂😂😂😂

  • @ErickTym-u2m
    @ErickTym-u2m 2 หลายเดือนก่อน

    Kkkk Amozy kudya phazi kkk nde muli chidendenitu angathamangedi kkkk😂😂😂

  • @MosesDicostar
    @MosesDicostar 2 หลายเดือนก่อน +2

    Aname anga 😂😂😂😂😂😂😂😂 awagenda

  • @bridgetmajor3646
    @bridgetmajor3646 2 หลายเดือนก่อน +5

    Amozy dzulo ndawawona ....Atakhala ....kape wapolisi wa mkadzi unja kaya alibwanji😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅

  • @EzekielBanda-r7r
    @EzekielBanda-r7r 2 หลายเดือนก่อน +1

    Kkkkkk koma kalindo ndiye wachipogwe ,chakwela apite kundilande akacheze kkkk

  • @ShanilSindo
    @ShanilSindo 2 หลายเดือนก่อน +2

    Km anthu amenyedwa n ana ndalezi😂😂😂😂odi mkadule chovotera

  • @MavutoFodya-p1u
    @MavutoFodya-p1u 2 หลายเดือนก่อน

    Yomweyo ndilande amozy athamanga ngt sinduna hahaha kma ndaseka ndilande ndi dziko palokha

  • @chigomezgohara
    @chigomezgohara 2 หลายเดือนก่อน

    Kkkk wandiwaza ka intro

  • @gracemandala880
    @gracemandala880 2 หลายเดือนก่อน

    Amozy ayenda wauyo uyoooooi😂😂😂😂

  • @allanmakwiti5145
    @allanmakwiti5145 2 หลายเดือนก่อน

    But that's how civil starts

  • @AmosShadreck
    @AmosShadreck 2 หลายเดือนก่อน +1

    Mudambisa nokha izi MCP, ndipo ngati simusintha mzochita zanu ai this will continue sure

  • @AlivetaFanizo
    @AlivetaFanizo 2 หลายเดือนก่อน

    Keep it up the dc

  • @BunnahAdamh-n7s
    @BunnahAdamh-n7s 2 หลายเดือนก่อน +3

    😂😂😂😂km Boni kalindo Mmmmmm ndi one 😅😅😅

  • @scoltenroma6240
    @scoltenroma6240 2 หลายเดือนก่อน

    Mwa a Mozy muli liwiro,eishhhhh 🙌😂😂

  • @SinsaKachale
    @SinsaKachale 2 หลายเดือนก่อน

    😅😅😅😅😅😅😅😅 amoseeeeee mumathamangaso😂😂😂😂😂😂

  • @CharyLand
    @CharyLand 2 หลายเดือนก่อน

    Koma kalindo ukanatipumitsako 😂😂😂😂

  • @PhunziroMaliya
    @PhunziroMaliya 2 หลายเดือนก่อน +3

    😂😂😂😂😂😂imeneyo nde ndilande

  • @PercyRoos
    @PercyRoos 2 หลายเดือนก่อน

    😂😂😂😂 Komatu ichichi amwene ndi nkhani zina 👊 👊 ☺️

  • @MisheWiliam
    @MisheWiliam 2 หลายเดือนก่อน +1

    Hi guy's what happened Mr Moses kumkuyu, ndizimene tikunzifuna zimenezo

  • @PaulThole-v8e
    @PaulThole-v8e 2 หลายเดือนก่อน +3

    Wayiona mbwaza ameneyu kwasala bwana president

  • @DuffyMthenga
    @DuffyMthenga 2 หลายเดือนก่อน

    A Mozy Awonetsa Malodza😅😅

  • @Kelvin-c2v
    @Kelvin-c2v หลายเดือนก่อน

    Munthu wamkulu kwambiri bon kalindo

  • @MitikuUrketo-l3x
    @MitikuUrketo-l3x 2 หลายเดือนก่อน

    😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅 koma Booooooon kalindo ukhalike.

  • @Alfred-lb4jw
    @Alfred-lb4jw 2 หลายเดือนก่อน +1

    The DC more fire

  • @AngolaChinga
    @AngolaChinga 2 หลายเดือนก่อน +1

    Kkkkkkkk km ichi guys eeee ndimachikonda

  • @shaibuabdallah8878
    @shaibuabdallah8878 2 หลายเดือนก่อน

    Thanks ķwambiri anthu a ku Ndix....Shakwera and his Thugs akujaira

  • @EmphraimNgwira
    @EmphraimNgwira 2 หลายเดือนก่อน +1

    Kkkkk😅😅😅😅😂😂😂 tiye nawo akuvuta

  • @AbdulrazackTCHALE
    @AbdulrazackTCHALE 2 หลายเดือนก่อน

    😂😂😂😂😂 Ndilande

  • @Staphelsavimbindhlovu
    @Staphelsavimbindhlovu 2 หลายเดือนก่อน

    😂😂😂😂😂 mr kalindo woyee 😅😅😅😅😅😅

  • @AdiniYUSUFU
    @AdiniYUSUFU 2 หลายเดือนก่อน +1

    Amuchita bwino

  • @MikePhiri-b2d
    @MikePhiri-b2d 2 หลายเดือนก่อน

    Ndirande can determine your future.ask the regends

  • @PeterMakaika
    @PeterMakaika 2 หลายเดือนก่อน

    🤣 🤣 🤣 🙌 🙌 🙌 Mozeee zanu sizili pabwno..

  • @EmmanuelNgambi-y6h
    @EmmanuelNgambi-y6h 2 หลายเดือนก่อน

    Zikomo kwambir anthu aku ndilande mwaitha kwambir😂😂

  • @JohnwysonBauleni
    @JohnwysonBauleni 2 หลายเดือนก่อน

    Okay koma yaa NDIX

  • @DonnaltaLengman
    @DonnaltaLengman 2 หลายเดือนก่อน +1

    😂😂😂😂😂😂😂😂 hiiii kuno 🙌

  • @IdrisahChuma
    @IdrisahChuma 2 หลายเดือนก่อน

    😂😂😂😂😂😂 kkkkkkkkk Wawa kwathu kundilande😂😂😂😂😂

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza 2 หลายเดือนก่อน +1

    😂😂😂😂😂 Amuchita bwino kumkuyu kuyerekedwa

  • @EDSONNAKULENGA
    @EDSONNAKULENGA 2 หลายเดือนก่อน

    Mukuwaseka azanuwo amoze akalido pajatu mumafikilalimozi kumuloza kulibuli koma zovuta

  • @MalewaEsnart
    @MalewaEsnart 2 หลายเดือนก่อน

    Ngakhale nsundwe imaopa ndilande

  • @giftmakwale-n5d
    @giftmakwale-n5d 2 หลายเดือนก่อน

    😂😂😂😂😂 Boooooon Kalindo kkkkkk

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy 2 หลายเดือนก่อน +1

    Matama onse anamuthera zulo 😂😂😂

  • @CaroKachingwe-m8d
    @CaroKachingwe-m8d 2 หลายเดือนก่อน

    😂😂😂 amozy aziona kk

  • @GriffinTheu-l6i
    @GriffinTheu-l6i หลายเดือนก่อน

    Afana Mossy aaminisa Ku Ndirande kkkkkkkk

  • @AdamMakala
    @AdamMakala 2 หลายเดือนก่อน

  • @ChixomoPeter
    @ChixomoPeter 2 หลายเดือนก่อน +1

    Eweeeeeee 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @kabitokbz
    @kabitokbz 2 หลายเดือนก่อน +1

    😂😂😂 koma adha 🤣😂🙌

  • @SibongileShumba-y2c
    @SibongileShumba-y2c 2 หลายเดือนก่อน

    😂😂😂😂😂koma ndaseka 😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @DalitsoTepeka
    @DalitsoTepeka 2 หลายเดือนก่อน

    Fireeeeeee

  • @UchizieFMtemela
    @UchizieFMtemela 2 หลายเดือนก่อน

    😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂koma bwana DC mumakwanira😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂Chakwera adzaponda pa nsana pa anthu ndithu abwere adzayenda mmalele adzachita kunyamulidwa😂😂😂😂

  • @RhodaChimoyo
    @RhodaChimoyo 2 หลายเดือนก่อน

    Nyimbo iyiyi ikufunika show 😂😂😂😂😂

  • @EmmanuelHarrisonTembo-k4t
    @EmmanuelHarrisonTembo-k4t 2 หลายเดือนก่อน

    Kkkkkkk amuchita bwino,kumkuyu

  • @patrickMakhumba-yc7rb
    @patrickMakhumba-yc7rb 2 หลายเดือนก่อน

    Congrastion Amozy

    • @LawrenceBelson
      @LawrenceBelson 2 หลายเดือนก่อน

      Ati amozy🤣🤣🤣🤣🤣

    • @bridgetmajor3646
      @bridgetmajor3646 2 หลายเดือนก่อน

      Ndipo zinalipo dzulo ife kurephera kudya Lunch😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @IbruraAmadu
    @IbruraAmadu 2 หลายเดือนก่อน

    Sanati kwasala ku ntchewu

  • @MacdonaldMasamba-e2x
    @MacdonaldMasamba-e2x 2 หลายเดือนก่อน

    Tikudikira ma demo aku state house basi🤔🤔🤔

  • @AlickZimba-n3t
    @AlickZimba-n3t 2 หลายเดือนก่อน

    More fire bone umaths

  • @PhilipoGoji
    @PhilipoGoji 2 หลายเดือนก่อน +1

    Koma ndiye wathamanga zedi moses.

  • @Samuel-c1j1t
    @Samuel-c1j1t 2 หลายเดือนก่อน

    😊

  • @MarkElia-i7q
    @MarkElia-i7q 2 หลายเดือนก่อน

    Kuseka kwanji kumeneko DC 😂😂😂😂😂

  • @RonaldTchapo
    @RonaldTchapo 2 หลายเดือนก่อน

    😅😅😅 koma the D.C aziona anthu

  • @chrisboyce2
    @chrisboyce2 2 หลายเดือนก่อน +12

    Tsiku lina kudzakhala Ndirande vs Nsundwe ndipomwe Zinyau kms MCP idzadziwe kuti Ndirande ndi Dziko palonkha

  • @georgeaiwa8661
    @georgeaiwa8661 2 หลายเดือนก่อน

    😂😂😂😂 ndamuwona wadutsa ku Tembisa (ku Sasaflika) akuthamanga 😂😂😂😂

  • @GraceMasiye
    @GraceMasiye 2 หลายเดือนก่อน

    Mix anapeza anthu magalimoto ali pa filling station akudikira mafuta chi line kuno ndi uko,anthu atakhalax2 ndiye eeeh 😂😂😂😂

  • @PamderaInvestment
    @PamderaInvestment 2 หลายเดือนก่อน

    Koma winiko eeeeeeeesssh iwe zuzathek😂😂😂😂

  • @LenadiMthandi
    @LenadiMthandi 2 หลายเดือนก่อน

    Kkkkkkkk ai dzikomo akuva bwanji kukuyu ndi usi

  • @JuniorMandala-r3l
    @JuniorMandala-r3l 2 หลายเดือนก่อน

    Mose watamanga mu Ndix 😂😂😂

  • @EphridaSanje-w1o
    @EphridaSanje-w1o 2 หลายเดือนก่อน +1

    Or momwe ndasekera ine mpka a police kuthawa wapansi kusiya galimoto ati sikuthamanga😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @ChimwemweMathyola
    @ChimwemweMathyola 2 หลายเดือนก่อน +1

    Kunoso kuphalombe tikuwadikila abwele aziwona malemu chilima tinamuwonesa

  • @KenzoNorman-i1x
    @KenzoNorman-i1x 2 หลายเดือนก่อน +1

    Tinatopa ife amwene the dc

  • @StellaMicheal-h1t
    @StellaMicheal-h1t 2 หลายเดือนก่อน

    Kkkkk amuchita bwino

  • @09914960051
    @09914960051 2 หลายเดือนก่อน

    😅😅😅😅😅Kupanda mzimu ndithu ,,,kusangalala ndi zipolowe

    • @ChisomoStiya
      @ChisomoStiya 2 หลายเดือนก่อน +1

      Inu simunakondwe nd anyamata a zikwanje???

  • @YahayaKondwan-mo8hu
    @YahayaKondwan-mo8hu 2 หลายเดือนก่อน

    Kkk a mozy koma ndaseka

  • @schubertcurthbertlubani3547
    @schubertcurthbertlubani3547 2 หลายเดือนก่อน

    Koma anthu azimangilira eeish

  • @amosnyongo6565
    @amosnyongo6565 2 หลายเดือนก่อน +1

    Chakwera akubwera kuzapanga ma push up konko 😂😂😂

  • @AlumakioChingalu
    @AlumakioChingalu 2 หลายเดือนก่อน

    Izi zikufanana ndi zikwanje be zija. Panoa Boni Kalindo akuyamikira zaxhifwamba za ku Ndirande...

    • @AtupereSadiki
      @AtupereSadiki 2 หลายเดือนก่อน

      Wanva kuwawa wa mcp kkkk

    • @symoldicky
      @symoldicky 2 หลายเดือนก่อน

      Chabe kunvesa nkomwe kwakuvuta cuz kod boma ndikangat lakha likungoyanganila nchitidwe ukuchita maka kwa otsutsa boma?? Ndi anthu akhala akufuna boma koma osachitapo kanthu so mmene zawachitila Iwo zakhala zofunika kuchitapo kanthu? Ukafufuza Bo upeza kut aliyese or abusa osata chilungamo akuuza kut izi zakhala chisanzo choti chiulule zolinga zawo

    • @HawardKalipande
      @HawardKalipande 2 หลายเดือนก่อน

      Iwe ukuona vuto?? Kapena MCP yakutuma et???

    • @BeatriceSaulosi
      @BeatriceSaulosi 2 หลายเดือนก่อน

      Yakubayani? Ndipo omwe athamangitsa kunkuyu sachipanitu koma athu dela

  • @abdulsalammkwepu3321
    @abdulsalammkwepu3321 2 หลายเดือนก่อน

    Kkkkkkkkkk nde wati chakwera apiteso ku ndix ,?

  • @RhodaKhonje
    @RhodaKhonje 2 หลายเดือนก่อน

    😂😂😂😂😂 Kwachema ndiku Ndirande

  • @jumawoposi4016
    @jumawoposi4016 2 หลายเดือนก่อน +1

    Komanso mudzimaliza dzinalo mukamatchula I mean mudzitchula ndi Surname yomwe like "MOSSES KASONGO" 😎😎 or Zikhale Kamajekete just like that kuti tidzimudziwa mwachangu

  • @HaroldBornface-b5p
    @HaroldBornface-b5p 2 หลายเดือนก่อน

    😂😂😂😂😂wawa kwathu ku ndirande

  • @Gladm-sy1se1tn6r
    @Gladm-sy1se1tn6r 2 หลายเดือนก่อน

    😂😂😂😂😂 Koma puliziii

  • @RobertNkhoma-h8e
    @RobertNkhoma-h8e 2 หลายเดือนก่อน +1

    😂😂 Ndix sisunga kape kunkuyu waziona