Here in Chitipa enafe tiribe nthawi yokaima pa nzere wovota... amene muli ndi nthw imeneyo kalembeseni. Koma sizikutanthauza kuti anthu Andale azasintha myomo yanu kulibe,, you are the one responsible for your own future ...anandale awa ndi asatana amenewo akuchedwetsani Inetu pena ndimazifunsa nati..kodi anayambitsa ndale ndi ndani? Chifukwa dziko linalolera kuti anthu andalewa ndi amene aziyendetsa dzikoli?
DK campaigned inside and outside. Kambala is very matured persona koma Kaya strategy yake inali yotani. Only two interviews with main media houses
Keep doing the great work never tired
Here in Chitipa enafe tiribe nthawi yokaima pa nzere wovota... amene muli ndi nthw imeneyo kalembeseni. Koma sizikutanthauza kuti anthu Andale azasintha myomo yanu kulibe,, you are the one responsible for your own future ...anandale awa ndi asatana amenewo akuchedwetsani
Inetu pena ndimazifunsa nati..kodi anayambitsa ndale ndi ndani? Chifukwa dziko linalolera kuti anthu andalewa ndi amene aziyendetsa dzikoli?
Exactly ndipo Simukunama. Andalewa ndi anthu oipa they just use us
Welcome Brian banda.lovely day
Wow anyamatainu musadzafe
Usually misonkhano imakhalako weekends,pipo go there to refresh themselves, not necessarily to listen to the liars
Sure amai agwira chipani tiyene mai Kaliati Mr Mtumbuka ndi azao aja achigwira chipani tiyene tiwathokoze ndipo alimbikitseni amenewa athandizani apulumutsa chipani mai iwa
Osamapanga zoom timadziwa kuti munatenga pena
NPK 😂 Koma yeah ndevu zamwayi ,,,,, and your right guys anthu omwe analuza aja amaoneka odabwa ka smile kotulukira komanso ka jealousy
We are working on the ground
Delegate adachenjeradi.
Atha kukupatsa 21🤣🤣
Malawi 😂
Bodza agalu inu