ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
Ayi, apa wafiika Dan takukhulukila momwe tinamukhululukilanso petulo pomukana yesu koma ataziwa kulakwa kwake anakhululukilidwa. Takukhululukila alomwe ife (let's repeat this song 🎉🎉🎉 🎉)))) 🎉🎉🎉) 🎉🎉) 🎉
My speakers are still suffering with this banger 🤣 Who else is here still watching in 2024
😂😂😂 zikhale Ng'oma koma
It is a big team😂
Ine😂
Iwe umati 🔥🔥🔥
Me
Ndabwera cfkwa ca nyimbo ya. Chakwera
Kkkkk yomwe wapala ija😅😅😅
Eshhhh koma Dan Lu umathaa mistake yomwe wachitaa ndikujoinaa Mcp.Adad for ever ❤❤
Dan Lu ndimamukonda, koma from today I don't... Walowa zandale m'phwanga, pitiliza mwina udya nawo kwamiyezi iwiriyi. U same like Nkasa=Dyera basi
Nyimbo ndiyomweyi sitikusintha😅😅😅😅 who is here november 2024😂😂
Iziii nde nyimbo 🔥🔥🔥🔥🔥🤸
Pali mwabi oti kalulu adamva may oyamba,ngakhale atayimba zotani ,tinamva yoyambayo basi.
Izi ndi nyimbo zoguguda mtima ndipo anaimba ndi mtima wake onse osati izii zangokakamizatu
Chipanda chilima munali ndani ag'alu inu,,, pano chilima mwagwetsa,,,, muziona nyekhwe...
Tikuwona kuchedwa kuvota bwanji ❤❤❤❤❤❤❤❤ 2024 bomaaaaaaaa
Nyimbo iyiyi eeeeish inabandulidwa honestly speaking
Who else is here coz ....kumenya kugwesa song 🎉🎉
Still watching this song 2024
Tonse tabwera chifukwa Cha nyimbo ya chakwera tidzeee pano
Wina ine pano
Nice much love from Zimbabwe he must collaborate with jah prayzah from Zimbabwe lol
apa ndiye number one ndipo ukanango yimba pano ina ukanapita patali kuposa mbuyomu😂😂😂😂😅
Mpaka nsapato zamakaka eee aseh udali serious
Chala chinaloza lelo mulungu watilanga kwambirir njala paliponse eee abale tikurila ife
Nyimbo mbambande 2025 Dpp iwinira zomwezi
Zomwe wapanga dan zandibowa sizikukomaso apa aaaah
uzatha ngat joseph nkasa phwanga nyimbo zandale sizipita patali ndinasiyaso kumvera nyimbo zako kape
Wakutuma ndani kuti umvere nyimbo yake? Kapolo wachabechebe. Umafuna anthu azivutika. Zinatha kale
Musatero naye angopangira kupanga makobiri basi
Chi team chowina wina my votes dpp
Nyimbo izi zinali nyatwa heavy
Ngakhale wasokoneza kumapeto after 4 yrs iyiyi udakwapula😅
Manyadzi bwanji a Dan? Mzingoimba Zama love zomwezi zinazi sizimakukhalani.
Nyimbo zomwez tivotele DPP
Danlu uganize kawiri ukuwonekera umbuli hvy
😊😊😊mnayamba mwaionapo nyenkhwe inu hahaha vizakukuzgokera siku linyake mzala 😉
Team A ndi one🔥
Nyimbo ndizomwezi basi
My best chipani 💯
Palibe angamake (peter Tate wa fuko)👍👍👍👍😂😂😂😂😂 nice talent sumasapota zoluza
Nyekhwe iyo ndiye lero udziti ukupepesa mwano onse uja shame ,nyekhwe waona ndani tsono
@@arthursinoya65 kasambe uko
Imene aimba yaachakwela siingafuke apapa 💯
Thaw imeneyo bora tikanakumvera dan lu
Kmatu Daniyele Nyimbo munaimba kale ku Dpp🤣
😂😂😂😂😂 Pot mwaopa kufa Nye stsya DPP uwone Danlu
Munaphelezera lero koma mulikomweko
Zovala zimachita kumukhala aaaaa
Ndipo Chala chinalodza🔥
Koma nyimbo iiiii ayi zikomo
wow i missed this ...Dan ndiwe dolo
APM it's our solution kwinako pita ukangodya ndalama zaphwekaxo
awona nyekhwe....atsegula mmimba kkkkkk..ili sharp ankolo
U got talent ndaonera nyimbo iyi not ya chakwera
Nyimbo zokoma zinali zomwezi
iyiyi inali hit eeeeeh😅😅😅😅
Na iwe anakoza Dan....
Hit song Of all time, siku apezekanso hit ina
Kod mukuyimba mutamwa moyo kapena chmba chomwechi
Awona nyekhwe ndi ambwiyache panyapako Dan lu uphawi si zinthu
Nyimbo ndi izi kma osati zatuluka zija
This guy is a Dpp ... kwinako akasaka ufa
M'busa wanj olimbikisa za mademo 😢
Zovala izi zimakukhala tu ase wachitilaji zopusazo
Pa ma artist achinyamata akumalawi amene amandiwa zaka za mbuyomu anali Dan Lu kma akuluwa atangoyamba nyimbo za ndale ndinatuluka sindimafilaso
Nice dressing,, ndiza Ana ogeza a dpp izi
Munachedwapo nice💯🎵
A Dan Lu ndinu a DPP osat za MCP zanuzo ndipo sizikukukhala😂
Iyi nde nyimbo
Limbikira umuchose zambriri mdala wakoyo.
Awona nyekhwe dpp boma ilooooo
Mnyamata wakwatu ku mangochi ili chenene kobasi brother tikuwonela ku joz Good song
Adaad in my blood
Tiwanyenya nyenyadi ambatatawa
Mbambande
KKKKKKK Ndalamadi zimapangitsa kuchemelela madzi a mu suwage
Keep it up brother more fire 🔥🔥🔥🔥
Ma die hard a DPP ife...... Dope 👌
Who is watching this in 2024 😢😢😢😢
Kkkkkkkkkkkkkkk ndawasegula ndiwetuuuu mbuzi
osabwelela mbuyo Dan lu maso pasogolo
Who come after chikangawa songs 😊
Iwe ndi 1 enawa anazolowera za usamunda pano tili mu democracy adad woyyeeee
We still whatchng this 😂😂😂😂😂
Ur super star aise
koma munalidi kale man,osati manyaka mwaimbao...
From team A to team C 😂akutame ndan😂
Ndipo adhawa ndimawafila heavy koma apapa kaya
Nxt yr ikuchedwa bwanj
Ndpo
Akuti akufuna kumanga Dhamu lanyuwani lang'ona. lol
Wanyafye
Mwaphat man
Nthawi imeney kaimba mtima uli malo ,not pano akuimba akucheuka cheuka
Dan lu is very talented. Watching it from Canada. where are you guys watching it from?
Ndugi Malawi (3D animation) where in Canada are you?
Great. Atleast you are not voting
Mozambique 🇲🇿
@@johnnsekanabo856 Halifax
Ndugi 3D Animation haha I didn’t know we had Malawians in Halifax, I’m in Halifax too
Munachitaya a man kuimba mumaimba bwino cholowera nyekhwe ndi chiyani shame
Malawi celebrate ulemu wanu
Please please song kulikonse tifika n
mumakwana mr Danlu. critical thinker
Pepani Mr my condolence to you....
Nyimbo ilibwino tiyamikile nawo ngakhale ndine wa chilima 😀😀😀😀
Bhobho
@@sitimulewa1027 bho bho ndithu
Koma anasankha molakwika DPP😭😭😭😭
But the leader is tired, senile & old. Mwina kapena atamusiyira Atupele.
Paribe anga make Apm
Asiyire atupele maybe Madala akalamba
Kodi tivota lit
From Tanzania we love dan!!!!
Here oooooooooo
2025 boma
Diamond u-verse tomorrow done room
Awonad nyekwe nice song big man
Fire fire 🔥