Thank you very much bakili muluzi zimene zikupanga boma lachakwera akuziwa ndimulungu ngat tinawalakwira kuwavotera watching from Mozambique never give up bg brother timakunyadirani kwambir potiwululira zisisi zambavazi
Is this man king of voice? a Malawi nsanje ndiye unakula, ndipo kusangalatsa andale. ine I do support zimene Dr. Michael Usi amanena ndi kuchita. And ulemu wanu olemekezeka a Vice president Dr. Saulosi Chilima,you soo gentle and calm.
Tsopano lesson yanji ku malawi.inde tikufuna kusinthaso mtsogoleli koma sitingavotele 80years reader kuti chiyani.msaka,mwanamveka ndi ena alipo but why 80yrs 😢
@@user-zy2nh4lj4h ine ndingoona kuchedwa kuti afe zikhare ndi munthu oyipa kwambiri ndipo ndikukaika ngat anabadwa kuchoka kwa Mai chifukwa Ali moyo oyipa kupotsa fisi
King of voices in Malawi ulemu upite kwaose okonda Chanel ichi
uyu samabisa kanthu ayi ubwino wake samakamba nkhan ndiso history za dziko lathu ayi koma maiko ose
Thanks❤
Uyu ndi dolo eve
Thank you very much bakili muluzi zimene zikupanga boma lachakwera akuziwa ndimulungu ngat tinawalakwira kuwavotera watching from Mozambique never give up bg brother timakunyadirani kwambir potiwululira zisisi zambavazi
Is this man king of voice? a Malawi nsanje ndiye unakula, ndipo kusangalatsa andale. ine I do support zimene Dr. Michael Usi amanena ndi kuchita. And ulemu wanu olemekezeka a Vice president Dr. Saulosi Chilima,you soo gentle and calm.
God will visit Chakwera and his cabinet
Thank you very much Bakili muluzi tv, yes indeed a leadership does not a size bed but knowledge and wisdom God bless Malawi
Thanks Our own trusted historian
Am hearing in juberg l ❤ you brother to talk street♥️♥️
Umakwana your are number one
Double salute bro, Mulungu azikutetezerani kuzinkhanilazi
Very educative, keep us slowly educated
Following every video which you post them here, Bravo Mr BM TV
Allah bless you brother
Ulemu wanu big ine ndimadikira zimenezi big l love you❤❤❤❤
History in marking,, wake up call for all Africans youth.
Congratulations to the president,let's pray for his success
Iweyo umatimililasa ase God bless you
Mukambek ya culture Joseph hill
Koma mulungu si muthu mmm ❤❤
Good big alekeni tiwonana 2025
Bakili muluzi TV more 🔥 and Bon Kalindo the DC more 🔥
TV mbambande my vote for APM ❤❤❤❤❤
Iyi ndiyomwe ndmaifuna thx bwana
I was waiting for this ..❤akulu,
Good job guys kumalawi nkhalamba dzavuta
You are the best always
Thank you for great job big keep it up dude ❤
Keep up best TV
Nicee Boiz Anyamata Omvana Kwambr
Ulemu wanu bakili muluzi TV timakunyadilani and simumapsyatila zichitika izi kumalawiko ishaa llah
I was waiting for this video
Thanks Big man
Ulemu wanu braz mumakwana
Koma timafuna history ya Muhammad Ali kaswili wa nkhonya waku America 🇺🇸
Man you are the best
Chakwerayo ngati anaonerepo missing in action 3 ya chack noresi azaona kwasala miyezi yowereblngeka
God bless you brother
Akamuna awa kuti ayimire upulezidenti atha kuwina ndimunthu olankhula chilungamo ndipo Bon Kalindo atha kudzakhala vice president. Titha kuona kusintha kwakukulu mdziko muno ndithu.
Dziko lathu lovesa chisoni kumanga muthu yemwe wagoyakhula audio. Kusiya muthu okhapa wathu eee
God is great
First watch
Best tv
Your best bro
Ndizomwe timadikila thanks
Best TV
Phwanga bushiri taima poyera ,,,kukhalangatiso nawe uoloka nyanja next year
God protect you my brother
Nice ndimadikilila nkhaniimeneyi
❤bg keeping updated malawian 😊
Mumatiimilila abwana
Africa tikufuna atsogoreri achinyamata amaganizo a fresh osati nkharamba zotha ntchito
Ulemu wanu mumatiyimilila❤❤❤
Well big
Good job 👏 👍 ❤
Malawi akuvesa chison ndthu Koma anyway timakunyadlan bwana
Tsopano lesson yanji ku malawi.inde tikufuna kusinthaso mtsogoleli koma sitingavotele 80years reader kuti chiyani.msaka,mwanamveka ndi ena alipo but why 80yrs 😢
watching from Bagamoyo pa Boma
😂😂😂😂
@@user-vz7gk1ed5g so why are you roughing?
@@maulidisaidibugudadi4091 Bagamoyo pa boma
Bon kalindo❤❤❤❤
Congrats
I love it
Pangani ya ku south Africa zikuti bwanji
Zoona kumalawi koo aaaa panopa zithu zizili bwino ndithu.
Mumakwana mani
Best TV series
Best update
Mumatiyimilila big man ulemu wanu
Mmatha Mr soldier
Mumatha chef
Zoona brother❤
Respect bigy
Tiphunzirepo kanthu a Malawi
Ulemu muzikngolandila any time kumalawi tiweluza posachedwapa
Sure
More fire 🔥 mr
Chimwendo Banda ndi dzakudula madzila one day
Big up man
Senegal ndi chiasanzo chabwino. Lazarus Chakwera komanso Nyusi waku Mozambique akunzunza anthu.
Koma Chilima akumulakwila revolution
Ikhalitse Bakili Muluzi Tv💪
Ndizomwe Inu adpp munkapanga kumanga mtambo kusiya chaponda
Give us update ya Israel and Ukraine
respect ❤❤❤
Iweyo ukulimbana ndi mcp osati kuwawuza anthu za history nothing wil. Change malawian what needed peter and hakwera not the same age
You're nothing brother
Koma malawi atipulumutse kaye peter muntharika
Posachedwa pompa Zimenezi zichitika kuno kumudzi pomwe Chakwera adziwe zakuti ifeso tatopa ndi uchitsiru wakewu ndipo nthawi ndi yomwei adyeretu bcoz posachedwapa azisaza ndalama za misonkho yathu
Long live!
Thanks
My TV!
I got you early today 😅
❤❤❤❤❤❤❤❤
Makina amwene
Nice
❤❤💪💪💪💪💪💪👍
Ma MP athu akufunikanso age limit.
Tamadya mabanzi amene akukupatsaniwo, kuno ndikunja. Nkhani ya ku Senegal, ife a Malawi ikutikudza bwanji?
Zikhare NG.oma mutu mometeka ngat ponyela panyani
Kod ndipo ameneuja afa lit zikhaling'omayo
@@user-zy2nh4lj4h ine ndingoona kuchedwa kuti afe zikhare ndi munthu oyipa kwambiri ndipo ndikukaika ngat anabadwa kuchoka kwa Mai chifukwa Ali moyo oyipa kupotsa fisi
Aise iwe wandiseketsa😂😂😂
@@user-bj6ig9zt9e 😂😂 fisi wachepa koma nkango
Zikhale ng'oma try to attack this brother I'm promise u'll see something bad sunu wako fucerk
Chakwela asamale nthawi yantha ametendwe mavunzi
From Johannesburg Kempton park
Koma yeah
Ulemu wanu big
Lazaro oukira Mulungu uyu
Inuyo palibenso ulemu wanu