This song remains one of the best campaign songs ever! I am not affiliated to any political party koma every time I hear this song I can't help but dance 🎉
A malawi tisapusitsike Dan Lu wayimba bwino koma zitukuko zose zomwezikuwoneka munyimbo anapanga ndi malemu bingu zimuwake uwutse mumtende chitukuko cha APM Chawonekapo ndi kutsengulila mwala wamaziko basi ambili mutha kundiyikila umboni komaso angoyiwala kuwonetsa majenileta chifukwa ndichitukuko cha Dpp basi a malawi tiyeni tilembetse mukalembela wazisakho 2019 kukasakha mwazelu.
Who is with me to make sure this song is massive.
am here
Me
@@jimmykachikuwa6701 Ineeeee
Ndpo Ina ija or umwe mowa sikumveka bwino 😂😂
Iwe umati 2024 boma 🥳🥳🥳🥳🥳 zangovuta kut waimba ya mcp km yokoma ndiyathu🥳🥳🥳🥳🥳🥳🥳
Ndangat tazaso kuzafila hit song yi after mbwelera
Iyi anapha not manyaka aja
Kodi amene tili kuno chifukwa Cha manyaka wainba Aja tikuphikira kuti❤
ku bingu stadium 😂😂😂😂
😂😂 am here after yaleroi aaaaa wapala
Up to now lozani zanu remains one of the best campaign songs❤ who agree?
Of course it's a masterpiece koma angwazi senderani is greatest
🎉
🎉
Sine wa DPP koma nyimbo iyi anaswa
Ndipo iyiyi ifika wani million kg
Who came here after the Chakwera song😂
Ine 🤣
Tilipo gulu
Ineyo
Ine
Ine pano😂😂😂😂
Those of us who are here because of the chakwera song we have a meeting kuseliku..😂😂😂Iyiyi koma anapha
😂😂😂
❤❤❤
Koma ndaseka😂😂😂
😂😂😂😂😂
Ndipo kwabasi 😂
Nyimbo ndiyomweyii iyi❤🎉 mabiggy sakhala awiri
This song remains one of the best campaign songs ever! I am not affiliated to any political party koma every time I hear this song I can't help but dance 🎉
Ur right bra
Kungoti dpp have good songs for campaign 🔥🔥🔥
Sound well composed
Straight man
Even dress yake aaa amwene awa amatha
Ndimazaonelaso iyi after laz's chakwe song 🎵 aaaah ijayi wapala
Ndukuuzani palibe chomwe wachita😢😊
Ai bola yomweyi ndiithu ina ijayo sikuveka bwino kkkk
Who is here after mbwelera waimba kwa chakwerazi 😂😂
😂😂😂Ine pano
Afunika 1 million views lero galu uyu
Ine pano
That chakwera song is ahit 🎉
@@ChifundoSagwirikahahaha siasisi angaso awa😂
Ndi angat amene takwiya nazo zomwe apanga nkuluyi 🥹
Iyiyi nde imandiwaza 🔥🔥🔥 osati iyoyo mwaimba ndi abusa 😅😅😅
Nyimbo ndiyomweyi😂👍🏼 zinazi ai😂😂
Coming back after loosing our only hope skc😢 adad tabweraso ife Ana anu
Iyiyi nde hit osati zachakwela zija
Nyimbo zabhoooo unaimba kale ukoko nfikuntchito we know ndipo vote yako ukuzavotera APM i know you dyomba iwe ndi dolo
Here iam to compare kkk aaah nyimbo ndiyomwei
Iyi nde nyimbo osati chakwera wanu uja
Basitu come here to refresh my Day...🤣🤣 Koma DPP naikonda ine eh eh
Nyimbo ndiyomweyi,zinazi ndimanyaka.
Ife tili kuno
Nyimbo ndiyomweyi sitikusitha 🔥🔥🔥🔥🤸🤸
This song is machine osati zomwe waimba ku NGO'na komwe akuka saka ndalama ko
Nah iyiyi ndiye imandiwaza ,koma Dan mwapanga zau savage kwambili
Nyimbo iyi sipazapezekanso nyimbo izapose iyi,munthu anaimba uyu .Amene angazaimbe kuposa iyi aaaa koma ndakayika.
Who is here today with me 😂😂😂😂😂
Ndili pano kuzasiyanisa 😅😅😅
Me😂
Me came straight ndisiyanitse bhobo 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Ine pano😂
ine pano
Iyiyi nde hit osati mwaimba kwachakwera zija kkkkkk
Lazani zanu yomwei ilibhooooo❤ team ma blues 💙 lets gather here blues woyeeeeeee 💙 🙌
Kkkk koma yeah DJ uzaponye imeneyo ku nsonkhano wa ngona ndizakunyadira heavy
Danlu ulibe nzeru ukuwona ngati tikuvotera wawupoda walemba m,madzi. UTM patsogolo zinazi ndi zopanda pake , Iwe danlu ngat ufuna kuti uwine bwera ku UTM .
Nyimbo za campaign ku Malawi kuno ndi ziwiri Yellow ya Lucius ndi Lozani Zanu basi🔥🔥🔥
Nyimbo iyiyi munaika boss osati manyaka mwawaimbira Mr C aja
ndili pano kufansnisa ndiya chakwera koma iyiyiii ndi moto kuja nde aphalaa nd2
Ndalama ija osazaiphwekesa ndaonera Dan lu
Nyimbooo iyiiiii ndichi vibeee🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
I love this song from Tanzania 🇹🇿 🇹🇿 big. Up Dan lu
Politics aside iyiyi unamenya aise ndipo sikufanana ndi ya achakwerayi.....i came here to confirm 🔥🔥🔥🔥
Kunena chilungamo,nyimbo iyi inayimbidwa bwino
Dpp ndi system osadzaiphweketsa🔥
Ambiri tapanga rewatch kufuna kusiyanisa akulu iyiyi inakungidwa
Nyimbo iyi nde mudapha bwana
Iyiyi nkhasako.. Si zinazo
Dan lu, apa anapha sound guys,,,, yakumenya kugwetsa ija singayambepo
Nyimbo ndiyemweyoi🔥
Iyiyi nde Nyimbo kaaaaa💙💙💙💙✅
Nyimbo koma iyii🔥🔥🔥
A malawi tisapusitsike Dan Lu wayimba bwino koma zitukuko zose zomwezikuwoneka munyimbo anapanga ndi malemu bingu zimuwake uwutse mumtende chitukuko cha APM Chawonekapo ndi kutsengulila mwala wamaziko basi ambili mutha kundiyikila umboni komaso angoyiwala kuwonetsa majenileta chifukwa ndichitukuko cha Dpp basi a malawi tiyeni tilembetse mukalembela wazisakho 2019 kukasakha mwazelu.
Kkkkkkkk ndaonaso kuti zitukuko akuonetsazi zayeni
Nkhani ndiyokut inapanga DPP
Akuti DPP
Akuti isabwere Dpp
Nyimbo ndi Yomweyi komaa......ichichi ndi chi Vibe
This is massive for this campaign hopefully it has to be on repeat!!!
Eeee we are here to take wat belongs to us😢🎉🎉🎉🎉alozedi zawo😢🎉🎉🎉
Ndipo inu
Galimoto ikaphwera pamsewu umatsika ndikukwera yokhuta matayara.
Ukamati maliro akatuluka sabwerera , sikuziwa kut maliro amawawa,maliro omwewo abwerela Dpp 2025 boma
Ineyo ndiokonda Congress koma nimboyi dan luu anakhazika
Ine panoo, kkk si ine wa dpp koma nyimbo iyi anapha
Singasapotere nyimbo ya chikangawa
The guy on 3:04 is a whole vibe! 👏🏽👏🏽😃😃😅😅❤️❤️ Great Song Dan Lu! 👏🏽👏🏽💯💯💯
Nyimbo koma izi osati phala lija
This is the best song,, you sang Dan osati zinazi iyayi
Aliyese wamvela chakwera song aze kuno kuli mkumano
Ine ndufuna ndisiyanitse sikuti ndili ndi mbali kwenikweni.. Kufikanso koyamba kunoko
Nyimbo kma iyi🎉
Dan Lu muli luso koma na lozanu zanu aaaaaaa sound anapha iyi
Mm inde ndalama zilipa minga koma muziyang'anira minga yake mutha kuferapo zabwere ku MUST udzawona kt apadi ndiye paminga. Takutuluka
Nyimbo koma iyi🎉🎉
Kuyimba nayimbakare osatizachakwera arozezawotiwone kumene
Wayamba misala ameneyo
Patatha zaka osanvera Lozani zanu koma naiyiyi unapha
Nyimbo yomwe waimbila MCP ija ndikuchita manyazi ndineyo😢😊
Dan Lu ndi wa UDF......But ku supporter zomwe waziona yekha palibe chifukwa chomu beefer ....he is a citizen too
am listening to this song. ija ya MCP wandithera nayo bundle😪
😂😂😂😂😂pepa
Sure tiyenazo uzayimbaso kachikena napayiyokha usazafe uzangosowa
Ndangofuna ndisiyanise😅😅😅
Me coming here uku ndikuonela exclusive interview pa zodiak
Despite mwakut mwakut km nyimbo yi anapha🙌
Lozani zanu remains the best song ever osat mbwelera atulutsayi
Despite difference in political idealogy hit anaika Dan lu
Yachakwera angosonyeza sitima 😢😢😢😢
We here again. Apapa Dan ku unaswa sound
Aaa zachakwela zija olo kukomasoiiiii aaaàaaa ndipo apapa adatsindika ntima kut akuimbiladi mtsogoleri wadzko komaso nzoonad, koma yachakwelai zungoonekelatu kut mkugulidwabasiii koma mfundo mulibee, siikugundaso ntimaiiíii aaaaaa
Realy this musician is a fool for leaving a revolutionery
adan uyu ndeye aaaa. kuchenjela ayi chenjelani 2b quaint is very enough 4 everything.
Hit koma iyi or voice ya adad ikuchita ku veka ngat ali pa condenser osati zinazi 🗣️🗣️🗣️
Hule wa zipani uyu👁️
Nyimbo kma iyii osati manyi aja
Nyimbo ndiyomweyi
Ngat Simon Peter anakwanisa kukana yesu pomwe thawi zonse ankakhalila likoz nge mwati Dan Lu angalimbepo 😅😅😅😅😅😅😅
Iyi ndi massive
Ndabwera kuno, ndapita ku Tulani pansi nditachoka ku chakwera song, hhhmm Dan watitangwanidwitsa mweee! Continue confusing us
Indeed remains the best song, mot deliberately atangoitenga nkuvayanayo panseupo with best speakers mgalimotoo it can shock the rulling side😂😂😂
Osafooka Dan lu we need u now campaign
Iyiyi adakwapula osati izi wapanga panozi😢😢😢
Ndali Ali kuno after the chikangawa song😂
This is big hit DPP More fire
Nyimbo iyi hit sizaguga🎉🎉
I am here ❤
Was massive
Am here after chakwela song, kusiyanitsa, iyi ndi hit mbambande😅
Big up to Dan.music is about hustle.make money bra n grow big in music.DPP ndi boma