Not all police officers are selfish, but few of them, our request goes to M D F, please come out to protect Malawians, otherwise Malawi is going back to one State
Hello hot current, Bayana Chunga umatha ❤ to say the truth Chakwera is the worse president ever. 2025 timudalire Mulungu atithandize kutipatsa president wokonda Malawi 😢
Ndimati ndilankhule ndi a president anthu Mr chakwera,are you show izi kumachitika dziko lathu la Malawi, anthu onsewo ayenera kupezeka kumangidwa, chifukwa ndi zigawenga ,and are sure you can't see kuti izi ndizosayenera mdziko lathu la Malawi, koma ngati simungathe hand over to our Milltary solder kugwila zigawenga zimenezi, koma ngati simungathe ndiye bola kupanga quite the post of been a President .chifukwa izi mzosayela been tonsefe ndi a Malawi.
A DPP ayiwala kale kkkk any way. Am watching from back seat. No politician can use me. That's why I have never seen a ballot paper ever since. #focus on ur own business. Make money and live a happy life.
Anthu omwe anatenga zikwanje anali a police omwewo omwe aatumizidwa Ku maphunziro a zachitetezo Ku ntakataka NDI Ku Israel by MCP government. If there could be any group attacking anthu a zikwanje definitely you could see the police, that was going around the people taking panga knives, protecting those taking zikwanje.
Big up guys ndakusokosera mkulinga utamvaa😮
❤❤❤❤❤ mulandile ulemu guys nonse pachilungamo chanu chakwera ndimunthu opusa kwambili sangalekerere Manyi omwe anapanga anthu a MCP
Mmmm ambuye mutithandize kusintha nyengo zowawazi
God bless you guys pakutiyimilira amalawi ife tikuchita mantha kuti Kodi ziko lanthu tiziyenda bwanji
I'm starting to love this radio
God bless times radio 📻.
Awuzen anyani amenewa ationjeza agologolo akuona ngat nthawi yatsamunda manyi amenewa kumalawi Kuno Ayi ndipo apa aMCP apa mwawaponda aMalawi pabala losapola
Congratulations kabambe manganya timusiye azivina mu mseu si wa UTM amene uja
Big up Apamkuku mumakamba zoona zeni.
Muthu ukamapita kofusila ukwat sitisuta chamba mukazaona izi ziwan muthuyo kt ,muthuyo ndi wamisala relo MCP ikupita luzisakho malo mopanga kapen akupha, mmm asiyen adalila machine obera koman pa live MCP sizawin
Not all police officers are selfish, but few of them, our request goes to M D F, please come out to protect Malawians, otherwise Malawi is going back to one State
God bless you guys Live from cape town
Nice hot current guys keep on pushing 🎉❤
Hello hot current, Bayana Chunga umatha ❤ to say the truth Chakwera is the worse president ever. 2025 timudalire Mulungu atithandize kutipatsa president wokonda Malawi 😢
Welcome
@@CharlesNyakuipa❤
Watching from Chicago you’re right this pipo ❤❤ amathaaaa
Congratulations guys specially bambo pankuku amayankhula mosabisa chichewa
Kumalawi ay zikomo tikapuma kumwamba basi ndpo mcp mulungu akuwonen
Ndimati ndilankhule ndi a president anthu Mr chakwera,are you show izi kumachitika dziko lathu la Malawi, anthu onsewo ayenera kupezeka kumangidwa, chifukwa ndi zigawenga ,and are sure you can't see kuti izi ndizosayenera mdziko lathu la Malawi, koma ngati simungathe hand over to our Milltary solder kugwila zigawenga zimenezi, koma ngati simungathe ndiye bola kupanga quite the post of been a President .chifukwa izi mzosayela been tonsefe ndi a Malawi.
Ndiokula mtima komanso wakampeni ku mphasa amene aja,,ma boza ngati mkazi,,bodza daily a Usi
Shame on you police and chakwera government lam from Mwanza
He is truly advancing the MCP agenda
Abwana Mr usi anali abwino koma sanakwanitse zofuna za anthu a utm
Hot current here is ur respect guys be sure umusnt take a part on any political in Malawi
And mbusa Ali phee...!lion in a sheep skin weniweni...
Help us God... Babylon must fall!
Mkazi wa pulambala ndi wochititsa manyazi. Anangotaya xul pachabe.
Iiiiiiiiii Malawitu yavuta ,,,,,zikwanje mpaka!!!!!!!!
Kungoika nkhope ziwili koma president naye adziwike
Atsogoleri akuziwapo kanthu , zoona mpaka malawi kumayenda ndi zikwanje? Mpopano aziyenda ndi mfuti kumaombera anthu osalakwa , atule pansi udindo
A police anagulidwa pano ndi aboma la mcp
STEVEN MASEYA unkanena zoona mmmmmmm koma ine kunsava
Okupha ndilupanga lupanga lomwero rizakuphan
There is no democracy here in malawi
Bravo times hot current 💪osaopa
We are not in Mozambique This is malawi
Eee guys mwatokotadi zoona
Zonsezi ndi za dziko la pasi mukayankha nokha kwa amene anakulengani kwayiwo amene adasankha kupanga chisokonezo adza kayankha yenkha.
Police yake yalowa congelence yi
Ili siboma ndi agalu akuyendesta zikoli, Vito kumalawi tilibe apolisi azelu
Koma guys mwayankhula koma anthu awa samara ishii
Koma paliso Radio yina yokamba chilungamo ngat Times?
No
Palibepo
Inde Usi ndi mthira kuwiri kuyambira kale
Awa ndi aguledi afiti anyapala next year akunya basi
Mkazi wa pulambala akhoza kuloza zikwanje
Ine ndinadziwa kuti ma yolamu adzativuta. Kuipa mtima ngati nkhope
Apolisi anapita kukaonetsetsa kuti anthu omwe anawatumawo akakhape. Apolisi athu ndi zitsiru
A DPP ayiwala kale kkkk any way. Am watching from back seat. No politician can use me. That's why I have never seen a ballot paper ever since. #focus on ur own business. Make money and live a happy life.
Ulemu wanu a Times radio. Chilungamo chimawawa... komano osafooka n osaopa oipayo amve komwe aliko ndithu
❤
Chisoni kwa apolice ,ndi tchito .
Ndpo chkangawa eeeee wationesa
It's fair kusasintha nkhope ya Chilima,,nkhope zingati?
Chipani cha masiye chapeza step father RIP SKC
Remember 2025 is not very far from here tionetsana
Anthu omwe anatenga zikwanje anali a police omwewo omwe aatumizidwa Ku maphunziro a zachitetezo Ku ntakataka NDI Ku Israel by MCP government. If there could be any group attacking anthu a zikwanje definitely you could see the police, that was going around the people taking panga knives, protecting those taking zikwanje.
Big up
Akuluakuru ambuye azikudalisani
Kuyamkhula kwanmbili sikuthandiza Koma action
Ndakukondani pitilizani kutiyakhulila zanyamata zathu mwalakhula zoona zeni zeni koma poti chilungamo chimawawa koma fisi ndifisi mwagwile mau amenewu
🤣🤣🤣🤣 We're not apologize!!!
Machend ako
Chitsiru iwe.
Awatu akuona ngati afika ku kenani apolice anthuwa zioneka zokha nthawi ikakwana ,,
Kodi mmene amayankhila a kabwila muja chovuta ndichani anthuwa kuwamanga ndiye poti azipani amakanilana aziwayitana ambali zonse kuti Tanga anthu awa anene okha kuti ndiachipani choti chifukwa zipani zonse timadziwa anthu ake
Very shameful mcp chikangawa party.. 💔💔
Jona do not waste time with foolish Chakwela, he knows whatever happened.
Zachamba
Mngowayika poyera kut chakwera ulamuliro wake ndamene akupangisa izi coz sakulakhura po ngat msogoleli waziko ndekut ndiyiyeyo akupangisa, mwana akamapanga zosokoneza vuto limakhara kwa kholo ndekut khololo silikulangiza mwanayo, or ku chikangawa kuja anapanga ntchito ndi iyeyo coz ma atsara sakubwera chifukwa chani??
Moses kumkuyu sangabwere poyera
Boma lamanyi iri kwambiri nde dzuona ngati awavotere ndani
Kuswa kuswa MCP chkwanje party
Chimwendo ,chonde ma 5 pin ukuwapasa anthuwa tsiku lina udzayankha.
HIGHEST TV IN MALAWI, PALIBENSO MALAWI YONSE
Police ya Malawi ndi manyaka ndipo ndi yosaalilika kuli mbava zokhazokha
One party system, that's what they are looking for
Kumalawi pano kulibe police. Vuto zomapasa utsogoleri akazi lero ndiizi
Alipo akazi ena amzeru koma yolamu ndi opanda mzeru
MCP ine ayi
Apolice awa ndiopepela
Osadandaula yankho lonse ndi Vote basi Namalenga amapenya
Kumkuyu nde galu wa agalu.
Palibepo olamulira apa
Eeeesh
Malawi wanga,tipempha mutidikire Ambuye,dzikoli musaotche moto
Anthu olimba mtima
Ngati kuli boma lonunkha nde ndilachakwela very shame
Eee boma ilili lilindinkhaza kwambiri
Km fuso nkumat inuyo mukufuna kut Malawi akhale wamademo mukutumidwa osadzudzulako mademo opanda tchito ndikukabera Muthu oti akubvutika kupanga bussness yake
Kaya afune kaya. asafune tidzakambabe zachilima paliponse chifukwa sanatiululire chilungamo
Ziuzeni mbuzi zimeneso
Muli ndimbar
Boma ili ndmanyak kapena lapAtumbo
Tikasitha Boma azama gidwayu. amenewa
Aaaa a MCP KUPANDA MANYADZI KUMATI MABOMA AMOYOMOTSO AMAYENDA NDI DZIKWANJE NDIMAYETSA INU GALU WANU MAI KABWILA AKUKANA NSONO UKUTU KUMVUMELA KUTI NDINU A MCP MUKAPA ANTHU MULUNGU ATICHITILE CHITSONI
Tinasankha zisilu zokhazokha kuwaika m'boma
Manyaka boma
Boma lazibwana ili
Maudindo akuluakulu siofunika azimay they're easily influenced look what yolamu is doing akugwilisidwa ntchito anakakhala mamuna bwenz asakusekelela zimenezo
True
Valentino uja akusekerera bwanji, ndimzimai?😂😂😂😂😂
Boma lolephela ili achoke
Mavuto
😂😂😂😂😂Hmmmm
Mau mau mau ayalutseni bs time its enough now
A MCP mitu Yao inayima kalekaletu palibe chodabwitsa apa
Boma ili nde panja peni peni
Malawi tu anafika pa manyi matuvi eni eni.
Powerful hot current 🔥 🔥 ❤❤❤
Mumakwana maguys
Zasangalatsa kuti a Usi sanapiteko,,,,kapilikoni