A police unikani bwino khani iyi Ine ndaiunika bambo uyu anali ozunguza wakhaza, wakuba or family yake ikudziwa bwino lomwe kuti anali mavuto amunthu. Wamuipitsila mbiri nkazi mweee
I think concluding kuti Mervis adapha Mark is very wrong. Its just very unfortunate kuti Mark wafa, koma nkhani yi kuipanga follow bwinobwino zikuchita kuonesa kuti Mervis mtendere weniweni analibe ndi khalidwe la Mark.
Mkazi she is innocent according to her explanation.If anything happens to her a hule ogenda maglass mkulowa nyumba kuuza anthu unthenga wabodza kuti chiwawa chiyambike wa ku chichiri inuso alinafe abale awo a mac waku wire sinanga nthambwa lija anakuonani musanamukomole.so sad
Akunama sadaphe yekha alipo wamuthandizira kupha koma akubisa,ndiri Ku Malawi ko, Ku phalombe, Kwa chanasa Munthu wina anaphedwanso Ndi achibale amkazi koma mkazi yo adati ndapha ndekha Mamunayu pamene amanama adapha Ndi achibale Ake koma iye adabisa sada ulure achibale Ake
Munthu uyu zikuoneka kuti anaphedwa ndi anthu ena omwe anatopa ndi khalidwe lake nkukamumangilila pakhomo pa nkaziyu,this is very bad,she is goin to suffer for nothing shame
Chemwaliwa amayenera kumusiya mwamunayo chifukwa adamuona kuti ndi wa nkhaza....azimayi inde ndizoona banja ndikupirila koma chonde mukaona kuti zafika poonjeza,indothetsani banja plz plz plz plz
Inu azimayi mukafuna kukwatiwa muzionesesa, same as men.nkhanza ukuziona masiku oyambilira osazitaya bwanji kuti aliyense akhale ndi mtendere wake, more over akuchimuna akuuza kale kuti wao ndi ovuta iwe nde ukanakamusintha? Munthu sasintha khalidwe atakula kale maka wa chakumwa pamakhala povuta
Azimayi amzanga ngati banja likusowetsa mtendele ndibwino kusiyana aliyese Ali moyo choncho amabvutika ndi ana
ineyo mmene ndikuinvera zitha kukhala kut anamupha ndi anthu ena nkuzamumangilira
Ine kuona ngati melvis amaziteteza mamunayu anali chigawenga anakamuphaso ndithu
100%,,,azibambo chonde tiyeni tikondane,pilizi
Mavutowa ayambika ndi Doctor Chikangawa.
The voice iyiyi madam anga ananvekako umanlhara munthu wankhunzika koopsya ndainva pain imenei ine 😢
Koma vuto nkaziyo akafelabe kundende
Nkhaniyi ndaimvetsetsa mayiyu sadaphe munthu koma mamunayo chidali chitsiru asakhale wabwino lero chifukwa choti wafa ayi wazipha ekha ameneyo galu wachabe chabe
Ine ndi chitsanzo ndinangochokako mmmmm kupewa zimenezo,umazakhala pamavuto ndiwe ,vuto achibale ake amamuikira kumbuyo,kupewa zimenezo azimayi umangosatsapo matako nkulisiya banjalo,ndipo ndinasiya nyumba yomwe tinamanga limodzi,ana ndikukwanitsa kusamala ndekha,sanandiimbirepo even phone chichokele,kusonyeza kuti ankafuna ndichoke,nchifukwa ankandisowetsa ntendere,ndiye azimayi kupewa kukhala ndi magazi mmanja mwako kungochoka ,moyo utsale.
Koma amai akuwafusawa eeh ndimotosotu alamu zipweteko mm ngolongolola akucita kuoneka ngati nkhani akufotokoza chomchi yamamunao ingatani mmh
She seems innocent.
Mark wapita ndi umboni wake basi
Mmm to be ownest nkaziyu siwakupha ayi vuto linali ndi mwamuna isatileni nkhaniyi bwino bwino
Ndathokoza kuti nkazi wake ali moyo im soooo happy
Anthu anga a mwalomosi tamadekhani kumeneko Maka azimayinu mmm mpaka kupha zoona. Team Mathyanga and chilenje ❤❤
Mkaz ameneyu ndi chigawenga ngat amabubowa mamunayo akanangosiyana naye ali ndi moyo bas mmmmmmm wandiopsa
Despite makhalidwe oipa koma killing each other is no solution...even the bible say
Komatu Mike anali ozunguza,,kungoti sizinakhale bwino zophanazo,,pena azimayi mukuwazunguza ana anzanu ndi zimankhwala nanga kumuthamangitsa osamva
Amuna tadzinenani zowona kulangizana ndi bwino Amuna ena akamamwamowa amakhala ngati amisala osanva kuthamangitsidwa mapetoake ndizimenezo
Nkazi ameneyo nde kt anatopa nazo, amuna ena ndi ankhaza ndipo zikatere amaoneka ngati oipa ndi nkazi pamene oipa amakhala amunawa,
Nde kt chilipo,amuna amaonjeza nthawi zina
Ndipo ife azimayi timapilila kwambili azibambo olezerawa ulemu alibe
@@SliviaJosephynaunuso muli ndi mzimu omwewu wakupha,,kuchotsa moyo wanthu. Mukuyankhulura chifukwa si m'bale wanu waphedwayo
Azimayi 0pusa inu😢
Hmmm it’s not always the case
It seems Mac D ntchto zamuchtira umbon,kma lamulo osamalitengera manja
A police unikani bwino khani iyi
Ine ndaiunika bambo uyu anali ozunguza wakhaza, wakuba or family yake ikudziwa bwino lomwe kuti anali mavuto amunthu.
Wamuipitsila mbiri nkazi mweee
Inensotu mkhaniyi ndikuyiwona chomcho apapa ikukomera wakufayo poti wafa
Wadźyipitsira mbiri yekha kupha ndi kùpha basi murderer ndi murderer kàya ndi Mkazi kaya mwamuna
Olo atakhala ozungunza mpaka kupha
Mwagendatu masana aliyense wakuonani mawa maina anu atuluka anthu akujamburani mutanyamula myala mukanamusiya okuphayo akagwire ndende koma apa akangomwalira mkaziyonso ndiye kuti mukagwura ndende ndiinuyo
Zimayiyo dzinalo akt chani😄😄😄😄
To me,the lady is innocent
Mark wazipha yekha to be honest mkazi wakeyo zangomukhuza kuti anali mwamuna wake
Kmaso fukwaa amayambana kwambiri
Mfumu yodziwa kulankhula Ndapeleka Credit
Pakufunika kuganiza mozama please 😢 khalidwe la mamamuna ndi lomwe lamupha zikanakhala kut mamuna wamowayo wapha kaziyo bwez mukut chifkwa chamowa sichocho apaso chifkwa chamowa
Mamunayi anali ovutisa amasaka pofera
Azibambowaso akalezela kusowesa ntendele ena amakhala chete ena mkazi kumamumenya amuna mukuonjezaso nkhanza mubanja zangovuta kuti mkazi wapha sakanafika pomupha mamuna wake akadangomusiya ndi moyo sanachite bwino alandile chilango
Mwatithawa appliso mpaka wauyo uyo mpaka kusiya zida Kodi amangokula ntima kumademokuja eti
Ndipo Mik amayenela kufa ndithu , chifukwa akanati a safe mkaziyu akanamupha
That's why kwao kwamamuna anatopa naye chifkwa chakhalidwe
Kwambiri
Dzachisoni kwambiri msikana makwatiwa kwatiwa kanyama kotchedwa❤ kanakangokudya ulere komaso ANTHU umboni otsaona ndimaso muphetsa munthu otsalakwa,chonsecho amatsatira potential adzipedza yomwera ataba dzankadzi
I think concluding kuti Mervis adapha Mark is very wrong. Its just very unfortunate kuti Mark wafa, koma nkhani yi kuipanga follow bwinobwino zikuchita kuonesa kuti Mervis mtendere weniweni analibe ndi khalidwe la Mark.
Ndiye mtendere ukamasowa mumaphana?
@@jeremiahmalikebu2393bambo ogani bwino ngati inu achulukilebe mamuna ngozunguza uyo azmai manyumbamu tikufela mau oti banja mabanja anali kale kwasalaku ndi phada mack zomwe amafuna wazipeza
@@mishecksipolo7153 mervis ngati wapangadi zalakwika sikuphana mwina anthuo amamenyena amaziteteza mkazi, kodi atakhala waphedwa ndimwana wanu wamkazi mungaweluze bwanji?zikuoneka kuti chenicheni chapha mak sichikuziwika ndikumvela momwe wafotokozela mkazi bola ngati sakuzibakila
Kulankhula kopusatu uku
@@dinganidzombe8517 kuti kopusako?
Mark anali chidakwa komanso wakuba mowa ndi njala zamupha mark. Guys mkadzi sangakwanitse kumumangirira mwamuna olo mwamunayo ataledzera motani. Komanso nangati kuli munthu wamakani ndi munthu oledzera ndiye mkadzi sangakwanitse kutenga chingwe ndikumumangirira mwamuna
Azibambo enani pena mumawonjeza mukamwa mowa , simufuna kungogona koma mkazi asowe mtendele basi.
Kolingana ndi momwe ndayimvera nkhani yonseyi, mkaziyu ndi osalakwa. Akangochira apite kunyumba ndi Mfulu. Second hand information imaononga zinthu.
Azimayi akati ayifere banja sopano, this level of desparetnes is demonic, woti amukanika ache abale ake sungamusithe ndiwe.
Eeeeh mabanja obvutisana mapeto ake amakhalatu awaa 😭🙌
Ankle akuti mkazi anabwela kumazammenya mwamuna wake osanena zomwe amamenyedwela, akubisa kuti ndiwakuba komaso ndichindakwa
Komanso azibambo ngati mukuziwa kuti mukamwa mowa siziyenda mumasowesa mtendere panyumba ndi bwino osamwa chonde zachitisa kuti wina kuti achimwe nazo mzimu wao uuse mumtendere pepani
Mkazi she is innocent according to her explanation.If anything happens to her a hule ogenda maglass mkulowa nyumba kuuza anthu unthenga wabodza kuti chiwawa chiyambike wa ku chichiri inuso alinafe abale awo a mac waku wire sinanga nthambwa lija anakuonani musanamukomole.so sad
Ambuye achitile chifundo dziko la Malawi 😢 sizilibwino ndithu
Malawi wa lero chikondi chinazilala
Ofcourse mark anali ozunguza koma pomupha pokhapo walakwa mervis chondee
Abale Mark wake uti
Ndimafuta kt hule amawuza anthu kt wavomela amupanikize ndi mafuso komaso ndikubwelera mbuyo zikanakhala bwino titavako kwa kamwana amakanena kaja
Azibambo muyaya kaza kwazimayi
Khaniyi koseku imayenda bwino ndipo mamuna anali ndi mvuto koma pomwe mwalakwa Amayi kumupha ozimangilila samafa choncho
Amai awa eeee ndotopola
Mark wolongeza longeza amakatani kwankaziyo usiku ngat umeneo
Umbava amakaba
Aaaaa km nkhanii ilibe umboni oti mwamunayo wadzimangilira chfkwa chakut
1.munthu podzimangilira amaphupha nde m,mkaziyo angalephere kuva pamene mwamunayo anadzimangilira panja aaaa kms
2.munthu odzimangilira amadziipitsira ,kms ririme la munthu yo limatuluka kms
3.nyumba yomwe wadzimangilira munthu yo ndiyamalata nde m,mene amkaphupha munthu yo iyeyo samkava aaa
Zomwe akunena anthu wazi ndizabodza kms akudziwapo kanthu
nkhani ikuveka kut mwamunayu anali wozunguza nde mkaziyo wangotenga soka
She might be innocent
Innocent for what ?
Zikuoneka kuti anthu onsewa sakudziwa zomwe zachitika zeni zeni . Pofunika a Police agwire ntchito yawo mwaukadaulo.
Mkazi anabvomera chifukwa anali under pressure 🎉
Why questioning patient hospital yotani yololeza reporters in
Akunama sadaphe yekha alipo wamuthandizira kupha koma akubisa,ndiri Ku Malawi ko, Ku phalombe, Kwa chanasa Munthu wina anaphedwanso Ndi achibale amkazi koma mkazi yo adati ndapha ndekha Mamunayu pamene amanama adapha Ndi achibale Ake koma iye adabisa sada ulure achibale Ake
@@dondamissonchdziwe3958 eti inu yekha nde amufusa kucipatala kuja kuti ayi adatulusa lilime amfusaso ozimangilila amatelo amvekele ayi kukhalangati sanatuluse lilime sindinaone bwino kuzikola yekhayekha eti
Mark akanakuwa
Mmmmm try to be control abale mpaka kumpha mwamuna iiiiii
Mamunayi akadziyamba dala nkaziyo anatopa nayo
She is sounding innocently..... Nanga anaaja anali munyumba mommo akunamanso???
Ndichifukwa chake Atumbuka akukana mwamuna kukakwatiwa kwa mkazi nde kaye khalidwe limenelo loti mkazi aziti chokamo munyumba mwanga eshiiiìiii zosakhala bwino km 😭😭
Imfa siithawika
Munthu uyu zikuoneka kuti
anaphedwa ndi anthu ena omwe anatopa ndi khalidwe lake nkukamumangilila pakhomo pa nkaziyu,this is very bad,she is goin to suffer for nothing shame
Chemwaliwa amayenera kumusiya mwamunayo chifukwa adamuona kuti ndi wa nkhaza....azimayi inde ndizoona banja ndikupirila koma chonde mukaona kuti zafika poonjeza,indothetsani banja plz plz plz plz
Ukalodzedwa sunukha ..amuna ena akalodzedwa amasowaa pofera ili NDI tsoka ili... Amakanika kusasidwa inu .... kukhala Ngati chiyabwee
Achewa muli ndi vuto mwamuna amakwatila osati kukwatiwa😂
Mmh koma mkwiyo otani umenewu Melvis?
Chifukwa ndichani mungolimbikila kumenya basi aaa nenani chifukwa?
Mkazi yu anali olimbatu tu mpaka kukomoka eee ndikudzidzimukattu😊
Banja la miyezi yochepa mpaka kuphana nanga munakatha zaka mmmmmmm mervis ndiwe olimba mtima
komananga mthawi yomwe amakangana amati chifukwa ndichani akuchimuna tsakunena,
Mark wadzipha yekha. Koma poti wadziphela kwa nkazi thats why zatelo.
Even explanation yankazi, ikuwonetsa kuti she knows nothing...
Inu azimayi mukafuna kukwatiwa muzionesesa, same as men.nkhanza ukuziona masiku oyambilira osazitaya bwanji kuti aliyense akhale ndi mtendere wake, more over akuchimuna akuuza kale kuti wao ndi ovuta iwe nde ukanakamusintha? Munthu sasintha khalidwe atakula kale maka wa chakumwa pamakhala povuta
Amati zopeweka pewani ndithu mmmm
Koma my lweyo uli pavuto bola ukanangofa sure 😢 pamenepo ukatuluka upita ku police
Cousin vuto linali chani maka maka mubanjamo , cousy Azemba funso eish Mark
Eti abale alithawaditu funsolo
Dziko langa😭😭😭
Yiiiii azimayi nchan ufit muzipanga kwanu konko
Dzina lachani??
Mmm koma zokhuza, mpaka kupha mamuna? Nkazi wankhanza uyu
KANTHU NKAKO.. KOMA MWACHIDULE MKAZI UYU NDI CHIGAWENGA. KUPHA NDIKOWOPSYA
Koma.zina kukava kamba mwala chikondi chikasowa ndichocho, Ambuye atithandize ku dziko lathu eish
Sad
Nkhani tikuisatila momveka bwino anthu akunena kuti mzimayiuyu ananena kuti amupha ndipo ananena kuti iyelero amupha ndipo mwamuna kumanda iyeyo kuchichiri nkazi uyu ndiwabodza akuyetsa kuthawa mlandu uyu ndiwakupha .amai amwamuna ananena kuti amumange kusonyeza kuti amai amwamuna anafuna mwana wawo wamoyo osati wakufa nzimayi uyu ndi oipa
Khaniiyi yuchita kuzikqmba yokha kti mevis is innocent 😢
Muganiza ngati ine mamunayu mkuona kuti kupepetulidwaa
Munthu uyu ngosalakwa i think
Mmm zosakhala bwino
Why Malawi 😢
A police afufuze bwino bwino
mowa womwa wopanda nako nzelu , zosatila zake ndizimenezo
13:57
Wanvano wokupha
Akundiyankhulira mojejemajejema mzimayiyu pa statement yake yokhudzana ndi imfa ya mamuna wakeyo
Yakwiya ndi mizimu apa.
Ameneyo adamudyetsa makhwala oipa coz munthu Mpaka aziyankhula mau okuti ineyo sindikudziwa chomwe chimandichitikira ? Mmmmm ,,,azimai tiyeni mamuna ngati sitikumufuna ndibwino kumukakamiza ndithu kuti azipita kwao osati mpaka tichotse moyo wake choncho ayi mmmmmh
Ndionama mayiyu mwezi iwiri sizingakhare choncho akunama kwambiri
Mark koma mowa amaonjezad, koma anali ochezeka ll!
Afumu anthuwa mumakhara nawo limodzi koma zikuonetsa kut simunapeleke uphungu uliyose kwa anthuwa
Musamadzinamize kuti tikapuma kumwamba mukunama tu inu
chigawenga chachizimayi
nkhaniyi ikuwoneselatu kuti Miki azuzisa mkazi wosalakwa
Don't interview kids
5:07
Zifunika kufufuza
Ndimanena mobweleza bweleza kuti mabanja anali akale, masiku ano kulibe mabanja bola osakwatila.
Eeeesh zosayendatu kwabasi
Tikapuka kumwamba bas eish
Wy Mack kwathu chikuchitika ndi chani
Mwapanga mbiri anthu amwa chunga, ndamudandaula mark zinazo nzake koma anali ochezeka😢😢😢😢
Amaiwaso abodza osasa mauwa
Ndipo ngolongola mmh
Mkazi yo adali kale mchiwembu ndi mamunayo anatani kumusiya Ali Moyo mpaka kupha mmmmmmmm