hot Current..Kumkuyu Vs Namalomba

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 22 ก.ค. 2023

ความคิดเห็น • 224

  • @shakajudahTV
    @shakajudahTV 11 หลายเดือนก่อน +6

    Kunkuyu is just talking nonsense he don't know how anger is in Malawians 😢😢😢😢

  • @georgesmart3791
    @georgesmart3791 11 หลายเดือนก่อน +10

    More fire Nambalomba 🔥 🔥

  • @mkhulukinyata5198
    @mkhulukinyata5198 11 หลายเดือนก่อน +2

    This is the best n' honest ever Hot Current ...Anthu adzikumadi mbali dzonse monga momwe mwapangira apamu. Apa mpomweno tikutha kudziwa kuti " Atambwali ndi atiwo kkkkk

  • @dominicmphepo-jk8lk
    @dominicmphepo-jk8lk 11 หลายเดือนก่อน +1

    For the first time I have to comment on this, from look of things onsewa ndi anthu oti palibe chomwe angapange kuti athandize dziko lino.
    Panopa from what I have Said palibe Ali ndi masomphenya ofuna kukonza dziko koma kutukula matumba awo.
    Sindikuwonapo munthu apa. Continue kutibela basi nthawi yanu. Inu a tonse alliance ibani monga momwe anzanuwo anabela zikuwawa nanuso a DPP mukalowa ibani basi osamangana

  • @ThoccoBondo-mx7vt
    @ThoccoBondo-mx7vt 11 หลายเดือนก่อน +2

    Kkkkkkkk koma mkukuyu zoti azabwelaponso apa ndakaika😄😄😄😄

  • @dicksonilimbani3443
    @dicksonilimbani3443 11 หลายเดือนก่อน +9

    🤣🤣🤣Kukuyu ukuwona ngati malawi ndi wa Abambo oka achakwera et

  • @user-og4oe5yp4w
    @user-og4oe5yp4w 11 หลายเดือนก่อน +3

    🔥🔥🔥🔥🔥 namalomba on 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @ismailkhuneya3346
    @ismailkhuneya3346 11 หลายเดือนก่อน +7

    Kkkk kmabe ngakhale dpp imapeleka ma figure olakwika ku imf kmabe dziko limayenda bwino kusiyana ndipano

    • @samsonmtumbati4855
      @samsonmtumbati4855 11 หลายเดือนก่อน +1

      Yeah zoona boma lomwe lilipanopa likuphweteka kwambiri ndibola dpp

  • @Andrew-nz9sh
    @Andrew-nz9sh 11 หลายเดือนก่อน +5

    ingoswananipo zithepo💪💪

  • @user-fp2qj6vm4d
    @user-fp2qj6vm4d 11 หลายเดือนก่อน +2

    Ndevu za mwayi ndiwe wa mcp bola Brian ndi fire

  • @user-og4oe5yp4w
    @user-og4oe5yp4w 11 หลายเดือนก่อน +1

    Kkkkkkkk ndevu zamwayi 😂😂😂😂😂 apa ndiye mwaitha sindinayambe kunvera koma ndimmene ayambira akunkuyu aaaaaa

  • @ChisomoMsiska-oi2vg
    @ChisomoMsiska-oi2vg 11 หลายเดือนก่อน +2

    Boma limene lasokoneza zinthu kwambiri ndilomweri la mcp

  • @alinafeanderson3065
    @alinafeanderson3065 11 หลายเดือนก่อน +2

    Wonder ur best ❤

  • @HashrouYassin
    @HashrouYassin 3 วันที่ผ่านมา

    Mega farms iyamba bwanji mutadya ndalama zake

  • @lewisbonongwe8518
    @lewisbonongwe8518 11 หลายเดือนก่อน +2

    Namalomba ndiwe galu kwabasi wandisangalatsa kwambiri uli ndi nfundo komaso phuma 😂😂😂😂 wakwana iweyo Namalomba Umatiyimilira tonse amalawi a DPP

  • @Marialongwe-nzlib
    @Marialongwe-nzlib 11 หลายเดือนก่อน +2

    Mungoona Mbava Mmene ikusekera Kusekelera 😂😂😂😂

  • @user-mx5zy7ci3y
    @user-mx5zy7ci3y 6 หลายเดือนก่อน +1

    A Shadreck namalomba kuwonesa kuchenjera satana akukugwitsani nchito koma one day is day muzakolora

    • @ShabaniKuswere-cp7ss
      @ShabaniKuswere-cp7ss 5 หลายเดือนก่อน

      Mmafuna munene kuti a Kumkuyu kapena aNamalomba? Chifukwa ine mkuona kwanga ndikuona kuti amene akuoneka kuchenjera kulankhula apa ndi akumkuyu chifukwa akuzembazemba pamene chilungamo akuchidziwa

  • @lewisbonongwe8518
    @lewisbonongwe8518 11 หลายเดือนก่อน +2

    Akunkuyu ndalama zikubedwa muulamuliro wa MCP komaso njala yaphwi anthua kufa ndi njala

  • @user-he6zq5iu5r
    @user-he6zq5iu5r 29 วันที่ผ่านมา

    Kkkkkk Koma wonder wandiseketsa 😂😂😂😂😂

  • @stanleyfraction539
    @stanleyfraction539 11 หลายเดือนก่อน

    This was hot🔥🔥🔥🔥🔥

  • @user-ed1rr2pw2t
    @user-ed1rr2pw2t 11 หลายเดือนก่อน +1

    Mr wonder mukuyener mukapeleka funso muziwapatsa mpata kuti afotokoze cfkw zikuonets ngat mukufusa funso pamene yankho mulinalo kale

  • @robertrichman9376
    @robertrichman9376 11 หลายเดือนก่อน +3

    Never trust any Politician

  • @vincentkamangamr9062
    @vincentkamangamr9062 11 หลายเดือนก่อน

    Mr Wonder muziwapasa mpata olongosola kuti amalize osamangowadula pliz

  • @louisgolden
    @louisgolden 11 หลายเดือนก่อน +1

    Kunkuyu siukuyankha mafuso Ungokamba mbalume zopusa

  • @victorbanda9039
    @victorbanda9039 11 หลายเดือนก่อน +1

    Namalomba ndimwana pandale Ndipo muli makani opanda ntchito atakhala m'boma anthu awa sangamatsutsike

  • @collinsmbewe3109
    @collinsmbewe3109 11 หลายเดือนก่อน +1

    This government is a headless government

  • @WakuMalawi
    @WakuMalawi 11 หลายเดือนก่อน +1

    These men are well aware of the real reason our Country is poor. We're not utilizing Malawians. We're too busy acting like servants. Where's a real Gov't with chidwi and commitment to improve us? Our Politicians are embarrassing.

  • @ganetkanzeru5153
    @ganetkanzeru5153 11 หลายเดือนก่อน

    Hot current yalero ndiye yandiwaza nyatwa kkkk

  • @salimmkumakumakitombi-yc7pw
    @salimmkumakumakitombi-yc7pw 11 หลายเดือนก่อน

    kkkkkk Osokonedza abwera

  • @frstyhavoc6678
    @frstyhavoc6678 11 หลายเดือนก่อน +1

    Koma ilyi ndi hot current for sure 😀😀😀😀

  • @pauldaka7966
    @pauldaka7966 11 หลายเดือนก่อน

    Komatu eeeeee! Amalawi timadziwa kudzibakira

  • @collinsmbewe3109
    @collinsmbewe3109 11 หลายเดือนก่อน +1

    Kunkuyu amalawi tikufuna moyo wabwino osati zomwe ukulankhulazo

  • @AbleGondwe
    @AbleGondwe 23 วันที่ผ่านมา

    Wonder musiye kunkuyu alankhule

  • @kho7676
    @kho7676 11 หลายเดือนก่อน +2

    Koma akukuyu amatha osutsa satinthandiza

  • @collinsmbewe3109
    @collinsmbewe3109 11 หลายเดือนก่อน +1

    If they are failing to buy a packet of sugar why? Is not because of expensive

  • @JohnNsona
    @JohnNsona 11 หลายเดือนก่อน

    anuwake a program safunsa manfunso mwa intelegent amafunsa mwa ubulutu kapena mwa usavage Kodi mumapitadi Ku school kukaphunzira zapa wailes funsani munthu mpatseni mpata ayankhe

  • @FefieTenisha-du7ge
    @FefieTenisha-du7ge 7 หลายเดือนก่อน

    The main problem that these leaders have is they politicize everything...Instead of coming up with workable technical solutions they are just busy backing up their parties....This is sickening!
    It appears Malawians are not just poor economically but they are also poor mentally..
    These leaders are not on their seats to fix Malawians problem but to fix their personal and party problems...

  • @piliranimphepo1920
    @piliranimphepo1920 11 หลายเดือนก่อน

    I think there is no need to b inviting these failed politicians... palibe chanzeru angatiuze adzingolozana chala basi.. continue your program mmene mumapangira kale

  • @user-rd4lf2gg7g
    @user-rd4lf2gg7g 11 หลายเดือนก่อน +4

    DPP ibwelele plz cement 20,000😮

    • @eliffagondewe8214
      @eliffagondewe8214 11 หลายเดือนก่อน

      Ndipo mavuto alipo nde mkuka voter so imbwaa zimenezo ayi zikomo mcp🙌🙌🙌

  • @Littlefair7
    @Littlefair7 11 หลายเดือนก่อน +2

    Wonder usamabwere utakhuta cyclone mbatata wamva, ukumagunda posagunda bwanji😂😂

    • @dyba-x9w
      @dyba-x9w 11 หลายเดือนก่อน

      akuonesa mbali

    • @Littlefair7
      @Littlefair7 11 หลายเดือนก่อน

      @@dyba-x9w
      Ayi sanaonetse mbali koma inuyo muli ndi nkhawa ndi mbali yanu.

  • @thomasgamah764
    @thomasgamah764 11 หลายเดือนก่อน

    Program iyi ndiyandale amalawi muzisamala pomaoonera manyaka awa, this is another part of compaigning

  • @harrisonnavayah6480
    @harrisonnavayah6480 11 หลายเดือนก่อน

    Wander ndiwe Garu

  • @molicieeosama8877
    @molicieeosama8877 11 หลายเดือนก่อน

    Izi zikadalongosoka chikhala Kuti khaniyi ikukambidwa mwadongosolo. Koma Vuto Lake zikukhala Ngati Wanda wabwela Atalawa.

  • @ThomasChiwaya-qx9mf
    @ThomasChiwaya-qx9mf หลายเดือนก่อน

    Kod akukuyu kod wasowetsa sugar ndan mesa Inu atonse ( a mec akazangotulutsa kut mwawinaso muzaiputa khondo cuz mukuziwaso kut 3coters simukufunidwa dziko lino )

  • @fatimautilah5648
    @fatimautilah5648 หลายเดือนก่อน

    Both parties palibe chomwe amayakhula zogwiea mtima,mitima mwawo mwangozaza mikwiyo

  • @ThoccoBondo-mx7vt
    @ThoccoBondo-mx7vt 11 หลายเดือนก่อน +1

    Big up Namalomba

  • @EmercianahKasiku-en6hl
    @EmercianahKasiku-en6hl 11 หลายเดือนก่อน

    Namalomba uli ndi nzeru koma wamushayinitsa Kinkuyu chifukwa uli ndi phuma next time uxizaupeza komaso kukhalitsa ndi APM sungakhale ndi nzeru bcz ija ndo mbatata ya mtsogoleri yomwe inkangona pa chiongolere,mwachidule nonse mbava zobera a malawi

  • @adamkudzala186
    @adamkudzala186 11 หลายเดือนก่อน +1

    Kumkuyu ntchito yamukulira

  • @millionsenenje5010
    @millionsenenje5010 11 หลายเดือนก่อน +1

    Kumkuyuyu mkatundu

  • @RobertChipala
    @RobertChipala 3 วันที่ผ่านมา

    Palibe chomwe akudziwa Namalomba zachuma samazidziwa

  • @victormmbewe961
    @victormmbewe961 11 หลายเดือนก่อน

    You must agree that the past affects the present.

  • @user-hp7xe2nu6w
    @user-hp7xe2nu6w 11 หลายเดือนก่อน

    Kukela kwazinthu kukhala ngati munabadwa kwachinyama agalu achakwera ndi adzanuwo ndiposo kumkuyu ndiwe kape

  • @harrisonnavayah6480
    @harrisonnavayah6480 11 หลายเดือนก่อน

    Trillion kuitchula nganti pin

  • @phanuelgryn858
    @phanuelgryn858 3 หลายเดือนก่อน

    mr msisya improve your questioning skills when you have big dogs

  • @serakillo8668
    @serakillo8668 11 หลายเดือนก่อน

    Athu ...onsewa palimbe chomwe akuyankhula zomve saname angopanga ngti akupanga nthano awa a mcp nawo athu olephera ...padzaka zitatu apanga chani bolako Dpp ndithu tinkhodza kulodza zomwe apanga azaowo ❤❤❤ Dpp awo ziphuphu kuba kwambiri mcp

  • @ShabaniKuswere-cp7ss
    @ShabaniKuswere-cp7ss 5 หลายเดือนก่อน

    Ntchito ikumuvuta uyu amene akuyendetsa program_yi kodi Brian Banda analikuti nthawi yomwe amamusiira mzake wa mcp_yu kuti apange Host program yofunika ngati imeneyi???

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 11 หลายเดือนก่อน

    Koma mmene likuzunzira dziko ili,anthu tikuvutika day in day out mkumati tikulonza mavuto amene anzathu anasiya three years down the line,like really Mulungu akuyendereni mwapadera sure😢😢

  • @nelsonkanjira2400
    @nelsonkanjira2400 11 หลายเดือนก่อน

    Zitsiru Za anthu iziii muwatenga amalawi Ngati a kapolo

  • @ronaldsinjeni7823
    @ronaldsinjeni7823 11 หลายเดือนก่อน +1

    Masanje okhaokha

  • @dyba-x9w
    @dyba-x9w 11 หลายเดือนก่อน

    ineyo ndikuona molakwika kwambiri ndikukumbukira mau omwe bon kalindo anayankhula week yatha kuti times ikubakira kwambiri tonse adminstreation, ndikanakonda a Wonder wo akufusa mafuso awo ndi a indipendent balancing sikutheka . akhale neutralas ngati mtolankhani

  • @hopeskafumbiphiri6011
    @hopeskafumbiphiri6011 11 หลายเดือนก่อน

    DPP imakwana kkkkkkkkk keep it up.

  • @user-hp7xe2nu6w
    @user-hp7xe2nu6w 11 หลายเดือนก่อน

    Koditu wakuba amayankha mwazelu cholinga awapusise amalawi pano nde tazukatu siife akale aja ayi

  • @stubish0p-fl2zf
    @stubish0p-fl2zf 11 หลายเดือนก่อน

    Ndikanakonda kuti msogolomo osamatenga andale kumapezeka pamenepo chifukwa wandale ndipovuta kuti azavomereze zolakwika zake, ndiye ife okonda dziko lathuli amatipwetekesa mitu.

  • @alihibrahim
    @alihibrahim 11 หลายเดือนก่อน

    Palibe gvn imene idzabwele ndi chilungamo ku Malawi mbanva zonse

  • @user-xs3pk1vp8i
    @user-xs3pk1vp8i 4 หลายเดือนก่อน

    DPP inakanika kale now we are looking forward namalomba wawononga chipani Cha ambuye ake

  • @yusufsadic2930
    @yusufsadic2930 11 หลายเดือนก่อน

    Kom Nyasa tim imakwanad
    Kuposa Akt kul zodiac
    Mpak mwakumanizad
    Ulendo win mudzamuitan chilim ndi Atuper
    Komanso chakwer ndi pit

  • @meditationmusic293
    @meditationmusic293 11 หลายเดือนก่อน

    A wonder ndachitsiru so buanj

  • @Theheritage86
    @Theheritage86 11 หลายเดือนก่อน +1

    Brian alikut

  • @thomchinjoka177
    @thomchinjoka177 11 หลายเดือนก่อน

    Nkukuyu or utakokera motani ,zakubvutani basi , palibe mukuchita ,komaso a wonder ndinu a MCP

  • @user-xi2ue2yq7b
    @user-xi2ue2yq7b 11 หลายเดือนก่อน

    Kunkuyu nchitsiru, chidzete, munthu opepera, nyapapi weniweni.

  • @MikeMerecah
    @MikeMerecah 2 หลายเดือนก่อน

    Kuchenjera kwatha mcp anthu oipa,

  • @TrysonChimenya4-fm8nt
    @TrysonChimenya4-fm8nt 11 หลายเดือนก่อน

    Namalomba ndiye dolo Akunkuyu sakundifikapo anta naye Wonder akuonena kuti sympathizer wa MCP

  • @CRMTV-pw9jt
    @CRMTV-pw9jt 3 หลายเดือนก่อน

    Mcp inatengadi mbuli

  • @user-yp3um6mf8d
    @user-yp3um6mf8d 11 หลายเดือนก่อน

    I think Kunkuyu is clever enough however he doesn't have enough data to tell the nation how and what to do to improve our economy.He is a good politian to protect his superiors.If he can be honest he will admit the failures in the regime.Please accept you have failed guys.

  • @petersoko4283
    @petersoko4283 4 หลายเดือนก่อน

    Namalonda sanakhakepo mbom

  • @andrewngowe8836
    @andrewngowe8836 11 หลายเดือนก่อน

    Mbuzi za anthu Malawi tili pa moto dziko loti lingathe kusitha mosavuta koma dyera mbuzi za anthu izi shupiti

  • @dyba-x9w
    @dyba-x9w 11 หลายเดือนก่อน +2

    a wonder try your best to be neutral change your system, it seems something is not ok with you.

  • @shupikayintuwaluwa-5899
    @shupikayintuwaluwa-5899 11 หลายเดือนก่อน

    Political z a deaty game a can agree na

  • @GloryKhondiwa
    @GloryKhondiwa หลายเดือนก่อน

    Politicians😂 this is just a game 🎯🎮

  • @JOHNMARK-sl5ff
    @JOHNMARK-sl5ff 11 หลายเดือนก่อน

    Malawi feeling pains😢

  • @frankphiri257
    @frankphiri257 11 หลายเดือนก่อน

    Muzamenyanisa akulu akulu
    Muzizikhoza bwino zithuzi

  • @sjrecordschannel7687
    @sjrecordschannel7687 11 หลายเดือนก่อน

    Mbuzi zokhazokha zinakumana

  • @simonpaul6567
    @simonpaul6567 11 หลายเดือนก่อน

    This hot current for today there is nothing you 2 you answer Mr Namalomba and Kumkuyu

  • @EfeloYovita
    @EfeloYovita 20 วันที่ผ่านมา

    munalakwa pochotsa dpp chomwe mwachita inu a mcp ndichani dpp imagulitsa feterizer 50 kg inu a mcp k90,000 anthu akumudzi angakwanitse kugula feterizer? mwaononga dziko a mcp anthu akuba okupha

  • @donnexmgabe4355
    @donnexmgabe4355 11 หลายเดือนก่อน

    Mungakweze bwanji lulimi pomwe feteliza ndalama mumapeleka kuma butchala ndi kuma Pharmacy anthu alimila chani mwalephela basi tatopa

  • @user-ne7rn4ki3c
    @user-ne7rn4ki3c 11 หลายเดือนก่อน

    Kalonga Shawa uiwale za 2025 ndipo muyembekezele kumangidwa

  • @user-gu5fy3tg2u
    @user-gu5fy3tg2u 4 หลายเดือนก่อน

    Kumkuyu galu mutu oumawo

  • @felixthomas1781
    @felixthomas1781 11 หลายเดือนก่อน +1

    Kumkuyu is an amateur. Childish so called minister.

  • @kennethmakweya3561
    @kennethmakweya3561 11 หลายเดือนก่อน

    Namalomba amakhala nditimajoker, atha kupweteka gulu

  • @thelondonbridge6605
    @thelondonbridge6605 11 หลายเดือนก่อน +2

    Wanda ndi wa MCP ...chitsiru cha agalu

    • @pauldaka7966
      @pauldaka7966 11 หลายเดือนก่อน

      Inde mchifukwa chake program iyiyi ikuveka monga akuyambana

    • @eliffagondewe8214
      @eliffagondewe8214 11 หลายเดือนก่อน

      Kkkkk sure anali ata coach na kale awa aaaa🔥

  • @dinganinedsontchongwe610
    @dinganinedsontchongwe610 6 หลายเดือนก่อน

    sindikufuna kutaya nthawi yanga ndikumvetsera uyo wa mcp uyo palibe chimene anganene manyazi alibe galu waanthu

  • @leveltrapper4322
    @leveltrapper4322 7 หลายเดือนก่อน

    DPP INACHOKA BOMA CHIFUKWA CHA MABUNGWE OSATI CHFUKWA CHOTI IFE SITIMAFUNA DPP AI KOMANSO INACHOKA CHFUKWA CHAAA ENAWO KULILIRA

  • @bayview4554
    @bayview4554 11 หลายเดือนก่อน

    Mukukambila zopusa zokhazokha amalawi akuvutika

  • @user-ux8bc6wy1i
    @user-ux8bc6wy1i 11 หลายเดือนก่อน

    😂😂ya lero yachema

  • @enockjailos6233
    @enockjailos6233 11 หลายเดือนก่อน

    This one the dog of the dogst🇲🇼👁

  • @StevekantickKantick
    @StevekantickKantick 11 หลายเดือนก่อน

    Kodi Mesa amatcalenger kt after 2years akhala atapanga client kukanika apamga lisine pano tree years apamga apamga chani mbava

  • @ThomasChilemba
    @ThomasChilemba 11 หลายเดือนก่อน

    Mtolamkhani wa usilu ndale izi

  • @kennedychinguwo1640
    @kennedychinguwo1640 หลายเดือนก่อน +1

    I think Wonder Msiska u are the one who is bringing chaos in this interview-U are very unprofessional

  • @MotivatedI
    @MotivatedI 11 หลายเดือนก่อน

    Ma trillion being mentioned like it’s nothing.

  • @josephinemisomali6840
    @josephinemisomali6840 11 หลายเดือนก่อน

    Dpp ndi Mcp sitikuisowa kudzalamuliranso dziko onsewa ndi anthu akuba munthu akakhala okuba ndi okuba basi bolani tiyese anthu opanda chipani