ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
Eeeeee uko sikufuna amatama 😆😆🙌🏿🤗💔🙊🙊ohooo ...Great koma ... beliefs & culture its what shapes the behaviour of human being 🙏🏿🙏🏿
Joab ndi tolankhani oziwa kufunsa mafunso ngati Brian Banda, timakunyadirani Joab ndipo timakukondani taziwa nawo
I went to this island before.....nice place to be especially at night mmm
Queen of the coast ameneyo, from the marine kingdom, it's only the Lord Jesus Christ who is a saviour!!
🙌🙌🙌🙌
Joan za mowa 😂 akut palibe ufulu 😂😂 palibe zaka 5... Akut ai sindimwa ndkungolingalira zamowazo
Mizimu imeneyi muipemphe itichotsere zowawa zili kumalawizi
One ku mvako za malo amenewa
Mmmmm komande muzikokomezatu
Yes eee abwana Mulungu akudaliseni apilingizo
Beautiful scenery ❤️
😂😂😂😂😂😂 ati sindimwa kkkkk😊
I like this ❤❤❤
Zobisika zayamba kuululika ino ndinthawi yoti mulungu akutulusa zomwe Ife sitinali kuziona
OK mowa ayi nanga chamba zimakhalabwanji
Nchifukwa chake amati marine spirit
Good place for tourism !
Komatu 😂😂😂ati" museweretsa chakudyatu" mumakwana inuyo 😊
❤
❤❤❤
Those are geographical spirits don't worship nor embrace them.
Jaobu umakwana mpaka kuletsana kachasu aaaaa wachibwana ameneyu😊😊😊
Kuteta kuli ndi tanthauzo lake mu chitumbuka.... Ndiloleni ndinene kuti awanso akuteta
Akutanthauza ku theterela pachitumbukapo mesa 😂
Ada awa 😂
❤❤❤ nice
zoona mizimu yilikoro eti
Team loving things kuona agalu amichombo🤣🤣🤣🤣
Wawooo
Incredible😮😮😮
Need full VD
May home village
Ndava mawu mkati ma program akuti ayawo ndi a christ Ndeno fuso langa ndilakuti chiyawo ndi mpingo wanji?
Ati ndingolingalila kkkkkkkk @mowa
I am proud of our customs and traditions
Good work
Amaletsa azimayi chifukwa choti azi bambo ambiri amakhala maliseche chilungamo chake ndi chimenecho
Oky
Ngati malamulo ake ndiolesana mowawo palibe ufulu
izi ndizoona ndili ndi umbon
Nkhani ya Lazalo? Osati Yobu? Lazalo ndioukitsidwa kwakufatu
Ok
Palibe chi khrist ngati mupembedza satana
Mmmmh lazaro wazilonda😂😂 not yobu
😂😂😂 Lazalo yemweyo 😅
Lazaro waumphawi uja naye anali ndi zilondatu
Eeee malo oipa kwambiri
Life is Lesson
😂😂😂 munakanatu apa
Km ajoab mandiwaza kwambili ulemu wano bwana 🎉😅😅
What happened to cada when she visited Malawi especially mbenje Ireland 😂😂
Mesa boma ndi amabungwe amati pasakhale kusiyana pakati pa amuna ndi akazi apa azimayi muwathandiza bwanji
😅😅😅😅
Wokoho 🙌🏻🙌🏻😂😂alcohol uja
Kkk
Mizimu
Pa mowa pokhapo aaa
guyx kd ikamakan kupang donwlod mumatan
Hahahaha mpakana ajoabu zamowazi zakukhudzani kkkk
Koma mwati zonsezi konkuno ku Malawi 😂
Or utapitKo muufit sungafikedi ndimati ndiyesere
Osayiwala kutipatsa lift tidzikajambula 😂
😮😮😮
❤❤❤❤ 6:53
Ai taziwa nawo Malawi muno tilinso ndimalo amizimu kani
Alipotu ambilitu
Umakwana Joab kkkk
Amafuna kundiph
Koma guys uku kulizithu
Munabwera
Mnamva kuti kumakhala njoka zambiri that's why azimai sapitako
Koma ndee zoopsa
Kkkkk...mafotokozedwe awa siamasewera
Eeee koma ndiye eeeee.
Komayaa mumakwana a joe
😮😮😮😮😂😂😂
Anthu mudusa nyengo zowawatu
Km cada adali nkaz kapena mwamuna
Anenatu kuti wamkazi lol
Ndipo anthu ena Adah 😅😅😅 mafunso omwe amafunsa@@myheartforkids2876
Achiyao makani ajatu mixu yao ndiimeneyo
Zaboza izi
Koma Joab kkkkkkk😂😂😂
Mwanionetsa fumu ya kwathu kuchikombe tinazizolowela ife izii zakwathu
If you are a Christian didn't embrace them those are geographical spirits (demons)
Singapiteko ine uku 😢
Zakele izi nanu aaaa
Yelekeza upiteko
Chiyao ndechipephezo chaji
Ndizoona sakunama
Serious?
Nzungu ndi wamakani naziwa sangalephere kufika. Samafuna zakumva amafuna kupanga prove
😮😮😮😮
Ine dzapita tumizan trans ndikafike muone
A chakhaza mwayera liti
Ecotourism on its Best
Eeeeeee eee kma joabu
Zakumbenje,Kumari,kwabwino,kaonekoni
Ufa wake oyera bwino osati za njala zija koma adha amanewa andiwaza
😂😂
Mukapeza manyi ku phiriku mumati munthu wanyera. Mukapeza chakudya mwati mizimu? Zachamba.
Ati tikusamala kut tikudzweni😅
Nde si kwabwino
Oqjo😅😂9😂
At ufa wabwino osati za njala zija😅
Ndi yobu osat lazalo😂
😂😂😂
😂😂😂 Ati sindimwa koma ndingolingalira kuti 😅😅😅
Heeeee
Kkkk km ziliko
what if anali or Ali ma aliens
Asena ndiomwe amati phenembe not alomwe
Hahah ya ufulu wamowa yavuta
Nkuluyu ngwambalume ndithu
Ndikowopsaso etii
😢😢😢😢😢😢😢😢
Eeeeee uko sikufuna amatama 😆😆🙌🏿🤗💔🙊🙊ohooo ...
Great koma ... beliefs & culture its what shapes the behaviour of human being 🙏🏿🙏🏿
Joab ndi tolankhani oziwa kufunsa mafunso ngati Brian Banda, timakunyadirani Joab ndipo timakukondani taziwa nawo
I went to this island before.....nice place to be especially at night mmm
Queen of the coast ameneyo, from the marine kingdom, it's only the Lord Jesus Christ who is a saviour!!
🙌🙌🙌🙌
Joan za mowa 😂 akut palibe ufulu 😂😂 palibe zaka 5... Akut ai sindimwa ndkungolingalira zamowazo
Mizimu imeneyi muipemphe itichotsere zowawa zili kumalawizi
One ku mvako za malo amenewa
Mmmmm komande muzikokomezatu
Yes eee abwana Mulungu akudaliseni apilingizo
Beautiful scenery ❤️
😂😂😂😂😂😂 ati sindimwa kkkkk😊
I like this ❤❤❤
Zobisika zayamba kuululika ino ndinthawi yoti mulungu akutulusa zomwe Ife sitinali kuziona
OK mowa ayi nanga chamba zimakhalabwanji
Nchifukwa chake amati marine spirit
Good place for tourism !
Komatu 😂😂😂ati" museweretsa chakudyatu" mumakwana inuyo 😊
❤
❤❤❤
Those are geographical spirits don't worship nor embrace them.
Jaobu umakwana mpaka kuletsana kachasu aaaaa wachibwana ameneyu😊😊😊
Kuteta kuli ndi tanthauzo lake mu chitumbuka.... Ndiloleni ndinene kuti awanso akuteta
Akutanthauza ku theterela pachitumbukapo mesa 😂
Ada awa 😂
❤❤❤ nice
zoona mizimu yilikoro eti
Team loving things kuona agalu amichombo🤣🤣🤣🤣
Wawooo
Incredible😮😮😮
Need full VD
May home village
Ndava mawu mkati ma program akuti ayawo ndi a christ
Ndeno fuso langa ndilakuti chiyawo ndi mpingo wanji?