Olo kodi kukokerelako angakokere bwanji.look at the gap .olo mwana atakuuza kuti aphunzitsi andibera marks ungoziwa kuti uyu akunama uyu atakhoza 10% . bola difference ikanakhala yaying'ono koma eee ma 100 plus
SKC WAS A VISIONARY NEW GENERATION ALPHA LEADER FOR MALAWI 🇲🇼 HE WAS VERY STRONG AND COURAGEOUS ❤🎉 DONT SAY HE DIDNT PLAN WELL HIS LEGACY CONTINUES THROUGH DR DALITSO KABAMBE HE WILL CARY MALAWIAN 🚩 🇲🇼
Vuto ndiloti anthu omwe anatsara ku chipan cha UTM pakuchoka kwa achilima ndi anthu okhaokha adyera. Komaso atsankho. Koma chilima mwini amadziwa kuti usi ndi amene angakhale mtsogoleli wamaso mphenya. Chinthu china achina kaliati kuluza kwawo ssanave kuwawa chifukwa amafuna kuti kabambe akamuike pa public koma iwo akudziwa kale kuti adya ndalama za kabambe kugulisa chipani
Koma muziwe kuti kukhara ndi mwayi oyankhura pa radio sizikuthanthauza kuti chilichonse chomwe mukulankhura ndi chanzeru ayi alipo konse ena anzeru koma mwayi alibe so watch your back
Kabambe samayenera kukhala president wa UTM, munthuyi ndi wa DPP. Onse amene akumusapota kabambe ndi ma cadets, Kodi UTM yakoma Pano? Chipani chija basi chajiwa
Kaya convention sinaende kaya yaenda bwino zopanda ntchito zimenezo bola DK wawina...and if u remember well mwini wake malemu SKC amanenetsa kuti chipanichi sichamunthu wina aliyense meaning aliyense akhonza kutsogolera.... ngati munali ndi anthu anu oti achitenge nde mwanya
UTM has gone to the Lomwe belt.President and secretary general can't come from the same Lomwe belt.Panayenda chinyengo size kukana.Anabweretsa ma delegate achilendo amen ambiri anabwera kudzavotera amene awina.
Koma ine ndikufuna kungomuuza uyuyu kuti akamalongosolera zinthu a DPP awasiye kumbari course malawi wawara chifukwa cha DDP end munthu sakhara %100 ndipo palibe azakhare so gyz bwerani ndikukonza zinthu course nkhani zanu zimaonesa kuti zimalunjika ku dpp so zimatichotsera chilakolako course enafe ndi a DPP
iwe wakonza ndani yemwe azagwire ntchito ngat iwe ....manganya siwalephera yekha makolo amatiphunzitsa tonse koma tili ndi zisankho zathu aliyense payekha ngakhale mulungu amaiuza izi ayi ndi ntchimo koma tokha zisankho zathu timasankhabe kuchimwa
Ukunama.
This is the Best convention ever.
What we need is the VISION of the Party.
Wait and see, SKC legacy shall prevail through his vision.
Anthu akuonangati panali chinyenge because kunali comption this is a best conversation in Malawi is UTM
Mlendo sanakonzere ayi zachitika kale.
At least it makes sense
Zinthuzi mzopanga
Kweni mpaka 21, mzopanga
Zibwana
Olo kodi kukokerelako angakokere bwanji.look at the gap .olo mwana atakuuza kuti aphunzitsi andibera marks ungoziwa kuti uyu akunama uyu atakhoza 10% . bola difference ikanakhala yaying'ono koma eee ma 100 plus
SKC WAS A VISIONARY NEW GENERATION ALPHA LEADER FOR MALAWI 🇲🇼 HE WAS VERY STRONG AND COURAGEOUS ❤🎉
DONT SAY HE DIDNT PLAN WELL
HIS LEGACY CONTINUES THROUGH DR DALITSO KABAMBE
HE WILL CARY MALAWIAN 🚩 🇲🇼
You with me
Za boza izo zoti anakoza wa winadi munthu uyo
Program iyi yakhazikika pa chilungamo yekhayo yemwe mutu wake sugwira sangaone zimenezi. Bravo Chawezi 😊
Iwe wako umagwira?
Chaweze take care kunja kumacha,,,
Komatu Chawezi ukuzionongera tsogolo lako. Mawu awa uwasunge udzandikhulupilira. Ukumbukire Malemu Chisanu mmene amachitira
Izi ndiye mbwerera zeni zeni amafuna akanawina manganya anthu asankha amene anali kumtima kwao mtsogoleri kumachita kukukakamizani mufune musafune palibe angapikisane ndiuyu komaso anthu Pano atopatu akudana ndi azitsogoleri ozipopa ngati chimwendo banda oyankhula mwathamo amalawi akuti ai zimenezo
Chawezi usamale malemu hope chisanu ankapangaso ngati iwe you are ukuononga mbili yako
Chawezi pita uzikangodya nao misonkhoyo
Zaziii ubwino wake tonse tinaseka makutu timangomva za kabambe basi utm my vote
Tell them
Otsati tose koma iwe. Enafe Kabambe tilibe naye ntchito koma wanthu ndi Atupele
@@khwimamtonga954 kwanu konko
Nde chuukukhudzan nd chan osowa zochita Inu...tkumana next year....
Vuto ndiloti anthu omwe anatsara ku chipan cha UTM pakuchoka kwa achilima ndi anthu okhaokha adyera. Komaso atsankho. Koma chilima mwini amadziwa kuti usi ndi amene angakhale mtsogoleli wamaso mphenya. Chinthu china achina kaliati kuluza kwawo ssanave kuwawa chifukwa amafuna kuti kabambe akamuike pa public koma iwo akudziwa kale kuti adya ndalama za kabambe kugulisa chipani
Amuna chilima kumutenga usi inali nkhani yongo panga attract large mass boss mulibe leadership mwa usi
Fact
Amalawi akuvutika MCP sitikuyifuna 2025
Zaziiiiiiiiiii
Ndiwe wamzelu ase Chawezi sungafanane ndi apumbwa enawa and you know how to explain momveka bwino
Za mziiiii
chawez ulibe nzeru
Keep it up guys
Chawezi akunena zoona, chilumgamo chimawawa. This UTM yatha basii. Mzimu wa Chilima wakwiya, zoona munthu kukwera 3 months ago lero ndikutenga chipani? Ma cadets ndi amene akusangalalatu zokonza izi
Anthu anzeru komanso wopita ku sukulu,woganiza ngati anthu amenewa, wolankhula mwanzeru
Koma muziwe kuti kukhara ndi mwayi oyankhura pa radio sizikuthanthauza kuti chilichonse chomwe mukulankhura ndi chanzeru ayi alipo konse ena anzeru koma mwayi alibe so watch your back
Olo ine ndikanavota nawo DK could have taken my vote
Koma chaweziyo akuwonetsa kuti ndiwanzeru kwambiri,maka nkhani ya utm iyi ayi akuyifototokoza momveka
Anthu awa alibe chulungamo alibe and ine sindimafira and amakhla kumbali kwazithu zoipa.
Chilima sadangochoka koma kuphedwa. Uziyankhula zomveka iwe
MaAnalysts awa ndiomwe alibiased aMCP.
Wawina basi Kodi ndimayese pamafunika owina chavuta ndichani??
Kabambe samayenera kukhala president wa UTM, munthuyi ndi wa DPP. Onse amene akumusapota kabambe ndi ma cadets, Kodi UTM yakoma Pano? Chipani chija basi chajiwa
Chokani inuyo ife ayeniwake a UTM tasagarara ndikusakhidwa kwakabambe
Chawezi ndiwe wa emcp
Chawezi plz usamanthe imau izi ndi ndale unfunse maseya ndi hope zinanthera bwanji udziyankhula bwino
Aaah agaru inu mxiiiw
Ubwino wake adanena zomwe adakumana nazo ndinu azibambo opanda nzeru pngakhalitse chilungamo chidzafziwika
Kaya convention sinaende kaya yaenda bwino zopanda ntchito zimenezo bola DK wawina...and if u remember well mwini wake malemu SKC amanenetsa kuti chipanichi sichamunthu wina aliyense meaning aliyense akhonza kutsogolera.... ngati munali ndi anthu anu oti achitenge nde mwanya
Sichinasukuluke Chawezi ndiwe wabodza UTM sinasinthe amaiwononga anali Usi wanuyo
Kodi Chawezi uli mbali yanji?
Iwe chawezi ndiwe wa mcp aliyense akudziwa nde chakukhudza ndichani olo zitakhala zochita kukonza
Palibe vuto ndi mmene zimakhalira ngakhale ku mcp chikangawa anachokera kunja.
Namiwa ndi anzake ndi anthu osokoneza zikoli. Moti okhawo ofoila ndiomwe azimbira mmanja Namiwa
Adzaphedwa osati adzachoka
Athu wa akukamba chilungamo chokha chokha
Kabambe adapambana chifukwa cha fundo zake
Ausi sakanawina chifukwa amakakamila kumgwilizano ndi.mcp
UTM has gone to the Lomwe belt.President and secretary general can't come from the same Lomwe belt.Panayenda chinyengo size kukana.Anabweretsa ma delegate achilendo amen ambiri anabwera kudzavotera amene awina.
Panyini pamako chawezi kumtumbo kwako konunkhako
Achawezi tsekani pakamwa panu. Nzeru. Mulibe ingodyani. Ndalama za MCP.
A usi ndi a chipani cha chikangawa aliyense amadziwa
Zisiye ni kambani za awa zikuwanyerawa
Chawezi ukuyakhula manyi kwambiri
Azibambo opanda mzeru ngati inu simnawaonepo mdziko lonse lino....chilungamo chizaziwika 2025 ndingotero
Munali guru komweko inu kambani zazelu apa , inu chakwera mukuikirana kumbuyo IFE tili pano kudikira
0:17
Chavez mmutu mwake mulibemo nzeru koma phokoso lokhalokha muti iyeyu sakudxiwa kuti titanena kuti Jane Ansah sanayebdetse bwinobwino chifukwa anali wa dpp anachotsedwa ndikuikapo Dr Chifundo Kachale?
Of coz Jane ansah yo anachoka after ma demo ambirimbiri, mwina awawaso akufuna asachoke mophweka
Komanso mumalimbana ndi zakunja malo.molimbana ndi zinthu zomwe zili pa ground meaning inu ndi ma followers a MCP kapena mukutumidwa
Wa MCP iwe chawezi timakudziwa,ku MCP wakale ndani ?
Chipanicha utm sichabanja ndichaaliyese chifukwatu oloinumunakayimapo munakawina inuyo uwundipikisano
Komanso kumugulitsa chikangawa
Koma ine ndikufuna kungomuuza uyuyu kuti akamalongosolera zinthu a DPP awasiye kumbari course malawi wawara chifukwa cha DDP end munthu sakhara %100 ndipo palibe azakhare so gyz bwerani ndikukonza zinthu course nkhani zanu zimaonesa kuti zimalunjika ku dpp so zimatichotsera chilakolako course enafe ndi a DPP
Izi nzitsilu zawanthu musamaye nthawi yanu kumvera za awa definitely aliyense amadziwa kuti ndi amkunkhapanyo a mcp
Iiiiii a chawezi kukonda maboza awaa ngati nzimai uyooo UTM ikanapita ku mcp mukanamuona kukondwa nanga chavuta nchani ngati in akeo avotela kabambe vuto nchani
Tayankhulaniko za mafuta akusowawa please
Yakhani zazikwanje inu mukukamba zaziiii
Aaa awa a mcp akulila amafuna MANGANYA AWA MWANYANAYO A MCP INU
Udyetu aise kunalibmadolo eneni kumeneko ask them alikuti pano.....
Ineyo sindingataye nthawi ndi kumvera abwampini otumidwa ndi chikangawa ayi gate out.
Hahaha shame on you gyz ine ndinalibe chipani now ndili ku UTM. ❤
Chawezi ndiwe WA MCP just shut your mouth. Remember that it is a transformation movement.
Akulira amafuna kt kabambe asawine mukanakhala kt mawin ndnu akhala kale munavuta nsanje basi
Aliyese amene mutu wake ndiozungulira atha kumanena kuti Chawezi watumidwa,nchifukwa mutu mwao anazolowera zomva za mademo basi, za ziiiiiiiiii, za anthu wosowa zochita
Anyamata achikagawa inu 😢😢
Km chawazi ndikape akudya ndalama za mcp😅
Chawezi ndiwe chitsiru kwambili, watumidwa ndi MCP
Inu mcp musatinyanse anthu oyipa inu sitingakhulupilile zimenezo inuyo munanva chinawapha ndi chani tiuzeni simwati ananena?
Izi ndiye mbwelera zeni zeni ,zikadakhala zokonza sakadangopanga endorse ? Monga mmene munapangira ku MCP kuja ? Muganiza kuti a UTM alibe nzeru koma inu ? Mwasowa chonena ? Chani kwenikweni zonsezi boma lamu likuchitazi chaka ndi chaka kuba ndalama za fertilizer bwanji osanena Imeneyo ,kodi amakupasani zingati kuti muziwaphimba a mcp wa? Chitani manyazi muzinena zoona
Chawezi umadya Za MCP asatipusise
A kuopa kuphedwa anthuwo
Amafuna awine ndani za ugaru basi
koma bambo chawezi .
deligeti chala chake chaloza basi
Za ziiii
Mukukambilana zopusa kwambri makape inu zeru zanu zopusazo mungafanane ndi Namiwa maboza inu
Uyu amati chawez amalimbana ndi dpp koma apitila limodzi
Awa amayesa amalawi onse ndiofoira madolo ndi iwowo akunama palibe number one aunile chole mbiyajo
Kulibwino kuvotela udf boma
A MCP inu
Chawes ndigalu
Akapolo aboma awa agalu
iwe wakonza ndani yemwe azagwire ntchito ngat iwe ....manganya siwalephera yekha makolo amatiphunzitsa tonse koma tili ndi zisankho zathu aliyense payekha ngakhale mulungu amaiuza izi ayi ndi ntchimo koma tokha zisankho zathu timasankhabe kuchimwa
Chawezi nawe uli gulu lodyanawo ndalama comishion yake yabodzayo
Chawezi banda kuipa ngati kuthako kwa mai ake a Ben longwe
Zaonetsa kuti mmutumo mulibe chirichonse
Manyi awo makapewa
Za zii
A UTM musatinyase munagulisa nonkha chipani chapita basi😂😂😂😂
Za manyiii
Mazulu amati walala wasala iwo amagonelanji
Bodza la anthu akalu akulu achayiniyake anagwirzana bwino bwino
Cz samalankhura zomveka km lero alankhura zomveka bwno, akabambe abera olo kusiyana sangasiyane choncho sizoona tiyen tisegure maso