DC a PAC pa ucisilu pa mawo cifukwa anthu amenewa ndi mbuzi za anthu alibenso tcito.Mwana wa ng'onayi palibe cimene angatiuze tipanga cina cili conse koma smart matic sigwila ntcito ifenso tinafa kwambiri, mcp palibe kutenga mmalawi muno muvuta cimene cikufuna cikangawa ndi anabelo cimeneco tiwapatsa palibe kunyengelelana.
Aaaa PAC anadya zambili ku mcp awa ndi galu KWABASI NDI MCP YAKOYO MACHINE OTSALOLA MAYI UYU NDI NDIFITI.KATI MALEMU BAMBO AKE JOHN TEMBO AKAKAMILA CHANI NDI NKHONDO IYI 2025
Koma kungowina chipani china anthu ambiri adzapeza ntchito mmboma mmabugwe komanso mma company osiyasiyana tizasese ku cleaner from judicial executive ndi ma government bodies onse kwadzadaz mbava zosakonda dziko lawo mulungu amaulula zinsinsi zobika mwanjira yake mmalawi mu a muli anthu oipa amabisala mmbuyomonsemu koma pano awoneketa Babylon akugwa basi
Kodi iwe kalindo uli mbali iti? Why are you not recognising Dr kabambe as the people's choice, repeatedly ukumanena kuti Kabambe mulendo, how dare you!! Iwenso zikukuwawa kuti Dr kabambe adawina? Wosakhale chete bwanji mesa unatuluka utm chifukwa cha dyera. Amalawi akufuna munthu woti azakonze mavuto azachuma omwe ali mdziko muno, and kabambe is the right guy for that job. Palibe zaumwini apa, merry Chilima anakukanilanitu- mumamuwona ngati ndi mbuli ngati inuyo-, . Kabambe is the president, period. Bwanji sukupanga accuse amene akubweletsa mpungwepungwe like manganya. Ndimakupatsa ulemu koma ndadzindikira kuti ndiwe idiot.

Hte dc mukunena zoona
😢😢 Akugulisa ufulu wawo ndi R6
koma Bon kalindo musanene kut opposition ndiopoila mesa munapangisa ndinu ku mcp ilowe boma lero mukukanika kuyichosa boma kupanga blame opposition
Kuno ku mchinji 😢dzulo amagawa soya pieces ndi sopo kwa omwe Ali ndi kovotera k
Tsopano mukuuza ndani poti bomali munalika ndinu mulira nalo musatinyansepo apa
Popemphera omwewo ndi amene akuchita zoipa
Ntchito yamukulila bon kalindo paja ndi chitsiru chosaphunzira saziwa kena kalikonse
Ulenje umasimba wako😅
Aaaa PAC anadya zambili ku mcp awa ndi galu KWABASI NDI MCP YAKOYO MACHINE OTSALOLA MAYI UYU NDI NDIFITI.KATI MALEMU BAMBO AKE JOHN TEMBO AKAKAMILA CHANI NDI NKHONDO IYI 2025
The DC. Bwanji. tonse. Otsutsa. Utm dpp. afford. UDF. Tisankhe. azitsogoleri. anthu. Oyendetsa. ma vote. Chifukwatu. MCP. Sichipani. Koma mbavaaa. Zonkhankha. Ndie. Bwanji. Tipange. Azanthu. Kut. Sisankhe. mutsogoleri wanthu wachilungamo. Tiwone. Iwowo. Kut. azawavotela ndani. Zipani zonse. Zotsutsa. Pangani ngwilizano. Musankha. Musankha oti atiyimilire. Munyengo imeyi owowo azapanga zawo
Koma kungowina chipani china anthu ambiri adzapeza ntchito mmboma mmabugwe komanso mma company osiyasiyana tizasese ku cleaner from judicial executive ndi ma government bodies onse kwadzadaz mbava zosakonda dziko lawo mulungu amaulula zinsinsi zobika mwanjira yake mmalawi mu a muli anthu oipa amabisala mmbuyomonsemu koma pano awoneketa Babylon akugwa basi
Xmesa alempkheleka