God protect you Brother Man Kamangira Man of integrity we need people like you we know that Lawyer wama Lawyer and Judge wama Judge is God himself keep it up
There was this popular song in those days ..one line went as follows...' mnyamata wa ndebvu zampanda ngati Silombela!! '.... very popular it was . I can say that song was prophetic. Here is ' wa ndebvu zampanda uja' in reality..l adore you Council Kamangira. God bless
Mulungu amumenyere nkhondo Kamangila chilungamo chipambane, Satana ndi atumiki ake asapeze mpata kupondeleza amalawi osalakwa. Let justice win. Long live Kamangila, come, come to Malawi justice. 🙏🙏🙏
Pempho langa likupita kwa Sylvester Namiwa,,,plz Hear what Mr Kamangira talking en take an action plz we got our brothers,, sisters in prison but nothing gone wrong plz help 😢😢😢😢
Uyu yekha watumidwa ndi Mulungu, musamukhudze akukanthani Mulungu ndithudi. Imagine how many helpless Malawian are praying for him. Justice has come to Malawi.
We need reform n private or independent judicial body,. Not ma department okondela Bomba kuseliku akumaba. Z Dziko lathu luonongeka tungoonelera we the youth let's join our hands with mr A Kamangila to overcome this challenge
A Kamangila taonani ku Industrial Court pa nkhani ya ku Press Corporation. Anthu amalandira munthu mmodzi mamillion 30 pa mwezi. Tayifufuzani. Kuba kudzela mu masalary ndi ma allowance.
My sister was having a case at Neno magistrate court and a judge ruling was a protection order to be granted to my sister but to my surprise we were ordered to pay money for the free protectinon order forms.
Ilekeni imeneyo inenso not even my belongings,after I contributed a lot using my graduity. Ma court ndi a Chimuengo, the judgement was good but ma Shellif ofunikanso kuwaona bwino.
KKKK YOU ARE LIKE ME SPIRITUALLY IN 1995 .I PRAYED TO GOD IN JESUS NAME.THAT " LORD JESUS I PRAY THAT I BE PROMOTED UP TO P5 OR CHIEF AUDITOR.AND I SHALL.RETIRE.BUT NEVER EXCELL ME TO EXCEEDING.THAT POST OF P4 AND ABOVE THE POST THAT ARE POLITICAL..WHICH STATES " IT HAS PLEASED THE STATE PRESIDENT YOU ARE PROMOTED TO SUCH X2 POST." @ THESE POSTS WHICH ARE CONTROLLED BY PRESIDENTS ARE SINFUL.SO I DONT.WANT TO DIN OR BE SINFUL PURPOSRLY..> AND JESUS CHRIST ANSWERED ME..AND HERE I AM.HAPPY...THANK YOU JEDUS CHRIST.AMEN.
God protect you Brother Man Kamangira Man of integrity we need people like you we know that Lawyer wama Lawyer and Judge wama Judge is God himself keep it up
There was this popular song in those days ..one line went as follows...' mnyamata wa ndebvu zampanda ngati Silombela!! '.... very popular it was . I can say that song was prophetic. Here is ' wa ndebvu zampanda uja' in reality..l adore you Council Kamangira. God bless
Allah kutsogolele ndikuteteza , akubawa akuda koma alibe phamvu zoposa za Allah, allah mutandizeni fana yu ndia malawi 🇲🇼 onse
Mulungu amumenyere nkhondo Kamangila chilungamo chipambane, Satana ndi atumiki ake asapeze mpata kupondeleza amalawi osalakwa. Let justice win. Long live Kamangila, come, come to Malawi justice. 🙏🙏🙏
Pempho langa likupita kwa Sylvester Namiwa,,,plz Hear what Mr Kamangira talking en take an action plz we got our brothers,, sisters in prison but nothing gone wrong plz help 😢😢😢😢
Allah akafuna kuyalusa anthu oipa amapangadi
Mulungu akukulitseni 🎉🎉🎉🎉🎉 you are really good citizen
You're the best may the good Lord protect you
Uyu yekha watumidwa ndi Mulungu, musamukhudze akukanthani Mulungu ndithudi. Imagine how many helpless Malawian are praying for him. Justice has come to Malawi.
Vyetee ❤❤keep on fire 🔥🔥 burning,,,,fear not
Kuti zinthu ziyende kumalawi kuno zikufunika anthu olimba mtima chomchi...opanda mantha...osaopa...keep it up...Mulungu akusogolelani komanso kukutetezani
This guys is a true brother to saulos chilima ,anamva kuwawa ndi infa ya brother wake😂
Amen amen mulungu akonzedi Malawi yathu mulungu akhale mbali yanu zitheka
Malawi judiciary needs reforms and don't stop doing this we are going to support you bro we need to end injustice.
Fire 🔥 akamangila OSAOPA OSAFOOKA OSATOPA
We need reform n private or independent judicial body,.
Not ma department okondela Bomba kuseliku akumaba.
Z
Dziko lathu luonongeka tungoonelera we the youth let's join our hands with mr A Kamangila to overcome this challenge
Am happy when i see you happy
Respect 🎉Mulungu yekha ndiye akutsogolereni Big
may God protect you and increase your teritories
Shortly you will be minister of justice
Bravo ❤,keep it up
A Kamangila taonani ku Industrial Court pa nkhani ya ku Press Corporation.
Anthu amalandira munthu mmodzi mamillion 30 pa mwezi. Tayifufuzani. Kuba kudzela mu masalary ndi ma allowance.
My sister was having a case at Neno magistrate court and a judge ruling was a protection order to be granted to my sister but to my surprise we were ordered to pay money for the free protectinon order forms.
Good Roya Kamangila number one ❤
God bless you Mr lawyer
Fantastic bro ❤❤
Ma Jaji omwewo kugawa chuma omwewonso kutenga nkazi wa malemu yo pena amauza nzawo kutenga nkazi uja.
Ndangonena zongoganiza.
Zikomo kwambiri Mr ndi uthenga mukupelekawu
Malawian needed to be like this guy it will be 100 %
Malawi needs public reforms,, judiciary n defense forces first
You are definitely the best
ine banja linatha sinatenge kalikonse oweruza analephera kundipatsa katundu cauz of chiphuphu
Musandikumbutse😢, passed thru the same
Ilekeni imeneyo inenso not even my belongings,after I contributed a lot using my graduity. Ma court ndi a Chimuengo, the judgement was good but ma Shellif ofunikanso kuwaona bwino.
Our next minister of security
Munthuyu akhangat ndi mgero anthu inu tichenjere
God reward you brother
And we only have 1 Malawi 🇲🇼 ❤
Zoona azimayi ambiri akuvutika coz abambo akupeleka ndalama ku court
Nanga alibe mkono Aja akutchukaso nkupanda chilungamo
Amalawi let's help him speak up, and report to ABC, newspapers, social media, etc.
How can we hold them accountable Sir?
Pakanakhala anthu ochulukilapo malawi muno monga awa bwenzi malawi ali Pena ndithu.
He must be a chief justice
God sent you to open up malawians eye
More blessings for you mn
Tiuzileni big zochita ndicholinga tiziyendera limodzi mudziko Muno Kuti tithane zopusazi
💯💯Mr kamangira
Khan ya network ija wayikamba kkk km apapa ziko ndee likulangidxadi
Inetu pemphelo langa ndilokut ambuye azikutetezela ndipo Malawi wathu asithe athu tikuvutika ife
Kkkkkkkkkk komano ife amene tilikuno kusafikuno ndikgathandizebwaji pachithandizo
Siolemba ntchito onse omwe amalakwa. Ena olembedwa ntchito akumawalakwiranso mabwana awo. Munthu amalandira K120,000. Amamanga nyumba kumudzi kwawo. Analemba mnyamata woti adziyang'anira katundu. Mnyamatayo amamupatsa K30000. Pano lawyer wina anamuuza kuti akadandaule ku IRC kuti mnyamatayo adzimupatsa K90000 basi. Zitheka bwanji munthu wolandira K120000 amulipire wanthito wake K90000?
Chilungamo ndiye ulinacho koma pakufunika kulimba mtima
Tikumupempha Mulungu kuti akuteteni achimwene. Chifukwa chipani cha ng'ona chi kwake mkupha basi .
Ine pano nachosedwa ntchito mpaka pano sanandipatse ndalama zanga, ku labour bwana yo osapitako
Good speech
Big man saruti mulungu asikudaliza man
He is the best ❤
Kuima pa choona ndibwino. Osaopa umfumu wadziko
Ndiye wina nkumati kumalimbikila ngati amatiwona kuti timangokhala
Love more reality.....
I will be your assistant
AND A COMMON VISSION.FOR THE COMMON.MALAWIAN.
Don't give up ❤❤❤
KOMA IWEO BIG ULEMU WAKHO ALLAH BRESS U
Mulungu aikepo chitetezo pa moyo wako brother
And guess what ❤❤ there's sense in every nonsense
Try to make your presentation, as short as possible. 30- 45 minutes I think is enough thats my opinion.
Chilungamo chiyende ngat madzi umakwana Iweyo
Akamangira tiphuzitseni kukhala ndi chilungamo tisamapondereze azathu
Welcome bro
Zakuntchitozo ndiye ndipo zooona tinazion
Our pangolin 😂😂😂
Mulungu akudalitseni akamangila
Ineyo uyuyu mene akunenela sindikususa paliponse chifukwa nanenso ndili ndi umboni onveka bwino kwabasi moti atandilola kuti ndiyankhure ndizachita kufotokoza bwino popanda kunyengelela chifukwa file ndilinayo
Tell him don't cool quite
Ndimaku Dalila aise ulibho
Ndikazangotenga boma 2025,Iweyo uzakhala nduna yanga ya za Malamulo. Osaopa, Osafooka, Osatopa. Kusesa nyasi zonse. Zikhale pa mbalambanda.
No one like for bakili tv
Mulungu akuyang.anileni
Km iweyo ndikatundu umakwana
Osaopa osafowoka osatopa❤❤
Mumakwana bwana
Eeeedi bt magistrate mmmm
Pangolin achinyamata.
Mulungu akusogoreren
Kodi mumaveraso bakili muludzi TV ? Kkk chimwendo akut tisamavere
Komatu Chimwendo yo ,ndiye amakhala oyambilira kumvera Bakili Muluzi TV.
Bmtv ndi TV ya dziko lonse la pansi.
Achinyamata dzukani choncho muthandize I ka mangira mukapeza 4 Malawi isintha
Good amalawi nthawi yakwana especially achinyamata tiyeni tithandizane nate lawyer uyu kamangila
Amuna muna
Amen
Uyu Mulungu amuteteza basi
❤❤
Achina manwel sianthu wamba
Unabwela kuzakhala
HAVE TOO MUCH. X2 THAN THE COMMON.MALAWIAN.NOT TO MUCH..
✊✊💯
Big umakwana
KKKK YOU ARE LIKE ME SPIRITUALLY IN 1995 .I PRAYED TO GOD IN JESUS NAME.THAT " LORD JESUS I PRAY THAT I BE PROMOTED UP TO P5 OR CHIEF AUDITOR.AND I SHALL.RETIRE.BUT NEVER EXCELL ME TO EXCEEDING.THAT POST OF P4 AND ABOVE THE POST THAT ARE POLITICAL..WHICH STATES " IT HAS PLEASED THE STATE PRESIDENT YOU ARE PROMOTED TO SUCH X2 POST." @ THESE POSTS WHICH ARE CONTROLLED BY PRESIDENTS ARE SINFUL.SO I DONT.WANT TO DIN OR BE SINFUL PURPOSRLY..> AND JESUS CHRIST ANSWERED ME..AND HERE I AM.HAPPY...THANK YOU JEDUS CHRIST.AMEN.
TO SIN NOT TO SID
Amen
❤
❤❤❤❤
❤❤❤❤❤