Kodi Jane Ansa,analibe calmness? Chakhaza yenweyu sanamupatse mafunso okwima? Nanga kuyankha kumanveka kovuta? Koma zisankho sizinasokonezedwe? Wake up from your slumber!
MEC ikulemba qualified Malawians. John Tembo was a Malawian and children are also Malawians hence fit to be employed by any organisation. Mtalimanja being a Malawian, she is able to be a MEC chair if her qualifications allow her.
Zodabwitsa m' mene akufotokozela mayiyu. Akuti MEC inachita approach makampani ogulitsa machine a chisankho. I thought they were supposed to advertise so tha the interested suppliers could apply. To me the basis of approaching the supplier looks questionable.
For those who believe that our God is the God of war let's gather and cry to Him for He hears our players and He is going to choose a good leader for us let's leave avery thing to Him for He is not corrupt
Why can't MEC have the special and deliberate effort going to the remotest to find out if NRB registration is going on. The other thing Anabel should take note of is the distance from the remotest area to the DC office
Si onse aku central or Blantyre even mzuzu amene angavotere mcp, Dpp, utm& etc aliyense Ali ndi ufulu wakavotebwe nde what ever God will choose a good reader
Of course technology ikupita pasogolo komano tidziwe kuti Pali anthu ena ochuluka akumidzi mpaka pano sakudziwa kuti data ndi chani, an example. Nde izi za smartmatic zi ife sitikuzifuna chifukwa sitikukamvesa kanthu kameneka tizawerenge ya manual basi
Mayi ameneyi ngati sachita bwino pazisankho zimenezi azaotchesa ziko lino Hule limeneli must very care because we are watching what is going on behind closed door
Mai inu ndi abodza pitani ku Blantyre cha kumpembako anthu mpaka pano ma id sadalandilebe adakajambulitsa 5 months ago koma till now akowawuza kuti sizidatuluke
This lady so called Annabel Mtalimanja is not bigger than Malawi. Besides, she's not the only Malawian with a good qualification and credibility to manage the elections. She should pave way for others who can be trusted my all Malawians. This is for the Nation and NOT for the party as one might take it.
Joab u are the best junalist ,ukufusa mafuso ngati munthu ophuzira pa ntchito yako ,u don't take things personal,koma awa a Brian banda aku times zikukhala ngati akumwa mowa kwambiri
it could be the same professional but what the personality in the profession are different so I don't think your take is right rightly said your being personal and your a liar Brian is good just as joab is stop being picky
Awa akufuna kusokoneza dziko,kwina mwana wasowa ndiye wina akuti ndimadutsa ndamva khanda likulira nyumba mwa awa chosecho alibe mwana akukayikirani kuti ndinu ndiye kutsimikizira kuti si inu tilowe tisake inu mukukaniza muganiza kuti anthu ati chani za inu ?ma plan anu sakusiyana ndi zakugwa kwa ndege ku chikangawa mwachulutsa zobisa ndi ndale zothawathawa chilungamo.
With bad reputation munthu salembedwa ntchito why still going ahead with bad reputable company ngati imeneyi? This could have been avoided even choosing from the start.
U West Ur time for this electronics igwira mtchito yake opanda olesa umbuli ndiwumene umapangisa kubera maboti ngati mmene anabera Peter Ndi joice nanda
Ife, if chakwera insists to use iweyo ndi machine akowo, it'll be Israel and parestinians war, yomwe atazaithese ndi wamoyo Yesu basi. Iweyo anabwlo nkhondo umazidziwa kakamila kukhala ndi machine akubawo, uzapita kwa mako Ku Botswana usakufuna. Amen
Kd chakhaza mutumo zimayenda? Muthu wanna KT center iliyose akutulutsa nambala ya amene alembetda ndiye pamapeto adzatuiutsa pingera sum of all center's registered. Akayikiraso motani poti ma morniter nambala alinawo.
I think our members of Parliament anapanga lamulo lovuta zedi poyang'anira kupelewedwa kwa ndalama mdziko muno , taonani azathu omwe Ali ndi ndalama zambiri monga SA mgwirizano wa zipani umayamba after voting yemwe wayandikira ndi amene amatsogolera kuyendetsa boma
MEC , nrb zonse ndi za mcp ,bwanji nrb sinayambe kulemba before kalembela wa chisankho, imikani kalembela wa chisankho cholinga nrb nrb ilembe Kaye Anthu .and kwao kwa mcp nrb inalemba Anthu ochuluka kwambiri including under 18 years old.
This very clear, wosamva apapa ndiye nkhutukumve. Good questions and good answers from a very calm Lady. We hope for the best with few or no madando
Kodi Jane Ansa,analibe calmness? Chakhaza yenweyu sanamupatse mafunso okwima? Nanga kuyankha kumanveka kovuta? Koma zisankho sizinasokonezedwe? Wake up from your slumber!
This far I have liked this woman.keep it up
I salute you Joab your line of questioning proves you are so conversant with the PPDA Act and its Memos on sourcing suppliers
History is the best teacher big up bakili muluzi tv
Very good exprenation with wisdom thanks very much a mtalimanja
Most intelligent woman well composed cool and corrective.God bless her 39:07
Well stated, Anna.
MEC ikulemba qualified Malawians. John Tembo was a Malawian and children are also Malawians hence fit to be employed by any organisation. Mtalimanja being a Malawian, she is able to be a MEC chair if her qualifications allow her.
Loud and clear
God help us to choose good leader we need powerful prayer and fasting
There are no good ones from the list
Very true! This is spritual event
Good questions and good answers
History is best teacher Guys
Zodabwitsa m' mene akufotokozela mayiyu.
Akuti MEC inachita approach makampani ogulitsa machine a chisankho. I thought they were supposed to advertise so tha the interested suppliers could apply.
To me the basis of approaching the supplier looks questionable.
Keep going mama
Well explained mama, God bless you
This is true
For those who believe that our God is the God of war let's gather and cry to Him for He hears our players and He is going to choose a good leader for us let's leave avery thing to Him for He is not corrupt
Indeed you must go
Indeed history is a good teacher
Anabel nzimayi wachilungamo ndipo Mec yaulendo uno ndiyodziwa ntchito yao..owina adzawine oluza adzaluza kulibe kuti wina azidzati ma vote abeledwa ai.
Why can't MEC have the special and deliberate effort going to the remotest to find out if NRB registration is going on. The other thing Anabel should take note of is the distance from the remotest area to the DC office
Akuyankha ngt cha dzeru,tikuonera ndithu, congratulations Mr Joab
Nde machiniotu achitidwe Audit before the elections to make sure there's no numbers in the system komanso after.
Very well elaborative. The Chair is very collected and she is saying the truth.
Mmm only lies to us always. We ar watching u Anabel
This Chair is very interigent, cool calm and collective
Respect Joab 🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Guys what I can see the best is that rather hire from other countries so that everyone must have peace of mind
Nice guestion Frank
Si onse aku central or Blantyre even mzuzu amene angavotere mcp, Dpp, utm& etc aliyense Ali ndi ufulu wakavotebwe nde what ever God will choose a good reader
Mai mwafusidwa kuti o😢susa atenge anthu awo oziwa za machini pamenepo simunayankhe zolongosoka mupweteka ambili zomwe mukufuna
Akuti sangachite kuti azawonese zakuchipinda kwawo pomwe.
Be transparent, zikhalebe pambalambanda koma
Jowab❤💯 ndimakina i like mafutso akufutsidwawo mbalameyo ikuzemba😅
Mmmmmm sizikumveka. Opita ku court pitani basi
History is the best teacher tionesana 2025 agalu inu
Mai muzitenge bwin coz chisankho ichi chili nd zovuta kwambiri simukumva madandaulo a otsusa boma
Yes mafunso abwino kwambiri ndipo ayambireso kuitanitsa machine ena nkhondo iyi
Of course technology ikupita pasogolo komano tidziwe kuti Pali anthu ena ochuluka akumidzi mpaka pano sakudziwa kuti data ndi chani, an example. Nde izi za smartmatic zi ife sitikuzifuna chifukwa sitikukamvesa kanthu kameneka tizawerenge ya manual basi
Kungoyerekeza kubera wina tizakwirira WA Moyo ndithu😢
😂😂😂
Naweso tizakukwilila wamoyo chifukwa nafeso tilipo womuteteza mayi yo
@@GeshoMwakitwilebasitu mukozekele kuyikidwa nonse amoyo nonsenu sikuti ife tisekelela kuti tivutikeso 2025 never
😂😂😂😂😂
Chilungamo chake bro otse tizakwilila amoyo @@AlihIbrahim-s7v
Mayi ameneyi ngati sachita bwino pazisankho zimenezi azaotchesa ziko lino Hule limeneli must very care because we are watching what is going on behind closed door
Joab, amwene inuyo you deserve,mukufunsa mafunso abwino.
This guy is brilliant
She knows something about that.....
Mmayi wadyera ,, ukufuna kutipwetekesa amaliwi ndi chi company chakubacho
Please we don't need smartmatic and Anabelle you should step down
Kodi mesa athu akudzavota ndi omwe akulembetsawo,,,APA zikuonetseratu kuti pali mabvuto apapo security for what? Mavoti athuwo???
Ndye akutenga company yot akudziwa kut ayendesa mmaiko enawo km mpaka nkhan zili ku court yelekezani muzabele muone
APA palakwika apakonze
Mai inu ndi abodza pitani ku Blantyre cha kumpembako anthu mpaka pano ma id sadalandilebe adakajambulitsa 5 months ago koma till now akowawuza kuti sizidatuluke
This lady so called Annabel Mtalimanja is not bigger than Malawi. Besides, she's not the only Malawian with a good qualification and credibility to manage the elections. She should pave way for others who can be trusted my all Malawians. This is for the Nation and NOT for the party as one might take it.
Koma mai iwe😊😊😊😊 nditukwana kwinakooooo..!
Joab u are the best junalist ,ukufusa mafuso ngati munthu ophuzira pa ntchito yako ,u don't take things personal,koma awa a Brian banda aku times zikukhala ngati akumwa mowa kwambiri
it could be the same professional but what the personality in the profession are different so I don't think your take is right
rightly said your being personal and your a liar Brian is good just as joab is
stop being picky
Personal heartiledge nothing else
Brian ndiye munamuda vuto ndi chani
Ndipo ablian Banda aaaa
I dont trust this lady the way she explained why akukana kupanga zomwe amalawi akufuna uyu with no doubt ndiwa kokoliko she must goooooooo
Uyu paja radio yake iri mu nkhwapa mwa boma who don't know that
Awa akufuna kusokoneza dziko,kwina mwana wasowa ndiye wina akuti ndimadutsa ndamva khanda likulira nyumba mwa awa chosecho alibe mwana akukayikirani kuti ndinu ndiye kutsimikizira kuti si inu tilowe tisake inu mukukaniza muganiza kuti anthu ati chani za inu ?ma plan anu sakusiyana ndi zakugwa kwa ndege ku chikangawa mwachulutsa zobisa ndi ndale zothawathawa chilungamo.
❤❤❤❤❤❤
Machine amenewa nd obera mavote kd chakwera kt apeze mavote anagwilisa cito nd njira imeneyi walandira ndlama zambili mai ameneyu
Come on ! That's the problem with universal principles. Enafe tinkafuna Ulamuliro wamuzigawo but you couldn't listen .
Awa akunama ,safunika ife takhalapo pa zimenezo, asiye taziwa maganizo so.
Mayi ma voti tipange chonchi a chakwera ndi amuthalika akaime kutsogolo Ife tizikaima kumbuyo kwawo owina aziziwika pompo pompo
Smart matric ndikapani yobela zisako mavoti amaenela kuwelengedwa manyo ose Ali ku mec nga mcp ndipo oseo cholinga Chao nchimozi kubela chisakho koma ziwani Malawi mukumuika pamoto chifukwa iyo ndikhondo mavoti anji okhazikisa khoti yapedela yoyendesa zisakho zakutumbo Basi zimenezo zitsiike ukunama Mai iwe
Joab umatha
With bad reputation munthu salembedwa ntchito why still going ahead with bad reputable company ngati imeneyi? This could have been avoided even choosing from the start.
Koma ndiku ziwa kuti ana panga kare vote kufuna kunamiza athu tikufuna manual ife
Integrity ya mayiwa kuti ikhale mbambande asangwiritse chija akutcha Smartmatic machine
Mayankhowo akunveka potsatila malamulo,koma kuseliko ndikumene kuukhale kupinda malamulowo kuti zikomele win winawake. Komanso zinthu zinazo sizikunvekabwino konse ayi.
Koma mzimayi iweyo mmmmm palibepo cha nzeru chomwe ukunena smartmatic sitikuyifuna tizawerenga manual
U West Ur time for this electronics igwira mtchito yake opanda olesa umbuli ndiwumene umapangisa kubera maboti ngati mmene anabera Peter Ndi joice nanda
Abera peter kuhwesa joice Banda munamuyuza past chilima
Mai awa zimene akulongotsola kumbali ya ineyo sindikuwavesesa ai
Mesa anthu akufuna zinthu zichitike poyera bwanji akukana auditing
Uyo akunama ameneyo.... And wapezeka pamenepo
Udindo wathu ndikufuna kudziwa zilimkati mw machine basi 51:24
Konseko ukunenako anabera zisankho a smarmatic ukunenawo
Inu dzina lokha latchulikatu kut ndi wantali manja tanthauzo okuba kapena kut wosolora awa ayi zawabvata ife tikufuna manual system
Mukuziwa kt company sinagwire ntchito bwino bwanji mwaitenga Kuno kwathu
Uyu achoke ndi system yakeyoooo ife tikufuna manual 🎉🎉🎉
Momwe timapangila mbuyomu smart matic ndi kapani yosokoneza gayz
0aa
Mukhaula sakuchoka uyu
Why MEC before they introduce or before they buy this machine all parties didn't informed especially opposition parties????
Ineyo ndikufuna chisankho chizayende ngat chapita chija awa akutinamiza apapa
She deserve the position
Mama muli pachiophyezo Jeni Ansa anathawa mdziko muno likondeni dziko lanu
Pa nkhani yoti anayeserera ndiimene yandikayikisa, zoyeselerazo mwina azisunga mmakinamo, mmmmm kuli bwino njira yakale yovotera.
Ife, if chakwera insists to use iweyo ndi machine akowo, it'll be Israel and parestinians war, yomwe atazaithese ndi wamoyo Yesu basi. Iweyo anabwlo nkhondo umazidziwa kakamila kukhala ndi machine akubawo, uzapita kwa mako Ku Botswana usakufuna. Amen
Ku Mozambique akuthibulanatu kamba ka smartmatic yomwei ndiye inu mukukakamila yomwei bwanji
Agaluamenewa akuikamalawi pamoto mbamvazimenezi
Jowab iweo ndi dada respect on u
Pa security po ndipo palinkhani. Chimene sakufunila ena adziwe nchiani?
Kd mulikunja kwadziko lino mungotukwana zauchitsilu bas fwetseke
Kd chakhaza mutumo zimayenda? Muthu wanna KT center iliyose akutulutsa nambala ya amene alembetda ndiye pamapeto adzatuiutsa pingera sum of all center's registered. Akayikiraso motani poti ma morniter nambala alinawo.
EMTs yobera masankho. Iwe ufe basi.
Ife mawa pansewu cheteeeee.Kunai amzanu mayi lelo kulibe.
We don't need that machine finish story
Zilipo zikuchitika pa zokozekela za chisankho ichichi
I think our members of Parliament anapanga lamulo lovuta zedi poyang'anira kupelewedwa kwa ndalama mdziko muno , taonani azathu omwe Ali ndi ndalama zambiri monga SA mgwirizano wa zipani umayamba after voting yemwe wayandikira ndi amene amatsogolera kuyendetsa boma
Koma akuyesetsa kunena chulungamo koma wandare ndiwandare basi sasowa chonena
Mai uyu akunama pazose zimene akuyakhulazi and there is already communication with boma l beg you joab continue ask her she will tell us truth.
MEC ikufunika reform before its too late ndani angakondere kuona bambo ako akulephera pomwe mwana wawo ali oyendetsa mpikisano
Machine akhala bwanji ndi security it means kuti iwe uhule utha kuyitembenuza kuti ambuye Ako awine hule nyani iwe
😂
Aaaaaaa mbava iyi Ife sitingalole apo biiiiiii ndikulowa nthengo muyaka Moto muno ndikuti osatiputa dala Ife tili chelu tikutikitani mademo akuyamba owophya kwambili
Inutu kaloweni mthengomo ifeso tikukudikirani omuteteza mai Yu and we are ready for any attach
Moti muli ndi mphanvu kwabasi zoteteza mbava?@@IdrissaAbdullah
@@ShabaniKuswereKape uyu
@@IdrissaAbdullahiwetu ndi wamisala kwabas pitilizani zopusazo muzawona polekera si 1964 iyi 2024 be careful
Mupindula chiani mukalowa nthengo kuno Ku Malawi kulibe chilichonse mukafa ndi njala nthengomo kufuna kusangalasa Andale zamanyazi
Why not just advertise to open companies
Kungowina president wina
All of you out
i don't trust machine mmmm atipweteka
Akanatil aziyakha mafuso osati azifotokoza zimai iwe ndiwe wakubaaaa chakocho ndichikangawayooo mukawelengela kunyumba kwanuuu ife tikufuna kuzawelengela pamanjaaaa
Simubela mukunama mayi 😅😅 nkhanga zaona.kampani yanuyi ife ayi.
MEC , nrb zonse ndi za mcp ,bwanji nrb sinayambe kulemba before kalembela wa chisankho, imikani kalembela wa chisankho cholinga nrb nrb ilembe Kaye Anthu .and kwao kwa mcp nrb inalemba Anthu ochuluka kwambiri including under 18 years old.
My Malawi
Mwana wa Jonh temboyi Satithandiza koma ukazapanga chibwana uzawona nyekhwe
Aseh kuseli kandalama akupasazo uoneko kuli imfa kumeneko mcp ngt singakuphe imatha kukudutsitsa njira yot uphedwe so check this out
Chikangawa achoke sitikumufuna ife iya