Ah akulu, za SKC zo wayamba liti iyeyu? Bwanji sitidamuoneko Bhiyeni Ali moyo akuchita china chake limodzi? Kambala Newton sakunama kuti delegate sakuyenera kukavotera anthu oti philosophy ya UTM sakuidziwa.
In Malawi positions out of merit is not based on their ability to deliver but compensating those who helped them to win. Current MBC director is a good example
Bambo amene akuti a Chilima amanama za fertilizer ,,bambo uyu saziwa za ndrama za Malawi,,fertilizer atha kukhala olo pa k2,000..Malawi ili ndi ndrama,,zonse zija zikumabedwa zija,,maulendo onse aja ndi ndrama
I want Mr Humphries Mvula to make a comment about Kabambe today. Chisoni chinandigwira hearing him akumunyodola. Let us exercise maturity by reserving our negative comments. Let us give people the right forum for them to exercise their capabilities. Look now what we are hearing from the son of the soil.
As patriotic citizens of this nation for once, let's show love to our nation. For so long takhala tikuvotela ndale zamitundu and zigawo as a result taononga nazo Dziko coz talisiya mmanya mwa anthu osayenera mudzila loti ndi wamtundu wanga. For once let's put that aside and vote for a candidate who has the capacity,the energy to drive our nation from where it is to another level. As a nation we can do better, for so long I've refused and I will continue to refuse kunena kuti Malawi ndi Dziko losauka. Malawi is a blessed Nation zinangovuta kuti timasogoleledwa ndi anthu omwe sakonda Dziko lawo ndipo amatsogoza kuba mmalo motumikila omwe anawaika pampando. Titati tapeza the like of Traole or Magufuli in our country, Malawi will never be the same. Let's give kabambe Chance
Kukhala president wabwino kumafunika choyamba ukhale ndi nzeru komaso chifundo ndi chisoni chifukwa ukakhala ndi nzeru zokha sumava kudandaula kwa anthu pena
Your excellency Dr DK please remove us ku Malo oipawa tathawa mmalawimo chifukwa cha uphwawi tili mu ziko laenuwake kuzuzika chifukwa cha mavuto plz tithandizeni sir
Mr Ken ku Ntcheu, mwafunsa mafunso amphamvu. Ndale za ku Malawi, ambiri amalowera kufuna kulemera. Dzombe ku Dowa anadapanga kale makobidi, tiwapemphe kuti atithandize kutukula dziko.
Aubrey from Mpemba am with you and your has really yaonetsa kuti mmatsata politics ❤ bro The late SKC +Chakwera ndomwe akutionetsa mavutowa 😢 this is only facts we have tired
Chipani chili ndi atsogoleri oti atha kutithandizadi ichi,,, koma vuto la a Malawi anthu ambiri ndi mbuli,, or chimene chikuchitika mu dziko sakuchidziwa,,,, koma ineyo i support UTM.
Akabambe ngat kwalembedwa kut muzakhale president muzakhala koma don't promise us too much things, why timaziwa kut pofuna kuwina mkazi sitinena zoipa always good things 🤭🤭🤭🤭🤭🤭
And izizi ndizimene tidapanga thawi ya tonse alliance amatinamiza kulonjeza za mbili mbali koma pano palibe chikuchitika vuto anthu andale mumachulutsa bodza zithu zoti simudzachita
Is kabambe going to fight nepotism and tribalism today after he was a beneficially of the same behaviour? He was elected governor when the Lomwe were in power, and why is it that he dumped DPP to join UTM after the death of SKC? Where were u Mr. Kabambe when SKC was building this and why did u wait that long to join him? Is it not power-hungry?
At least mwanena Chilungamo. I agree with u. Mafunso anzeru. Akuona ngati taiwala how he rose from his ground to where he is. Vuto la anthu we grade speech and make decisions kuti atithandiza without letting the waters settle and pass thru to see clearly..... It's a Shame...
Bro. DK anasankhidwa on merit. He is a very educated person on the economy. Should someone be denied an opportunity to work m'boma only becoz president on that day ndi wa Boma la kwao? 2. Aliyense amakhala ndi nthawi yochita zinthu. Again, mwachilengedwe anthu timayang'ana opportunities in life. Tsoka la wina ndi Mwayi wa wina...... And that's the law of life bwana.
Ine Keneth ku Chanco, ife tipemphe ku Chipani cha UTM ndi a Malawi onse, its time to vote for munthu amene sanakhalepo wa ndale koma ali ndi mbiri yabwino ya chuma cha dziko, koma amaso mpenya ngati Kabambe. Now all delegate sankhani mwa nzeru and ife a Malawi tikusowani Mai Patricia Kaliati mu osogoleri wa u SECRETARY GENERAL koma bwanji ndinu katundutu mbali imeneyi.
Dr kabambe your the best.Choose ma position according ndima merit will save Malawi chifukwa muchepetsa ntchito.Ma udindo m'boma mbwee costing alot looks you know what your talking about.Ican see SKC on you umati adapita ntchito alinayo enawo 🥺
Ameneyu anaba ndalama zambili end 2017 ati amalandila 18 million + ma benefits ambili pamene khalamba zikuvutika athu a ndale ndiwozikundikila ndi ndalama zedi thawi ya DDP makhwala amavuta iye amatenga 18 million + si ufiti umenewu
Dr Kabambe is too smart and so clinical with his explanations.Makes sense
He is sharp
Dr Kabambe remember me in your Kingdom for sure you will win. I see presidency in you.
😂😂
Ndi dolo sukunama
Dr. Dalitso Kabambe you have my Vote... u are such a smart guy.
Keep the fire🔥burning.Kabambe for presidency 2025.Lets try an economist .We are done with church politics.
We want an economist like this Guy... Muno osati manyaka...
This guy is a genius
Ma reverend takana!
Aaahh
I will support whoever wins Ku convention ya utm going forward
We are proud of UTM. Whoever wins deserves my vote too
Dr. Kabambe is a good and smart man and i love him
Dr Kabambe is fit to blaze a UTM political trail to bliss.
APM tinamuchotsa mu Chaka cha 2020 coz analiso naye ndi mavuto ake Pano tikufuna utm nayo tiwone kt itisamala bwanji.
Inu utm inali koko simungaeine chifukwa chilima anamwalira ngoooh 3 years ali momk ndee inu ndan
Akambapo za APM apa .....anthu enanu ndmakape et
Kabambe has just impressed me, for the first time. He has won me.
If kabambe wins at convention, dpp forget my vote. This guy has impressed me
@@chifundomatumula1652 awuze mtchana 🔥😂
@@TsArKhaii uku ayankhula bwinotu
😂😂😂
It’s DPP in UTM
Me 2
Dr. Dalitso Kabambe is the right person to drive this nation forward.
Facts
Not fit for him.He sounds a lot of lies.mmm
Mmmmmmm kut Malawi ndichoncho
@@wassiematula-fp9hqexactly
Zoonadi koma akangolowa m'boma eee shegeeee 😅
Dr Kabambe is the right candidate
I love his confidence....he's SKC by heart ❤
Facts
Ah akulu, za SKC zo wayamba liti iyeyu?
Bwanji sitidamuoneko Bhiyeni Ali moyo akuchita china chake limodzi?
Kambala Newton sakunama kuti delegate sakuyenera kukavotera anthu oti philosophy ya UTM sakuidziwa.
Dr Kabambe is the right person to drive this nation to a right direction.
In Malawi positions out of merit is not based on their ability to deliver but compensating those who helped them to win. Current MBC director is a good example
Dr DK is the wise and right candidate for president of this country not Abusa n MCP. God lead Malawi through DK
Bambo amene akuti a Chilima amanama za fertilizer ,,bambo uyu saziwa za ndrama za Malawi,,fertilizer atha kukhala olo pa k2,000..Malawi ili ndi ndrama,,zonse zija zikumabedwa zija,,maulendo onse aja ndi ndrama
Bambo amene uja wanena zoona ndipo chilima anali mbava
Bodza ilo
kwambiritu, inenso ndikuvomera ,Chilima anali khuluku ndi bodza
True
I agree with the caller million% ,he is absolutely right.
Kabambe has really impressed me.The guy is a genius.You have my vote in 2025
DK my vote 🗳, SKC Legacy still lives
🎉🎉
We need an economist in this country as a president and the only person i can see is Kabambe, keep it up big man, muchotse manyaka awa
Let's campaign for this guy guys
It's not him who will run the government kuli anthu Ku capital Hill mpamene muziziwe Kuti economics ndi zero
@@emmanuelkamwendo2295 fact
Like Captain Traore is doing, he also promised that and the government is surely developing so wonderfully
I want Mr Humphries Mvula to make a comment about Kabambe today. Chisoni chinandigwira hearing him akumunyodola. Let us exercise maturity by reserving our negative comments. Let us give people the right forum for them to exercise their capabilities. Look now what we are hearing from the son of the soil.
Ndipo zinandikhudzaso nane kulakwa ndale zonyozana
We as Malawians, let's think wisely, we need a good leader who have a heart of helping not a heart of destroying Malawi, Dr Kabambe my vote
Its sad athu oyenela kuyendesa zinthu sapasidwa mwayi
Nanga si anthu timasankha kutchuka kwa chipani
Coff yokhayo 100% and to me Kabambe the right Candidature ku UTM
100%🔥
You deserve the position of president of Malawi Mr Kabambe. My vote is for you and I know you will win with flying colors. Much Love from Blantyre.
Glad to hear all the explanations on all the heresy and rumours about this man out of his own mouth clearly.
Akunama ameneyu
Iweyo ukuziwa tiuzen @@ancientnkhata1137
😊😊
I'm the one of utm member and am ready for voting for leader of utm after masankho apa 17 wa
As patriotic citizens of this nation for once, let's show love to our nation.
For so long takhala tikuvotela ndale zamitundu and zigawo as a result taononga nazo Dziko coz talisiya mmanya mwa anthu osayenera mudzila loti ndi wamtundu wanga.
For once let's put that aside and vote for a candidate who has the capacity,the energy to drive our nation from where it is to another level.
As a nation we can do better, for so long I've refused and I will continue to refuse kunena kuti Malawi ndi Dziko losauka. Malawi is a blessed Nation zinangovuta kuti timasogoleledwa ndi anthu omwe sakonda Dziko lawo ndipo amatsogoza kuba mmalo motumikila omwe anawaika pampando.
Titati tapeza the like of Traole or Magufuli in our country, Malawi will never be the same.
Let's give kabambe Chance
Ndiwe wanzeru koma vuto most Malawians ndi mburi
Mr. Kabambe you are a future of our country
The man is fit , can make a good leader
Facts
Koma A Malawi amzanga musamangoti aliyense my vote my vote chofunika ndikuganiza bwino malingananso ndi mmene zinthu ziliri panopa
My vote your excellence DR. DK wish you all the best for the next convention
Kabambe deserve to represent us as malawians
Aubrey ask very gd Questions
Amwene mwafunsa funso labwino zedi, ndipo mulindi nzeru
Tiyeni tizilankhula zoona ngati bwana Aubrey God bless you
It's my wish for kabambe to win the conversation
Let's pray for him
❤
I salute Mr kapembe mfundo zamphamvu kwambiri
May the best candidate win at the UTM convention.
Keep them coming,, Bravo Bryan n times ttv
Kabambe can make a good leader
Kukhala president wabwino kumafunika choyamba ukhale ndi nzeru komaso chifundo ndi chisoni chifukwa ukakhala ndi nzeru zokha sumava kudandaula kwa anthu pena
Your excellency Dr DK please remove us ku Malo oipawa tathawa mmalawimo chifukwa cha uphwawi tili mu ziko laenuwake kuzuzika chifukwa cha mavuto plz tithandizeni sir
You will be back soon God will make him our leader oneday
We need a leader not an economist only
Bingu an Economist ruled Malawi perfectly, lets try Kabambe and UTM hope we wil have a better direction
Let's go and vote Kabambe guys
Let's gooo
The guy is genius
The Lord is with you UTM members very soon tifika ku kenani 🎉🎉🎉🎉🎉 kabambe more fire we are proud u always
l will support whoever wins Ku convention ya UTM ...Koma za fredokiss zilipt
Fredo Saima ngati president,aima pawu Director of youth.
Fredokis akayima pa director of youth
DPP nthawi zonse ndithu imataya mwayi okhala ndi atsogoleri wamphavu. Kabambe has my vote. Keep the fire burning 🔥
Thanks Mr kabambe I love your answer
Kabambe would you please team up with atupele I think you guys can drive Malawi to a next level tapangani zimenezo
How come I missed this interview
Am impressed with DK
Kabambe s the right man to go with ❤
🎉🎉🎉
Mr Ken ku Ntcheu, mwafunsa mafunso amphamvu. Ndale za ku Malawi, ambiri amalowera kufuna kulemera. Dzombe ku Dowa anadapanga kale makobidi, tiwapemphe kuti atithandize kutukula dziko.
APM is not a solution to failures of kongelesi. UTM is
President ndiemwei bass we endorse you Dr kabambe
President ndiemweyuuuu
Aubrey from Mpemba am with you and your has really yaonetsa kuti mmatsata politics ❤ bro The late SKC +Chakwera ndomwe akutionetsa mavutowa 😢 this is only facts we have tired
Then you no little about SKC...
Zowona kwambiri, Chirima anali Shasha, amalakhula zamabodza
Obly from mpemba inuyo ndi akatundu osafuna lamba
Awa sangatithandidze angolubwalubwa ine ndi ndizavotera chakwera🤗🤗🤗
@@EmmanuelSikwese no bro skc ndinamudziwa akuyamba kumene ndale ndi APM ,
Aubrey ndinu wanthu
Chabwino akabambe welcome to utm you have my vote
Our UTM LIVES ON🎉🎉🎉
Anthu amakoma mkamwa before kulowa m'boma. Mbiri imatero ndithu. Wina adanenako ndithu Ku presidential debate kuti "kuyendetsa dziko sikophweka, zimafunika dedication and passion".
DK 2025, my vote!
Kababe the president of Republic of Malawi next year 2025
Tell them🎉
Dr Dk ambuye akusogoleleni ife tonse a SKC
A MCP mukuchedwa pati kumumanga wakuba salareyu bwanji amaberala amalawi ndalama zake ndizimenezi akugawazi
Chipani chili ndi atsogoleri oti atha kutithandizadi ichi,,, koma vuto la a Malawi anthu ambiri ndi mbuli,, or chimene chikuchitika mu dziko sakuchidziwa,,,, koma ineyo i support UTM.
Wayankhula za nzeru aseh honestly atsigoleri abwino ali ku UTM
I love this gentleman. I can see utsogoleli mwa Kabambe
Ndidolo hvy
Kababe akawina Ineyo ndizapanga campagna ya UTM dela langa lonse
Ndidolo hvy
Wa winatu muti bwanji
Why is Brian always focused on kabambe than the rest of the presidential aspirants. I feel this is an indirect campaign for the guy . My view
😂
Don't forget Brian is a politician
Musalankhule zokhuta apa mesa ndi wa ddp uyu brian bwanji osafusa kuti bwanji mudalephela ukoza ali Mboma la ddp
Anali minister chabe he wasn't the president
@@TsArKhaiiadali governor RBM not even minister
Kabambe tinyamule ndithu tose a UTM 🔥🔥🔥🔥🔥
Akabambe ngat kwalembedwa kut muzakhale president muzakhala koma don't promise us too much things, why timaziwa kut pofuna kuwina mkazi sitinena zoipa always good things 🤭🤭🤭🤭🤭🤭
And izizi ndizimene tidapanga thawi ya tonse alliance amatinamiza kulonjeza za mbili mbali koma pano palibe chikuchitika vuto anthu andale mumachulutsa bodza zithu zoti simudzachita
Kabambe is a right person guys vote yanga mwatenga.
Payekha payekhazi muwinisa MCP anyway ndiine wa UDF but I would've loved kuti tipange m'gwilizano with one of these parties
Bwelani mukwele utm woyendesa alipo kale
Kodi apm pokusankhani kukhala governor wa wa reserve bank,anatengela kuti ndi wakwanu kapena munali ndi kuthekera kutero?
The right man for the Job.
The guy is brilliant
Very brilliant
The man DK is going to win from Bishop Andapo Happy Kalagho.
Is kabambe going to fight nepotism and tribalism today after he was a beneficially of the same behaviour? He was elected governor when the Lomwe were in power, and why is it that he dumped DPP to join UTM after the death of SKC? Where were u Mr. Kabambe when SKC was building this and why did u wait that long to join him? Is it not power-hungry?
At least mwanena Chilungamo. I agree with u. Mafunso anzeru. Akuona ngati taiwala how he rose from his ground to where he is.
Vuto la anthu we grade speech and make decisions kuti atithandiza without letting the waters settle and pass thru to see clearly..... It's a Shame...
@@chimwemwelungu1934 nanga si akumaona ngati a Malawi tikanagonabe, tinachangamukatu
Bro. DK anasankhidwa on merit. He is a very educated person on the economy.
Should someone be denied an opportunity to work m'boma only becoz president on that day ndi wa Boma la kwao?
2. Aliyense amakhala ndi nthawi yochita zinthu. Again, mwachilengedwe anthu timayang'ana opportunities in life. Tsoka la wina ndi Mwayi wa wina...... And that's the law of life bwana.
Ngat uyu angawine ngat president wa UTM straight up watenga vote yanga ❤🎉
I like his momentum
More support to this man
DK is the right person
Mtima wanga dekha aka sikoyamba kumva muntu akafuna mpando wau president 😂
😭Mtima wanga dekha usadzanvenso mfundo za abusa
A Aubry fire 🔥burning kufunsa with confidence
A utm ndinu anthu abodza including late Chilima
Zoti manifesto yomwe ilipoyi ndi ya utm ndi mcp idali imodzi koma zinthu sizikusintha mukukana?
Chicukwa chilima ujanso adali ongolubwalubwa
Dk my vote 2025 moto kt buuuu!!!!!!
Boma ndi DK basii
Ine zandalezi zayamba kunditsokoneza mutu.... Hahahha lets vote for utm
Nane ndimati nkavotela dpp koma aaah candidate wapezeka
Ine Keneth ku Chanco, ife tipemphe ku Chipani cha UTM ndi a Malawi onse, its time to vote for munthu amene sanakhalepo wa ndale koma ali ndi mbiri yabwino ya chuma cha dziko, koma amaso mpenya ngati Kabambe. Now all delegate sankhani mwa nzeru and ife a Malawi tikusowani Mai Patricia Kaliati mu osogoleri wa u SECRETARY GENERAL koma bwanji ndinu katundutu mbali imeneyi.
Eya ndiwakuba ameneyu AKUFUNA kudzaononga Malawi
I think this is the guy
Watching from Mozambique
Tilipambuyo panu bwana from mzimba please mcp & dpp iyiiii
🎉
Dr kabambe your the best.Choose ma position according ndima merit will save Malawi chifukwa muchepetsa ntchito.Ma udindo m'boma mbwee costing alot looks you know what your talking about.Ican see SKC on you umati adapita ntchito alinayo enawo 🥺
Best man in ruling.
Lets try UTM guys and i very much wish KABAMBE to win at convention coz this country needs to be ruled by an economists basi.
Ameneyu anaba ndalama zambili end 2017 ati amalandila 18 million + ma benefits ambili pamene khalamba zikuvutika athu a ndale ndiwozikundikila ndi ndalama zedi thawi ya DDP makhwala amavuta iye amatenga 18 million + si ufiti umenewu
Komatu wafotokoza pompa za salary structure ...
@@UlemuChifentheanthu ena amasankha dala kusamva olo chilungamo chitapelekedwa.
@@maur-k8e anthu omvesa chisoni ndithu
Ayankhatu koma
Atleast zinthu zinali zotchipa
I like the confidence ❤
You deserve my vote
Ngati idali formulae ndekuti amaba moopsa kobasi shaaa.