If it's possible I get chance to there I need to continue to be a soldier working to protect Israel the promise country of God. Allow me to come there plz😂😂😂😂😂
Athu akumalawi kugona mumango kokoloka ndi zithu zopanda Pake Akunkuyu tu Ali ndi bodza kumalawiko ngati kuti muthu.wabodza mdziko mooo nde ndikunkuyu iiiiiiiiiiiiiiiii moti ngati achakwera akudedwa ndi athu number one ndi kunkuyu moti kunvera kunkuyu ndekuti iweyo ndiwe wakufa muzimu muthu wabodza lankukhuniza kunkuyuyooooo cchikangawa part one
Malawi ndi dziko lopusa kwambiri. Monga dziko lili busy kugulisa anthu kumakagwira ntchito zakumunda ku Israel chonsecho boma likulephela ⁰ kulemba ntchito achinyamatawo....kodi mmesa boma limati liri ndi ma mega farm?.... where's one million jobs they promised? Dziko likufa ndinjala chonsecho muli busy kutumiza alimi kunja... mbuzi za atsogoleli.
Nkhani yantchito ku israel ndiyabwino koma why israel yo kubwera kumalawi ndikukhazikisa makapani kumalawi ko kuti amalawi azitukula ziko lawo. Sibwino kuti zika zamalawi zizipita kunja kukatukula mauiko ena
Ana ena Ananyamuka Kuno kukafika ku Israel ndikuwabweza ma expand kuwasiyitsa kuwanamiza kuti a pitaso mpaka pano ana akuvutika, sindikudziwa kuti anawa mukuwaganizira Chani????
Kkkkk mcp yalepheratu apa chifukwa ngati boma sizimafunikanso ma agent ,okay ndiye pamenepa ubale wa maiko awiriwa adatsayinira ndi boma kapena ma agent?
Pa program Pali Patrick kamkwatira ndi wonder iwe wa BS TV pa poster choikikila nkhope ya brain ndichani ambiri akaona nkhope imeneyo anthu akaiona ambiri satsekula video imeneyo
Kod atsongoleri awa munawayikilanji Ankukuyu udindo wakulemerani, the way you speak aaa malawi Ayaka uyu no time wasted🫵
Please the youth of Malawi must be very careful
This is modern slavery the country of Malawi is doing
Let's gather here watch in Cape
Imeneyi sinkhani yabwino imeneyi anthu akusiya zikorawo mukonse zikoranu
Anduma seems to ignore what the agent has said instead of having interest with the agent so that Malawi can continue sending people to Israel.
Watching from mzimba eswazini
MMA hotel azikachita seldomise Malawi be careful
Kod ku Israel-ko kulibe anthu oti Atha kumagwira ntchito zimenezo koma Amalawi okha 😂😂😂😂
Kupusa amalawi eish, ku Israeli kulibe anthu osauka oti azigwila zimenezo koma ku Malawi? Boma la mcp likungolemelera anthu awa mudzadzindikila patsogolo
@ChimsyUlemu anthu akupitawo sakudziwa zoti ikupindula ndi MCP, nankha ndizomwe anatilonjeza zot azizatitengera ku Israel 😅makape achabe chabe
Kodi Anyamata apita bwanji Ku Israel kuli nkhondo mabomba utsana ndi utsiku akuphulika penapaliponse, Ndeye anyamata awa adzikamenya nawo nkhondoyo mwinatu?
Ndikhale bulutu
The whole minister speaking noisence
Work force is going to lsreal
Who will develop Malawi?
No plans for government to help it's citizens shame
Agents please help achinyamata azipita ku Israel monga munkachitira muja Boma lingochedwetsa anthu
😂😂akathela ku gaza ena anathawa ndipo anagwida knkubwezeda
Nthito one million zimenezo
Boma likupezapo phindu powatumiza anthu ku Israel sichabeyi, kumkuyu ndi wabodza mukutumiza anthu ku Israel inu a boma osapanga zaulimi konkuno bwanji, mkuwalemba ntchito achinyamata kuti ndalama yathu izingozungulira mudziko mwathu momuno, kuti mwinako dziko lathu lingachite bwino kusiyana ndikulemeretsa dziko lolemera kale kusiya Malawi adzingosaukirabe
Kuizalaeli aMalawi tichenjre ukotu ndi kumido East.
Zaziii
Abwana enawo nde akunyezimilat
If it's possible I get chance to there I need to continue to be a soldier working to protect Israel the promise country of God. Allow me to come there plz😂😂😂😂😂
Gwirizano oyamba unalinopha chilima ndipo zinatheka
Wachiwiri ndiofuna kubera mavoti😊
Malawi yemwe anatitembelelayo ayi atikhululukire ndithu
Athu akumalawi kugona mumango kokoloka ndi zithu zopanda Pake Akunkuyu tu Ali ndi bodza kumalawiko ngati kuti muthu.wabodza mdziko mooo nde ndikunkuyu iiiiiiiiiiiiiiiii moti ngati achakwera akudedwa ndi athu number one ndi kunkuyu moti kunvera kunkuyu ndekuti iweyo ndiwe wakufa muzimu muthu wabodza lankukhuniza kunkuyuyooooo cchikangawa part one
Kodi mukamati m'gwilisano umenewu ndi waphindu mukutanthauza chani? Kodi phindu lake lilipati?
Kanyama akakaa ndkabodza kwambiri 😅
Kodi anthu oyambilila anapita pa mgwilizano utiyo poti pano akupanga mgwilizano kumene
ndeno Fuso ndirakut. Mafot. ndichaka chamawa. nde andu okwana 3000 akupita koma dzikuyenda bwino
Kunkuyu u can be clever to all Malawians but not on God ,u need God iweyo
Vuto ndilakuti anthu amene amagwila ku office kwa pre amafuna ndalama ma 200,000
Boma likusekeredza anthu mwai wantchito, poimitsa ma ajeti kutenga a Malawi
Malawi ndi dziko lopusa kwambiri.
Monga dziko lili busy kugulisa anthu kumakagwira ntchito zakumunda ku Israel chonsecho boma likulephela ⁰ kulemba ntchito achinyamatawo....kodi mmesa boma limati liri ndi ma mega farm?.... where's one million jobs they promised?
Dziko likufa ndinjala chonsecho muli busy kutumiza alimi kunja... mbuzi za atsogoleli.
Koma ku Israel kuli nkhondo ndie anthu akupititsidwanso komweko,zovuta kwambiri.
chinyamata kod kugwira tchito zolima kunoko mukanika bwanji
It's too much Anthu awawa need to run NGO nit government
A nkukuyu ali ndi bodza lamanya
Nkhani yantchito ku israel ndiyabwino koma why israel yo kubwera kumalawi ndikukhazikisa makapani kumalawi ko kuti amalawi azitukula ziko lawo. Sibwino kuti zika zamalawi zizipita kunja kukatukula mauiko ena
this minister is a big liar, and mostly forgets what he said already,,,mmmmmm ukawalala basi
Ana ena Ananyamuka Kuno kukafika ku Israel ndikuwabweza ma expand kuwasiyitsa kuwanamiza kuti a pitaso mpaka pano ana akuvutika, sindikudziwa kuti anawa mukuwaganizira Chani????
So sad and bad. Anthu anasiya katundu wawo
@chisonimponda363 Ndipo Zimandiwawa mwana wanga anali mgululi, tinaononga ndalama zambiri mkukawasiyisano zikwama ku Israel komko
You are damaging agriculture sector in Malawi
That's noses program to the malawias, and we don't want to continue with that program useless
Kodi ku Israel ko onse ndiolemera?????
ku john onse ndi olemera ? eni dziko ambili amafuna tchito zofewa thats why akufuna athu amayiko ena
Kod MCP ntchito 1 million zomwe amalonjeza zija ndizimenezi, ndiinu makape kwambiri
Bomali ndi manyaka
Kkkkk mcp yalepheratu apa chifukwa ngati boma sizimafunikanso ma agent ,okay ndiye pamenepa ubale wa maiko awiriwa adatsayinira ndi boma kapena ma agent?
Aaaaaaa yai mmmm
1 Million jobs in malawi 😂😂😂😂😂
Ma agent Ayambe kutumiza anthu osati a boma, alemphera
Chikangawa night business 😂😂😂😂😂😂😂😂😂 yooooo
Mafuta kulibe
Akunkuyu mukamayankhula muzidziwa kuti kulimulungu you're lie to Malawi
ndiye iweyo osagoleka osavera azako atolapo kathu
Pa program Pali Patrick kamkwatira ndi wonder iwe wa BS TV pa poster choikikila nkhope ya brain ndichani ambiri akaona nkhope imeneyo anthu akaiona ambiri satsekula video imeneyo
Very useless comment
ndipo sukunama chifukwa ameneyo ali ndi mnkwiyo wochoka ku state