MCP achievement ndi Kupha bas Chomwe ikuchita Ku Mtundu wa Amalawi. Fisi ndi Fisi, Ng'ona ndi Ng'ona 🐊🐊🐊👹 Stay safe brother Mtanyiwa Stay blessed brother Mtanyiwa Be protected 🙏🙏 and you are Loved ever ❤❤. Never give Up Mchimwene Mtanyiwa fight for the better Malawi
Ntanyiwa umakwana JAH BLESS You all the time,ndikanayandikila Ku Dowa ndikaithila Moto nyumba ya chisiru yo kuno kuzomba muzipasa map ndi ndandanda was China chawo chokubacho tiwotcha zimenezo chifukwa ndizathu zomwe kapena Kuwabera basi
MATHEW 27 VS 45 TO END. A NTANYIWA ZIWAZEN MWAZI MWA AMBUYE YESU UKUPULUMUTSENI NDI KUKUTETEZANI KWA ADANI ANU ONSE NDI IZI ZATHEKA MDZINA LA AMBUYE YESU WATHU AMEN..
Aaaaaah ine nde nsaname zomwe zafikapa ndaona kuti palibe chabwino ayi tikadzuka rikungigwetsedwa ndi mau okha basi mmmm ma demo ma demo boma likangokhosomola basi ziiiiii aaaah ntanyiwa apa zafika pokwana tsopano titqni kut8 tikhale ngati mu nthawiyi ya adad yomapanga zinthu mosanva zokamba za aboma mkuima pa ma demo?
Mr ntanyiwa awuzeni anthu avetse a mcp ndi chipani cha mai joice banda akumakomana amalawi asamale pamenepo komaso anthu Wa zao ndi zapasi pa madzi ndichifukwa sakufuna kusintha China chilichonse cha amalawi cos chakwera wapanikuzika kwambri ndi gulu la anthu amenewa ulamuliro umenewu ndi Wa satanici ife aaaa zumoo taonaso
Chakwera ndy wafika pokwana eeeeeeeeeee ineyo ndy wandikwana guyz
Umandifika mtanyiwa Allah bless you all the time until 2025 wooo!!!
Zoona zake may almighty protect u Mr comrade ntinyiwa we love you for sake of almighty
Good bless you ntanyiwa
Timakunyadirani Mr Comrade Mtanyiwa chifukwa mumatimenyera ufulu ife a Malawi ndipo musadzadere nkhawa ayi timakupemphererani kuti Mulungu akulitse malire a moyo wanu ndiposo ndinu otetezadwa nthawi zonse ndi Mulungu yemweyo inuyo ❤❤❤❤❤❤ ndipo pitilizani kutidziwitsa zonse zomwe a MCP akuchita . Ambuye azikudakitsani kwambiri 🎉🎉🎉🎉
Comrade mtanyiwa nyimbozo muxitiponyera
Ineso ndufuna ija imati achakwela ufumu wanu akubwela a mec azautenge
MCP achievement ndi Kupha bas Chomwe ikuchita Ku Mtundu wa Amalawi.
Fisi ndi Fisi, Ng'ona ndi Ng'ona 🐊🐊🐊👹
Stay safe brother Mtanyiwa
Stay blessed brother Mtanyiwa
Be protected 🙏🙏 and you are Loved ever ❤❤.
Never give Up Mchimwene Mtanyiwa fight for the better Malawi
Akusewela yoduka akunama
Zaithwa
More 🔥 Mr ntanyiwa timakunyadilani
Amboni za yehova mwayamba ndale atilipano mwatayaha Jehova apa🙌🙌🙌
Mulungu akudalitseni , akupatseni Moyo wautali Ntanyiwa
Ntanyiwa umakwana JAH BLESS You all the time,ndikanayandikila Ku Dowa ndikaithila Moto nyumba ya chisiru yo kuno kuzomba muzipasa map ndi ndandanda was China chawo chokubacho tiwotcha zimenezo chifukwa ndizathu zomwe kapena Kuwabera basi
Chitanipo kanthu ngati muli ndi kuthekera
MATHEW 27 VS 45 TO END. A NTANYIWA ZIWAZEN MWAZI MWA AMBUYE YESU UKUPULUMUTSENI NDI KUKUTETEZANI KWA ADANI ANU ONSE NDI IZI ZATHEKA MDZINA LA AMBUYE YESU WATHU AMEN..
I love you so much mr ntanyiwa mooo 🔥🔥💯👊🤓
More faya my comrade
Timadziwa zambiri chifukwa Cha inu a comred mtanyiwa mulungu adzikusungani ndimoyo ndipo azikutetezelani kwa Adani Anu onse
Ambuye aremekezeke mnthawi zose ndimakunyadirani acomrade ntanyiwa l love you zikomo ambuye azikudarisa mnthawi zose
Zosayenda
Chonde chonde mrs Tanyiwa musatinyanyare chonde
God bless you
Inutu simufa pano MULUNGU AKUSUNGANI NDI KUKUSAMALIRANI kuti kusamalire Malawi.
God bless you always
Katundu oopsa kwambiri eee oyes
Chakweli mbuzii meeee
Ndimakukonda Mtanyiwa ndipo Mulungu azikuteteza ndiwe Mpulumutsi wa ife aMalawi
Ntanyiwa timakukondani ❤
Kufuna kutamika ndi zinthu zopusa basi muone abwino ndi mabodza anuwo
My radio
Ambuye wakumwambako apitirize kukutetezani, tioloseni chonde tifike ku canana
bwana comred moyo uli bwanji.mulungu akutetezeni kwa adani onse.timakusatani kwambili.kukumverani kuchokera ku tete.
Big boss
Koma iweyo Chakwera Ambuye akukuwona zonse zomwe ukupanga ndipo Mulungu sizikumukomera misonzi ya a Malawi ili pamutu pako
ANTANYIWA timakunyadilani kwambili mumagwira tnchito yotamandika
Timathokoza mumatiziwisa zimene stinakatha kuziwa. Koma chonde tayesesani kumafotokozela mwachidule ndimomvekabwino kuti tizimaliza kunvela yose. Ngat zachuluka muzipatulako ndikubwelaso ngati mmene amachitila wa bakili muluzi tv timanvela mpaka kumaliza. Tikufunila masiku abwino MULUNGU akusamalileni
Mumatiimilila
COMREDE NTANYIWA umakwana❤you
Zikomo Mr mtanyiwa kumeneko ndiye kumangirira
Game on Mtanyiii 😅😅😅😅
🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Mmmmh 💔 💔 💔 komano amalawi osamawapasa fake news Tilipano wake uti kumunamizira.... Nkhani xa zipani zanuzo osamapanga add anthu amene simukuwadziwa , munthu wa Mboni za Yehova angakhale wa ndale ... uzichita manyazi ukamadyetsera a Malawi nkhani za bodza ndipo ndiwe munthu oipa ndikuuze chilungamo.
Ulula timadalila inu bwana ndithu
Chakwela patumbo pake galu oleredwa ndisatana panyapake chikangawa mbolo yosadurayo galu
Eya shop yimeneyi yilikonkuno tayidziwa ndithu Comrade koma anthu alindi chintchito choopsa
Katundu wa Boma Comrade mtanyiwa musazamuphwekese
Chifukwa amene aruza aja mitima yawo ikhala mpansi chifukwa Inu mukubweretsa gwirizano takumyadirani munthu ankulu
Malawi dziko lodana ndiziyanthu za nzazeru
Mavuto ku Malawi mmmmmm
Ulemu wanu bg boss
Aaaaaah ine nde nsaname zomwe zafikapa ndaona kuti palibe chabwino ayi tikadzuka rikungigwetsedwa ndi mau okha basi mmmm ma demo ma demo boma likangokhosomola basi ziiiiii aaaah ntanyiwa apa zafika pokwana tsopano titqni kut8 tikhale ngati mu nthawiyi ya adad yomapanga zinthu mosanva zokamba za aboma mkuima pa ma demo?
500 000 000 ndi ndalama yambiri itha kugula ma vote by supporting poor people at rural areas, koma awa a president achakwela
😮
Kodi inu andale mukuzikonda tisanakuvoteleni ndiye mukavoteledwa???
Mr Comrade ntanyiwa uremu wanu
Koma crocodile akufuna a azayendese dziko athu a sakumufunaso koma iwe crocodile ukutayisa thawi yako uruza uzaonaso machine sakugwira ntchito kumalawi
Mr ntanyiwa awuzeni anthu avetse a mcp ndi chipani cha mai joice banda akumakomana amalawi asamale pamenepo komaso anthu Wa zao ndi zapasi pa madzi ndichifukwa sakufuna kusintha China chilichonse cha amalawi cos chakwera wapanikuzika kwambri ndi gulu la anthu amenewa ulamuliro umenewu ndi Wa satanici ife aaaa zumoo taonaso
Mtanyiwa🤣😅
Machine asmartmatic athera mu njira ndithu
Ulemu wanu bigman
Ntanyiwa iwe umatisegula Mason kod chakwerayu anapangidwa kut azingopha bas mavaics present onse aaa koma abuse zoona many azimuth mulibe
Ndi wa satanic uyu si busa ayi
Ndale kumangokhala zophana gangata walakwa chani ka mtundu aka ka mcp mmmm ayi
Koma ziliko
Zikomo
Comrade ndili ndi nkhani ndi kufuna number yanu
M.C. P meaning Mumuchose Chakwela Pampando 😂😂😂
Mcp akuti akawina mcp 2025 azasisa feteleza ndi chimanga ndeno pano ali m'boma kale bwanji osasisa pano poti ali m'boma kale
Ndi zitsiru Chakwera ndi zimzake
Smart matic ai, manual only
Matsiku ano ndi mboni za satata asati mboni za yehova
Tili pano kudikila
Bg ku hewe kurumphi sangapeze votiyanga
Loud and clear Mr Ntanyiwa inuyo ndi mo fire
Ife timakukonda anthanyiwa fay mabomba😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Galu alimuboma kale koma akuti azasisa ameneyu ndi galu kwambili sindikufuna kutukwanatu ai
❤
Ulendo wa 2pin pano ndikulipira 6pin mabvuto awawa mulungu kumwambako muliko tichoseni pa moto
Please please
ife tikavotela chakwelayo osati zopusazo
Bola inu mukugula zinthu zotchipa
😂😂😂😂❤
Apatu Sali mboma,Ali mu MCP.koma akachoka ku MCP ko ndi pomwe atsise fetereza,kkkkkkkkk koma chakwera ndi buzi ya kukasiya
Ntanyiwa ulimbo❤
Amen
KATUNDU wa BOMA
Eeee😮😮 kma
😂😂😂😅
❤