Ngati mkudziwa bwanji otsauza dziko chilungamo busy fighting with manganya we know that this is politic everyone is fighting for the chair. This is jealous. Instead of loving one another
Be quiet is a good idea, you are educated Usi. Don't worry God is watching you and your leadership don't fight with a fools. Always people judge the book by its cover but thy don't know what is inside. You are a hero. Some of them are stepping stone s.
I used to think this guy is smart upstairs, koma ai ndithu...little did I know kuti he is wise in his own eyes. akuti sanakamuone S.G wake because he was right. Galu ameneyu asatipusitse akufuna kundiuza kuti atamangidwa nkazi wake kapena mwana wake sangapite kukamuona chifukwa cha zoduka mutu akunenazi. Uyudi ndi ka madrama eti. Ma self enriching okhaokha awa...same same ndi nzake Chakwela. Empty heads just hurting and reaping off the poor Malawians. Zimatiwawawa tikamadulidwa misonkho knowing kuti opindula ndi anthu amitu yowuma yosamva chuma ngati ya Manganyayi. Zitsiru.
Akunama ameneyo anauzidwa kt akhare chete anauzidwa kt apatsidwa iu vice president wa dziko Amapanga btray Chilima ndi ameneyo ku MCP ndi nzake Chakwera
Usi alii wisdom, enene akudana ndi usi ndi ma cadets,, Joabu musamunamizire kuti anakwiya, Kwa amene tikumudziwa Joab face complexion yake akamafusa mafuso samaseka AI kodi abale tatiyeni tinene chilumgamo a Kaliati n angakhale president wa dziko? Kabambe within 3 months since he joined the party basi akhale president wa UTM? We are not serious, umburi and u Cadets opusa wakuchulukirani
Ambwere poyera anene chifukwa chomwe a kumundera usi nanga gongore yikukambindwayo yinachokera kut vuto anthu sakudziwa kut KU UTM KULI ENA AKUFUNA KUSOKONEZA BASI IFE KUNO TINACHIKONDA CHIPANI CHANTHU MPAKA PANI WE STILL LOVE.
Umbuli osamuopatsa mpata that's why Malawi tidzazuzika mpaka kale interview imenei ikutsekula zeru Kwa Malawi zomwe anthu andale amapanga one ku UTM palibe chifukwa choti azilimbilana udindo ngati zolinga ndi zimodzi zolinga ngati zili zimodzi mutha kusakha munthu modzi koma izizi zikusinyezelatu kuti aliyese Ali ndi zoganiza zake chipani kuti akwanilitse zofuna zake paiye yekha
Usi palibepo chomwe akudziwa iwee, akudziwa ndi Army commander Vallentino, Chakwera, Mkaka and Chimwendo ndi ena a Police ndi Army. Mungomulakwira munthu, mufunse anthu amenewo akuuzani
A vice president palibe chimene analakwa koma a malawi ufiti ndi nsanje chonsecho alibe or fundo zosinthira dziko, zitsiru zi achina ntanyiwa zikusokeresa anthu, ndi ma uthenga Onama komanso kunyoza umbuli upose apa?? Kumupasa mwayi ntanyiwa angaliyendese dziko, manganya ali ndi nzeru kuposa wina aliyense ku UTM, chakwera sakuyendesa bwino dziko yes koma kutukwana kungathandize, tonse ndife amalawi dziko sikuti ndi la ntanyiwa or bakili muluzi TV
That's mudzalila mpaka kale usi akuposa chakwera akuposa peter akuposa kaliyati this man amagwilitsa tchito zeru , let me tell you coz if zolinga zili zimodzi akulimbana chifukwa chani kulimbanako ndekuti wina aliyese alindi zolinga zake paiye yekha that's why akulimbana usi akuyakhula mau amene andale amaopa
Dpp Woye !!!!!🌽🌽🌽 Hit a like 2025 muzikakangana kunja and Mcp out nonsence and a usi zikuonekelatu kuti chilima mudamukonza lero musakhale ngati abwino utm yakhala liti okudya zake alibe milandu izi ndi zabodza UTM idapangidwa usi kulibe 🎉🎉🎉🎉
Makambidwe amunthu pena amalungama,km cilungamo za cimene iye Ali amaudziwa yekha ndi Mulungu wake,km tiyeni tikhale cete mbali zawo tiziwona mtsogolobmuno
Nkachitsiru aka ka Michael Usi,kanamugulitsa Chilima pano kakuona ngati kakudyelera,samapanga zinthu zosonyeza kuti ndi wa UTM even Chilima ali moyo,pano amumangitsa Mayi Kaliyati chifukwa akuona kuti ndi amene atsalako ndi mphavu ku UTM,
Though I'm just listening to it recently, I salute bwana Usi for his transparency and wishing him good in all areas
UTM current leaders are power hungry. Right Hon. is the right person to unite the party.
Mtirakuwili uyu serious wallah akuluwa akuziwapo zayifa yachilima chifukwa salibuys kuziwa kuti ndege lnagwabwanji nanga black box yilikuti
@@JamesAhmed-w9p musalowelere zinthu zoti simukuziziwa, black box mumafuna kuti abweretse komwe inu mukukhala amalawi why this kind of life, manganya wafotokoza mosabisa zifukwa zonse zimene zikumupangisa kuti iye ssakhale busy kwambiri ndi UTM, nkhani ndi ufiti umene mukuchita inu amalawi, musalowelere nzeru za zitsiru izi achina ntanyiwa ndi bakili muluzi TV muvutika amalawi, ufulu samamenya choncho tsatirani ndondomeko za John chilembwe ndi chakufwa chihana, kodi anthuwa akanakhala ndi nzeru zanuzo akanalitenga dziko kukhalira kutukwana chakwera azawina muzathawa mumalawi chifukwa mulibe nzeru, ntanyiwa ali ndi mfundo yanji yothandiza kusintha zinthu mu malawi, kutukwana kungabwerese chakudya zazi, mukutipangisa manyazi inu amalawi
It's not like that uyuyu nde ndimunthu wabwino hvy wachilungo woopa Mulungu.
Uuiiiiiiiuuoiiuioo7777uuu77u7ju7ouoooioooooooohuuu7ooipipipipiioipipuuouoopupooououuu7uuuoouoooouuuuiuioioouioui
Inu mkudziwa kuti ndege inagwa bwanji?
Ngati mkudziwa bwanji otsauza dziko chilungamo busy fighting with manganya we know that this is politic everyone is fighting for the chair. This is jealous. Instead of loving one another
Mmmmmm koma dziko lino anthu ndi oipa.😢 I can't
believe kuti he experienced all this.
Be quiet is a good idea, you are educated Usi. Don't worry God is watching you and your leadership don't fight with a fools. Always people judge the book by its cover but thy don't know what is inside. You are a hero. Some of them are stepping stone s.
Dr Michael usi
Am one ofthem to vote mr manganya
Long live Michael Usi! Salute!
Chilungamo ndichowawa kunkhala leaders sintchito yakufuna kwa wathufe ai koma mulungu bax tikutsatani bwana akabwela wenawo tidzatsataso ishaAllAh
Ndikuona KUTI Michael usi ndimunthu wazeru osat zongolubwalubwa ngati enawa, usi my vote
Kwabasi and ku UTM wachilungamo ndi uyuyu
very true
I love DR Micheal Usi,,, ndi munthu wamzeru zinazi zikungolubwa pa social media
That's why I like this guy, my vote to you Mr VP
My vote🎉🎉🎉🎉🎉
Koma usi mmmm your blessed man from God
Even Joab was angry with him, his facial expression was showing he knew manganya was lying
Bodza limenelo
Manganya my vote
hahahaha manganya ndi legend,anthu akupanga chibwanadi awa.i love the interview
Inenso uyuyu ndi big brain si zinazo.
Munthu yu ndi Dolo kwambiri ma guy
Usi woyeeeeeeeeeeee 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Great Usi
Chilungamo chimawawa koma this is very true
Okhawo odana ndi chilungamo izizi aziwona ngati mkuluyu akunama komano usi muli zeru komaso upangiri wa bwino
True
I Love Joab's facial expression too...he knows akunama
God bless you vp
I used to think this guy is smart upstairs, koma ai ndithu...little did I know kuti he is wise in his own eyes. akuti sanakamuone S.G wake because he was right. Galu ameneyu asatipusitse akufuna kundiuza kuti atamangidwa nkazi wake kapena mwana wake sangapite kukamuona chifukwa cha zoduka mutu akunenazi. Uyudi ndi ka madrama eti. Ma self enriching okhaokha awa...same same ndi nzake Chakwela. Empty heads just hurting and reaping off the poor Malawians. Zimatiwawawa tikamadulidwa misonkho knowing kuti opindula ndi anthu amitu yowuma yosamva chuma ngati ya Manganyayi. Zitsiru.
Inuyo mukukwanitsa kuyendetsa banja lanu bwino bwino?
Pena umbuli osamaupatsa mpata chomwe akutathauza ndi udindo omwe Ali nao malamulo adziko Lina samalola zimenezo koma iyeyo payekha akanatha koma sakanatha chifukwa Cha udindo ndichifukwa anapeleka chitsazo chachilima kuti bwanji sanapite ? Zomwe zikutathauza kuti security yomwe amayenda naye imamulo zina pomwe Zina ayi
A Usi mukuyankha monveka bwino , mukuyeneradi pa utsogoleri .
Seriously how can one just from no where to come say he's standing for the UTM presidency seriously???
My vote
Proud for you Mr vice president
We love you Mr vice president
A Vp you are honest.GOD BLESS
Amen! Uyuyu ndi munthu wabwino kwambili
Ndipo ndixoona
Wa Mcp uyu asatinamize😢
Utm was saulos way of elevating himself. There was no utm agenda. There was ego and personal agenda. Utm was a vesel to achieve his own business
Long live
Eish this man is a good man
Kwambili amwene zinazo ndi mbava zoipa ku UTM
Small man we no need you. In our party
The problem is Michael usi is worth side MCP and utm
Akunama ameneyo anauzidwa kt akhare chete anauzidwa kt apatsidwa iu vice president wa dziko
Amapanga btray Chilima ndi ameneyo ku MCP ndi nzake Chakwera
Manganya wooooyeeeeee!
Manganya ingonena unali busy kuimbilana ma fon nda pule kuti dzatheka basi mpando ndi wako wautenga deal done full stop👺
Iyu ndiwachamba kuyakha kwa ukhuluku ndimaona ngat nsiwazeru koma ndamusika
Mthirakuwiri iwe bodza waphtsa Chilima ndiwe kuulura za kuthetsa mgwiridzano ndi MCP
I trust you vp Dr usi
Just resign we don't need yoy
And some of us need him
Can you tell us the facts why he should to resign?
VIP akunena zoona apart from usi kulimbe amene sangakwanitse kuyendetsa dziko kumeneko muzaziona izi muyerekeze kukasankha munthu wina.
Usi alii wisdom, enene akudana ndi usi ndi ma cadets,, Joabu musamunamizire kuti anakwiya, Kwa amene tikumudziwa Joab face complexion yake akamafusa mafuso samaseka AI kodi abale tatiyeni tinene chilumgamo a Kaliati n angakhale president wa dziko?
Kabambe within 3 months since he joined the party basi akhale president wa UTM? We are not serious, umburi and u Cadets opusa wakuchulukirani
Kuyankhula kwanzerutuh uk boss, anthu umburii udawakuliraa eeish ku church kuja nkofunikiraa 😂😂😂
Akhala tu Kodi...
Fact
UTM ikanavomeleza usi as their leader nkanavotera
Chonama chitsiru ichi a mcp kubwera kuzadya ndiye iweyo usi gwirizano ulipo na mcp ndiyetu ana akusiya ku mcp kwakooo
Ndale ndichithu chosavetsetse amati uli dele kulinga utayenda naye usi kukhala kumeneko zimuthandiza kuti adziwe udindo wa vp umayenda motani coz zomwe anthu amaona alikunja sizimene amaona Ali nkati usi ndi munthu wazelu kwamene anapitako kusukulu achivetsa one ndale zimayika munthu pachiopsezo ndiye ngati azakeyo akutsutsana naye ayitanitse zodiak si zao watanitsa
Ambwere poyera anene chifukwa chomwe a kumundera usi nanga gongore yikukambindwayo yinachokera kut vuto anthu sakudziwa kut KU UTM KULI ENA AKUFUNA KUSOKONEZA BASI IFE KUNO TINACHIKONDA CHIPANI CHANTHU MPAKA PANI WE STILL LOVE.
iwe chisilu manganya zomwe ukuyankhula ngati mwana zaziii ie
Umbuli osamuopatsa mpata that's why Malawi tidzazuzika mpaka kale interview imenei ikutsekula zeru Kwa Malawi zomwe anthu andale amapanga one ku UTM palibe chifukwa choti azilimbilana udindo ngati zolinga ndi zimodzi zolinga ngati zili zimodzi mutha kusakha munthu modzi koma izizi zikusinyezelatu kuti aliyese Ali ndi zoganiza zake chipani kuti akwanilitse zofuna zake paiye yekha
I like his honest
Mr usi uxani anthuu zoona mukuziwapo kanthu za ifaa ya mzanuu koma remember GOD is watching u
Usi palibepo chomwe akudziwa iwee, akudziwa ndi Army commander Vallentino, Chakwera, Mkaka and Chimwendo ndi ena a Police ndi Army. Mungomulakwira munthu, mufunse anthu amenewo akuuzani
iwe ndi mbuli kwabasi
Inu a Zodiac mubisiranji maina akutchula USI wo? Si bhoo we need transparency
good Papa akulamulira anthu angapo
Pakali pano ndinu mtsogoleri wa UTM ndipo lipirani kumvesion kuti mukapambane ndikupitiliza utsogoleri wake mukawina.
Galu iwe manganya bwanji sufunsa kalikonse za ifa ya chilima unatenga nawo gawo usanamize amalawi
Kkkk ah he's very cruel
It's only God who knows
Bola malawi imazowa pazimene unapanha ndichakwera won't worry uzion 2025
Zapamwba uso🎉
A vice president palibe chimene analakwa koma a malawi ufiti ndi nsanje chonsecho alibe or fundo zosinthira dziko, zitsiru zi achina ntanyiwa zikusokeresa anthu, ndi ma uthenga Onama komanso kunyoza umbuli upose apa?? Kumupasa mwayi ntanyiwa angaliyendese dziko, manganya ali ndi nzeru kuposa wina aliyense ku UTM, chakwera sakuyendesa bwino dziko yes koma kutukwana kungathandize, tonse ndife amalawi dziko sikuti ndi la ntanyiwa or bakili muluzi TV
Palibe iliyose
Usi ndi mtira kuwiri kosonyeza kusoweka utsogoleri mwa iye sure awa koma MA drama basi iyaah
That's mudzalila mpaka kale usi akuposa chakwera akuposa peter akuposa kaliyati this man amagwilitsa tchito zeru , let me tell you coz if zolinga zili zimodzi akulimbana chifukwa chani kulimbanako ndekuti wina aliyese alindi zolinga zake paiye yekha that's why akulimbana usi akuyakhula mau amene andale amaopa
Usi ankhoza kumaliza Malawi yese anthu osadziwa chikuchitika usi ndikatundu
Joab inu ndi dolo paka kuwaliza amanga shee respect ulendo uno sadathawe ndi mawu
Mulungu akukhululukire
Amukhululukire walakwa chani?
matumbo mpaka hahaha,this guy is a genius
from the day our SKC was killed I saw this as a traitor
Iweyo manganya utava pa masamba achezo unafusa ndani? Komaso ............. Mmm mafuso ndi ambiri
Ndiwe galu kwabasi ukusangalala kufa kwa chilima uziwona sungamake utm sikukufunaso
Abambo asikono ndinu azibwana please don't sale utm to chakwera start on your on party
Uyu ndimuthu waboza wapapeza potulukila he is not in utm
Believing in hearses
Manganya munthu oyipa kwambiri amatenga a Malawi kupusa panyini pameke
Iweso pamako
@Kulinji Mwana wa nfiti iwe usandinyase mbolo yosadulayo
@felixjoseph8161 wukanakhala pafupi nkanakuone koma akapolo ndiamene amalimbana ndi anthu oti salimbana nawe,, iweso pako
Akuti matumbo awo amawatembenukira koma sangawanyanyale kuwasunga
Dpp Woye !!!!!🌽🌽🌽 Hit a like 2025 muzikakangana kunja and Mcp out nonsence and a usi zikuonekelatu kuti chilima mudamukonza lero musakhale ngati abwino utm yakhala liti okudya zake alibe milandu izi ndi zabodza UTM idapangidwa usi kulibe 🎉🎉🎉🎉
Makambidwe amunthu pena amalungama,km cilungamo za cimene iye Ali amaudziwa yekha ndi Mulungu wake,km tiyeni tikhale cete mbali zawo tiziwona mtsogolobmuno
Usi ndi munnthu oganiza bho osati zomangolubwalubwa zilizonse
Ku court oko tsiku limodzi manganya,ndege yagwa kuli zii olo kunenako kathu assss
Kwamene akumudziwa chilima anali wazeru zomwe akuyakhula usi kuti Zina amamuletsa zikhoza kukhala zoona chilima samafuna khondo zake wina alowe chifukwa amadziwa kuti apanga hundle okha kuyakha zandenge moyo wake unali pachiopsezo let me tell you chokhacho achilima kutenga usi kukhala wachiwili wao zinabweletsa khondo chifukwa kumene kunja kunali akaliyati anachoka nao ku dpp ndiye usi anangobwela from no way or utakhala iwe ungave bwanji kuti achina kaliyati anachiva motani pamenepo mpamene mungadziwe kuti usi analidi pa khondo coz sionse amene angachilole chinganizo chomwe bwana chilima anapanga
Yudasi skaliyot ameneyo manganya wachiwiri kwasatana wankulu chakwera
Mzimu wa Chilima uzalira ngati Kabambe otumidwa ndi Peter angakhale president wa UTM.
GOD should forgive you😢😢
Akut anali a kuchokera kokawaimilira a chilima ku maliro a laugh kasambara?? Mensa iwowo amapita kumaliro komweko
Uyu ndiwaboza amazitenga ngati dolo koma ndikape bwanji ngati amamukonda CHILIMA bwanji sanayankhulepo chilichonse chokhuza chilima
Chilichose sakuchidziwa chomwe nec ya utm yakambirana. Nde amakhala alikuti? Uyuu aaaa sadziwa chomwe akupanaga...
Muyakhulatu ngati mbuli iwe sunaoneko anthu akakhala kuti sakufuna amapanga zaseli banja anthu mukukhalila limodzi koma bambo kumadya kadyenya moyenda iwe uganiza kuti nkazi amakhala Alikuti ?
Mutayen sakuziwa kanthu@@LastonBezeni
Kudedwa kwamunthu sizachilendo koma anthu amakuonani ngati ndinu anthela kuwili kuyambila asanamwalile chilima
Manganya ndimfiti lwe aaa zaifa tachilima ukudziwapo kanthu
Usi galu iwe ukuwona ngati iweyo ndiye ungakwanise kuyendesa UTM munthu woyipa iwe
Alankhule zomwe alankhulezo koma sitizamukhulupirilapo never ever 4ever tizamukhumbukila zamadrama zokhazo basi
What ever is saying doesn't build the party but to break it
Uyu akundivekera boza ine sinamuonepo akuvaka makaka a UTM mumisokhanao waboza😅
Angela kaliati Godpapa awononga chipani
Ndiye iwe ngati mtsogoleri, zakukanikatu chifukwa akusogolera ndi ena siiwe
😮😮😮 uyu sitikumukhulupilira uyu
This man has really changed 😂
Nkachitsiru aka ka Michael Usi,kanamugulitsa Chilima pano kakuona ngati kakudyelera,samapanga zinthu zosonyeza kuti ndi wa UTM even Chilima ali moyo,pano amumangitsa Mayi Kaliyati chifukwa akuona kuti ndi amene atsalako ndi mphavu ku UTM,
Iwe unali Running mate not vice present wa UTM
@@MosesKaselema Running late amakhala vicepresident
Manganya za madilama Akowo ai ndi chipani Cha UTM iwe ndi mnthira kuwiri wachabe chabe ,wa utsiru
Zoona anthu ochuluka munthu wachilungamo amadana naye, ndilo dziko lapansi.
Uyu ndi thila kuwiri, uyu ndi yudasi sikailiyoti
Chilima amafuna kuchoka mungilizano ndiye bwanji osachokamo mu mcp ausi kweni mukufuna mutiuze chiyani
Koma akuluakulu tiyeni tizimphela nthawi yatha
Chilima adadzipha, ngati ndi zoona zomwe kumvekazi za godpapa. Kaliati, angella ndi enawo ndi zida zomwe wagwiritsa ntchito kuchotsa moyowakeomwe.
Kikumba dzenje kugweramonso yekha. Anthuena mkumamtchula saint
godpapa ndi chani?
Koma manganya munthuyo ndi waboza lopanda nalo manyazi uyo ndi wachipani Cha chikangawa party MCP