ineyo siine wa DPP. ndayesetsa kumukwiyila Dan lu kuti akuimbila za ndale, koma nyimbo iyiyi ndi maifila, beat ili bhoo.. and u r so talented Dan Lu. Koma suti ndingavotele DPP. izi zanyimbo basi.
Kunena chilungamo. Peter uja zinthu nde ankaonetsadi. Boma lililonse anayesetsa kupanga zofunika. Za kuba ndi izo koma let's see mmene Munthuyo adagwirira ntchito. Sizikufanana ndi Chakwera tu nkomwe. Tikafika kumbali ya nyimbo yi. Ai ndithu bwana Dan Lu katundu mudakwapula. Well talented
Zipani mbweee!!!......everyone tryna take down and pull down the other kuti akhalepo iyeyo dziko litukuka bwanji??.....mmalo mopangana support wina akakhala pampando koma mwati ayi tiipitse ameneyu asazawineso timuonele kuti zitha bwanji.. shaaaa!!!....Malawi wanga mayooo hehe
bola inu mumatha kuimba,,,apapa kuteleko akupatsani ndalama (gawo la ma tax athuwa)malawi mukuimva kukomer.. ife nde tatopa ndikumangonamizidwa ndi andale!!! mtendele si msima yokha!!
Ayi zilibwino ena amene akubwelawo ndiwozaba koma pita eyemweyo basi Dan uli bcoz pali anthu ena odana ndi PETA koti ntchito yawo yodula ziwalo inayima pano
Chomwe timadziwa a Malawi ndi kupanga complain basi!!!!......if you are not part of the solution you are part of the problem....osamapaka boma chilichonse. Everyone has potential to make a change......we citizens don't love our country that's y we end up cheering maiko a anzathu nkumanyoza lathu lonwe.....APM kaya MCP kaya SKC....palibe wabwino and wabwino sadzakhalapo mpaka tizaphunzile kukonda dziko lathu....Amen mpingo.....
ineyo siine wa DPP. ndayesetsa kumukwiyila Dan lu kuti akuimbila za ndale, koma nyimbo iyiyi ndi maifila, beat ili bhoo.. and u r so talented Dan Lu. Koma suti ndingavotele DPP. izi zanyimbo basi.
Nyimbo Ili pa repeat iyi🙌Dan lu killed it🙌
Kunena chilungamo. Peter uja zinthu nde ankaonetsadi. Boma lililonse anayesetsa kupanga zofunika. Za kuba ndi izo koma let's see mmene Munthuyo adagwirira ntchito. Sizikufanana ndi Chakwera tu nkomwe.
Tikafika kumbali ya nyimbo yi. Ai ndithu bwana Dan Lu katundu mudakwapula. Well talented
Ndipo live koma manyaka awawa nde mbola
Vuto ndiloti anthu sayamika
Uyu zimukopa mndalama koma
Here is 2024🌈♥️♥️waiting fo 2025
Ali pano ndani after kuonena nyimbo yosakoma ya chakwela chikangawa
Ine
😂😂😂ine
Dun luu ndichitsilu basi 😂😂
Ndipo live
😂😂😂
Inde iweeeeeeee Nyimbo ndi izizi💙💙💙✅
Hate him or love him, guy is talented and give him respect for that...love the composition despite everything 😘😘
Fact and true
Nyimbo zbho Nd izi❤❤❤❤❤❤
Iziii nde nyimbo 🔥🔥🔥🔥🤸
Tiziyikayomweyi PA msonkhano WA APM. WAP APANGAMAN, YAZITUUY GARUYUM, mbarewachikangawa
Keep it up my brother chakwera walephela kusamala anthu
Despite his mind of joining unnecessary party of MCP but he makes good compose hits
apa ndiye number one osathi chikangawa
@Dan_lu apa nyimbo iyi udadekhatu kwambir bwanji Koma???
Guys no matter what this guy is so talented ❤
Mtsogolo ndani??? Peter yekha 💙💙💙✅💪
ife amalawi tili ndivuto losowa chikondi mmalo moti tikhale athu awumodzi vuto mkunyozana palibe yemwe adzakonzeso dziko lathu ngati tilibe chikondi tikuyenera kuyamikila pazithu zina zomwe ena akuchita ndikuwalimbikitsa kuti dziko lipite pasogolo . Dan Lu kwake mkuyamika pazithu zomwe ena apangapo kutukula dziko adzabweraso ena adzayamikila muthu paiye yekha sangakwanise kuthandiza onse mkusangalala tiyeni tikhale athu okondana kuti dziko lathu likhale chitsanzo kwa ena
Business yako imeneyo
Ndipo tinagwilizana bwinobwino koma aaaaa
Nyimbo iyi❤ 2025-2030🎉🎉🎉🎉🎉APM BOMA🎉
Eeeh kunena chilungamo Dan lu umatha, komañso peter amatha,,, but time tells,,, zonsezo kulibe lero ulemu wapadziko uli ndi limit
Ndiposo zonsezi kusowa umuthu wa muthu Ali tilibe chilungamo kmaso stitha kumanga umodzi
Tsogoleli ndani ,, Peter yekha ❤❤❤
Our guy is talented 100%
Adadiiiiii my vote🎉
Dolo katatu my artist since i was born zandale apo mwenewa amatha
Chipani ndi chomwechi DPP 2025 boma💥💥💥
Tabweraso ife adad ana anu tilandireni ana osochela 2025 we're waiting for you
Nde mwati kumenya kugwetsa 🤣🤣apa mukuti APM akhale wina ayi mukuziyendetsa bwanji kodi zikukhala bwa 👀😂
Watching from Durban, apitilize ,peter, Dan Lu 🔥
Imatikumbusa patali❤🥱❤
Zilibho more fire dan lu more fire dpp APM akulamulanso mpaka 2024 wooooo
Koma nyimbo umakutumula mophyesa mtima ayise..
Dan Lu.....still a legend
Zipani mbweee!!!......everyone tryna take down and pull down the other kuti akhalepo iyeyo dziko litukuka bwanji??.....mmalo mopangana support wina akakhala pampando koma mwati ayi tiipitse ameneyu asazawineso timuonele kuti zitha bwanji.. shaaaa!!!....Malawi wanga mayooo hehe
boma ndi ili likubwera 2025 li dpp oyeeeee
Tiyeni tifikitse 1 million views
Big up Dan DPP Niboma ufune usafune Peter yomweyo wina alira .
🤣🤣koma ndalama guys..APM🔥
Dan lu bwererani
Ku DPP kubwerera sikupusa koma ndi chiyambi cha nzeru
Ine siwandale koma nyimbo iyi anandiyimbila bwino maka paja poti undindo amapeleka ndi chauta pamandimvekela gospel gospel eeeee..
Ndipo. Nyimbo zomwe zakalezi. Tiziziyika mmisonkhano avulalanazo a MCP okha
Nyimboyi inaimbidwa mwa luso koma the message Aaaa zanu izzo
Ineyo nyimbo iyiyi ase sinxasiya kunvera ngakhale ndili wa MCP, imandiwaxa hvy, ndipo unafatsilila, nde padxima speaker dxogunda bwino iwee
😂😂😂
Hayibooo!!! no comment God will choose by himself for nobody is perfect
despite it's a political song but I have much feeling with this song well composed, good melodies, so danceable.
Nyatwa I wish DPP can take over the government again 🔥🔥🔥
At least sanafufute. Ife tizibwerabe kudzaonera nyimbo ndiyomweyi🎉🎉
bola inu mumatha kuimba,,,apapa kuteleko akupatsani ndalama (gawo la ma tax athuwa)malawi mukuimva kukomer.. ife nde tatopa ndikumangonamizidwa ndi andale!!! mtendele si msima yokha!!
Awapatsako za cash gate
Zako zimenezo
Apa akudyanso zina ndithu,, kudyera luso
Mwalowaso bwana💪💪💪
Zinazo ndizake koma masound onse a DPP Dan lu Anamenyaa osati za ku NGO'na zija
Kuja akukakamiza ndie fundo. Zikusowa
Dan Lu apandewanamatu man
This song is so good really love it ❤
We remember that time things are going well where are you peter mtalika😢😢😢
Wasachisankho lakwika zowona aka joina MCP, ma hit nde amatimenyera
Kun ndimemeyo osat chikangawa 😂😂😂😂😂😂have
Km ndale kuponya apo a dan Lu Dpp imamukhala and nyimbo zabwno zokhazokha osat zokakamiza zija ai kkkk 😂😂😂😂
Boma ilo❤❤❤❤🥳🥳
Ayise ugwanayo mmadzi 2019 , APM palibe chochitika usogoleri sitikuuonamo ,
Mbola
Iyiyi ndye munapha sound koma na ya chakwela chkangawayi mmmmm mwapepela
Winanso ayi dpp woyeee😗
My vote APM 🔥🔥🔥💯💯
abwerere kwapita a hoke kuchikangawako Kung, ona
Winaso ayi zoona Dan Lu APM yemweyo 2019 kuti moyo buuuuu
follow me i will follow u
Ayi zilibwino ena amene akubwelawo ndiwozaba koma pita eyemweyo basi Dan uli bcoz pali anthu ena odana ndi PETA koti ntchito yawo yodula ziwalo inayima pano
That’s you Dan Lufan i like your mingoli keep it up bru listening 👂 you on TH-cam all the way South Africa 🇿🇦
Za zii,, ife pambuo pa SKC 2019 BOMAAAAAAA
Nde iti imeneyi
Congratulations
DPP my vote 🔵 🔵 💙💙💙
Nyimbo Kawawa osati misala wayambayo Dan ..Kodi akupepetula chikangawa?
Making money bro he is a musician not a politician
Nyimbo za DPP umayimba zokoma ase. koma ya MCP ija wapala
Kuyaruka Dan kusowa ma plan sopano apitara ake ati,ndalama zathu zomwezi misonkho yamthumba mwanthu zimenezo uchisiru uzakupha
Dan lu if u keeping hitting studio lyk diz loool.u wll lose more fans.any 1 agree
These are our taxes indeed man! So what is this guy saying?? Crazy man. Singing sin! ati bwana!
Mungoona kuti mupanga bwanji truth be told Muntharika ngwachitukuko zina kambu
Musova
Muyisova pa nyasa apo Dan lu lekawaka Kuyimbila Agogo awo Anthu akuchoselapo waka mano
U are number1 malawi♥♥
Akunama, ukubwera boh Dan my Brother. 😘
Winanso ayi Ife tufuna APM basi.....chitukuko chipitirire.Bravo Dan lu
Dpp morefire
Wasochera iwe bwelera
Dan lu ndi dolo❤
Honestly DPP developments were real😂
Tikufuna Peter pano😂😂😂
Nice song 🔥🔥
Izizi nde umaphatu not mbwelera mwapanga zija😅😅😅
Ndipo mbwelera😂 or mwana akuseka
Chirungam si zachakwela zakozo ampwala
chikangawa km kuyenda Enda bas
Ineeee P yekha basi
Am here from fb 😅😅😅
APM kasupe wachitukuko 2019 akupitiridza kutukula Malawi.
Chomwe timadziwa a Malawi ndi kupanga complain basi!!!!......if you are not part of the solution you are part of the problem....osamapaka boma chilichonse. Everyone has potential to make a change......we citizens don't love our country that's y we end up cheering maiko a anzathu nkumanyoza lathu lonwe.....APM kaya MCP kaya SKC....palibe wabwino and wabwino sadzakhalapo mpaka tizaphunzile kukonda dziko lathu....Amen mpingo.....
Louder for those at the back .Mawu ndithu 😍
Osati manyaka watulutsa awaa😂
APM woyeeeeee thax Dan lu cop motomoto
Udali kale Daniel Lufani iwe.....pano ndiye aaaaa ukubowa
Utm bomaaaaaa manyadzi akugwila
mulipobe? ndi tonse yanuyi?
Umaimba bwino mmakukonda though chipanichi smmachikonda am still ur fan hommie
Nyimbo koma dzimenedzi
Moti nyimbo zabwinozi udangoyimba zabule adad pano akuwedza somba kumangochi ngati kumalototu😂😂😂😂😂😂😂😃
Koma nthaw nkachitsiru akudzudzikiranji Dan Lu ku mcp
Apm❤❤❤❤❤❤❤❤🎉🎉🎉🎉🎉🎉
Big up Dan lu nakubaĺi sana sana natamani kufanya colabo na wewe
Came here after Peter kuluza kkkk. Koma zoopsa
Zovala zomwe unasokesa za DPP zo bwelesani mbali ya kuno Inu muzikavala za kuchikangawa😅😅😅😅😅
Ndiwe chi kape...
Dan lu uimbe ina ya dpp ukuziwa kale caka camawa tikulowa ipase moto
APM ndi bwana di... Ndipo winanso ayi ife Dpp
This guy I talented sure
Blue for ntendere kawa Bravo
Personally lov&love this song