This song made me shed tears 😭😭😭it reminded me of someone 💔I wish u wello dear wherever u r💔 Whenever someone likes this comment I will be coming to watch again and again
I love your songs my brother umatimvetsa kukoma osati zandale ndipo usasadzalole zachima Dan luh udzawononga tsogolo, umatiyika pa map nyimbo zako tikamawonela ndi anzathu osamva chilankhulo chakwathu amangovina nawo kamba ka ukhondo osati zojambulila pa phulusa
To my own side he is the best so far from Malawi and I love this gentleman songs 🎉 I patiently waited for the full song my cousins from Malawi like my comment
Ena nde akumati Video silibwino aaa Guyz this is the best video with this type of song. Mukachurkaso zochita mu video ngati iyi zimabisa uthenga wamunyimbo. Kudos Timon💯
A DAY IS COMING. TAIMON TIPA WILL BECOME ONE OF MALAWI'S GREATEST MUSICIAINS
Amen
I'm praying for this🥺
Ndipo live🥳🥳🥳🥳
Ndipo si kale😊
Biggies-wa ndi handsome plus alinkutchena🔥🙌
Anyways nice track keep it up✊🏻
Nyimbo zako zimandipasa chimwemwe pamoyo wanga,may God bless u dear🎉
If you believe that this is pure talent from God like my comment
My artist
100%
100%
Yes bro
Proud cheba here love this song
This song.......eeeh🙌 amene tikudutsa nyengo ya nyimboy like my comment❤
" Ndiambiri okudalira ndipo akuchulukira ukazisiya adandaula" mawu awawa andilimbikitsa. Nice one iyiyi nyimbo mwakunga Bro🔥🔥🔥🔥💣
I love this song! Keep it up Taimon.
Kwambr inesot ndipomwe pandilimbikisa kwambr
Aisee ndiwe Shasha u got talent anthu akuchedwa kuzindikira chimenechi this is great man
I like this song❤
Nyimbo imeneyi imandilimbikitsa muzambiri, big up 💪
Zambia is proud of you bro 🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇲🇼🇲🇼🇲🇼❤❤ I will be liking my comment alone kaili no one will ever like it ❤😂
This song made me shed tears 😭😭😭it reminded me of someone 💔I wish u wello dear wherever u r💔
Whenever someone likes this comment I will be coming to watch again and again
I wish i could give million likes but am advertising it
Song of the moment big up
Ndipaseni ma like ndipo nthawi yonse ndikabwera ndivera nyimboyi kutengera momwe achulukira ma like❤❤❤❤❤😂🎉
osadanda bro
My favourite ....
Amen
I like this song please ago head❤❤❤
God bless u bro good talent
Nyimbo ili nd uthenga iyi Ndipo ngat ukufotokoza za ine 🙏🙏🙏 keep it up fadah
Ndipo mbali yakuno ngt wandiona ine
@@ChifuniroMisiyasimaka apopo poti ukazisiya anthu Ena adandaula... Ndalimbikisika kwambiri 🔥🔥🙏🙏
Nyimbo iyiyo olo kumaimvera daily singakutopese rather kukulimbikisa
Ili ndi luso losakakamiza lija.
❤️ big up young man.
Keep going Twin brother from another Land 🎶🎶👏🏽
Tiyeeeee iwe tiyeeeee🎉🎉🎉🎉🎉
I love your songs my brother umatimvetsa kukoma osati zandale ndipo usasadzalole zachima Dan luh udzawononga tsogolo, umatiyika pa map nyimbo zako tikamawonela ndi anzathu osamva chilankhulo chakwathu amangovina nawo kamba ka ukhondo osati zojambulila pa phulusa
Yes Nyimbo zanu Big zimandiwaza havy palibe nyimbo yako yomwe unapala Big up prz Malawi Mulandilen Mu2yo kuno Watifilisa kwambiri
Kuswa kugwetsa basi , nice song
Na nyimboyi mmmm repeat the whole day. Kuchita kumveka tseketseke
😂😂
This Man is completely talented. I love your music ❤❤.. sending love to you from your die hard fan from Zambia 🇿🇲 ku Chalo 🌏
Iwe ndi dolo kwambir
Congratulations 🎉❤
To my own side he is the best so far from Malawi and I love this gentleman songs 🎉 I patiently waited for the full song my cousins from Malawi like my comment
Keep fire burning 🔥
Powerful song brother
Big up taimon tipa umayimba nyimbo zabwino kwabasi
Your my favorite artist in Malawi your on high level dzina munapanga kale bro
Proud of your music big man I like it
Those who are coming from tiktok let's gather here and show some love❤❤❤❤❤🎉🎉
Mwatilimbikitsa brother, Big up
For example uli mu galimoto yako pamene paja 🔥🔥🔥ingamveke bwino
Ndipo chingakomeditu
😂😂😂 ine tikuivela mu mgalimoto ya mmaganizo zanga phee apa ndili pa chingeni
Nyimbo iyiyi eeee muli uthenga wachilimbikitso ❤❤❤❤❤❤
nyimbo zopatsa chilimbikitso ,🎉🎉
Ohh this is nicee❤❤❤
Iweyo ndi dolo kambirimbiri. Luso ilili ndi mdalitso wako adah
Almighty God, bless this lad for me. I have always enjoyed his music. Big up, day ndiyimozi nfanayi azafikapo pamene amafuna.
My favorite artist.chaka chake ndi chino.ishuta ndithu
Nc song bg boss your number one music yachilimbikiso kwambiri 🎉🎉🎉🎉
Viewing from Zambia 🇿🇲 it's my dedication from my family. But I promise this year I shud overcome my dreams
U a bad news dude 😊😊😊😊kip it up
Nyimbo iyi yawona nyengo zanga ndipo ndi ambiridi okhomererawo 🙏🥰
Mmmhhhh talented man God bless you always
Fadah uli luso kwambiri 🔥🔥🔥🔥
Mupatseni plot munthuyi, wafika aise
Apa ndapeza nyimbo ina ku playlist yanga. You're a blessing to Us ❤.
Mtima wako watopa thupi lako lafoka pena ngati ungozisiyaaaa 😢 ndiambili okudalila ndipo akuchulukila ukazisiya adandaula,,,,,,pamenepooo Ambuye titsogoleleni
Powerful massage 🙏
Aisee you we become a legend very touching song🔥🔥🔥
Zambians let's gather here 🇿🇲🇿🇲🇿🇲 to support this man 🙏
❤❤ We're here 🇿🇲🇿🇲🤦👍💕🇲🇼 Zambia Malawi
Here
We ae here❤
Nyamata woziwa kuyimba uyu🎉🎉🎉🎉🎉🎉 ulemu wanu
Matipatsa chilimbikitso God bless you all time
❤❤❤❤❤Ndipo zoona
I like this guy ❤
Umayimba bho kwambiri 🔥🔥
We got a talented one here in our country ❤❤❤❤❤
WOW congratulations all guys tiuzeni zokhuza oyimba a gospel
Big up brother
Iweyoo aseee nde pakufunikaa kukuomberaa bs cz nde eshiii ndili ndi nsanjee utipwetekaa ❤❤❤❤❤❤ God continue blessing u🎉🎉🎉🎉🎉
Komatu ukukamba zoona kungot nyimbo zako zose ndi zamathandauzo , koma iyi ngat ukundinena ine ayi zikomo wandimasuladi choona siine ndekhad
great message,yandigwira mtima,big up Taimon
Wabwera taimon
This song 🎵 ❤❤❤ achuluka okudelera Ena wokukhomelera kma tiyeee🎉🎉
Koma uyuyu nyimbozakezose ndi minyanga yokhayokha mmmm umathaaise
Awawa ndi akatakwe pamaimbidwe ndipo nyimbo zawo ndizopatsa chilimbikitso.kudos Mr Meleka n keep it up big man ❤❤❤❤❤❤❤
Iyiyi nde mwapha akulu big up fada
Ndipo live .....okudalila ndi ambiri koma kungoti uzisiye mmmm adandaula nyimbo iyi yandipatsa chilimbikitso ndayikonda❤❤❤
Dolo🎉❤🎉
Boss mwejo abwanaa
😢😢😢😢 nyimbo iyi waimbira ine pena ndikuti bola ndingozisiya😢😢😢😢😢😢 udindo wakula ndakanika
Silidutsa tsiku osaonera nyimbo iyi🔥🔥🔥 keep it up 💃💃
Ena nde akumati Video silibwino aaa Guyz this is the best video with this type of song. Mukachurkaso zochita mu video ngati iyi zimabisa uthenga wamunyimbo. Kudos Timon💯
Anthu ena anabadwa Ali afiti kale
Nyimbo iyi imandpasa chilimbikiso mmoyo wanga.... God bless you bro...osalora satana akulamure...
One of my favorite song
Taimon you are the best musician.. Ndiwe doro aise
If you really like this song give me like
Keep up the good work nyimbo dzanu muli ma phunziro aphavu mulungu apitilidze kukudalitsan ndi mzeru
This is fact nyimbo iziveka ndi2 like this one
Ndikuyamikire ulimoyo bro...... UMATHA AND KEEP IT UP 🔥🔥🔥
Osadzilembeka malire ,uyuuu nyimboyi waimbila ma fans ake lunso koma ili aise pitiliza
Am speechless bro mwaganiza kwmbr 💪💪🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼
Siine ndekha ndikuonera nyimboyi, dnipo siine ndekha ndaipang Like.
Aàaa nyimbo iyi simagona nayo tulo kodi ukungoona nyengo zanga??? Taimon nyimbo iyi imandilimbikisa ❤
I would like to meet this guy, you going places my guy
Muli uthenga aise uli ndi luso heavy
Ma views mmene akuphaphalikila ngat mvula ya matalalatu❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️
Uyuyu nthawi yake yakwana basi
@@chimwemweligomeka9188 ndipo chikaloza chimakhala chaloza
Ndipo nde yakwanadi eeeeee@@chimwemweligomeka9188
Iyi ndi one of the songs we need, pure music kutilimbikitsa brother keep it up
Umatha aise iwe ndidolo kwambir nyimbo ikuchita kuyakhula mumtima kupelekaso chilimbikitso
This is nice Hit Bigman.. work hard. The message is Just too great
You are talented
That's great 👌Well done and may the good Lord enrage your territory👏👏
Landed his music today. He's full of life and hope. Thank you. From Zambia
I like you aisee ,,,,, continue nyimbo zako zimandiphunzitsa ndisaname
Amen nyimbo yoti ukamamvera kumangomwetulira wekha eeshii❤
🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🎵🎵🎵🎵eshiii ayi zikomo
Kunena mwachirungamo ndima konda adh awa amamenya ma hit abwino hvy keep up good job bro 🙏
Woow this song is nice
Receive your flowers 💐💐💐
Can't wait for the day you will blow pipo will see your talent continue hoping in Jehovah❤
Your songs always encouraged me that one day God wil bless my hustle 🙏
Dolo katatu iweyo😘
Keep it 💯 man. This is lit
Luso ilili ndi mdalitso ochoka kwa yehova ❤
🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥nyimbo iyi indithera ndalama🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉❤❤❤❤❤❤
Kma yaa Taimon iweo landila ulemu komwe uliko #🔥🔥🔥