Amuna Misso Tv
Amuna Misso Tv
  • 343
  • 3 911 300

วีดีโอ

DPP IDAONONGA INFRASTRUCTURE KU MALAWI - DR JOHN PAUL- TREASURE GENERAL WA MCP WAUZA BRIAN BANDA
มุมมอง 5K18 ชั่วโมงที่ผ่านมา
DPP IDAONONGA INFRASTRUCTURE KU MALAWI - DR JOHN PAUL- TREASURE GENERAL WA MCP WAUZA BRIAN BANDA
Malawi Congress Party Vice President Catherine Gotani Wayankhula motere ku MCP RALLY Ku Dowa East
มุมมอง 3.3K19 ชั่วโมงที่ผ่านมา
Malawi Congress Party Vice President Catherine Gotani Wayankhula motere ku MCP RALLY Ku Dowa East
GRIEZEDA JEFFREY LERO WANTHA MAU KU MCP RALLY AKUTI NTHAWI YA ARTHUR PETER MUTHARIKA INATHA
มุมมอง 3.1K19 ชั่วโมงที่ผ่านมา
GRIEZEDA JEFFREY LERO WANTHA MAU KU MCP RALLY AKUTI NTHAWI YA ARTHUR PETER MUNTHARIKA INATHA
KUMACHENJERA PATAWUNI INU - CHANGE GOLO ULADI MUSSA WATOKOTA IZI KU MCP RALLY KU DOWA EAST
มุมมอง 4.3K20 ชั่วโมงที่ผ่านมา
KUMACHENJERA PATAWUNI INU - CHANGE GOLO ULADI MUSSA WATOKOTA IZI KU MCP RALLY KU DOWA EAST
DPP ILI NDI UFITI - JESSIE KABWELA WAUZA ANTHU LERO KU DOWA KU MCP RALLY
มุมมอง 4.6K22 ชั่วโมงที่ผ่านมา
DPP ILI NDI UFITI - JESSIE KABWELA WAUZA ANTHU KU DOWA KU MCP RALLY
JESSIE KABWILA WAYANKHULA IZI LERO KU MCP RALLY KU DOWA EAST
มุมมอง 3.2K23 ชั่วโมงที่ผ่านมา
JESSIE KABWIRA WAYANKHULA IZI LERO KU MCP RALLY KU DOWA EAST
ZOMWE WATOKOTA DAN LU PA INTERVIEW YA ZODIAK POTULUKA DPP NDIKULOWA MCP
มุมมอง 8834 ชั่วโมงที่ผ่านมา
ZOMWE WATOKOTA DAN LU PA INTERVIEW YA ZODIAK POTULUKA DPP NDIKULOWA MCP
PRESIDENT LAZARUS CHAKWERA URGES GLOBAL UNITY AND ACTION AT THE 79TH UN GENERAL ASSEMBLY IN NEW YORK
มุมมอง 4234 ชั่วโมงที่ผ่านมา
PRESIDENT LAZARUS CHAKWERA URGES GLOBAL UNITY AND ACTION AT THE 79TH UN GENERAL ASSEMBLY IN NEW YORK
VP Michael Usi Champions Energy Innovations at 2024 National Energy Conference in Lilongwe
มุมมอง 5337 ชั่วโมงที่ผ่านมา
VP Michael Usi Ignites the 2024 National Energy Conference with Bold Vision for Malawi's Future at BICC, Lilongwe
President Lazarus Chakwera Addresses Malawi-Partnership Conference 2024 at Matinique Hotel UNGA 79
มุมมอง 9649 ชั่วโมงที่ผ่านมา
"President Lazarus Chakwera Addresses Malawi-Partnership Conference 2024 at Matinique Hotel, New York during #UNGA79"
SAULOS CHILIMA CANDLE LIGHTING CEREMONY IN LUCHENZA WITH NEWTON DAVID KAMBALA - UTM. 22 SEP, 2024
มุมมอง 1.8K12 ชั่วโมงที่ผ่านมา
SAULOS CHILIMA CANDLE LIGHTING CEREMONY IN LUCHENZA WITH NEWTON DAVID KAMBALA - UTM
DPP’S HON. SAMEER SULEMAN HONORS FALLEN VP CHILIMA WITH EMOTIONAL TRIBUTE AT CHIKANGAWA CRASH SITE
มุมมอง 1.5K12 ชั่วโมงที่ผ่านมา
DPP’S HON. SAMEER SULEMAN HONORS FALLEN VP CHILIMA WITH EMOTIONAL TRIBUTE AT CHIKANGAWA CRASH SITE Hon. Sameer Suleman, MP and National Organising Secretary of the DPP, paid his respects to the late Vice President Saulosi Klaus Chilima at the exact spot in Chikangawa Forest where he tragically perished in a plane crash in June 2024. Rest in peace, Biyeni.
President Chakwera Wakutemwa Wanthu Wake, Catherine Gotani Hara Waphalira Wanthu ku - MCP RALLY
มุมมอง 1.5K14 ชั่วโมงที่ผ่านมา
President Chakwera Wakutemwa Wanthu Wake, Catherine Gotani Hara Waphalira Wanthu ku - MCP RALLY
DAUSI WAPA DZANA - KUNALI ZINTHUTU MAKOSANA 2020 DPP x UDF RALLY NJAMBA
มุมมอง 6K16 ชั่วโมงที่ผ่านมา
DAUSI WAPA DZANA - KUNALI ZINTHUTU MAKOSANA 2020 DPP x UDF RALLY NJAMBA
GRIEZEDA JEFFREY WALERO NDI WAPA DZANA (DPP x MCP x UTM x UDF) WONERANI MPAKA KUMAPETO
มุมมอง 10K16 ชั่วโมงที่ผ่านมา
GRIEZEDA JEFFREY WALERO NDI WAPA DZANA (DPP x MCP x UTM x UDF) WONERANI MPAKA KUMAPETO
BRIAN BANDA KUCHEZA NDI MATTHEWS MTUMBUKA | UTM MEMBER 2024
มุมมอง 31916 ชั่วโมงที่ผ่านมา
BRIAN BANDA KUCHEZA NDI MATTHEWS MTUMBUKA | UTM MEMBER 2024
LERO BRIAN BANDA NDI CATHY MAULIDI APHAPHALITSA MAFUSO PETER MUNTHARIKA - DPP MEGA RALLY IN MZUZU
มุมมอง 1.5K16 ชั่วโมงที่ผ่านมา
LERO BRIAN BANDA NDI CATHY MAULIDI APHAPHALITSA MAFUSO PETER MUNTHARIKA - DPP MEGA RALLY IN MZUZU
MCP MEGA RALLY - EKWENDENI, DAN LU AMULANDILA KU CHIPANI CHA MCP. Chimwendo Banda, 21 September 2024
มุมมอง 8K16 ชั่วโมงที่ผ่านมา
MCP MEGA RALLY - EKWENDENI, DAN LU AMULANDILA KU CHIPANI CHA MCP. Chimwendo Banda, 21 September 2024
PETER MUTHARIKA WANENA IZI LERO NDIPO WAPEMPHA ZINTHU ZITATU KWA PRESIDENT CHAKWERA - DPP MEGA RALLY
มุมมอง 1.8K16 ชั่วโมงที่ผ่านมา
PETER MUTHARIKA WANENA IZI LERO NDIPO WAPEMPHA ZINTHU ZITATU KWA PRESIDENT CHAKWERA - DPP MEGA RALLY
JESSIE KABWILA KUTOKOTA LERO KU MCP MEGA RALLY - ZILIKOLIKO KU MZUZU
มุมมอง 5K16 ชั่วโมงที่ผ่านมา
JESSIE KABWILA KUTOKOTA LERO KU MCP MEGA RALLY - ZILIKOLIKO KU MZUZU
Jessie Kabwila quits MCP, mulls over joining UTM (PA DZANA) Tidzikupatsilani Kanema wapadzana
มุมมอง 1.8K19 ชั่วโมงที่ผ่านมา
Jessie Kabwila quits MCP, mulls over joining UTM (PA DZANA) Tidzikupatsilani Kanema wapadzana
SAMEER SULEMAN WASAMBWADZA MCP NDI DAN LU - “A MALAWI SAMADYA MUSIC” KU MZUZU KUCHEMA LERO
มุมมอง 3.2K19 ชั่วโมงที่ผ่านมา
SAMEER SULEMAN WASAMBWADZA MCP NDI DAN LU - “A MALAWI SAMADYA MUSIC” KU MZUZU KUCHEMA LERO
PA DZANA BRIAN BANDA ANACHEZA MOTELE NDI AKWENI PATRICIA KALIATI ATAWA THOTHOLA PA UNDUNA
มุมมอง 3.3K19 ชั่วโมงที่ผ่านมา
PA DZANA BRIAN BANDA ANACHEZA MOTELE NDI AKWENI PATRICIA KALIATI ATAWA THOTHOLA PA UNDUNA
TIMOTHY MTAMBO ANAYANKHULA IZI KU RALLY YA MCP NDI UTM. WA LERO APOLOGISES TO MUNTHARIKA
มุมมอง 1.1K21 ชั่วโมงที่ผ่านมา
TIMOTHY MTAMBO ANAYANKHULA IZI KU RALLY YA MCP NDI UTM. WA LERO APOLOGISES TO MUNTHARIKA
ZOMWE ALANKHULA LERO A VP MICHAEL USI ZOKHUDZA MALEMU SAULOS CHILIMA NDIPO UTM YAYIMBA MWANSANGALA
มุมมอง 598วันที่ผ่านมา
ZOMWE ALANKHULA LERO A VP MICHAEL USI ZOKHUDZA MALEMU SAULOS CHILIMA NDIPO UTM YAYIMBA MWANSANGALA
Fredokiss ndi Jomo Osman Atokota izi
มุมมอง 6Kวันที่ผ่านมา
Fredokiss ndi Jomo Osman Atokota izi
A Moses Kunkuyu ati Ku Africa Internet Yotchipitsitsa ili ku Malawi” Pomwe akupitanawo ku UNGA
มุมมอง 662วันที่ผ่านมา
A Moses Kunkuyu ati Ku Africa Internet Yotchipitsitsa ili ku Malawi” Pomwe akupitanawo ku UNGA
Malawi President Lazarus Chakwera Kunyamuka kupita Ku Nsonkhano wa UNGA Komwe Ku America
มุมมอง 3.6Kวันที่ผ่านมา
Malawi President Lazarus Chakwera Kunyamuka kupita Ku Nsonkhano wa UNGA Komwe Ku America
Ena Paja Sanamuoneko Marcus Pasenje DareDevils Akuwelenga News Pa MBC Tv. News Bulletin
มุมมอง 124วันที่ผ่านมา
Ena Paja Sanamuoneko Marcus Pasenje DareDevils Akuwelenga News Pa MBC Tv. News Bulletin

ความคิดเห็น

  • @chrischikozera6981
    @chrischikozera6981 57 นาทีที่ผ่านมา

    Aaasaa athu awa ndi about ndithu njaji ku Malawi kulibe

  • @BenardMwale-z4g
    @BenardMwale-z4g ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Koma Ali nu mmalo moti as ankle wina ai Ziwani kuti kamuzu adaluza chifukwa chokalamba Zaka zapakati pa 90 na 100

  • @ChibaleKunsamale-si8qf
    @ChibaleKunsamale-si8qf 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Iwe kayuni ndi fisi wamva mmene zikuvutila ukafanizile ndi nthawi ya DPP kma umaganiza

  • @DixonChimanya
    @DixonChimanya 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Pamtumbo pako galu

  • @LiffaChinkhota
    @LiffaChinkhota 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ndiopusa ameneyu misewu ikadakhala kuti ikumangidwa ndichakwela bwenzi Ikumalembedwa kuti CHINA AID osalemba kuti chakwela derived

  • @Amirkhan-nn6pz
    @Amirkhan-nn6pz 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    May God guide you mama 🙏

  • @NosiphoMazibuko-e9z
    @NosiphoMazibuko-e9z 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Km amwene uladi ndichisilu kwabasi palibe mfundo yomwe wakambapo zokunzana ndidziko latu tikufuna chitukuko dziko lamalawi

  • @NosiphoMazibuko-e9z
    @NosiphoMazibuko-e9z 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    kd mwayiwala kuti inutso amcp umakaphemba kwa bushiri munalibe ndalama lero muliboma mukuba ndalama zingakuvuteni bwanji poti chitumba chili ndi inuyo

  • @NosiphoMazibuko-e9z
    @NosiphoMazibuko-e9z 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kd anakumangani ndindani amcp ka mukuwopa kuchoka angakumangenizo adpp zadakumangeni

  • @NosiphoMazibuko-e9z
    @NosiphoMazibuko-e9z 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Chokani inu mukuwopa kukumangatso inu anakumangani mwayiwala mulandu wanu wopangila anthu akunja ma passport mwayiwala kd mukalowatu inu mumagwidwazo inu mukuwopa kumagwidwa ,

  • @BlessingsFredd
    @BlessingsFredd 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kodi mbulutu ameneyi ndiye UTImuzitibwelesela athu oti atithandiza osati zozizila akukambazi mbava ndi chikangawa wakeyo

  • @HestingsZiba-d6k
    @HestingsZiba-d6k 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Galu uyu kwabasi machende ake pati...

  • @moseskavalo3304
    @moseskavalo3304 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Politics is dirty game.. mtambo now ku Dpp and Dausi ku Mcp 😅😅😅😅😅 maso ndimaso ndi George Kasakula hahaha koma ku Malawi mkobeba

  • @beinhardkausiwa7107
    @beinhardkausiwa7107 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    4 kilometer ya njanji koma mmisonkhano ya mcp nkhani ndiya njanji njanji njanji eeeeee mcp muzichita manyaziii

    • @kingsleyhopematchaya5184
      @kingsleyhopematchaya5184 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      @@beinhardkausiwa7107 dpp chinavuta ndi chiyani kukoza njajeyo or doko la msanje lidakukanikani kod simuyamika kungova kt ndinu otsutsa ndiye zilizonse

    • @beinhardkausiwa7107
      @beinhardkausiwa7107 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      @@kingsleyhopematchaya5184 tiyamikre 4 kilometers are u serious??

    • @kingsleyhopematchaya5184
      @kingsleyhopematchaya5184 24 นาทีที่ผ่านมา

      @@beinhardkausiwa7107 nanga dpp inapangako or 1km kod pa zaka 15

  • @beinhardkausiwa7107
    @beinhardkausiwa7107 6 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kodi mukuwanamiza anthu kuti mwachokera ku DPP,Mesa muthamangitsidwa kalekale?

  • @beinhardkausiwa7107
    @beinhardkausiwa7107 6 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Boma ndilomwelidi koma chipani tisintha next year DPP,UTM,UDF,AFORD zikulowa

  • @JosephMalizani-u7s
    @JosephMalizani-u7s 6 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Alibefundo

  • @JosephMalizani-u7s
    @JosephMalizani-u7s 6 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Uyo ndiwamisara

  • @ManalYahya-q6o
    @ManalYahya-q6o 6 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Brian ndi asatana awa bechodi

  • @WilsonKaomba
    @WilsonKaomba 6 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Uyu ndi mbuzi ya chitsilu

  • @IshmaelNgeyani
    @IshmaelNgeyani 6 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    and almighty god was thier in chikangawa we 'il continue pray for you shone n Elizabeth us we will not stop ask God antil he will give us the truth about biyen's death

  • @rabsonDimba
    @rabsonDimba 6 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    😊

  • @IshmaelNgeyani
    @IshmaelNgeyani 6 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mery I knew that the late biyen was killed with chakwera but we mouns together

  • @TiyanjaneMkwate-we8gu
    @TiyanjaneMkwate-we8gu 6 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mumuziwe yesu ndi ophunzira ake 12.

  • @TiyanjaneMkwate-we8gu
    @TiyanjaneMkwate-we8gu 6 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ndinkangoti ngati muthu Ali Dr amakhala wanzeru koma awa u Dr wao ndi opanda mawo nzeru,apa bola osaphunzilafe mwina tikhoza kubwera ndi ma facts, alibe so manyazi, DPP fertilizer 20 MCP 107, fuel DPP 850 MCP 2750 ,dpp sugar 750 MCP 2500,chimanga 20,000 MCP 50000+, ngati alipo otsutsa anditsutse

  • @Victoriabwaira
    @Victoriabwaira 6 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ameyo ndiopusa kwambiri

  • @BeckhamDavid-v6c
    @BeckhamDavid-v6c 7 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mukutha guys ulem wanu

  • @AdamuKasimu-x5o
    @AdamuKasimu-x5o 7 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Akuiwopa dpp 2025

  • @AdamuKasimu-x5o
    @AdamuKasimu-x5o 7 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Hule ameneyo kubalalika kuchikhope kutalika zachison

  • @BlessingPhiri-br5kv
    @BlessingPhiri-br5kv 7 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kd angokamba za DPP bwanji ayankhe ameneyo nkhan ndiyokut akuba misonkho yathu ife Malawi

  • @BlessingPhiri-br5kv
    @BlessingPhiri-br5kv 7 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Km akuthawamafuso bwanji ngat akut dziko akuliendetsa bwino muwudzen ayankhe nkhan ya fetelezayo asathawe

  • @kingsleyhopematchaya5184
    @kingsleyhopematchaya5184 7 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Fertiliser siwondula brain iwe alimi tikugulitsa 2bags ya chimanga kugula thumba la fertiliser koma 2020 timagula 21000 koma timagulitsa chimanga matumba 7 panopa kwa alimi fertilizer siondula

    • @AndersonChinkwapulo
      @AndersonChinkwapulo 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      @@kingsleyhopematchaya5184 koma iwe udapita ku school? Chimanga ndi feteleza choyenera kudula ndi chani? Wekha ukuti umagulitsa matumba 7 chimanga kuti ugule feteleza, pano matumba awiri achimanga kugula fetereza

    • @kingsleyhopematchaya5184
      @kingsleyhopematchaya5184 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      @@AndersonChinkwapulo ndipamene alimife tikusamgalala koma alesinu ndiye zikuvutani chifukwa mulibe chogulitsa kukwera kwa chimanga kwapangitsa kt tisaone kudula kwa fertilizer iweyo panga masamu

  • @kingsleyhopematchaya5184
    @kingsleyhopematchaya5184 7 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Alimi tasitha chifukwa cha chakwera fodya akugula chimanga tikugulitsa mitengo ya bwino

  • @kingsleyhopematchaya5184
    @kingsleyhopematchaya5184 7 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ndipo dpp sindiyifunaso kuva

  • @GiftMambiya-fh7xb
    @GiftMambiya-fh7xb 7 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    John Paul you are a big fool Malawians sadya njanji you are very stupid guy and you are cursed

  • @RebeccaChikalenda
    @RebeccaChikalenda 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kma lnu muvota mokha kutsogoroku mwava 😢😢

  • @CassimMbalaka
    @CassimMbalaka 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Aaaaaaa akukanika kukuyakhani mafuso ndi mbuli ya muthu sitidya jaji

  • @ChristopherNgoma-c9y
    @ChristopherNgoma-c9y 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Umapita kuzipani zomwe zilu zowina kale...usatinyatse wadanzi iwe

  • @Milanzi-nb5fv
    @Milanzi-nb5fv 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mcp simungawinenso😅😂 mukuziwanso ap

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Sukulu munachita Koma mulibe nzelu

  • @edsonnyasulu5394
    @edsonnyasulu5394 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kunena zoona palibe kusiyana mcp ndi DPP onse ndimbava anthu awa ndiamozi

  • @BarwickSalanje
    @BarwickSalanje 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Munthu uyu wadya ndalama za mcp kuti alankhule za mcp

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Nose a MCP machende anu😢😢

  • @juliochiwalo
    @juliochiwalo 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Munthuyu ndi opanda nzeru chakwera walephereratu iyeyo akuziwa zimenezo ndipo an thu ndi okwiya akuvutika koopsa anthu sadya njanje

  • @MeriaMasinga
    @MeriaMasinga 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Dpp 2025 boma

  • @LemieMwalendo
    @LemieMwalendo 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    We don't need information,we need delivery shupit

  • @MosesDzonzi-em5px
    @MosesDzonzi-em5px 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Boma ndi limwelidi palibeso kusitha ngati wina akufuna kusitha angositha dziko Kaya apita ku joni Kaya ndi dziko liti koma kumalawi kuno sitikusitha boma olo fulu atadukula

  • @paulnyondo7572
    @paulnyondo7572 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kodi kokonza kukhale kulilongwe kokha.

  • @FolamiTowing24
    @FolamiTowing24 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mbuzi scrape politician

  • @Davis-qo4qp
    @Davis-qo4qp 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Zoona Brian waona kuti udokitara wa uyu kulibepo