On the issue about the phone..... Comrade you are right. Even ku convention he never touched his phone pamene enawa ku convention kuja anali busy ndi ma phone.
😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢 A aaàaaaaa inu spending much time on the Phone 😢 kuumiranso 😢😢😢😢 koma ndaseka Akabambe anapereka ka nthobwa enawo busy ma Phone, Iphone kikikiikiki DELEGATE wavota Molilitsa kikikiikiki 😅❤🎉❤

KUZITUKUMULA KWAMBIRI KOMASO NDALE ZONYOZANI SIZIMATENGELANA PATALI ESPECIALLY NOKHA-NOKHA
Zowona zake
Fact
The root cause of political ignorance in Malawi is self- centredness.
Bola komwe aliko ngati akumva asinthe makhalidwe onyoza anzawo akamachita compaign lero ndi izo azionera okha kupeza ma 20 votes chifukwa chakudzikonda.. lero mkumati aberedwa vomerezani apa kuti mwalephera koma mochititsa manyazi..
Zoona izi bro Kabambe ndi munthu woyenera amadzichepetsa
Zoona my brother
Komabe onsewo adakakumverani ndie bwenzi kuli ma president angati?
😂😂😂😂😂 koma mtumbuka uyu
agwilire ntchito limodzi basi , masankho adayenda bwino
Eya zoona
Lwara umakwana
Nanga manganya titani naye bwana Sam??
Maka pa zomwe akuchitazi
😂😂
Usi sanapite kumavoti umbuli bwanji
😂😂😂😂
😂😂😂😂😂😂